Shehe uyuso wagagada ulariki wake mopanda mantha kusiya anthu akungoombera mmanja

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 5 июл 2024

Комментарии • 156

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b 5 дней назад +16

    Tayesedwa ndi president wakhaza chakwera ndie timupempha Allah kuti atichosele chakwelayo ameen

  • @HusseinAdamLidezo
    @HusseinAdamLidezo 5 дней назад +10

    Sheikhe ulaliki wanu siukugwilizana ndi ma aya omwe mumatulutsa pakamwa panu, uku ndikugulitsa mawu amulungu, ambuye akumvelen chison Ameen

    • @omardyman8083
      @omardyman8083 4 дня назад

      Analandila ndalama nkhani anaiyamba bwino kukasokoneza kumapeto zachamba

    • @rasulmaulidi2224
      @rasulmaulidi2224 3 дня назад

      zikomo kwambiri m'bale wanga ndimaganiza ngati ndindekha ndimaganiza choncho..ndikufuna number yake ndimuyankhule mwapadela ndi galu wamunthu uyu ali ndidyela simasewera akuyalutsa chisilamu

  • @abdulhameed7808
    @abdulhameed7808 5 дней назад +5

    Basi sitilankhula zambili tingokusungirani ulemu Sheikh Anthu.

  • @NenehMasanje
    @NenehMasanje 5 дней назад +12

    Sheikh mwadya now ndrama

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv 5 дней назад +3

    7:53 7:53 Chikangawa akupatsani million yinu zaziiiiii nkhanizanu
    Mayeselo aifa muyesa ife sitimaziwaaa,
    Nde imfazake zochita kumugwira munthu pakhosi mwadaladala , kumuombela mfuti mkamwa munthu ,kodi yinu mulankhulabwanj muli ndiwumunthuyinu ,aaa muzichotsela ulemu nokhatuyinu mwangotengana nonse odya ndalama zamagazibasi ,
    Afitiwo alimwetuuuu ati zikuyenda malawi wake utiyo amene mungamunamize lelo ,
    Azibusa muzichotsera ulemu nokha mwamva

  • @SulaimanaJames-b9v
    @SulaimanaJames-b9v 2 дня назад

    Maa Shaa Allah
    May Allah bless this message and make it beneficial

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 5 дней назад +3

    Wadya nawo ndalama zamagazi iwee, usatinamize asilamufe pamodzi ndi amalawife, ifenso ndife asilamutu, mayesero ukunena apawa simayesero ochokeraxkwa ALLAH, awa ndimayesero ochokera kwa satana kudzela kwa chizukulu tudzi chake chotchedwa chakwela ndi boma less lake 😂😂😂😂😂

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya 5 дней назад +3

    Odya ndalama zamagazi ngati akumasowa zoyankhula zawo? Allah mukunenayo akuyendereni Sheik😢

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 5 дней назад +2

    Ameen sheikh Allah ahead u. From Cape Town centre

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 5 дней назад +3

    Chemoto alipomwepo anapha ALLAN WITIKA, anapha chilima kuchikangawa 😂😂😂😂

  • @SteveriaZimba-qs1id
    @SteveriaZimba-qs1id 4 дня назад +1

    Amen and amen uthenga wamphavu ambuye alemekezeke ndipo akhululukire zochimwa zathu

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 4 дня назад +1

    Naam sheikh ma shaa Allah ulaliki wabwino ndithu ❤❤❤❤

  • @BrownMatonyola-xi3lb
    @BrownMatonyola-xi3lb 2 дня назад

    Mwadya zingati
    Aliyese wanyambita ndalama zoti azizilise za imfa yachilima ndikupepha Yehovah Mulungu wathu amuonetse kiyama akumane ndi mavuto

