Feeling happy when listening the voice from our beloved president, president for the poor, proud of you always, the Dddddd!!!! Cccccc!!!!!, the only true and trusted freedom fighter remaining on the ground 🔥🔥🔥🔥
A DC mwayankhula kwambiri next year tivota inu muoneka kuti umphawi wa amalawi muudziwa tangoyambitsani chipani chanu tidzakuvotereni kuti inu mzapangire amalawi munenazi I hope inuyo msidztivuta tizamva nanu kukoma
Chonde a DC athu auzeni amalawi Kuti chakwela atule Pasi udindo chifukwa akuyimbilidwa fone Kwa biligate kumuuza chakwela Kuti akwanilitse program ya catemela pakuti chakwela anatenga ndalamà zambiri Kuti amphe amalawi , ndipo chakwela akufuna kubweza ndalama Kwa biligate Koma biligate akukana akuti akufuna mbuzi zake mukhola la kumalawi tangoganizani amalawi tikuntchulidwa mbuzi Za biligate chifukwa cha chakwela,China chimene chinamumphetsa chilima ndi Ichi chilima amamuuza chakwela Kuti anthu asalandile katemela pakuti katemela uyu ndi wakupha Koma chakwela anapanga makani pakuti anali atalandila kale ndalamà Kwa biligate komaso asilikali Aku Israel anabwela Kuti azakakamize anthu kumbali ya katemela chonde amalawi tisagone Ayi
Kodi funso ndilakuti aborn kalindo basi inuyo kukhala pa air basi kungokhalira kuchauta boma basi palibe china chommwe mungapange musanene kuti onse amalawi ayi uzinena amene ukudya nawo zonazo ukuwonjeza tatopa nawe ukungofuna kusochelera amalawi ndalama umadya wekha zomwe amakupasa kuti uzipanga against ndi boma koma ma plan iweyo ulibe bwanji ubwelere kuzisuzu basi kukacha tingomva maboza akowo zaziiii tatopa nawe kape iwe ukufuna kugalukusi ntundu wamalawi munthu opanda nzeru iwe ineyo ndilibe chipani koma iweyo palibe chimene ukuthandiza amalawi koma uli porukwana ziko basi
Mumatiimilira bwana kalindo keep it up watching from Port Elizabeth SA
Feeling happy when listening the voice from our beloved president, president for the poor, proud of you always, the Dddddd!!!! Cccccc!!!!!, the only true and trusted freedom fighter remaining on the ground 🔥🔥🔥🔥
Boon kaaaaaaliiindooooooo!!!!! 💥💥💥
Dank Mr dc
Yooh koma dzikoli lapita ndithu
DC Inu ndi #1, tikumva nanu kukoma Inu a president athu amphawife, keep the 🔥🔥🔥 burning
I even forgotten that yesterday was 6th July independent day I used to know through past years
thanks the DC
The DC 🔥🔥🔥🔥
Dangerous Child 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mumakwana the Dc
Thax Dc maliwi anavunda ine ngongole anandikaniza ndinadandawulakwambi ndine wakumangochi
Waganiza bwanji kkkkk
Chakwera mbalame zed
Ameneyo ndi nyoooo
Thanks dc for the update
Keep it up MR BK DC were under you Mr 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Good Messnge Mr bon kalindo Chakwela you mast go
Kodi galu iwe kwenikweni umafuna chani
Amalawi ngat mukuona kut chakwera sakuyendesa bwino tangopangan zomwe achita ku kenya ndipo zitha kuthandiza koma ngat muzingotokota palibe chomwe chingayende
Umakwana DC
Mwakwanila big
DPP boma
DC Kalindo 😂😂😂🇲🇼🇲🇼🇲🇼 🔥❤️🔥❤️❤️❤️🔥 Kulankhura kopanda mantha
Mwana oooooopsa kwambiri from njedza village
Chakwela ndioipa ntima kwambili, the whole malawi kukhululukila ma prisoners 30. Ma president ena onse sanationetseko izi
A DC mwayankhula kwambiri next year tivota inu muoneka kuti umphawi wa amalawi muudziwa tangoyambitsani chipani chanu tidzakuvotereni kuti inu mzapangire amalawi munenazi I hope inuyo msidztivuta tizamva nanu kukoma
The dc mwana wachabe kwambili ❤🎉
❤❤bon karido
Boooooooooooooooon kaaaaaaaaaaaaliindoooooooooooooooo 🔥🔥🔥
Zoona DC timenyeleni ufulu pa malawi
THE DC 🔥🔥🔥🔥
Ndife anzeru palibe kutipusisa💔
Very soon tivota.... ulemu wanu captain DC‼️
The Dc❤❤❤
The DC mwana oopsa kwambiri . Mwana amene ana pachika mantha mkumamenyera ufulu wa Malawi
Good job Mr kalindo
Zoona apule
😂😂😂😂the diisiiiiii! 🔥🔥
❤❤komatu relo
Mwana uyu eeee
Eee koma bon kalindo akanakha plezident wa anthu onse mmalawi bwezi tikunva kukoma
The deceeee more 🔥
Ndipo iweyo umangolankhura zaziii ungayendese boma iweyo umangonena chifukwa chilindazako zina ndisanje kape iwe
Ukunena ndani?
