ACHAKWERA AWAPANA KUTI ATULUTSE REPORT YA NDEGE |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 20 окт 2024

Комментарии • 83

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 2 месяца назад +5

    Good Message Dziwe TV

  • @Fridayasani
    @Fridayasani 2 месяца назад +6

    Wakupa ndiyemweyo chakwelayo awawudza andu bwanji 😭😭😭😭 mulungu akulanga Santana iwe

  • @JohnKatiko-no6yn
    @JohnKatiko-no6yn 2 месяца назад +3

    A Malawi akuyenera kumpatsa Chakwera masiku osapitilira 10 kuti akhale atapereka lipoti ndipo akapanda kutero, mdziko muno mukuyenera kuchitika ma DEMO okakamiza Chakwera kuturutsa lipoti.
    Limpopo Fm yalengezanso kuti kuomberedwa kwa nsilikali ku Zomba barracks kuja idali plot yochokera kwa anyamsta a ku STATE HOUSE.
    DZIKOLI NDILANTHU A MALAWI.
    Tikulamulidwa ndi chipani cha magazi mudziko muno.
    Tipempgere kwambiri Ambuye atiturutse mu dziko lino la Farao.

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 2 месяца назад +3

    Apa ndiye mwadziwikatu mukubisilanji hehehe mwabisara mu kholowa 😂

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 месяца назад +2

    Dr chikangawa ife musawone ngati tiliphee ngati tayiwala ife tikudikira iwe Dr chikangawa uwona zomwe zinameta chona mchira

  • @VladimirThagreat
    @VladimirThagreat 2 месяца назад +1

    Mmesa anapha chilima ndi emweyi machende ake

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko 2 месяца назад +5

    Chikangawayo akuyenera aturuse lipoti mwangu

  • @HaliJana
    @HaliJana 2 месяца назад +3

    UMENEO NDI UMBONI OTI ANAPHADI ANTHU CHAKWERA,UNBONIO NDI WAKE ALENGEZA BWANJI?

  • @violetpotani
    @violetpotani 2 месяца назад

    Eeeeish koma Malawi wafika potopetsa bodza mmm😅

  • @trifoniachilunda6263
    @trifoniachilunda6263 2 месяца назад

    Mr chikangawa ndiye anapha

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 2 месяца назад

    Chakwera watchera kumwezi nkhanga zaona.iye amaona ngati ndiwochenjera koma apapa ndiye wapezeka.akufuna kumpasa deadline 10 days kuti amalawi awapasire report la ngozi ya ndege gulukunyinda ameneyo Dr chikangawa

  • @innocentkandulu2825
    @innocentkandulu2825 2 месяца назад

    akuziwapo kanthu

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 2 месяца назад

    Chaka chake ndichino chakwera azimangilira ku tomato kamba kakupanika kkkkk

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 2 месяца назад

    Good message

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Месяц назад

    Okupha sangaziulule yekha pabwalo lamulandu ,
    Chodziwika komanso mosachosela , Saulos Cláuds Chilima anachita kunyongedwa,aphelana udindo

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 2 месяца назад +2

    boma la zigawenga zokha zokha atulutse lipoti akubisa chani iye ayaluka timudula mapwala chakwera chaka chake ndichino

  • @KyleAdams-o3y
    @KyleAdams-o3y 2 месяца назад

    Ife tikudikilatu chilungamo kwa iweyo chikangawa😢😢

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 2 месяца назад +1

    Koma zingatheke wakupha udziulula kuti ndinedi .
    Chikangawa chakwera kaya ngati angatiuze koma tili ufunadi ripoti

    • @MercyChipeta-h4d
      @MercyChipeta-h4d 2 месяца назад

      Ngati sangawerenge report lo basi apase mkulu wa asilikali awuluse report, mesa iyeyo akuchita mantha

  • @imraanJafal
    @imraanJafal 2 месяца назад +1

    Kkkk chikangawa akuziwa bwino lomwe yeyo

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 2 месяца назад +1

    Ayakhe amenewo achikangawawo 😂😂😂😂

  • @OsmanGift-f4p
    @OsmanGift-f4p 2 месяца назад

    This is truth akuyenela kuti ayangule 😢

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 месяца назад

    Kukhala cheteko ndi chitsimikizo choti akudziwa po kanthu president wa dziko ndamene akanakhala oyambirira kutiero koma akuti asankha kukhala chete, nde anthu tingakhulupirile bwanji?

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani 2 месяца назад

    😂😂😂 adalengeza bwanji ndege Itasowa?

