KONDWANI NANKHUMWA WAULURA PA INTERVIEW ZOMWE SAULOS CHILIMA ANAMUUZA ASANAMWALIRE ZOKHUNZA DPP

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 23 дек 2024

Комментарии • 147

  • @rexmatewere8743
    @rexmatewere8743 2 месяца назад +1

    Thank God you were just fired but not killed and you are able to build your own house freely and you are a free man

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 4 месяца назад +16

    Mbuzi iyi inu ndi amene mumanama mabodza kwa mutalika okhuza chilima 😢😢😢

  • @ChikuFrankKakande
    @ChikuFrankKakande 4 месяца назад +2

    Adzikangopha Mbuzi ndi mkhosazo basi 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 4 месяца назад +13

    Ndiye bwanji chakwera anamupha chilima😢😢😢 iweso unali mgulu lopanga plan yomupha

  • @dorissalamba9365
    @dorissalamba9365 4 месяца назад +23

    I’m glad Saulos wanted to make peace with the former President APM..May his soul continue to rest in peace

    • @chelseajackson3200
      @chelseajackson3200 4 месяца назад +10

      Zabodza izi, timve akwini koma. Kondwani is an opportunist with no direction.

    • @paulmgombebanda-mr19sate
      @paulmgombebanda-mr19sate 4 месяца назад +1

      Zilibe umboni wakufa sangayankhe kanthu

    • @esthermkwapatira1693
      @esthermkwapatira1693 2 месяца назад

      There is no peace my dear malw pip are died and crying because of hunger end so on tiyeni tipemphere kut tisaweluze koma chilima mulungu amukhururukire chifukwa choipa chimatsata mwini

  • @kadijachilwan967
    @kadijachilwan967 4 месяца назад +6

    Nankhumwa sapanga ndale zotukwana nkana a dpp amadananaye he do smart politics he is gentleman

    • @AdamMedson
      @AdamMedson 3 месяца назад

      Ithink unakunaku ndi smart politics eti?

    • @ruthgama1122
      @ruthgama1122 3 месяца назад

      Sukudziwa iweyo

  • @DaudiHAllie-kk1en
    @DaudiHAllie-kk1en 4 месяца назад +5

    Chilima anali wadyera that fact
    Very confused soldier who never knew what he was fighting for.

  • @FineasKhoriyo
    @FineasKhoriyo 4 месяца назад +2

    How I wish this came out to the public same year.

  • @AllanMajanga
    @AllanMajanga 4 месяца назад +2

    SKC he loved his country and he was a man of peace.

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza 4 месяца назад +7

    Chilima anatipwetekesa kutibwelesela mcp

  • @DavieTebulo-l2l
    @DavieTebulo-l2l 3 месяца назад +1

    Ndale zakumalawi mmalo mot anthu akhale pamodz kukonza dziko koma aliyense akufuna kupakula zake😂😂😂...ngat iyeyu akufunira zabwno dziko bwanj osapanga zomwe skc amaganiza.. komanso akuonetsa kut sanayende maiko ambiri... and zambiri akuzionera munyuz.. ngat momwe amaonera chakwera.. ruling acountry isnt ajoke Mr Nankhumwa...

  • @MosesNkumaniza
    @MosesNkumaniza 4 месяца назад +1

    Koma akulu awa ndi kazitape zonse ayakhula zokhuza skc akapangisa ndi kodwani munthu woipa lero ali kunja Kwa chipani Cha DPP chauta wamulanga athera pomwepo god is great

  • @FrancisGomani-w5d
    @FrancisGomani-w5d 3 месяца назад

    May his soul continue resting well... He was indeed a genius.