  • @FebbieMaulidi
    @FebbieMaulidi 5 дней назад +1

    God bless you sheik for unity message ❤

  • @SayidiIshmael
    @SayidiIshmael 3 дня назад

    ❤Allah give you more life and imaan to defending this deen

  • @IshaaakKango
    @IshaaakKango 2 дня назад

    Maashallah sheikh

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv 8 часов назад

    Aaaa sizomwezija Izi inu asheikh opanda manyazi ,
    Panja peni peni wadya ndalama Za Chikangawa uyu,
    Sali pachilungamo uyu

  • @muhmmadsarwer9527
    @muhmmadsarwer9527 3 дня назад

    Ameen thuma ameen Allah tichotseleni President ameneyu..ndipo tipatseni mtsogoleri wabwino mdziko mwathu muno

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 5 дней назад +1

    Mukufuna mutamike. M'nungu tam'nyekule ngulumbira une

  • @mosewallace9717
    @mosewallace9717 2 дня назад

    mweye che kuntamba 🔥🔥

  • @kekeaufi9834
    @kekeaufi9834 5 дней назад +2

    *WA ALYKUM SSALAAM WARAHAMATULLAHI WABARAKATUHU,,,,Inna lillah wa Inna ilayh rajoon*

  • @TWAIBAKBANIES
    @TWAIBAKBANIES 4 дня назад

    Ma vesi ali apa zili kutali tali . Aaaaaaa koma akulu akulu sheikh mudziima pachilungamo komanso ma ves osamawakhitetsa ai

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 4 дня назад

    Kkkkkkkkkkk wabodza ndiwe ma inovolopu yakutseka pakamwa ya chakwela, zikhale ndi kunkuyu 😂😂😂 waukape ndani sakudziwa.

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv 5 дней назад +1

    Sheikh awa salibwino akugulitsa mawu aMulungu ndi ntengo wotsika mukankhanthidwa mutsiku lomaliza

  • @AndersonTsoyo
    @AndersonTsoyo 15 часов назад

    100% shehe uthenga omanganga dziko

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f 2 дня назад

    Ili ndiye gulu loyitana chakwela ku Eid atawapasa mbia makwacha mashehe adyera ichoooo!

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 5 дней назад +1

    Usatiipisile Islam yathu iwe wamva , bwanji sukuwalesa makafiir omwe ulinawo pomwepowo kuti azikha okonda anzawo?

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv 5 дней назад +2

    Mwapatsidwa ndalama

  • @Macsaidi
    @Macsaidi 4 дня назад

    Komabe sitinganame pa chilungamo.
    Saulos Chilima anaphedwa ndi ndege ya boma la mcp

  • @omardyman8083
    @omardyman8083 4 дня назад

    Ndine msilamunso koma sheikh uyu wapochelaapo nkhani anaiyamba bwino kukasokoneza kumapeto akatero anali ku state house

  • @MollenMponya
    @MollenMponya День назад

    Awa ndye mau ochokwera kwa Mulungu osati Za Anja amaziyesa Okha opambana

  • @PeterThomas-lw3io
    @PeterThomas-lw3io 5 дней назад

    Alhamudulillla sheih my Allah bless you all the time what's a sweet Message like 💋💗 this Marshall ( port Erizabeth SA missionvale

  • @johnarushamasese108
    @johnarushamasese108 5 дней назад +1

    Ana usawi chemwalimu apochele silingwa

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 5 дней назад

    God bless you Sheik all the time ❤❤❤❤❤

  • @juntoiman
    @juntoiman 4 дня назад

    Mmmmm sheikh zoona malo molankhula chilungamo pamaso pa anthu muli busy kubisa choona.Pamenepotu padali anzanu koma lero alikyt

  • @JeanKambala-gm1zr
    @JeanKambala-gm1zr 5 дней назад

    Nyasi zenizeni pamaso pamulungu chilungamo mukuchidziwa Shehe iwe. Wadya ndalama

  • @MafumuBanda
    @MafumuBanda 5 дней назад

    Sheikh ilim yanu ndiyochepa mupite mukaphunzirenso, ngati mukuzitenga zinthu za Allah maso mmwamba eeeeee chilango chaukali chkupezani pompo mulipo asakutameni awowo andalewo ndizotsala , ifenso tinaphunzira kwambiri kuposa iweyo xxx

