HOT CURRENT YAKALE YABWELERA KULI KUYANKHULA KOSAMUNYENGELERA MUNTHU |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 6 июл 2024

Комментарии • 30

  • @user-sy3fz5nz3v
    @user-sy3fz5nz3v 26 дней назад +4

    Keep it up Guys don't give up tell them the truth you do we all know it, more fire 🔥🔥🔥

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 25 дней назад

    Apapa nde mwabwera guys mooo fire 🔥🔥🔥

  • @user-sy3fz5nz3v
    @user-sy3fz5nz3v 26 дней назад +2

    I'm listening you from Sandton SA i love you Guys ❤❤

  • @user-sh5wq4uf6r
    @user-sh5wq4uf6r 26 дней назад +2

    Keep it up mall 🔥🔥 osaopa

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 25 дней назад

    Good

  • @wilisonbornface4282
    @wilisonbornface4282 25 дней назад

    Live from south Africa cape town

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e 26 дней назад +2

    Kuyankhula chilungamo mosawopa aliyese kapena udindo kunali anzao anachoka ndiye akumapanga kuti anthu aziwagwadila ngati Mulungu nthai imeneyo inatha ndi kamudzu Chihana anadigulila ufulu RIP Chihana

  • @user-rz9rm4cb8x
    @user-rz9rm4cb8x 25 дней назад

    🔥 🔥

  • @SteveChapola
    @SteveChapola 25 дней назад +1

    Iwo koma kupha azawo basi ndi kuika paulemerero abaleawo

  • @DoreenEmmanuelj
    @DoreenEmmanuelj 26 дней назад

    Choonadi Ichi osabwerera mmbuyo pa chirungamo ❤

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel 25 дней назад

    Mwayamba kusoweka zelu anthu inu

  • @Kamwachale
    @Kamwachale 25 дней назад

    Analysis tells that only Bingu did a lot of developments within 8 years. Look and sample out at what Bingu did in Mzuzu, Lilongwe and Blantyre, No president will ever bit him. Another analysis is looking at the background of each president. So far we have 3 presidents who have never stayed abroad for many years this Muluzi, Joyce Banda and Chakwera. The other 3, Kamuzu, Bingu and Peter. Looking at these two categories and follow the type of presidency, the analysis shows that those who stayed abroad had a passion to develop Malawi whereas the other 3 had a passion to make themselves rich and it is very evident.

  • @wilisonbornface4282
    @wilisonbornface4282 25 дней назад

    Ife programyi imativesa kukoma osawopa ay abwera liti amenewo kt anthu azichita matha

  • @robertm.aganizani8463
    @robertm.aganizani8463 24 дня назад

    Koma ma guys inuyo. But i like the truth shared if only listenned to

  • @NumbDee
    @NumbDee 26 дней назад

    Big up

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli 26 дней назад

    More fire guys tiyenazoni zimakape zimenezi kuti mwaaaaaaaaaaaaaaa kkkkkkkkkk ayi zikomo

  • @user-ii2sh1mz3r
    @user-ii2sh1mz3r 26 дней назад

    Yowoyani wanangwa wanthu awa wakhumbikwa unenesko, especially ma MPs , ma ministers awa kukomezga Kuti chitukuko chikuchitika Mmmmm, pa campaign wakwiza mwakuweya ngeti mbaweme kweni khale Waka pampando wayamba kuofwa wanthu

  • @user-oq5rg5mz7q
    @user-oq5rg5mz7q 26 дней назад

    ❤❤

  • @ChawasoMlotha-ys6bf
    @ChawasoMlotha-ys6bf 21 день назад

    Keep it hot,

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np 25 дней назад

    Ambuye akudalitseni kwambili poyankhula chilungamo choncho

  • @DoreenEmmanuelj
    @DoreenEmmanuelj 26 дней назад

    😂😂😂😂nyazi palibe eti kkkk

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 25 дней назад

    Koma mwang'alura guys

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 25 дней назад

    Inuyo muzinenadi aaaaaah.....kodi andalewa ndi anthu komaaaa???

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita 25 дней назад

    boma la mcp palibe chomwe lapanga koma kubweletsa umphawi wadzaoneni akapume amenewa atikwana

  • @SteveKanongwa
    @SteveKanongwa 25 дней назад

    Koma maguy awawa amatha

  • @SteveChapola
    @SteveChapola 25 дней назад

    Awa alephera koma kupha azao

  • @user-hb2hr5oc9l
    @user-hb2hr5oc9l 26 дней назад

    Katangale Kuti anthe Malawi yese okuba akaziwika Kuti waba azinkhala kundende Moyo onse Kaya president waba amangidwe anthu aziopa Kuba

  • @user-el1fr5hn3g
    @user-el1fr5hn3g 26 дней назад

    Please guy's more and more fear no one

  • @SteveChapola
    @SteveChapola 25 дней назад

    Mcp faya