  • @johnteddy6928
    @johnteddy6928 4 месяца назад

    I love u my president ❤❤❤

  • @paularason
    @paularason 4 месяца назад +5

    Komatu anthu mukutukwana molakwika
    Nankhumwa ndiyemwe amatenga dzinthu ku DPP kumamuza Chilima Amene amapangila kuti Chilima aziziwa zi nsisi zaku DPP anali Nankhumwayo

    • @samsonpadiwa9185
      @samsonpadiwa9185 4 месяца назад

      And I think ma meetings amene amachitika wo there was something cooking and APM anawelenga Anthu amenewa

  • @samsonpadiwa9185
    @samsonpadiwa9185 4 месяца назад +2

    And I don't blame APM for not meeting him coz we don't know what's his plan for sure

  • @jezalakaphuka7325
    @jezalakaphuka7325 4 месяца назад +2

    The conditions that APM alined were perfect

  • @DinhLawck82
    @DinhLawck82 3 месяца назад

    Mmmmm Ine nankhumwayu sindugwirizana naye.. I think iyeyu ndyemwe ankamuuza muthalika zonama Za chilima

  • @ChrispinEdward
    @ChrispinEdward 4 месяца назад

    Muthu ameneyi muli zelu and is humble

  • @esthermkwapatira1693
    @esthermkwapatira1693 2 месяца назад

    Chilima lest in peace koma anar osokoneza mulungu amukhururukire

  • @ChikondiKammaluwa
    @ChikondiKammaluwa 4 месяца назад +3

    Chipani chosokoneza ichi Ife sitingachivotelepo ataa Ife koma Peter basi

  • @AdamMedson
    @AdamMedson 3 месяца назад

    Man Kho ndinu osokoneza

  • @DominicYohane
    @DominicYohane 3 месяца назад

    Ndevu zili mbali.. ndi style kod? Kkk ndaseka..😂😂😂

  • @PamelaSumbuleta
    @PamelaSumbuleta 3 месяца назад

    Koma ndie mutu oumatu mpaka kulephera mayeso a 8 kawiri😂😂😂😂😂

  • @frankiechasokoneza5802
    @frankiechasokoneza5802 4 месяца назад +1

    Kukana kwa Peter Muthalika kulandilaso Chilima was a gud choice chifukwa APM amakhulupilira kut his late brother Bingu was poisoned nde iyeyo was trying to avoid same incident eg mene zinakhalira ndi Chakwera n Chilima lero kulibe

  • @AdsonPwele
    @AdsonPwele 3 месяца назад

    Mmmmm koma 😭😭😭😭

  • @ThokozaniBondo-em9fr
    @ThokozaniBondo-em9fr 4 месяца назад +3

    Malemiya mabodza 😂😂😂😂😂😂

  • @AngelsGift-o7p
    @AngelsGift-o7p 4 месяца назад

    Joab anthu andale adzakukhadzulirana sure🤣🤣🤣 ukufuna m'nzako ataniiiiii kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

  • @kanekulisewa
    @kanekulisewa Месяц назад

    Wayankhula zomveka aka akweni

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 4 месяца назад +6

    Kodi amagwa chifufu kondwaniyu

    • @DinhLawck82
      @DinhLawck82 3 месяца назад

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @GrantBello-m7o
    @GrantBello-m7o 22 дня назад

    Pdp❤

  • @giftkanjuchi-qm8hf
    @giftkanjuchi-qm8hf 2 месяца назад

    Nakumwa is a good man

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 4 месяца назад +1

    Osamatchula mulungu,ngati Chakwera wa mulungu Wake wakupha, adamupha Chilima Panopa Ali mutu phwi ngati phiri la Mulanje angochita manyazi

  • @EmercianahKasiku-en6hl
    @EmercianahKasiku-en6hl 4 месяца назад

    Dr Chilima anali munthu okonda kwambiri dziko lake than anything else and anali odzichepetsa kwambiri

  • @MacdonaldMasamba-e2x
    @MacdonaldMasamba-e2x 4 месяца назад

    Dziko la Malawi 😢😢

  • @johnteddy6928
    @johnteddy6928 4 месяца назад +1

    Love pdp

  • @carlossadimba595
    @carlossadimba595 4 месяца назад +1

    Bingu was a good man

  • @joelkamanga4646
    @joelkamanga4646 4 месяца назад

    I wonder ambiri andale akumalawi amanena zamlungu koma akalowa m'bomamo zimakhala bamva zoopsa. Too much corruption. Pathetic!