  • @AbouzaidahSayeed
    @AbouzaidahSayeed 5 дней назад

    Kkkkkk sheikh wasanjatu uyu 😅

  • @NuradinaAbrahima-rt9ip
    @NuradinaAbrahima-rt9ip 4 дня назад

    No i was interested ndi ulaliki wanu Sheikh koma kumapetoko mwandionongela data yanga😭😭😭😭

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 5 дней назад +1

    Ine ndine Msilamu, uyu ndi sheikh wa chishiya uyu kafiir weniweni uyu,

    • @HusseinAdamLidezo
      @HusseinAdamLidezo 5 дней назад +1

      Sheikhe wamanyi uyu mbuz

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 4 дня назад

      @@HusseinAdamLidezo zoona angamasinthanise chisilamu ndi ndalama?, bwanji sakulesa asatana anzakewa kuzunza ndikupha anthu mdziko muno ?

  • @trickermussa472
    @trickermussa472 4 дня назад

    Kukangotinyasisila deen yathu mbuzi ya shaikh

  • @marvelousmadzimure1811
    @marvelousmadzimure1811 2 дня назад

    Masha Allah ❤❤❤

  • @Sasha-g3z
    @Sasha-g3z 4 дня назад

    Bas allah awadalotse ndi ulaliki wawow

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 3 дня назад

    Msilamu wolakira zau Mulungu osati enewa .Akuti ngati munthu wa mulungu walalika osanyoza president akuti ndiye sadziwa kulalikira. Shame

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember 5 дней назад +1

    Soka kwaiye akupindisa chilungamo popeza akuziyandikisa matako ake kumoto

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 5 дней назад

    Zikhale ng'oma akuwombelanso mmanja pamfundoless zomwe wanena, kodi unamulesa kuti asamaphe ma ruandaniz and Burundians komanso amalawi?.

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv 8 часов назад

    Inu nde muletsa zoipazooo suyu muyamikira mfiti ,wakuba, musatinyase

  • @Musa-cz1nm
    @Musa-cz1nm 5 дней назад

    Ma shaallah ma shaallah ma shaallah

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 5 дней назад

    Izo mzoona zoti tiziphunzisana zabwino ndikulesana zoyipa, funso kwa iweyo shehe ndiloti;
    Kodi zoipa zomwe akuchita chakwelayo wamulesa?
    Kupha kumene akupha aboma anthu kumalawi kuno wawalesa aboma ako awusiluwo ?,

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo День назад

    Thanks shelk potipatsa ulaliki wabwnowu

  • @KasundaAbbasi
    @KasundaAbbasi 5 дней назад

    Ngakhale mawu akewo akupepuka zoyakhula zakeso kumalemelera abusa aja

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 5 дней назад

    Mzimu wa Chilima ukunyetseni nonse amene mukugawa ma yellow band ndi inu amene mukudya ma bans

  • @AminahMussah
    @AminahMussah 5 дней назад +3

    sheikh zamanyazitu iziii kufuna kuoneka wabwino pamanso pa pule mwadya zingat

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 5 дней назад

    Chemoto akhale Kunkuyu😅😅😅😅

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv 5 дней назад

    Munthu angopha anthu inu mukamuyimile , munthu onyoza chisilamuyo inu mukamuyimile angapilile zimenezo ndani
    Kodi yinu mufuna azakupheleni agogo anu mpamene muzaone? Kuti izi ndizilombo!!!? Aaaaa mwatipsesa mitimatu nsilamu wantundu wanji osadzudzula munthu akupanga zoipa , bwanji simukuyima pa deen ndikulalika chilungamo aaaaa yinu nde mwalalika mophusa bolani abusa aja nawonso yinde anyika koma yinu mwanyanya ,
    Ndipo palibe akutameni kupatula okhawo akulipilani ndalamawo ife ndife asilamu eni eni choipa timadzudzula basi angakhale Allah anamudzudzula ntumiki wake Muhammad ( saw ) sametime atabwera munthu kuzamfutsa koma ntumiki anayang'ana kumbali
    Alkah pompo pompo anamudzudzura awa ndayani aaaaa musatinyase mwamva

