The DC ndimakunyadirani ndipo l love you ndimakunyadirani Mr karindo usazafe murungu azikusunga ndimoyo wautari ndipo Adani wose murungu wakanthe tikupemphera ndithu
Kodi paliso kudikilaso 2 wks Mesa ayankhilatu dzana lomwelija amecwo akuyenera kulowa. Kunsewu basi changuchangu namalomba ndi achabare ako azipani zinazo workup please mupange machawi izi sizolekerela this is main issue for Malawian to sortout
Chakwera zimene amaziwa iye ndi kupha athu basi sanayambire pano anayambira ku church kupha anapha mbuza nzake kuti iye atenge usogoreli zinatheka pano mukuona ndi athu akuphedwawa Athu 9 aja chakwera Sadic Mia chakwera Lafu Kasambala chakwera ndi ena amene sitikuwaziwa chakwera yenweyo Ndiye crocodile usamaone ngati dziko ndilakwanu iweyo uchoke
The DC ,,,,bakili muluzi TV and Mr Namiwa you're true fighter ❤❤❤❤❤❤
The first one to view ❤ Dangerous Child
The DC ndimakunyadirani ndipo l love you ndimakunyadirani Mr karindo usazafe murungu azikusunga ndimoyo wautari ndipo Adani wose murungu wakanthe tikupemphera ndithu
Freedom fighter the DC ♥️
Bon Kalindo The courageous man ❤❤❤❤
Timakunyadirani kwambiri mumatiyimilira a Pre athu ambuye azingopitiliza kukupatsani moyo komaso kukuchotserani mantha💞🙏🙏
Ndimakunyadikani Mr the DC
Big build up the DC we love you so much
Ndipo inuyo a DC and namiwa mulungu azinkhala nanu
mbambande the DC msogoleli yekhayo woyamba wanthu osauka muno mmalawi muno
The DC ulemu wanu, chakwera anabwera kudzapha di anthu
Kuliza mulandu kwa bungee la mec pa nkhani kalembera zikutanthauza kuti chair person WA mec atule pansi udindo chifukwa sakuziwa malamulo
The man from Allah....The DC come please rescue us
Kodi paliso kudikilaso 2 wks Mesa ayankhilatu dzana lomwelija amecwo akuyenera kulowa. Kunsewu basi changuchangu namalomba ndi achabare ako azipani zinazo workup please mupange machawi izi sizolekerela this is main issue for Malawian to sortout
Zoonadi comrade malawi wanukha.
Timakunyadiran a president athu inuyo ndi one mumakwana inuyo❤❤❤
Tilibe president kumalawi koma tili ndi mbava yayikulu kapena chigawenga chooopsa kumalawi
Iwetu ka lindo ndimakukonda chifukwa suwopa
Chakwera anabwera kuzapha anthu n not kuyendetsa dziko ndipo mademowo tipange ndthu,,, osaopa osafooka osatopa 🔥
Salute DC
kulankhula mwachindunji kodi bwana DC chimachitika ndi chiyani kuti akati tipange ma demo imapezeka kuti 2 mits imapezeka zarephereka kodi chimachitika ndiyani bwana please menyani nkhondo bwana kuti mademo asarephereke please
Mr kalindo your so specil big up
Mkazi ameneyi 😂😂 oyendetsa zaMEC apha anthu
Kkkkkkkkkk koma inuuuu
M'matimilila bwana kalindo
Mwana oopsa kwambiri auze dziko silamao ili 😢
Ndipo,, sono akalesa anjinga yamoto adya Chan poti amapanga business kt adye pakhomo pawo kkkkkk km kt muwalembe ntchito mukukanika munthu apange business mukukanisa ndinu zisilu bwanji 😂😂😂😂
The Dc❤❤❤
Eeeeee zafika povuta zedi.kalindo timenyeleni khondo zafika povuta zedi
iweyo umatha suchulusa nkhan umangoponya zofunikazo uremu wako
Mukuona, ngakhale a Katolika mukuwaona akulongolola? Angoti ziii chifukwa akulandira ndalama mtseri,atsogoleri akulandira ndalama mtseri,a PAC amazuzula mtsogoleri yemwe sakuwapatsa ndalama ngakhale mtsogoleriyo akuyendetsa bwino alibenazo ntchito.
Chakwera zimene amaziwa iye ndi kupha athu basi sanayambire pano anayambira ku church kupha anapha mbuza nzake kuti iye atenge usogoreli zinatheka pano mukuona ndi athu akuphedwawa
Athu 9 aja chakwera
Sadic Mia chakwera
Lafu Kasambala chakwera ndi ena amene sitikuwaziwa chakwera yenweyo
Ndiye crocodile usamaone ngati dziko ndilakwanu iweyo uchoke
Kkkkk ati osamugwila ndikumukhudumula eeeeeeh
Mlungu akudarisen abon mmatiyimirira amalawi
Number 1
Mau mau
The DC🔥🔥🔥🔥🔥
😂😂😂😂😂. 𝐂𝐇𝐀𝐊𝐖𝐄𝐋𝐀 𝐖𝐚𝐛𝐰𝐞𝐥𝐚𝐚 𝐤𝐮𝐳𝐚𝐩𝐡𝐚𝐚 𝐚𝐧𝐭𝐡𝐮𝐮𝐮
Zodiac yinasocera
Makwana a Dc
The DC!
The DC
Koma bon kalindo phone yako imatha moto??😂😂😂
Ndipo where is he getting the energy to continue moving around abale.
This guy mmmmm no
Akuti waposa tsiku transport kkkkkkkkkk
😂😂😂😂 agaru.afiti.satanic ziko silamanu eeeee the DC hahahsh
𝐊𝐀𝐋𝐈𝐍𝐃𝐎 𝐮𝐦𝐚𝐤𝐰𝐚𝐧𝐚𝐚 𝐢𝐰𝐞𝐲𝐨 𝐧𝐝 𝟏