  • @mackrichman9643
    @mackrichman9643 4 месяца назад +1

    Koma kuyakhula ndiphaso ndithu,ndakhulupilila sopano.amwenewa alibe phasoyi

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 3 месяца назад

    Suukanawina pa APM iwe chomwe ungamadziwe ndichakuti suunganyere pomwe umakhalira mphwanga

  • @UchizieFMtemela
    @UchizieFMtemela 4 месяца назад

    Go between alwys amaononga zinthu coz kwa a chilima amapita yekha and kwa munthalika amapitanso yekha. Uyuyu uyu ndiye kavuwevuwe

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 4 месяца назад +3

    Wabodza ndi mwa anthu omwe ankanamiza muthalika kuti chilima akufuna kumulanda dziko.

  • @violetpotani
    @violetpotani 4 месяца назад

    Nawonso awa 😅😅atilakwitsa

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 4 месяца назад +2

    Koma malemya longosoka unali modzi mwa anthu owononga chipani cha dpp ndiye ukuwona kuti pano pdp ikoza zinthu foolish mwana wa ng'ono iwe unataika unasanduka ng"azi

  • @chelseajackson3200
    @chelseajackson3200 4 месяца назад

    Zabodza izi, timve akwini koma. Kondwani is an opportunist with no direction. Munthu amene amawuulura zinsinsi wina atamwalira, dziwani ndi wabodza ndiwodzikonda yekha.

  • @josephmwamadi-m3i
    @josephmwamadi-m3i 2 месяца назад

    Wabodza iwe nakhumwa osapezelapo bodza pakuti anafa okutsutsayo chilimayo

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 4 месяца назад +6

    Komatu ndiye ukupumila mwamba 😅😅😅😅😂😂😂iweyo ndiye Bp ingakukutumule mwachangu😅😅😅😅😂😂😂

    • @ShamilKumwembe
      @ShamilKumwembe 4 месяца назад

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @DonPhiri-u2j
    @DonPhiri-u2j 4 месяца назад

    Anthu andale kumalawi ndioipa akakhara pampando amatitengangati anthu opanda ntchito amayamba kumati ndife osalimbikira chonsecho akudya misonkho ya anthu omwefe azisamala coz one day mulungu azatiyamkha muzisamala mukamati mindset change

  • @EdwirnMatewele
    @EdwirnMatewele 4 месяца назад +1

    Wabodza nankhumwa akukamba poti anamwalila amatani kunena asanamwalile

  • @AlnordKalambo
    @AlnordKalambo 3 месяца назад

    Ndinu osokoneza inu

  • @LawrenceChimela
    @LawrenceChimela 3 месяца назад

    Chilima anali ozindikila that's why anthu ambili amamu hate !

  • @BILALAJASIMVERANI
    @BILALAJASIMVERANI 4 месяца назад

    Zomwe mukunena inu anankhumwa Kaya ndi zoona Kaya zabodza koma kwa ife tikuziona kuti ndi zopanda ntchito ndipo ndizosathandiza olo pang'ono chifukwa Chilima wo kulibe ndiye ndizopanda ntchito sizingathandize ndipo sizikupindulirani olo pang'ono.

  • @FrancoJollam
    @FrancoJollam 2 месяца назад

    Iwe.unarikut.aaaa

  • @kinovatthowa52
    @kinovatthowa52 4 месяца назад

    Nanga why were you so silence in parliament when things are going astray .zinthu kumangokwera basiiii

  • @AnnieKwisanja
    @AnnieKwisanja 4 месяца назад

    Wabodza iwe nakhumwa mboni Yako ndindani?

