NAMIWA WAULURA ZINSISI ZODABWISA ZOMWE ANTHU SAMADZIWA ZA KAFUKUFUKU WA IMFA YA CHILIMA PA INTERVIEW

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 31 окт 2024

Комментарии • 130

  • @AdamBwanali-kr5fw
    @AdamBwanali-kr5fw 26 минут назад +2

    Namiwa ....you are so brave ...zikuonetseratu kuti chakwera anamupha Chilima .....uyuyu wachita bwino kuchokamo akanaphedwa

  • @McshonWilliam
    @McshonWilliam Час назад +6

    Mr namiwa anakubelekani wo sanaluze ai ndipo komwe aliko alandile maulemu and isaid may god continued kuwapasa zosowa zawo 🙏🙏🙏🙏

    • @TendaiGwiriza
      @TendaiGwiriza 39 минут назад +1

      A Namiwa mumakwana heavy

    • @DicksonLingsonmulauzi
      @DicksonLingsonmulauzi 39 минут назад

      Ndipo pakanapezeka anthu oterewa malawi muno okwana 10 dzikoli bwnzi lili lolemera kwambiri

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 8 минут назад

    Mbambande,namateture weni weni.....Kulankhula kokhakokha..kwa chilungamo...Bravo Comrade Namiwa❤❤❤❤❤❤

  • @graciouskamwendo1873
    @graciouskamwendo1873 Час назад +5

    Mtola nkhani uyuyu ntchito yake ikuoneka ngati amangofuna kupeza vuto mwa a Namiwa.
    Sakuoneka ngati akupanga zosaka chilungamo ayi

  • @ThomuChiwanga
    @ThomuChiwanga 21 минуту назад

    Mr your number one In my country thanks mr namiwa keep up malawi

  • @RejoiceKaliya-i9t
    @RejoiceKaliya-i9t 42 минуты назад

    Ndatsimikiza kuti anthu anzeru, achilungamo, olemekeza chikumbumtima chawo adakalipobe mmalawi muno! Bravo Dr. Namiwa. Inuyo ndinu Dr kuyambira lero!

  • @lucksonmoonga4426
    @lucksonmoonga4426 55 минут назад +1

    Keep it up sir.may God continue protect u and bless u.

  • @InnocentHassan-m3r
    @InnocentHassan-m3r Час назад +2

    May ALLAH protect you Mr Namiwa you're true fighter

  • @JosephIsaac-s1c
    @JosephIsaac-s1c 17 минут назад

    Comrade Namiwa inu mulungu adzikudalitsani you are special ❤❤❤❤❤❤

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 59 минут назад +1

    Uyuyu akufunika award (2024 the best political activist Ndi Comrade NAMIWA 💪🔥)
    2024 the best Tv ndi Bakili Muluzi Tv 🔥
    Kalindo ndiye pangolin wathu 💪

  • @kakachimtengo7340
    @kakachimtengo7340 16 минут назад

    Wow what a guy ❤we love you sir

  • @AlexNjovu-j4z
    @AlexNjovu-j4z 2 часа назад +6

    Ifetikuwavesa anamiwa🙏🙏

  • @HassanChibwana-m8j
    @HassanChibwana-m8j 37 минут назад

    We love you Sir
    Keep it up.we trust you

  • @kinggasperagain
    @kinggasperagain 28 минут назад

    God bless you sir namiwa

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 25 минут назад

    Bravo boss kuwala ndi M'dima siziyendela limozi

  • @stevendemanje
    @stevendemanje 53 минуты назад +1

    Yehovah akutetezeni kwa mikango ya mcp mr namiwa

  • @MagretMpasu
    @MagretMpasu 6 минут назад

    Osaopa sir pic up Mr namiwa ❤❤❤❤❤❤

  • @Love-r7f8c
    @Love-r7f8c Час назад +3

    Ntolankhani iwe usamafunse mafunso ngati wadya chibanzi

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar Час назад +2

    Namiwa bravo man

  • @katalamajames4947
    @katalamajames4947 Час назад

    Well done mr namiwa ur very interesting to malawian people we need people like you,,,

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate Минуту назад

    ❤❤❤❤ lweyo namiwa ndi 1

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Час назад

    Ndakumvetsela Mr namiwa ndiwe big man more fire 🔥 ipulumutse malawi 🇲🇼 malawi 🇲🇼 akufuna athu onena chilungamo ndimopanda matha ndimomasula more fire 🔥

  • @MrMagombo
    @MrMagombo 41 минуту назад +2

    Abusa a Seventh day a Nyirenda ali konko kaya akutaniko kopanga zanserizo?

