![DZIWE TV](/img/default-banner.jpg)
- Видео 441
- Просмотров 3 790 179
DZIWE TV
Южно-Африканская Республика
Добавлен 31 дек 2019
Ngati Muli ndi Maganizo kapena mukufuna kuwadziwitsa anthu zomwe mumapanga tilembeleni pa dziwetv@yahoo.com
Dziwetv ndi Channel Yomwe makamaka ikuyang'ana kwambiri nkhani Zandale Mdziko lino. Kuwadziwitsa anthu zomwe Mtsogoleri wadziko lino walankhula ndi azitsogoleri ena azipani zina. Dziwe simalimbikitsa Ulamuliro wankhanza ndipo timapanga Support ulamuliro Osamala Malamulo.
Anthu omwe alibe information zomwe zikuchitika mdziko mwawo ndi anthu omwe ali otayika.

BON KALINDO LERO PA 12 JULY 2024 | KUPITILIRA KUNG'ALURA |
BON KALINDO LERO PA 12 JULY 2024 | KUPITILIRA KUNG'ALURA |
Просмотров: 330
Видео
GWEDEGWEDE LERO NDE KUNALI KUGUDULA NDIWO ZAGULU | ZITHUNZI ZA ANDUNA KUNO |
Просмотров 4,6 тыс.8 часов назад
GWEDEGWEDE LERO NDE KUNALI KUGUDULA NDIWO ZAGULU | ZITHUNZI ZA ANDUNA KUNO |
ATENGA MA FORM | MWAMBO WA ANGONI WALEPHEREKA | AGULA MIPINDO 156 MILLION KWACHA |
Просмотров 6 тыс.2 часа назад
ATENGA MA FORM | MWAMBO WA ANGONI WALEPHEREKA | AGULA MIPINDO 156 MILLION KWACHA |
BON KALINDO APA NDE WALANKHULA MOTO KUTI BUU |
Просмотров 22 тыс.4 часа назад
BON KALINDO APA NDE WALANKHULA MOTO KUTI BUU |
DR CHAPONDA TIKUBWELERA KU ULAMULIRO WANKHANZA |
Просмотров 10 тыс.4 часа назад
DR CHAPONDA TIKUBWELERA KU ULAMULIRO WANKHANZA |
BON KALINDO KU MANGOCHI WAYAKA MOTO |
Просмотров 20 тыс.4 часа назад
BON KALINDO KU MANGOCHI WAYAKA MOTO |
DR KAMUZU BANDA KULANKHULA CHITUMBUKA NGATI MBADWA |
Просмотров 2,2 тыс.7 часов назад
DR KAMUZU BANDA KULANKHULA CHITUMBUKA NGATI MBADWA |
HOT CURRENT YAKALE YABWELERA KULI KUYANKHULA KOSAMUNYENGELERA MUNTHU |
Просмотров 7 тыс.9 часов назад
HOT CURRENT YAKALE YABWELERA KULI KUYANKHULA KOSAMUNYENGELERA MUNTHU |
BON KALINDO PA 7 JULY 2024 | KOMA WALANKHULADI |
Просмотров 19 тыс.12 часов назад
BON KALINDO PA 7 JULY 2024 | KOMA WALANKHULADI |
LEAH MALEKANO KUWERENGA NKHANI MADZULO ANO NDI MTSABATAYI MOSANGALATSA |
Просмотров 2,4 тыс.12 часов назад
LEAH MALEKANO KUWERENGA NKHANI MADZULO ANO NDI MTSABATAYI MOSANGALATSA |
REV YASIN GAMAH AWALAVULA AKE KU 6 JULY UKU |
Просмотров 4,8 тыс.12 часов назад
REV YASIN GAMAH AWALAVULA AKE KU 6 JULY UKU |
TITENGERE ACHILIMA CHITSANZO POFUNA KUIFERA MBENDERA |
Просмотров 2,7 тыс.12 часов назад
TITENGERE ACHILIMA CHITSANZO POFUNA KUIFERA MBENDERA |
BRIAN BANDA KUWERENGA NKHANI ZA MADZULO ANO WAPA 4 JULY 2024 |
Просмотров 5 тыс.16 часов назад
BRIAN BANDA KUWERENGA NKHANI ZA MADZULO ANO WAPA 4 JULY 2024 |
ZOMWE WALANKHULA PATRICIA KALIATI LERO |
Просмотров 30 тыс.16 часов назад
ZOMWE WALANKHULA PATRICIA KALIATI LERO |
DPP YATI MA MP AWA AKUYENERA NTCHITO YAWO ITHETSEDWE NGATI MA MEMBALA ANYUMBA YA MALAMULO |
Просмотров 11 тыс.19 часов назад
DPP YATI MA MP AWA AKUYENERA NTCHITO YAWO ITHETSEDWE NGATI MA MEMBALA ANYUMBA YA MALAMULO |
MCP AITENGERA KU KHOTI OMWE SANAMALIZE ZAKA ZIWIRI MCHIPANICHI |
Просмотров 20 тыс.19 часов назад
MCP AITENGERA KU KHOTI OMWE SANAMALIZE ZAKA ZIWIRI MCHIPANICHI |
