BON KALINDO AMAFUNA KUPHEDWA KU PARLIAMENT

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 5 сен 2024

Комментарии • 162

  • @user-yk4by8iy8k
    @user-yk4by8iy8k 6 месяцев назад +6

    Komatu ukatengera za kagame ukhala mmavuto anthu akulira misozi yamagazi chifukwa cha iwe mulungu alinafe AMEN

  • @uyosakala4880
    @uyosakala4880 11 месяцев назад +3

    I like this kanga zaona from Zambia

  • @GEORGE-yr7nx
    @GEORGE-yr7nx 11 месяцев назад +8

    😢komatu choti mudziwe choti Boni kalindo akangofa dziko lamalawi mudzakhala magazi chifukwa ife sitidzalola

  • @lyiemax
    @lyiemax 11 месяцев назад +3

    May the good Lord continue protecting our president for the poor and his family, our expectations rely on God through him

  • @user-lz2wy7fr4b
    @user-lz2wy7fr4b 11 месяцев назад +8

    Asilikali akumalawi amakanika kuuluka pa pala ndiye angakwanitse kulanda dziko mmmmmm zosatheka

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 11 месяцев назад +11

    I like Nkhanga zapenya mumaona pataaaaaaaaaali

  • @meganabigail-ye7fw
    @meganabigail-ye7fw 11 месяцев назад +6

    Iiiii asilikani ali pamoto bola kuno ku John timagwila in 8 hrs koma our salary is running to 400 pin iya ziveleni chison asilikali aku Malawi

  • @user-lz2wy7fr4b
    @user-lz2wy7fr4b 11 месяцев назад +6

    Nkhanga zaona mumakwana pitilizani kuulula zobisika osasiya ayaluke abakha amenewa

  • @Steven-hl6cb
    @Steven-hl6cb 11 месяцев назад +6

    ziko lomvesa Chisinau.mcp nonse mulungu akukatheni

  • @user-pi8mz3bx9n
    @user-pi8mz3bx9n 11 месяцев назад +6

    Satana ndi olephera May God protect the dc

  • @kassimwilson
    @kassimwilson 11 месяцев назад +5

    ama funa kumupha ngat ana muphela clement chiwaya

  • @alickalick6509
    @alickalick6509 11 месяцев назад +6

    Sindikudziwa kuti Chilima anali ndi zaka zingati nthawi imene timavutika ndi MCP ?
    Ndikutelo chifukwa chakuti ndi Chilima amene anapangitsa zonse amawona ngati kuti Chakwera ndi amalume ake lero ndi izi dziko labweleranso kumavuto akale.
    Anthutu koma timanena kuti njoka ndi joka singakhale somba zosatheka Chilima mukayakha pamaso pa Mulungu kudandawura kwa a Malawi.

  • @StanleyTembo-fl7cc
    @StanleyTembo-fl7cc 11 месяцев назад +1

    May Almighty God continue blessing him with more life

  • @amoschataika1284
    @amoschataika1284 11 месяцев назад +11

    If this nonsense of MCP continues i will report to the whole world blv me. Malawians let's save our Country from these Idiots. More fire Limpopo FM.

  • @yusufbakali-zm2hq
    @yusufbakali-zm2hq 11 месяцев назад +10

    Aululeni ndithu😂

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw 11 месяцев назад +4

    mulungu ndiwakulu ❤❤❤

  • @zacariasjoselemessonelemes9562
    @zacariasjoselemessonelemes9562 11 месяцев назад +3

    Kkkkkkkkkk i like this program, from Moz

  • @ErnestMussa-b6u
    @ErnestMussa-b6u 29 дней назад

    yes i want to be on line with this channel

  • @user-px5ew4ud9s
    @user-px5ew4ud9s 11 месяцев назад +2

    Mulungu amutetezera boni kalindo sangamuthe chilungamo sichifa akunama kwambili

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 11 месяцев назад +6

    We don't have soldiers in malawi

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr 11 месяцев назад +2

    Chakwera dziko tinachita.kulipedza komanso tidzalisiya siunalikonze ndiiwe kunali kamudzu muludzi malemu bingu joice banda peter onsewo anavomeredza.ndipo anasiya .ndiye ndiiwe ndani kuti udzikatenga zigawenga kuruwanda kuti adzitiopsyedza ndizosatheka utafe ndiiwe ifeyo utisiya ndipo iweyo chakwera chaka chino chikakuthere kumanda utisiye tizikhala anthu tisakhale mwamantha mudziko lathu chifukwa cha chakwera 😂😂😂😂😂