    • @AustinNangwale
      @AustinNangwale 27 минут назад

      Ndimene uziwe Kuti ndindani yemwe amakonda m'dima ndipo ndindani yemwe amakonda zamudima..Stop trusting people boss amipingowa akuchita nyasi kuposa satana

  • @petermanford3284
    @petermanford3284 51 минуту назад +1

    A tolankhani enawa ndiye ayitu.

  • @christopherkachione6323
    @christopherkachione6323 Час назад +1

    Fire 🔥🔥

  • @BrianPsalmist
    @BrianPsalmist Час назад

    Bravo Mr Namiwa

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 47 минут назад

    m'Malawi muno muli akatundu, m'modzi mwa iwo ndi Namiwa. Kip de 🔥 burning 👆

  • @MordecaiMafunga
    @MordecaiMafunga Час назад

    A namiwa keep it up god bless you

  • @AshrafShadid
    @AshrafShadid Час назад

    Mbambande speech with u mr Namiwa

  • @imraanJafal
    @imraanJafal 57 минут назад

    Mr inutu ndi boooon kalindo ntchito yanu imanditsangalatsa kwambili simuopa simutopa❤

  • @CleverChiumia
    @CleverChiumia 48 минут назад +1

    Mafunso opanda nzeru

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 2 минуты назад

    Anamiwa we are siding with you,son of the soil ,let us collectively clean this mess❤

  • @believersanddeciplesofjesu8602
    @believersanddeciplesofjesu8602 Час назад +2

    Tolakhani uyundi chisiru kwambiri koyamba kuona tolakhani opanda zeru osaziwa tchito ngati uyu buluzi weniweni

  • @chikondisatchipa7676
    @chikondisatchipa7676 Час назад

    Koma adhawa chilungamo amachidziwa and iwowa sakusamala zandalamad eee ulemu wanu anamiwa God bless you

  • @LevisonMalemba
    @LevisonMalemba Час назад

    Namiwa nkatundu ❤❤❤❤❤

  • @StephanohMoses
    @StephanohMoses 28 минут назад

    Oyakhula chilungamo saphethila ulemu wanu Mr namiwa

  • @WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un
    @WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un 3 минуты назад

    Dziko likufunika anthu ngt awa mr NAMIWA VS BON KALINDO tikusowekera anthu onga awa osati mbava zili ku mcp en chikangawa

  • @RuthMlenga
    @RuthMlenga Час назад +1

    Tamva za commission of inquiry yopusa ija

  • @DicksonLingsonmulauzi
    @DicksonLingsonmulauzi 41 минуту назад

    Mr namiwa osazawaphweketsa muli zilungamo umu

  • @MordecaiMafunga
    @MordecaiMafunga 54 минуты назад

    Mr namiwa you have truth like Patricia 😂😂😂😂

  • @ManfredNakhuba
    @ManfredNakhuba Час назад +1

    Mtolankhani uyu akhalangat wasyetsedwa banzi akufunsa zoti wafotojoza kale aaaaa

  • @TraverMbewe
    @TraverMbewe Час назад +1

    Km tolankhaniwe nde ata uli pachangu uzimpatsa mpata namiwayo azitambasula bwino osati zakozo

