Pakhale lamulo loti,amene akupikisana pa mpando wa u president azikayesedwa ku mento.Kutsogoku wamisala adzakhala msogoleli wa dziko.Muwaonetsetse akuluwa yankho mulipeza.
Times radio n tv siopa ndipo ilindichilungamo polakhula ❤ osati awa zikachitika muvera kwa ife arikuti zoti ziko laora saziwa pano ndi mcp radio etti zachisoni
a boma akusowa anthu odziwa timati stock controllers, timakhazikitsa timati ma stock levels. andilembe ndiwaphunzitse zimenezo and its on a serious note
Madoras amatha ndimaulendo a president osati kugura magalimoto kokha ai komansotu magalimoto ndi amene akubweresa ndalama ku M R A coz galimoto imozi imatha kulipira custom 30 million koma ndalamazi sizikugwirisidwa ntchito bwino bwanji osafusa anzowo kuti amaziyendesa bwanji zinthuzi.
Kodi ku UNGA KUJA ANA ONONGA MA US DOLLARS NANGA SAMKADZIWA KUTI KULI NGONGOLE YAMAFUTA ASANAPITE KU UNGA.NAGA MA US DOLLAR AKU OPITANA KU UGA ANAWATENGA KUTI? KODI MALAWI YAPONDULAKO NDIUNGA KULEKANA NDI MAFUTA
Bvuto la bomali zimene amalangizidwa amazitaya asanazimvesese and mubaibulo muli mawu onena kuti ena saziwa kuti saziwa mzeru za yekha anaviika msima m, mazi
I have been defending MCP but the way they have handled this fuel crisis, they have completely lost me
Kkkkkk
Pakhale lamulo loti,amene akupikisana pa mpando wa u president azikayesedwa ku mento.Kutsogoku wamisala adzakhala msogoleli wa dziko.Muwaonetsetse akuluwa yankho mulipeza.
Km programme iyi ay ndthu
Keep going,...... Mukusekula mmaso amalaw
It's only this program I love from Malawi radio stations
😂😂😂😂😂 nde mwat achakwera anaika m'botolo. Watching from kk
Bodza NDILOMWELI la mafuta ngambwingambwi, akudwala manyazi pano. 😊😊😊😊😊😁😁😁😁😁😁😁😀😀😀😀😀☺️☺️☺️☺️☺️😃😃😃🤗🤗🤗🤗🤗🤗🤗🤗🤗🤗
Jessie Kabwira 😂😂😂😂😂kuli ziiii
Wabakili muluzi uja osazamudela
Telling the truth without fear,keep it up gents
The spirit of negligence is flowing in this country and it was started on the death of Dr Saulos Chilima
Times radio n tv siopa ndipo ilindichilungamo polakhula ❤ osati awa zikachitika muvera kwa ife arikuti zoti ziko laora saziwa pano ndi mcp radio etti zachisoni
Good job guyz
a boma akusowa anthu odziwa timati stock controllers, timakhazikitsa timati ma stock levels. andilembe ndiwaphunzitse zimenezo and its on a serious note
Wonderful program and great atola nkhani a times
kodi mr Chikangawa kuti Bwanji pakhani ya Mafutai? and you Remember adalakhulapo kuti sakuziwa kathu Ziko liochedwatu ili
Gayez inuo nd more
Mbambande program
A bakili muluzi aja akuomeka ngati ndi awawa bwanji tagwirani Kaye ndevu zamwaiyu Kaye akuomeka kt ndiameneu wa bakili muluzi
Mbambande guys,mukuimililadi anthu a kumudzi Shure,big up.
Chizukulu chananja I can confirm ndindani zilingat akamat kamajekete😆😆😆
Brian ndiwe pangolini, when you are with these guys amayankhula fundo kamba ka mafunso anu Mr Brian!😅
Kumkuyu umayakha zosaveka galu iwe.... anthu akupangitsawo osawachotsa tchito bwanji...?
Mesa mumkazi musitha zithu agalu Inu...
Ayi guys abomawatu chilipo ndichakuti akusowetsa dara mafuta chifukwa kalembela wa chisankho wayambirila ku mwera akangoyamba ku kulembetsa achigawo cha pakati mudzaonanso mafuta ngabwingabwi zimenezo amalawi ndiye musunge
Madoras amatha ndimaulendo a president osati kugura magalimoto kokha ai komansotu magalimoto ndi amene akubweresa ndalama ku M R A coz galimoto imozi imatha kulipira custom 30 million koma ndalamazi sizikugwirisidwa ntchito bwino bwanji osafusa anzowo kuti amaziyendesa bwanji zinthuzi.
U Guys munabwera kudzakhala Ku Malawi Ulemu Wanu Mumayitha
Dziko likulamulidwa ndi makawadi zitsiru akuziwa zomwe akuchita
Akulu akulu inu mukwana pa Times tv. Chakwera ndi munthu olephera ndipo mulibe utsogoleri. Mbuzi yeniyeni.
Ulamuliro opanda matso phenya, ulamuliro wongoziwa kulakhula pa ground bas 😢
Abusa alemedwa akusowa madola kom alinazo zopitila kunja zilipo 😂😂😂
Kkkkkkk l can confirm oh yes Malawi wafika pa mwana wakana phala
Ndiye echina boma nilomweri mkumati wa bakili muluzi tv amanama mzimenezi ma guys inuyo pitilizani mmatsekula mmanso amalawi
Network olo ku mpira ilipo
More 🔥 fire guys mumatha 💪💪💪💪
tiyankhulileni ndithu guys m'ma officemo sizikuyendadi aganizire anthu plz
Auzeni zoona asamangoti noma ndilomwari
Boma losamva chisoni ndi anthu Ake omwe tinawaika pampando. Zafika posauzana. Kukhala pa filling station ngati tiri Kukalandira zakudya pa que
very bad indeed
Mulungu anawachotsera mzeru anthu amenewa
Together with wedson Chiwoko It's me Rajab Bonomali Watching from south africa Eastern Cape❤
Koma people you can talk...indeed chilungamo chimachotsa mantha
Is not like neglegence is arrogance thinking that they r on top forgetting that that nobody's seperior than the community
Y the top dont knw hw to blame those behind him? If he doesn't knw hw can he lead?