    • @blandinabonaventure
      @blandinabonaventure 11 месяцев назад +1

      Ndipo asilikali aku Rwanda atiopseze dziko lathu lomwe Mulungu Chakwera akuoneni ndi, ng'oma ija, mulungu wathu ndiwamoyo

  • @yusufbakali-zm2hq
    @yusufbakali-zm2hq 11 месяцев назад +5

    Nkhanga zaona mulibhooo

  • @yusufbakali-zm2hq
    @yusufbakali-zm2hq 11 месяцев назад +3

    Mademo akhalaso liti I'm ready kk47

  • @ShaId-qc9bh
    @ShaId-qc9bh 11 месяцев назад +3

    Bwino angakusowese nawe .koma mosaopa bon kalindo alingat kamuzu I think zimu wakamuzu walowa mwabooooon ine ndilikumbaliya booooon mulungu azimudalisa .aboon kalindo akuyenela mubuku la history m'malaw ndimunthu oyamba kuzipeleka muno malaw ulem wanu booooon kalindo

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr 11 месяцев назад +2

    Limpopo ndikupemphelerani mwayi nzeru mphamvu kuchita bwino zisikire kwainu nonse mukufukula zonsisi za.nkhandwe chakwera

  • @user-ty5ih9uo3r
    @user-ty5ih9uo3r 11 месяцев назад +2

    Bangolini sangamuthe.Dc Dengelous child

  • @VictorTembo-mp7hd
    @VictorTembo-mp7hd 2 месяца назад

    I like this kamga zaona from Zambia

  • @user-vu8pb5wp8y
    @user-vu8pb5wp8y 11 месяцев назад +3

    Malawi wafika poipa ndipo tikapanda kusamala ana Athu azavutika

  • @RashidKusum
    @RashidKusum 3 дня назад

    Phiriwake garu ngati ameneyu buzi yamwana

  • @promixphotography8056
    @promixphotography8056 11 месяцев назад +2

    Pitilinzani kuunza anthu choona ndipo ziko liziwe choona chifukwa moyowu ukupitilira zigawenga. Malawi wake up, wake up. Iyi si Democracy ai,

  • @user-en8bk1hm7z
    @user-en8bk1hm7z 11 месяцев назад

    More anointing to all fighters. Be extra strong because you are doing a great job. More fire comorade mthanyiwa Bon kalindo, Ben longwe. Be protected in all corners

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 2 месяца назад

    Mulungu ndiwazatheka bwanji Bone Kalindo amulephera ndi Mwana wamulungu amene akutisegula maso Ife ana ama 2000 tithokoze Mr Mtanyiwa mulungu azikutetezani Kwa adani kut tizithabe kudziwa zomwe zikuchitika mu ziko lathu

  • @user-iy8zi2gs7i
    @user-iy8zi2gs7i 8 месяцев назад

    Nkhanga zaona akuti aliyese atenga chikwanje chake yemwe alibe agule akakukhapa nawenso uwakhape aliyense amve kuwawa😂 like your news Nkhanga pitilizani kuwona patali, may God protect the DC president of poor people.

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 11 месяцев назад +2

    Amene zikukunyasa usamamvere palibe akukutuma kuti uzimvera

  • @carenchikwe268
    @carenchikwe268 11 месяцев назад +2

    Ambuye atichitire chifundo ndithu mmh

  • @innocentissah2636
    @innocentissah2636 11 месяцев назад +3

    Tsiku lomwe adzaphedwelo, nkhondo yayamba pompo

  • @user-nb7xr9vb4t
    @user-nb7xr9vb4t 11 месяцев назад +5

    MR ntanyiwa mumakwanira

  • @user-oh3mb9ym7r
    @user-oh3mb9ym7r 11 месяцев назад +9

    ALLAH umutetesele boni kalindo

  • @Goliath461
    @Goliath461 11 месяцев назад +2

    Koma tinene zoona asilikali akumalawi sangangokhala kumayang'ana kagame akutumiza asilikali kuno ,athuwa adyesedwa banzi, chifukwa sizoona asilikali athuwa kumangozisiya zikuchitika pamaso pao ayi m'malawimuno tilibe asilikali otiteteza akwera chipani