  • @PeterRabson-z3w
    @PeterRabson-z3w Час назад

    Namiwa ndiwe katundu madzi👍

  • @ChrisMsonyo-yq2ko
    @ChrisMsonyo-yq2ko 46 минут назад

    Anthu ngat inu mutapezekapo atatu malawi wll be saved from fire💥

  • @ChristinaStambuli-q3e
    @ChristinaStambuli-q3e Час назад +1

    Commission of inquiry izakhalapo 2025 just after a new elected president ..Mcp ndi Caikwera waoyo ali pa bench anzao akuvinamo ngat momwe akuvinra Chikangawa ndi kunkuyu,Chimwendo Banda..,iyiyi com of inquiry ndiya mcp anthu aja akochedwa kale palibepo phindu amalawi sitipezamo mayankho.Rip Skc and all the victims

  • @GanizaniChinchembere
    @GanizaniChinchembere Час назад +1

    Koma ntolakhaniyi bwanji?

  • @MussaLenard-s2t
    @MussaLenard-s2t 53 минуты назад

    Tir oambuyo panamiwa🔥🔥

  • @AishaJibu-u6y
    @AishaJibu-u6y Час назад +2

    Mtolankhaniyo ndi kape satha ntchito munthu osamusiya bwanji alongosole

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole Час назад

      Musaiwale kuti zodiak imatsamira kuboma sangafuse ngati a times akuopa .

  • @mwaiwaobanda2691
    @mwaiwaobanda2691 46 минут назад

    Ulemu kwayemwe analera Sylvester ndi nzeru...Ambuye mutetezeni namiwa

  • @alicechinyama4155
    @alicechinyama4155 58 минут назад

    Ndipo anamiwa iiii mulungu awasunge

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr Час назад

    Ine momwe ndinkafunsira ntchito, ndinagwiritsa ntchito keyala ya school. Koma polemba kalata sindinagwiritse ngati school yonse, ndinalemba kuti ine, Pondiyankha anandiyabkhanso ngati ine, osati school yo. Ndiye Namiwa analemba Kuti I, means Namiwa.

  • @JulietMrsAndrea
    @JulietMrsAndrea Час назад

    Keep up

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Час назад

    Bravo Namiwa

  • @AustinKhan
    @AustinKhan 45 минут назад

    Broval man

  • @TaulayeDesmond-e9v
    @TaulayeDesmond-e9v Час назад

    Jesus Christ of our country❤

  • @believersanddeciplesofjesu8602

    Namiwa ndikatundu kwambiri ndamukonda Muthu olimba mtima kwambiri

  • @ElizabethMaononga
    @ElizabethMaononga Час назад

    Mmmmm.khalani chete anamiwa

  • @ThomasChiwaya-qx9mf
    @ThomasChiwaya-qx9mf Час назад

    Iweyo namiwa ukhara presedent popano

  • @HamzahTwaib
    @HamzahTwaib 39 минут назад

    Iweyo Namiwa mulungo azikudalisa serious,, mmmm ndikungopemphela kwamulungu kt zikhala kumbali yako,, ndipo za mec zo zitelodi mmmmm

  • @UchizieFMtemela
    @UchizieFMtemela 2 часа назад +1

    Wachita bwino kutulukamo coz ena onsewo ali mu same boat ndiye zomangovomereza zilizonse kumangoyenda ngati madzi amvula

  • @AnysonChimkwita-w2o
    @AnysonChimkwita-w2o 11 минут назад

    Mumakwana Anamiwa

  • @JuntaKafalimani-iu3ct
    @JuntaKafalimani-iu3ct 2 минуты назад

    Ntola nkhaniyo akuphimba chiyani pofusa mafuso owatchinga a Namiwa nayeso wadyapo

  • @GeofreyMkhala
    @GeofreyMkhala 25 минут назад

    Palibe chadzelu apa😢

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt 57 минут назад +1

    Journalist Ndi waphuma

  • @BenjaminMtima
    @BenjaminMtima 23 минуты назад

    Zodiak uyo sintola nkhani sadziwa ntchito ngobowa

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 Час назад

    Azibusa oipa aja ndithu adakana chilungamo akamalalikila ngati akumudziwa yesu

  • @FreedahKabaghe
    @FreedahKabaghe Минуту назад

    Ulemu wanu achimwene anamiwa, mulungu akusamalireni

  • @EdsonKamwendo
    @EdsonKamwendo 31 минуту назад

    Mbambande Namiwa mmasule ntolankhani wopalamkamwa uyu pamene sakumvetsa mpati

  • @KingdavidNkhata
    @KingdavidNkhata 42 минуты назад

    Muli bwino pangolini wathu Mulungu azikudalitsani nthawi zonse timamakunyadirani nthawi zonse