  • @MatthewsLex
    @MatthewsLex 3 месяца назад

    Munthu wakhala pas kma ayakhula ngt watopa zukhala bwnj kd

  • @SteveAngaMuwellah
    @SteveAngaMuwellah 4 месяца назад +1

    Kuyetsera madzi otayika kuwatolera

  • @SildaKatundu
    @SildaKatundu 4 месяца назад

    Zopanda nchere ,za ziiiiiiiiiiii ndipo sizikumveka ataaa

  • @CeniaMayeni
    @CeniaMayeni 4 месяца назад

    Ndamva,mfundo zako zopanda nzeru, khala pansi

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita 4 месяца назад

    kuyambila lero boma pena lizikhalako ndinthawi yomva maganizo awanthu pa wilesi or p tv mwina zikhoza ko kukhala bwino democrancy ingKome pamene boma silikuchita bwino anthu azizuzul bomalazo lizimva maganizo awanthu paZomwe zikuydnda komaso zomwe sizikuyenda

  • @IdianMpindeni
    @IdianMpindeni 4 месяца назад

    Waziulura yekha kuti ndiamene amatenga za ku dpp kukasiya ku utm uyu ndioipa ndithu

  • @EssaSimon-qw8cl
    @EssaSimon-qw8cl 4 месяца назад

    Kondwani ndi wabodza komaso amatumidwa ndi mcp kuti asokonedze
    DPP galu iwe ndani angakuvotele

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 4 месяца назад

    Koma nankhumwa zomwe ukukambazitu unakati ukutsutsa mpaliyament muja zili bwinotu iwe mmmmm

  • @yankhomichongwe4694
    @yankhomichongwe4694 3 месяца назад

    Ndaonela yonsei..all i can say is, adha awawa can't be trusted..

  • @jonathanshonga4742
    @jonathanshonga4742 4 месяца назад

    Koma nditukwana kwinako

  • @AlfredNazombe-js4go
    @AlfredNazombe-js4go 4 месяца назад +6

    Aaaa inali pln yawo kut aphe apm asale nawo APM ndiwankulu adaona patali

  • @Josephchiunjila
    @Josephchiunjila 3 месяца назад

    Inu munapita ku chipani Cha chibanja muthalika party ijakaaa

  • @PatricaTchuwa
    @PatricaTchuwa 4 месяца назад

    Waboza uyu, akusowa kolowera

  • @ThokozaniBondo-em9fr
    @ThokozaniBondo-em9fr 4 месяца назад

    Aaaaaaaaa koma uyu wapenga mensa ndinuyo munayambisa kumamuwudza chilima mabodza cholinga kuti zikamuwawa atuluke muchipani ndye muzitinamidzapo chifukwa chilima poti palibepo.....

  • @MalawiOne
    @MalawiOne 4 месяца назад

    Panfundo zimene achilima amafunazo zinali zabwino kwambili kuti abwele ku dpp kodi inu anankhumwa osapanga chisankho chobwela ku dpp bwanji zikhoza kuchita bwino kwainu

  • @Mphangala
    @Mphangala 4 месяца назад

    Ili ndiye bodza la mkukhuniza basi kungomva kuti wakufa salankhula ndiye basi kumangolankhula zilizonse

  • @ishmaelsiffah9900
    @ishmaelsiffah9900 4 месяца назад +2

    So when are u going to make peace with professor Arthur Peter wa muthalika

  • @BLM-cp5rm
    @BLM-cp5rm 4 месяца назад

    Etii!! 😂😂😂

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi 4 месяца назад +2

    Mbuzi nankhumwa wa jealous

  • @andychingwalu
    @andychingwalu 4 месяца назад

    kodi interview yi mumapangila ku khola la nkhuku?

  • @HamanjaManyela
    @HamanjaManyela 4 месяца назад +2

    Don't judge this guy

  • @GodfreyMando
    @GodfreyMando 4 месяца назад

    Pano sitikufna kudzaonaso ma galimoto amanambala plet achimanga komaso sitkufuna dziko lamakadet

  • @EnossDzuwa
    @EnossDzuwa 4 месяца назад

    Kma potengera mbiri yake yomwe akufotokoza anankhumwa apapa sanayenera kuonetsa khalidwe lomwe anaonetsa ku DPP