Network sabwerekana.😊
Simukulakwa a brian
Kachaje and kumkuyu akanaima kaye pa ntchito zawo coz ananamiza a malawi pa za mafuta a galimoto
Koma zinthu sizilibwino adindo plz chitaponi kanthu
A MBTS alephera kubwera ku xool kwathu kuzatenga magaz ati disel alibe zoona izi ?
Kodi ku ministry of energy ku kuli PS??
Waoh kukamba mosambisa zizitero amalawi
Chikangawayu kupha kugwetsa sakuonapo bvuto koma. Za mafutadzi ndie kupha kutani???? Ndiudzeniko a Kachaje
Ku dedza tikumatha 3days tili podikira mafuta
Anthuwa atipha because kuli njala maluzi mafuta kulibe
Kodi ku UNGA KUJA ANA ONONGA MA US DOLLARS NANGA SAMKADZIWA KUTI KULI NGONGOLE YAMAFUTA ASANAPITE KU UNGA.NAGA MA US DOLLAR AKU OPITANA KU UGA ANAWATENGA KUTI? KODI MALAWI YAPONDULAKO NDIUNGA KULEKANA NDI MAFUTA
Abale tiyeni tichotse chakwera ndi anzake achoke watiwonongera dziko tikamulora kuti asokoneze zisankho mulungu atikantha kwambiri
Komatu ndevu zamwayi😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🎉
Your falling but kukakamilaa udindoo!
Achina chikangwa kkkkkk
Wozasiya kulangula mulimu dimokalasi andu akufutika kwambiri
Kodi president ngati ali wakuba angakhwimitse bwanji malamulo chakwera ndi idiot ndipo since I was born sindinawone chidzete chamunthu ngati chakwera
Uku ndikuwapangira campaign a opposition
Ndiko kudyako Mr nsima
Bvuto la bomali zimene amalangizidwa amazitaya asanazimvesese and mubaibulo muli mawu onena kuti ena saziwa kuti saziwa mzeru za yekha anaviika msima m, mazi
Powerful gays
Koma ngambwingabwi alikuti
Zikafika apa President amasiya pansi usinado akakhala Olikonda dziko kake
❤❤❤❤❤❤
Mwarakwisa mkanawafusa kut Kodi nanu anduna Moti galimoto anu alibeso mafuta??
koma azibambo awawa akuti I can confirm kudalibe kaya akunena ndani kaya ,am failing to ques 😂😂
Abulayani komaso andefuzamwai komaso azukulusi futondi achakwela zasiwa chirichose anangotenga boma koma zamasiwa kandu
Misonkho ikupita kut and maiko akunja amanthandiza mumatiuza ahhh
Koma Chakwera ndi nduna zako aaaaa mwelephera
Too bad for Malawi,poor planning,poor implementation, poor organisation.please take advice from your friends u people.
Maudindo enayo lembani a zungu, kuti zinthu ziziyenda bwino
Guys mumatiyimilira kkkkk nde adziti boma ndilomweri za ziii kkk
Thanks guys for talking this story ❤
Zina ndi mbuzi
B0ma ndilomweli basi kkkkk
Kwanu mafuta alipo
😂😂😂😂😂 km azibambo awawa mmmm mumakwana guys ntchito mukugwira kwambiri
Koma ndaseka nsima mpaka pa kabaza 😂😂😂😂
Ma guys amayitha, ndipo sabakira
Ɓòma ili lationetsa mbonà oña
Anthu olembela panya pawo
Azanu akamati MCP siyabwino inu mkuti boma ndilomweli muva bebe ngat simuchosa uyu
Live from joburg
Muli busy kuba ndalama za amphawi basi.....
That is the results of kugwetsa Kwa ndalama yathu kumeneko who is benefits now about this stupidity Mr president tikufuna mayakho
OK
Tulutsanika mafutawo alikuti nanga
Mcp mcp mcp ndanena kangat please tulan pas udindo mwKanik
Tikuyendela mafuta a mu jumbo(walk man)
Poor my malawi
Apa mpomwe mbudzi zonse zosapota mcp zazindikira kuti zinakwera yakuphwaa!!!
Dzikoli likunka kuti
Game ya mafuta siyamakape,
Boma ndilomweli,
Anyamata tokotani makape onse aku Mera apakile azipita akutinyasa palibe chimene akuchita maka amene ali incharge achoke walephera
Ndiye wina avekere boma ndilomweli aaaaaa zachaba, MCP park and go 2025.its government without a leader!.
Boma losava chison nd anthu ovutika ngt ife boma lankhaza ili tiona 2025 tichosa boma ili take my words kwasala miyez yochepa
pepani ku times akulu akulu adadi salipachongolelo why cant u guyz continues speak about chikangawayo chifukwa it's the man who is in front seat
Msiska wakwiya kwambir. indeed they're failing😂😂😂😂😂😂😂😂 kma boma nd lomweli
Kpma azibambo inu mumayitha kwambiri. Wakumva akumva.
Mwana akalirila nyanga ya nsasi musile imufotere yekha
There's no need for you guys to apologize what ever you are saying nd ma facts okha okha😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 sakuchoka Chakwera Dan Lu song😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Network ya achakwera ndiyaku assemblers of God ndi ku chipiku stores very useless one