  • @WilliamKawaza
    @WilliamKawaza Час назад

    Uyu ndemuthu

  • @BrazioNtondo
    @BrazioNtondo 32 минуты назад

    Ndiwe munthu wanzeru aise

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz Час назад

    Eeee namiwa ndi machine amalawi tinangokhala anthu opepela ndithuuuuu

  • @AustinBottoman-x1y
    @AustinBottoman-x1y 2 часа назад

    I like Namiwa

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c Час назад

    Koma namiwa ndi munthu ozindikila kwambiri osafooka mr

  • @AshrafShadid
    @AshrafShadid Час назад

    Nyatwa man no need smart Matic here in nyasaland

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 36 минут назад

    Awa ndi achisilu amafu na kuti anthu 18 aziyendela zaiwo ndi kape

  • @IslamMapepa
    @IslamMapepa Час назад

    Koma achita bwino kutuluka chifukwa tonse amalawi maso anali kwanamiwa chifukwa enawo ndiosakhulupilika koma anakapezeka independent achita bwino

  • @PeterPhiri-nd6op
    @PeterPhiri-nd6op Час назад

    Kuyakhula kwabwino namiwa athu if tili ndi vuto timaombela mumaja chirichotse

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu 3 минуты назад

    A Namiwa anangokuikani kuphimba anthu kumaso akanazikuzembani kumeneko kumapanga zawo ndipo ndiye mukanapusa akuziwana awa anakumana kayedi kumbaliko ndikuuzana chochita mwachita bwino mwachokako

  • @PeterGrant-ih1sr
    @PeterGrant-ih1sr 13 минут назад

    Nzimu wamuthu ndi nkhan zina chaka Chino ziliko

  • @thatgirrroskrr3570
    @thatgirrroskrr3570 37 минут назад

    Mtolakhaniyi nde ayi. Namiwa akumane ndi Byani Banda interview izakoma

  • @ashingsmvula3357
    @ashingsmvula3357 32 минуты назад

    Kumanga mseu ndi kupepela? Sure?

  • @YaqoobStandwell
    @YaqoobStandwell Час назад

    Zoonad ose abwele poyela kodit mcp ikuziwa chilungamo chenicheni

  • @ashingsmvula3357
    @ashingsmvula3357 58 минут назад

    Kambuli aka kakulephera kusiyanitsa cedep ndi iye mwini

  • @ChancyDzinkambani
    @ChancyDzinkambani 2 часа назад +2

    Mmakwana a namiwa tithandizireni MPAKA chilungamo chidziwike

  • @CosmasChikwindi
    @CosmasChikwindi Час назад

    Uyu ndiwotsokoneza, akanakhala ndinzeru akanakhalakomweko kuti awone mene ziyendele ndiyeno kaya zinazo sizimukomela ndiyeno mpamene akanabwela poyela, khuthawako sizikupeleka nzeru.

    • @FracksonMadani
      @FracksonMadani 14 минут назад

      Ndizoona wakambazo, koma udzafa ngati Chilima,,,,munthu ukudziwa ndikuoneratu kuti sukondedwa basi ndwiiiii😂😂😂😂😂ndionetsetse chili apachi anathetsa nkhuku pakhomo😂😂wachitabwino kutengako mwachangu cause anamusungira kampeni kupha......

  • @HopeNamaheya
    @HopeNamaheya Час назад

    Namiwa katundu omanga ndi mawaya

  • @MarkoMayuni
    @MarkoMayuni Час назад

    Uyu uyu wathawa kufunsidwa mafunso nayenso akayankhe chifukwa anapitako kwa god papa

  • @JosephyKambalu
    @JosephyKambalu Час назад

    Stupid move by Namiwa. Apa ndiye azitiuza kuti chani.