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka 2 месяца назад

    Atulutse lipoti akubisa bwaniji pomwe ma Germany ananena,Lazaro akudziwapo kanthu kuti iyeyo ndiyemwe anapanga chiwembucho.black box ilikunyumba kwakeko

  • @CastenkWhite-fr4ne
    @CastenkWhite-fr4ne 2 месяца назад

    Samgatulutse mfiti mulumgu achite naye😮

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 2 месяца назад

    Liwuzeni dziko chilungamo than kumangokhala chete

  • @DumisanPhiri
    @DumisanPhiri 2 месяца назад

    Inde ndizowona atuluse liport tilimve

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 2 месяца назад

    Akusowa poyambira kuti anama motani, anapha yekha galu uyu.

  • @ThumbikoChipofya
    @ThumbikoChipofya 2 месяца назад

    Report ya imfa ya Bingu ,JB sanachedwetse Koma iyi ikuvuta pat?

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 2 месяца назад

    Give him time to meditate on that iissue.It's a very crucial bone of contention.However,he is here in the North accost him democratically to divulge what transpired.It is more than a grief to lose nine Malawians without knowing the apparent cause of the demise.

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 2 месяца назад

    Eni anthu anamwalira aja ndi apule amafunika ku pepesedwa ndani?

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 2 месяца назад

    Awulula bwanji alipo malizasimo cnanga iwowo akuziwa kale 😂😂😂😂😂 alibisa cz chani asadandawule atiwuze basi amenewo asachedweso akubisa chani nanga 😂😂😂😂

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no 2 месяца назад

    Tsono ngakhale muwakakamize adzuka akufawo ?

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 2 месяца назад

    Bro chakwera ndi munthu oipa kupha zake chifukwa cha 5 year's anzalowe wina kd mavoti achaka chamawa chakwera adzabela km kuti kuvotedwe bwino kutali dzangawine chifukwa moyo umene adaphanga pompha zache

  • @HildaSingin-vm2tr
    @HildaSingin-vm2tr 2 месяца назад

    Apasidwe 10 days imeneyo ngati sathero asiye undindo pasi munthu osakonda anthu ake

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 2 месяца назад

    Ndipo ife tikudikila asakhale chete Amalawi akuyembekezera ndipo akuyenera kupita pa malo amene Chilima anafera

  • @CharlesBanda-kv8bh
    @CharlesBanda-kv8bh 2 месяца назад

    Report yofufuza wins amatulutsanso ndiwina.. umbuli eti mbuzi yamunthu ikufuna Report kwamunthu emwe sikumukhudza

  • @ManninLongwe
    @ManninLongwe 2 месяца назад

    Naye ndiufulu wake

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela 2 месяца назад

    Ayankhe abwanawo zaphinja pa khosi

  • @sanlakedickson6780
    @sanlakedickson6780 2 месяца назад

    anthu aku Israel Aja amakatani ku Malawi mr chikangawa plz report muzituluse nokha apa

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 2 месяца назад

    Anthu awa sazatheka bodza lalowa mmagazi mwawo ndipo sakunda dziko lokhala lawo.

  • @emmanueljelemani4203
    @emmanueljelemani4203 2 месяца назад

    WE NEED A REPORT

  • @LingstoneLing
    @LingstoneLing Месяц назад

    Chakwera walikukoma chilima kwene nawe ufwenge no matter what you will go to dei , you will stay longer but the day is coming

  • @mastonmacford-l7k
    @mastonmacford-l7k 2 месяца назад

    zachison liport atulutse maina amene akumutchula mtsogoleli ife tikuchita manyazi monga amalawi lituluke basi

  • @charlesmasauko4651
    @charlesmasauko4651 2 месяца назад

    Report Silituluka chifukwa zinali zochita kukonza. Mwachidule achakwera ndiwo anakonza kuti ngoziyi ichitike.

