MCP AITENGERA KU KHOTI OMWE SANAMALIZE ZAKA ZIWIRI MCHIPANICHI |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 2 июл 2024

Комментарии • 45

  • @AmosScott-z9x
    @AmosScott-z9x Месяц назад +6

    Osangochokako bwanji paja munanyelera kwina konse

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt Месяц назад +4

    Ife amalawi sitikufunaso kuti tizimva za manyi a chipani Cha mcp ndiyakupha chipani Cha tsoka chimenecho

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Месяц назад +3

    Chakwela anakhala zaka zingati kkkkk

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 29 дней назад +1

    Chakwera mwini wake anakhala president atangolowa mu chipani chonyansa cha MCPigs. Leroli akuti pathe kaye zaka ziwiri?😂😂😂

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r Месяц назад +3

    Change Golo akufuna kuchotsa Tambala Wakuda M'boma

  • @TisopeChagala
    @TisopeChagala Месяц назад +2

    Ken Msonda amene ndimamudziwa ine ndi ameneyo aline chilendo

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 29 дней назад

    Dzipitani kunyumba chakwera ndi gulu lake akuphani musiya ana paumasiye😢

  • @georgejim51
    @georgejim51 Месяц назад +1

    Atengereso Ku court khani ya imfa yachilima

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki Месяц назад +1

    We don't want mabodza criminal party in malawi again.

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 Месяц назад +1

    Kumkuyu ndiwe opusa zed chakuti chako ndi chakwera wakoyo muwaleselsnji anthu kuti apikisane nawo mbudzi

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Месяц назад

    MCP or alimbirane patokhala azawina???😂😂😂😂😂😂

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v Месяц назад +2

    Achina Msonda amaonangati atenga maudindo Ku MCP anthu adyera awa agalu

  • @azunguauskay4903
    @azunguauskay4903 Месяц назад +1

    Yakwiya ndi mizimu

  • @SteveBanda-wf8uq
    @SteveBanda-wf8uq 29 дней назад +1

    Chipani ichihashi chilowele tikuluza athu ofunikila okhaokha why , oimba andale athu wamba were guys sorry for Malawi

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 29 дней назад

    Aaaa mungofuna kuti mudye ndalama mwachita kupangana muziti atilipila pa nkhaniyi

  • @user-by6ky8qm8v
    @user-by6ky8qm8v Месяц назад

    It's pay back tsopano,mukuona ngati mzimu osalakwa mwachotsa uja mupeza nawo mtendere ai,inutu muziona mwangoyambapo

  • @hackwellkagolo6614
    @hackwellkagolo6614 Месяц назад

    Munali angelo khani za azanu aku DPP lero ndi inu sopano

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo Месяц назад

    Musawaphe chonde...

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms Месяц назад

    Zochitisa manyazi kwambiri zoona, I think achina malata nd mzake uja mosqueto

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk Месяц назад

    Skc influence

  • @user-fr3ge2hf6s
    @user-fr3ge2hf6s 29 дней назад

    Mufela kusata athuinu apanga bwino

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt Месяц назад

    Chipani Cha mcp Kodi chikukakamilabe kumazitchula amalawitu sakuziwa kuti mcp ikadali moyo idafatu

  • @user-ww9rj2wx8d
    @user-ww9rj2wx8d Месяц назад

    Zanu zimenezo komweko ziyambanani za usilu basi

  • @Kamwachale
    @Kamwachale Месяц назад

    Angolowa chipani anthuwa kufunsa maudindo basi. Why did they not join the party the last four years. MCP don't allow these fortune seekers, they have to complete their probation period.

  • @DylesMtenje
    @DylesMtenje Месяц назад

    Mcp iona chipan chakupha munya agalu inu
    9:00

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk Месяц назад +1

    Nthata zanjala

  • @andrewmandawalaphirithepillar
    @andrewmandawalaphirithepillar Месяц назад

    Achina Msonda ndi achina change golo anya nawo

  • @ahmedmsume1489
    @ahmedmsume1489 Месяц назад

    Eya 😂😂😂😂😂

  • @GloryMbale
    @GloryMbale Месяц назад

    Zangoyamba muona zosaona

  • @calvinjamal7117
    @calvinjamal7117 Месяц назад

    Mumva kuti wafaso ameneyo chipani cha mwazi ichi

  • @user-xd1cm7tm7t
    @user-xd1cm7tm7t Месяц назад

    Achenji golo ukut bwanji

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma Месяц назад

    Mcp sitikufuna kumaimvaso or dzinalo chipan chamwazi

  • @user-vl8uw8mc3u
    @user-vl8uw8mc3u Месяц назад

    Chipani cha mfiti

  • @LamieTiger
    @LamieTiger Месяц назад

    Apsotane dzen zen

  • @user-zx3pz2wy1j
    @user-zx3pz2wy1j Месяц назад

    Amkati atani aziwonatu amenewo.

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba Месяц назад

    Msonda amandiwaza bwanj 😂😂😂😂

  • @MarthaChisiza-jr9cg
    @MarthaChisiza-jr9cg Месяц назад

    😂😂😂😂

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana Месяц назад

    Adziphana okhaokha nde bwino 😂😂😂😂