  • @RhulaniMukasi
    @RhulaniMukasi 2 месяца назад

    Olomwam,bera ndalama kalindo musaganize kut akusiyan choncho kuyaluka muyaruka ndithu apolice otan inu minyeromwanu nonse

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 11 месяцев назад +3

    Asilikali tilibe

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev 11 месяцев назад +3

    Pena kumachita manyaz ukaziganizila kut ndiiwedi mmalawi dziko lomvetsa chison

  • @PetuloMoyenda-bp3gl
    @PetuloMoyenda-bp3gl 11 месяцев назад +2

    Ambuyetu Ali naye ndipo mulungu akumugwiritsa ntchito Ali ngati mose wathu ameneyo

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 5 месяцев назад

    Achakwera ndimayesa munali busa apa mwawoneka kuti ubusa wanu unali wachinyengo bon kalindo akafa ndinu achakwera ziko lonse likuziwa ichi mulungu amuteteze amuteteze amutetezebe kalindo

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 11 месяцев назад +2

    Komatu zikuwonjezatu mmmmm

  • @user-iu6mr5xu6r
    @user-iu6mr5xu6r 2 месяца назад

    Ndimuuza Chakwera kuti wagwa mdzanja la Mulungu ndipo aipa kuposa Cinkhanira, Mulungu akugwetsa isanafike nthawi imene uiganizira.

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO 2 месяца назад

    Mulungu ndiwazifundo kwambili 🙏🙏🙏♥️

  • @user-fy7tm3ol3y
    @user-fy7tm3ol3y 11 месяцев назад

    Born kalindo keep it up

  • @user-mz1pp2su5v
    @user-mz1pp2su5v 11 месяцев назад +4

    Vuto ndiloti udindo waku Army amasankha ndi president kapena ndinene kuti ndiwandale chifukwa amasankha amene akufuna kuti azipanga zofuna ndikukomera iwowo.
    Tsono mkulu wa army alipoyi ndiwawo.
    Chifukwa how they bring army from Rwanda pamene ifeyo army tili nayo
    Pamenepo asilikali nonse amene muli ku army simukuwona kuti president Yu akunyozani kuwoneka kuti inuyo mulibe ntchito ndiwopanda pake komanso kukunyozesani ku dziko lonse lapansi kuphatikiza ku Rwanda ko kukhala ngati Malwi ndi Rwanda number 2.
    Ganizani bwino asilikali athu ndithu musawineke osafunika lero pomwe nthawi imene tinkapampanga ma demo kuti boma la DPP lituke mboma munagwira ntchito yayikulu kuti iyeyo Chakwera yo akhale President ndiye lero musakhale opanda pake kapena osafunika kapena ndinene kuti mukhale makape

  • @user-rf4br1fv2z
    @user-rf4br1fv2z 11 месяцев назад +2

    Mmmmmm mabodza awa

    • @user-uz6tr2db6g
      @user-uz6tr2db6g 11 месяцев назад

      Ulape ndi ndi mtsigoleri wakuphayi

  • @user-oh3mb9ym7r
    @user-oh3mb9ym7r 11 месяцев назад +3

    Kumalawi kulimbe asilikali guys tisadalile asilikali akumalawi 💪💪💪

  • @smt7036
    @smt7036 11 месяцев назад +2

    amalawi vuto timadana ndimuthu osati zochitika zake athu anamuda peter muthalika kuyikapo abalewa lelo ndi izi

  • @eliasmpita3916
    @eliasmpita3916 2 месяца назад

    Zikateto anthunu kumavoteranso chipani choterocho kupha kwambiri. Akufuna kupha achinyamata onse. Nkhanga Zaona pitirizani kufukula zambiri.
    Mfukuletso anthu amene abwere kuchita kafukufuku was ngozi ya ndege.

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure 11 месяцев назад +1

    Mulungu ndiwamoyo Palibe chida chosulidwa chomwe chizambane

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 11 месяцев назад +1

    Mavvto Malawi bon mulugu alipho

  • @user-mj3ms4jt3b
    @user-mj3ms4jt3b 11 месяцев назад

    Zabodza izi amalawi musazimvere Bon Kalindo palibe zoti amafuna kuphedwa. Chonde inu abale anga akumwera ngati ndi mkwiyo tisafike nawo pomanena bodza lotere. Poliza nonse amene mukunena bodza limeneli mmalo wa m'bale wanga bon kalindo ndikuti izizi ndizabodza ndipo nonse machende anu, Nyini zanu,mitumbo yanu.