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 4 месяца назад

    Muthu oipa iwe usatinyase

  • @Elizabethmanda-es7se
    @Elizabethmanda-es7se 4 месяца назад

    maboza sitifuna

  • @hashimmtelera9536
    @hashimmtelera9536 4 месяца назад

    Kodi Joab,Cruise 5 iyi sasankha nyimbo a nankhumwa wo?😂😂😂

  • @Jermah51kennias
    @Jermah51kennias 4 месяца назад

    Tchende la mwana ili

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 4 месяца назад

    Ndi olephela ameneyo ndipotso ovetela iye mwina family yake

  • @clementchimwemwekadzamira1675
    @clementchimwemwekadzamira1675 4 месяца назад

    Malawi is failed state kuchuluka bodza,nsanje ndi mtenda. Ma politicians ambili ndi abodza adyera komanso omangofuna kutenga advantage kulephera kwa a Malawi.
    Dziko lino likufunika REVOLUTION. Kwachuluka dyera.
    Anthu nonse a ndale mdziwe kuti ndinu abodza,akuba ndiwopanda chilungamo, MULUNGU sali nanu chifukwa sinu oyenera kutsogolera, shame on you,simukapulumuka. Mumafuna zambiri koma simudzazipeza zambiri chifukwa muli zambiri zolakwika. Ndinu anthu osauka, ndipounsauka ndi mzimu omwe ndipo mukuyenera kuti mupemphere akukhululukireni. Please don't take advantage of poor people.

  • @elizasingano
    @elizasingano 4 месяца назад +1

    PDP siufiti umenewo osasankha dzina lina bwanji

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya 4 месяца назад

      Ndiponso,ati kufuna kupusitsa anthu izimveka ngati DPP....get out

    • @CatalinaLupiya
      @CatalinaLupiya 3 месяца назад

      😂😂😂😂😂😂😂shame

  • @blessingsmdezasaizi9544
    @blessingsmdezasaizi9544 4 месяца назад

    DPP muli anthu a mzeru anamuona Yudas uyu mkumuponya kunja

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 4 месяца назад

    Eeeeee koma nthawi ya kampeniyo timva zinthu kulankhula mgati ngelommmmm

  • @FrancoJollam
    @FrancoJollam 2 месяца назад

    Chitsiru.chamunthu.aaaa

  • @emmanuelmanyozo
    @emmanuelmanyozo 4 месяца назад

    FUTSEKIII!

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 4 месяца назад

    Mmmm mbuli

  • @lysonmwale6956
    @lysonmwale6956 4 месяца назад

    Okufa sapeleka umboni

  • @EdsonKamwendo
    @EdsonKamwendo 3 месяца назад +1

    Ukuwala bwanji ndimaetsa unkasuma ndi iwe Joab mutengetse ameneyu wangokula mutu koma magabizo ake ndi chindasi

  • @ElizabethSawenga
    @ElizabethSawenga 4 месяца назад

    Wabodza uyu muthu oipa

  • @johnteddy6928
    @johnteddy6928 4 месяца назад

    All of u Malawians u blinds this guy is real

  • @ErickTym-u2m
    @ErickTym-u2m 4 месяца назад +1

    Otupikana iwe chisilu skc sanachezeko nawe iwe chenkhumba

  • @EmmanuelMkhumbi
    @EmmanuelMkhumbi 4 месяца назад

    Mnvula ikagwa

  • @GABRIELMASIYANO-s1c
    @GABRIELMASIYANO-s1c 4 месяца назад

    amangoyenera kumuchotsa uyu ndi nthera kuwiri leader of opposition nkumangosekerera ndizopusa zomwe dziko likuvutika. stupid kondwani

  • @Danielmaonga
    @Danielmaonga 4 месяца назад

    He was sellout this guy ,why in parliament wen he was a leader he chose to be quitt no opposition political is stupit game sometimes

  • @Martinmkapangakapanga
    @Martinmkapangakapanga 4 месяца назад

    anakhumwa inu ndi munthu oyipa kwambili mulibe dzelu kwambili

  • @MasautsoLameck
    @MasautsoLameck 4 месяца назад

    Apm amazwa kut akamuuza chlima zmenezo chfukwa chakukula mtima amazwa kut salora 😂😂