  • @PaulChombo
    @PaulChombo Час назад

    Umatha Namiwa tili pambuyo pako

  • @andreakalambula7723
    @andreakalambula7723 2 часа назад +1

    mcp why ishiii. 😅😅😅😅😅

  • @ThomuChiwanga
    @ThomuChiwanga 31 минуту назад

    Kodi nanunso kumeneko kunari group olo Mr namiwa nthawi zina inu mafutso zifutsaniko Ngati amalawi tikuverafe tikukuwonanitu zbs mwamva alutumani Kodi eti anamiwa anachita bwino basi kubwerera kumeneko basi

  • @terezazakeyo2285
    @terezazakeyo2285 Час назад

    Malawi itakhala ndi athu angapo ngati anamiwa itha kukhara lokoma

  • @ashingsmvula3357
    @ashingsmvula3357 34 минуты назад

    Kudana ndikumangidwa kwa mseu mumafuna tiziyenda mzigwembe...opusa iwe cadet

  • @EnockMvula
    @EnockMvula Час назад

    ayi akuwopa chifukwa mzimu ndiyovuta ayambiratu pachiyambi awona kurumbira ndikovuta murungu angamukanthe kkkk

  • @GeofreyMkhala
    @GeofreyMkhala 24 минуты назад

    Namiwa you not give answers but you explain 😂😂

  • @jimmywhitecollins
    @jimmywhitecollins Час назад

    Chisilu chadyera ichi

    • @sweeneykamwendo6251
      @sweeneykamwendo6251 52 минуты назад

      Anakakhala wadyera sanachoka mu commission of inquiry.

  • @EliasKawuwa
    @EliasKawuwa Час назад +1

    A Malawi ife ndife anthu oipa kwambiri, chinthu chikamuchitikira zathu ,timafuna timuweruze kuti nde wolokwitsa kwambiri,chifukwa Cha nsnje,nkhwidzi,komaso kaduka, Soulos Chilima ankamunena Ali moyo,kuti ndiwakuba,lero wachita ngozi wamwalira,anthu mukufuna kuoneka ngat munkamukonda ,kuyamba zoyankhulayankhula zosakhara bwino, lero mudziko muno,muli mavuto a fuel,mmalo mongwirizana,ndikungwirira ntchito limodzi,tithetse vutoli, iyeyo akufuna ku commission of inquiry,lero amusankha kuti akhare nawo mu commission, nde sakufunaso, nde akufuna chiyani kwenikweni? Anthu oipa kwambiri,Dziko lathu lovetsa chisoni kwambiri

    • @VerianoKingsley
      @VerianoKingsley Час назад

      Ase Malawians ndiolephera.... Sadziwa chomwe akufuna...

  • @zamanmwachumu554
    @zamanmwachumu554 41 минуту назад

    Ndan yemwe anakuuzan kut inapita kunzuzu

  • @StanelyPhiri-kg1ix
    @StanelyPhiri-kg1ix 2 часа назад

    Oyipa wathawa yekha

    • @AustinBottoman-x1y
      @AustinBottoman-x1y Час назад

      Munthuyi adali nkhosa pakati pa mimbulu

    • @viennasamuel2976
      @viennasamuel2976 Час назад +1

      ​@@AustinBottoman-x1yoipa ndiamene atsala enawa ndi a mcp tiwaleke

    • @EmmanuelGasiten-fo5dr
      @EmmanuelGasiten-fo5dr Час назад

      @@AustinBottoman-x1y Mwinanso mkati katimo akanatha kujiwa ndi mimbulu imeneyi.

    • @AustinBottoman-x1y
      @AustinBottoman-x1y 59 минут назад

      @EmmanuelGasiten-fo5dr ndipo exactly

    • @AustinBottoman-x1y
      @AustinBottoman-x1y 59 минут назад

      @@viennasamuel2976 Ndipo akhale tione abweresa zotan