  • @user-dm2dh3kk8p
    @user-dm2dh3kk8p 11 месяцев назад +1

    Umakwana bon

  • @user-uj5nl3sn3h
    @user-uj5nl3sn3h 10 месяцев назад

    Born kalindo God he protect u way you are

  • @FatimaUmali-pc8sy
    @FatimaUmali-pc8sy 4 месяца назад

    Zikomo tikuziwa nawo pitilizani kutiziwitsa allah 24:48 bless you inshallah😢😢

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 2 месяца назад

    Bon Kalindo the DC❤

  • @christinaibbu4339
    @christinaibbu4339 10 месяцев назад

    Alemekezeke wamwamba mwamba Alihamdulilla ana asatana ameneyooo pale angapange? mulungu pasogolo 🙏🙏

  • @louisemsowoya8235
    @louisemsowoya8235 Месяц назад

    😭😭😭😭 ooooh Malawi 😭

  • @mathewsmbaluko8522
    @mathewsmbaluko8522 11 месяцев назад +2

    Asilikali osalanda ziko bwanji ,Kodi mayesa job yanu ndikuteteza anthu ?

  • @ritabani274
    @ritabani274 11 месяцев назад +1

    Nthawi ya Mlungu ikadzakwana adzachoka pampandopo pemphero ndiye chida choti tigwilitse ntchito kuti dziko lathu liyende bwino ka M CP ndikachani Achakwera adzatha ngati Farao

  • @ebstonekonzani9126
    @ebstonekonzani9126 10 месяцев назад

    .... what kind of government is this

  • @user-um6yo6nc3e
    @user-um6yo6nc3e 11 месяцев назад +1

    Mposo M'mene ziswera nkhangazo kuchuluka kwake amagwetu.....!

  • @leonardjika2100
    @leonardjika2100 11 месяцев назад +1

    A WISE THINKER WILL GOVERN OUR LAND SO HELP ME GOD

  • @MARKZAKEYU-nh1zn
    @MARKZAKEYU-nh1zn 11 месяцев назад

    Aphedwa bwanji .Kugomva kuti mcp ndi yokupha achakwela ndi boma lao ndi olephela basi guleyu wa vina watopa

  • @aaronmbawa2884
    @aaronmbawa2884 11 месяцев назад +1

    Wise man

  • @user-ub1mw7ce5p
    @user-ub1mw7ce5p 11 месяцев назад

    Malawi is boring now. We salute you comrades freedom fighters

  • @promixphotography8056
    @promixphotography8056 11 месяцев назад +1

    Shaaaa

  • @MaggieGondwe-vn2wx
    @MaggieGondwe-vn2wx 11 месяцев назад +1

    Mulungu adzikusogolerani nthawi zonse , timakunyadirani

  • @AjibuTwalibu
    @AjibuTwalibu 2 месяца назад

    Inu madolo bas

  • @user-xq3xs2yh2r
    @user-xq3xs2yh2r 11 месяцев назад +1

    Asilikili amalawi amangowatuma kokalanda Makara basi ndikumalondera khalango basi not to protect the country

  • @user-pi6vr1ry4o
    @user-pi6vr1ry4o 11 месяцев назад +2

    Bwinotu bwino atha kuyaluka!

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn 2 месяца назад

    Amalawi chonde tigwilane manja tiwomboleziko lanthuli komatu timawuzidwa kuti Mcp ndi yakhupha ife ana ama 2000 sitimaziwa

  • @AjibuTwalibu
    @AjibuTwalibu 2 месяца назад

    Pitilizan ntchito
    Yanu mulungu ali nanu
    Akuthandinza

  • @user-el2tl4vg4c
    @user-el2tl4vg4c 11 месяцев назад

    Bon Kalindo god he protect u

  • @meganabigail-ye7fw
    @meganabigail-ye7fw 11 месяцев назад +1

    A MCP ndi anthu omvetsa chison kwambiri nanga chifukwa chani sakuzifunsa kut the whole Malawi Born Kalindo kukhala patsogolo kulimbana naye sakumutha? Ndipo angozisiya

  • @user-pn7ek7wb7n
    @user-pn7ek7wb7n 11 месяцев назад +1

    Zabodza zokhazokha

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 6 месяцев назад

    Amakachitako chiani ngati iye ndi MP.