Good massage
So onad Dc❤❤❤wi love you ❤
A Kalindooooo mmmhhhh
The Dccccccc.
More fire 🔥
Zonadi
Faka Moto Bon Kalindo
Sitizapangaso mastrk imeneo kumuvotelaso chakwela watizuza kwambili
Takulandilani abwana tokotani satana apse mtima
D.C the machine for poor people
Fire man THE DC
Musasiye kutokota bwana DC mumatiziwisa zambiri
The Deeeee Ceeeeee mwana owoooooopsaaaa kwambiriiii
The Dc machine
Just in time the DC❤
THE DC💥💯🤞🤞
Kodi a DC sizingatheke mademo akubwerawa kukaphwasula ku state house? Chifukwa chopangira izi ndikufuna kuchosa apule. Mademo akhala akuchitika sakuphula kanthu tiyeni tipange action. Munthuyutu chakwera akudzunza kwambiri.
the dc 🎉🎉
The DC Machine
❤❤
DC more fird
Mumakwana bwana The DC😂😂😂😂😂
The...DC mwana oopya
Ndipo inu nimumene zadurira zithu koma chakwera uyu watikwana kwambiri tiyi tinamwa nikare kwambiri pano sitikuziwakuti mukamwamu amaocha bwanji
A kwana the DC
Njeza boy
Dc❤
Mumakwana
Pangolini the DC
𝘜𝘮𝘢𝘬𝘸𝘢𝘯𝘢 𝘵𝘩𝘦 𝘋𝘊
D cccccccccc mwana mulanje
I think panopa ukumenyeradi ufulu amalawi
Akatundu
Osaziwazinthu inu akalindo muganiza kutizinthu zingakhale chimozmozi
Kape out of Kapeee
Ndi ameneyi muku Bon Kalindo uyuuuuuu
Mtumbo wake
Iweso panyapako wakutuma ndani kut uzimuvela wa mcp iwe
Mmmm mukudya nawo ku mcp ko
Nyau siimasowa pita kudambwe uku😢😢
Ndwe Gslu kwabas Nyawu pita kudabwe chitsiru chamunthu
Nyawu zakwakabudula kwa msundwe sizisowa zimangotukwana akazizidzula munya muwona akuvula vigoba mukuvala nyawu zachabechabe inu fwetsek
Kalindo came ❤
Timakuyamikilan chifukwa timaziwa zambili zathu anyawo
The DC
😂
Iwe nd katundu
Chonde a DC athu auzeni amalawi Kuti chakwela atule Pasi udindo chifukwa akuyimbilidwa fone Kwa biligate kumuuza chakwela Kuti akwanilitse program ya catemela pakuti chakwela anatenga ndalamà zambiri Kuti amphe amalawi , ndipo chakwela akufuna kubweza ndalama Kwa biligate Koma biligate akukana akuti akufuna mbuzi zake mukhola la kumalawi tangoganizani amalawi tikuntchulidwa mbuzi Za biligate chifukwa cha chakwela,China chimene chinamumphetsa chilima ndi Ichi chilima amamuuza chakwela Kuti anthu asalandile katemela pakuti katemela uyu ndi wakupha Koma chakwela anapanga makani pakuti anali atalandila kale ndalamà Kwa biligate komaso asilikali Aku Israel anabwela Kuti azakakamize anthu kumbali ya katemela chonde amalawi tisagone Ayi
Aboni ndimbulid eti
Mbiliii zakummwela zokhazokha
DC
Mcp motoooo
Bg up the DC
Kodi funso ndilakuti aborn kalindo basi inuyo kukhala pa air basi kungokhalira kuchauta boma basi palibe china chommwe mungapange musanene kuti onse amalawi ayi uzinena amene ukudya nawo zonazo ukuwonjeza tatopa nawe ukungofuna kusochelera amalawi ndalama umadya wekha zomwe amakupasa kuti uzipanga against ndi boma koma ma plan iweyo ulibe bwanji ubwelere kuzisuzu basi kukacha tingomva maboza akowo zaziiii tatopa nawe kape iwe ukufuna kugalukusi ntundu wamalawi munthu opanda nzeru iwe ineyo ndilibe chipani koma iweyo palibe chimene ukuthandiza amalawi koma uli porukwana ziko basi
Udzizitchula wekha osat tatopa ndi ndan wakoyo......
Yyuyu
Useless and misleading
The ddddddccccc
Mwakwanila big