  • @VanessaAlinafe
    @VanessaAlinafe 2 месяца назад

    Ngati akukana kupeleka report ndiyekuti akudziwapo kanthu koma akunama amati chouluka chimauluka koma sikulina chizatera

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 2 месяца назад

    A Lazarus Chakwerawa akuzolowera pajatu za Sattar Gate iwowatu anali mugulu lomweelo lakubalo ndalama za a Malawi ; inatero utube channel .kuti iwo ndi nduna zao zonse ku parliament .anadya nao. Ndi Sattar yu Anapeza umbavau linali boma mdziko la Britain .koma iwowa anangomupana Saulos chilima yekha kuti chilima anali mbava .koma iwo ndi anzawo onse anadzibisa. Pano ndi apa akubisanso report ya ngozi ya ndege .report from German investigators ..😮😮😮 iwowa aulule nkhani zonse za Sattar Gate kuti anali involved ndi a ndani. Ndipo chilima amuoheranji pangozi ya ndege

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 2 месяца назад

    Akubisilanji report, choncho anthu akamati chakwera akuziwapo kanthu ena ndikumakana

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 2 месяца назад

    Kukhala maiko ena president wa malawi' anthu akadakhala,ataiwala,zoti tidali ndi president ochedwa chakwela.koma, malawi' kaya tinaputsa, bwanji.taonani, anyamata ndi atsikana'aku Kenya Uganda Nigeria, koma kuno tingolidza konono koma kuziwa FB basi.kumangolongolola, kumeneko.

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 2 месяца назад

    Sangatulutse iwo Ali gulu lomwelo.

  • @RuthTimothyChirwa
    @RuthTimothyChirwa 2 месяца назад

    😢😢😢😢

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 2 месяца назад

    Kodi akuopa chani kuwauza anthu kuti dzinakhala bwanji ifetu tikudikila kuti tinve

  • @inamrigala
    @inamrigala 2 месяца назад +1

    Nyawu yajala kwambili

  • @PriscaMwarhinyu-px9bk
    @PriscaMwarhinyu-px9bk 2 месяца назад

    Asakha kukhala chete bwanji

  • @CHAMMELLEONE
    @CHAMMELLEONE 2 месяца назад +1

    😢

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 2 месяца назад

    Kodi ngt chikangawa satulusa report nde atulutse mndani
    Apatse anthu ena atiuze...akudziwa kut ali mu report lomwelo
    Mfiti ys munthu

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 2 месяца назад

    Palibe kusankha kukhala chete akuthawa nkhani yopeleka report abwana mulimva kuwawa dziko

  • @AnnaPhiri-b8t
    @AnnaPhiri-b8t 2 месяца назад

    Naenso azapselera wamoyo

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 2 месяца назад

    Manipulator... Silent killer.. chakwela inuso muzamwalila either you like it or not...

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 2 месяца назад

    Report perekani a MCP mesa mukati ndingozi

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 2 месяца назад

    Chakwela adapha chilima

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 2 месяца назад

    Chakwela machende ako iwe mbolo yosadulayo big

  • @FrancisMazamba
    @FrancisMazamba 2 месяца назад

    Wakupha chakwera

  • @feehasaidid.r.d
    @feehasaidid.r.d 2 месяца назад

    Plani imeneyi sikuti bozalo sabwelanalo ayi

  • @sanlakedickson6780
    @sanlakedickson6780 2 месяца назад

    ayankhe wasankha chete ife sitikufuna ayankhe by force chimapha Dala

  • @MarthaBango
    @MarthaBango 2 месяца назад

    😂😂😂😂

  • @SueWahna
    @SueWahna 2 месяца назад

    Akabisa report ndiye kut akuzowapo kathu akanakhala kut sakuziwa kathu akadawulusa kale kale

  • @MrsNankhumwa
    @MrsNankhumwa 2 месяца назад

    Sikusinja

  • @Elson-cf1gy
    @Elson-cf1gy 2 месяца назад

    Mapwalaake chakwela

  • @amoschisisi2070
    @amoschisisi2070 2 месяца назад

    Mbolo yake Chakwera

  • @EsawoChristopher
    @EsawoChristopher 2 месяца назад

    Wakupha uyu

  • @SamsonFole
    @SamsonFole 2 месяца назад

    Too bad

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад

    A bamusi ndiye ndaniso asaaa MCP boma

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад

    Timadya ndenge ife zachamba eti

    • @YamikaniPrince
      @YamikaniPrince 2 месяца назад

      Uzaziona abale ako atachitilidwa chiwembu

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад

    Tikufuna zitukuko osati za ndenge zatikwana

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 2 месяца назад

    Ndipo ife tikudikila asakhale chete Amalawi akuyembekezera ndipo akuyenera kupita pa malo amene Chilima anafera

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 2 месяца назад

    Ndipo ife tikudikila asakhale chete Amalawi akuyembekezera ndipo akuyenera kupita pa malo amene Chilima anafera

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 2 месяца назад

    Ndipo ife tikudikila asakhale chete Amalawi akuyembekezera ndipo akuyenera kupita pa malo amene Chilima anafera