  • @KamtambeSikelo-sy7io
    @KamtambeSikelo-sy7io 11 месяцев назад

    Inu achitetezowa amagwirintchito alive future plan niwanthu ovetsa chison mudziwe mulungu akupatsani chilango uyu simunthu mukuti chakwera or kwawo anthu akuvutika pothera ichiso .....

  • @aaronmbawa2884
    @aaronmbawa2884 11 месяцев назад +1

    Maganizo amuthu sichifunilo chamulungu

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 11 месяцев назад +1

    In Malawi is there any real defense force? Are they real soldiers? One thing Malawian people should, know is this during Kamuzu Banda, Kamuzu Banda was trying to erase Malawi defense force to Malawi young pioneer if you can remember very well, this is signal to that direction Malawi defense force must wake up now before it's too late look what is going on in D R C( CONGO 🇨🇩) who is behind the war there, is Rwanda under Paul kagame now Chakwera and his party are doing the same to bring that war in the country ,Chakwera is busy wagging the war in the country Malawian wake up now.

  • @MussaPanje
    @MussaPanje 11 месяцев назад +1

    Chakwela ndichilima machende anu angalu anthu woyipha kwambiri

  • @memoryedwin
    @memoryedwin 11 месяцев назад +1

    Eeee koma mavuto

  • @yusufbakali-zm2hq
    @yusufbakali-zm2hq 11 месяцев назад +2

    Ndili nanu limodzi ine yb

  • @user-dt9xc3yz1x
    @user-dt9xc3yz1x 11 месяцев назад +2

    MCP is a killer

  • @mansomo5683
    @mansomo5683 11 месяцев назад +1

    Tigulise NDI azugu bassss😢😢😢

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli 2 месяца назад

    Dziko zomvetsa chisoni very sad

  • @STARLIGHTGSM-cd8uv
    @STARLIGHTGSM-cd8uv 2 месяца назад +1

    Ai radio ili boh

  • @PatricklameckChimkango-cx6qe
    @PatricklameckChimkango-cx6qe 2 месяца назад

    Mumatha pitlizan

  • @michaeleliasmwahinga-mw4lk
    @michaeleliasmwahinga-mw4lk 11 месяцев назад

    Ndizoonad galu ameneyu Chakwela ndichisilud kwambili nyiye wakiongoz wa nyasa wapumbavu Sana

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 11 месяцев назад +1

    Zoona zokhazokha bigy🔥🔥dziko lavunda ili eesh.

  • @BensonChilundu
    @BensonChilundu 2 месяца назад

    MCP ikatuluka m’bomamu mudzwe kuti simudzalowanso.Tinakuvoterani kuseri kwa ubusa poona kuti popeza ndinu oopa Mulungu,komatu zafikapa sindinu m’busa koma ndinu satana Ndipo ku ubusako mumangofuna ulemelero koma dziwani kuti Mulunguyo akukuonani ndipo posakhalitsa mulandila msautso oti muzazindikila kuti bolanso kumangodya therere m’midzimu.Mawu anga awa muzawakumbukila

  • @MussapAli
    @MussapAli 10 месяцев назад

  • @mussamatonga3575
    @mussamatonga3575 11 месяцев назад +1

    😂 mukamati limpompo fm

    • @mussamatonga3575
      @mussamatonga3575 11 месяцев назад

      Mukanapeza zina lina osati lakunja😊

    • @patriciacraiton-sf5vu
      @patriciacraiton-sf5vu 11 месяцев назад

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂 iiiiii koma zithu zake eee ine yayi kkkkkkk 😂😂😂😂

  • @user-vu5gy8wf8y
    @user-vu5gy8wf8y 11 месяцев назад

    Ripopo FM 🔥 🔥 🔥

  • @duncainjimmy
    @duncainjimmy 11 месяцев назад

    Asilikali salary yake imeneyo kumangosekelera mbwelerazo

  • @user-iu6mr5xu6r
    @user-iu6mr5xu6r 2 месяца назад

    Kodi MCP ndi Chakwera angakhoze kutseka
    pakamwa anthu opitirira 20 000 000?