NKHANI MADZULO ONELANI NKHANI ZIMENEZI MULI ZOPEREKA CHIDWI | ZA UTM |
Просмотров 9 тыс.21 час назад
NKHANI MADZULO ONELANI NKHANI ZIMENEZI MULI ZOPEREKA CHIDWI | ZA UTM |
GWEDEGWEDE WA LERO NDE KUNALI KULANKHULA |
Просмотров 8 тыс.21 час назад
GWEDEGWEDE WA LERO NDE KUNALI KULANKHULA |
The DC mwana ohopya kwambili
Zoonadi Inu muli bwino kwambili
Munthu mulala tsopano tiye nazo asatijaile amenewa
Boss
Wanga kufa mwana chifukwa cha wa police wandigwira nayeso adzafera pompo ineyoso natopa nawo mbuzi zimenezo pofunika osamawanyengelera😢😢
Munadza makosana ❤❤
Ku malawi zimathera tikufufuza.
Ndipo apolice akumalawi ndinu otembelekdwa ndipo mukulephela kugwila mbava koma kulimbana ndi athu osalakwa
Nawo a MCP asatile malamulo a gwirizano wawo kuti apite s Utm asogoleke nawo
Za police mbuzi zaanthu izi kma kuba ndikupempha
If u stopped by the police officers on the road in ur 🚗 .who is supposed to follow the other? 4me i don't go out to a police office who stopped me coz i had no intention of stopping.u stop me,u come to me &tell me why you stopped me not me coming to ask u
Powerful GwedeGwede,,bambo banda
Nkaka akulembaso MSCE
Super super😂😂
Muli ndi mtopola guyz😊
Machende akoo chakwela
I salute mibawa
Chipewa cha khwangwala kuteloko amafuna anyemere kaye kuti adutse ndi mwana wodwala ,utsilu dyera
Va police palibe vomwe vikuchita vimangodziwa kupempha ndrama pamseu ndikumanga mbava yoti anthu aigwira kare anthu eniake,ndipo vitengelepo phunziro mwina vingayambe kugwira ntchito bwino vipewa va mbalevo
Apolice amaonjeza nkhanza pansewu😢
Bon kalindo iweyo umatha kulankhula bwino. Chifukwa kulankhula kwako umanena zoona zokhazokha kumvera chisoni amalawi munyengo zowawa zomwe tikudusamo kamba ka utsogoleri olephera wa chakwera. Osafooka , osatopa mpakana satana ameneyi tithana naye 2025 ino. Keep it up wakulu ndimakunyadirani kwambiri
Salute
Kkkk chipanda kuyankhula bwezi ali mumaguza omwewo kkkk
Kkkkkk
Apite uko
Well done job , ineyo ndikudabwa Kuti passport ili pa mtengo wa 50, 000, pa list akuti in twenty one days ikhala yatuluka , Koma kupita kuja aku immigration akuti unasiila ndani Kuti azikufufuzira, aaaa zikufunikaso munthu wofufuza , i thought it is the office, it has to do it's work, this must stop immediately ACB do something with these people who are robbing other people .😅
The DC!!!!!!!!!!!!!!!
Kalindo ndinyama zikuluzikulu samaopa .sikulina adzaiphulatu.
Wakuba ameneyo kamaso wakupha
😂😂the dc
❤
Wamisala ameneyo
Joyce chitsulo usakane ayi iweyo akupotoza adausi koma waila momwe timavutikilamu muja kuti uwine sorry uzatifuna
Hahaha kwachema 🔥
Following
The DC😂
Mulungu azikutetezera nkhondo mukuimenya
Bon kalindo dddccccc❤
Zoona akunena B kalindo
Apm my vote
Muma tiimila osatopa
God protect mr DC
Amalawi musavotele UDF chipani cha atate ndi mwana😂😂 dzausilu
🤣🤣🤣🤣🤣 ngati Malawi ndiwandani Mr DC
Ife si osauka ndipo sitisilira kukhala ndi president osauka😂😂😂😂😂
Ipondeni Fadah
Good boy
❤❤❤❤smdc
The DC keep the fire burning.
Mr Kalindo great soldier