DPP YATI MA MP AWA AKUYENERA NTCHITO YAWO ITHETSEDWE NGATI MA MEMBALA ANYUMBA YA MALAMULO |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 2 июл 2024

Комментарии • 38

  • @ThomasElijah-sg2hb
    @ThomasElijah-sg2hb 27 дней назад

    Kom DPP imayenera kungochimva ,,, osat kulimbananso

  • @JunaKananji
    @JunaKananji Месяц назад +2

    Amarawi akundikirira inua Dpp ooyeeee

  • @ActedLubakati
    @ActedLubakati 28 дней назад

    Akuyenera kuchosedwa chifukwa akanafuna kulowa M C P akanalowa b4 chisankho chapita pamenepo akuputsitsa dziko

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 29 дней назад +1

    Some laws in Malawi seem to be invalid. Is section 65 really abided in the parliament? It was only Hon.late JZU Tembo the political hero who validated this law.May his soul RIP

  • @danmbuzi
    @danmbuzi 29 дней назад

    Bola asasokoneza athu ena kupita nawo ku mcp please the must go the self not with others

  • @LiamChitsulo
    @LiamChitsulo 22 дня назад

    Joyce chitsulo usakane ayi iweyo akupotoza adausi koma waila momwe timavutikilamu muja kuti uwine sorry uzatifuna

  • @spargomw
    @spargomw 29 дней назад

    Achita bwino kuwachotsa, alondole mbuzi zizawo zija😂😂😂 Peter nd oganiza bho safuna zachibwana.

  • @lazaruschitsamba8394
    @lazaruschitsamba8394 29 дней назад

    🎉ndiye muwina bwanji politics is the game of numbers ndinu mbuli yeti bwanji kuchotsa antu muluza chifukwa changondo mayambitsa ngondo ina

  • @Sugerman-tw4do
    @Sugerman-tw4do 19 дней назад

    A choke

  • @PeterThomas-lw3io
    @PeterThomas-lw3io 29 дней назад

    We don't need alyance
    Again we need to change a better president

  • @JunaKananji
    @JunaKananji Месяц назад

    Dpp🤔💪💪😍😍apatu ndiyemwazukanotu

  • @DanielLekitala
    @DanielLekitala 28 дней назад

    Akuyenera kuchotsedwa chifukwa athuwa Ari Madera achewa Komaso awonetsa zatsakho lá choramura ndilhera lamuro ligwire nchito basi

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet 29 дней назад

    Washoke nadi

  • @Amina786Wayson
    @Amina786Wayson 23 дня назад

    Achosedwe basi amenewo

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Месяц назад

    Joyce chitsuro ndiwa mcp to be honest achoke kumene

  • @KhatweebDickson
    @KhatweebDickson 27 дней назад

    asiyeni akakhale kuchipani chokuphacho osalimbana nawo dpp 2025 bomaaaaaaaaa

  • @Bonisiwentamo
    @Bonisiwentamo Месяц назад

    AChoke chifukwa tinawasangha kuzela chipani chomwe akutuluka, athu amenewo angosatila komwe azipeza chuma okha bas

  • @user-xc1gk6bw6m
    @user-xc1gk6bw6m 29 дней назад

    DPP 2025 BOMA ❤❤❤❤

  • @KulinjiGoodsonnkhoma
    @KulinjiGoodsonnkhoma 29 дней назад

    Aliyense azayime payekha akalephelana ndiye azizapanga zagwilizanozo

  • @user-dv6wy1sq8g
    @user-dv6wy1sq8g 29 дней назад

    A DPP sazatheka osangokhalabwanji

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 29 дней назад

    Mukatha kuchotsa ma mp wo mudzuke mupange ZOKUPYA CHONDE PLEASE

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d 29 дней назад

    Azivaya anthu akupha

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d 29 дней назад

    Agalu mbava azipita ku mcp konko mbuzi

  • @HaliJana
    @HaliJana Месяц назад

    MUMUUZE CHAKWERA KUTI AWAPHE MWA LUSO MUJA ONSEO 4 NDI ADYELA GWILA TCHITO YAKO CHAKWERA AZIMISE

  • @ShadNkhoma-ju2kn
    @ShadNkhoma-ju2kn 29 дней назад

    Malawi akuvutika koma Nkhani zikhale zokangana basi zazipani basi koma Malawi ee ee tikadali kuvutika

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Месяц назад

    DPP ndi mbambande imadana ndiopepera zedi

  • @joaquegerman2250
    @joaquegerman2250 Месяц назад

    Achoke apite. Kuchipani chokuphacho

  • @user-yv3jp3it2t
    @user-yv3jp3it2t 29 дней назад

    Mp ngati wakomedwa ndi ndalama za MCP achosedwe Basi coz amapanga zithu zoti lamulo lake akulidziwa tikudziwa kuti ma mp amenewo analandila ndalama zokwana 50 million kwacha

  • @KennedyChitunda
    @KennedyChitunda 29 дней назад

    Yakwiya ndi mizimu

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m 29 дней назад

    achoke bass Mesa ampwanya lamolo

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Месяц назад

    DPP INABWERA KUZAKHALA, APM FATHER OF MALAWI ❤❤❤❤

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 Месяц назад

    Mp opusa ife sitikuwafuna,azipita ku ng'onazo😂

  • @EmmanuelChirwa-z3n
    @EmmanuelChirwa-z3n 29 дней назад

    Zopusa basi bwanji sanachosedwe pa u president mukulu wake atachoka ku udf

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft Месяц назад

    Dpp 2025 Bomaaaaa

  • @MustapherLino
    @MustapherLino Месяц назад +2

    Dpp ndi chipani chodzindikira

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td 29 дней назад

    Koma mbuzi Zina DPP Ina bwera kudzakhala KO tsutsa visiyeni MCP tengani mp onse amenewo Komanso lamuro lija la two years lija MCP ikanaimitsa Kaye kumenekumso malamuro ankhwima 2025 kuli mbola

  • @user-vp2he3ly5d
    @user-vp2he3ly5d 29 дней назад

    Akudziwa kuti ku mcp akaruza

  • @joaquegerman2250
    @joaquegerman2250 Месяц назад

    Achoke apite. Kuchipani chokuphacho