  • @FarhaazbashaMdoka
    @FarhaazbashaMdoka 3 дня назад

    Koma ma ayah wa tikugwilitsa ntchito molakwika 😆😆😆😆😆😆👏👏👏👏👏👏

  • @udkconsultancy5567
    @udkconsultancy5567 5 дней назад

    POWERFUL

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 5 дней назад

    SHEIH MWAPALA ULALIKIWANU MUMAFUNA AKUTAMENI A PRESIDENT PALIBE CHANZERU MWAYANKHULAPO APA ALLA WAKE UTIYO ANGAKONDEE NDI ZOMWE AKUCHITA CHAKWERAYO AYI INUSO ALLA AKUONENI

  • @Ishmael376
    @Ishmael376 5 дней назад

    Komati choti muziwe kulankhula boA pamaso pamulungu pomwe chilungamo mukuziwa muziwe kuti akakuwochani

  • @user-ti8ds7iq8z
    @user-ti8ds7iq8z 5 дней назад +1

    Chakwela akusapoter Israel shehe wa mabi

  • @AugustineIshmael
    @AugustineIshmael 4 дня назад

    Naam ena akwiya chifukwa mwayakhula zosephana ndizomwe Iwo akufuna

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 4 дня назад

    Awaso nawo aaaaaa zaziiii mazidyani wosatipusitsa

  • @emilynthite6545
    @emilynthite6545 5 дней назад +1

    Apasidwa ndarama alaliki adyela

  • @AnnieKwisanja
    @AnnieKwisanja 4 дня назад

    Akutuma Kodi sheikh wachinyengo iwe nde akupasa zingati ?

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv 5 дней назад

    7:53 Chikangawa akupatsani million yinu zaziiiiii nkhanizaunu

  • @Hassankazembe-d3o
    @Hassankazembe-d3o 5 дней назад

    Sheikh apatu nanu mwanama kwambiri 😂😂😂😂😂😂

  • @medicoastkzn
    @medicoastkzn 4 дня назад

    Mashala

  • @ChristianMtambalika
    @ChristianMtambalika 5 дней назад

    Anthu muzinena chirungamo osamabisala mukaona omunenayo kuti alipopo mamizimu anthu akuvutika pqmene iweyo ukufunq kukomesera president umenewo moyo oyipa ngati uli sogoleri wapingo ndiwe waboza liuze chirungamo dziko

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi 5 дней назад

    Walykum ssalam wakahmatul llah wabaraktu

  • @KassimIssa-bn3od
    @KassimIssa-bn3od 5 дней назад

    Kmatu musamapange zindu kut akutamen shehe Allah wanji angasangalale ulaliki zimayi sisi kunja osamvala pango 😢😢😢 dini ulindo bas inarilah

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 5 дней назад

    Moses kumkuyu akukuwombela mmanja pamfundoless zakozo, kodi unamulesa kuti asamaphe anthu ngati mmene anaphela ALLAN WITIKA uja?

  • @user-zf7xk8fk5s
    @user-zf7xk8fk5s 5 дней назад +1

    Km Inu sheikh ndinu opanda nzeru apurezident akunyoza chisilam kms amakokomezera nkhondo ku Palestine kut adziwapha asilam zoon Inu kumaim pagulu kwacemera

    • @user-zf7xk8fk5s
      @user-zf7xk8fk5s 5 дней назад

      Ndipo panop asilam akumalaw akuchititsa manyaz chisilam chifukwa chokonda ndalam mmmm zomvetsa chison

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon 5 дней назад

      Ndipo sheih uyu watinamizapo wadya nao ndalama za pule malawi sadzathekayi

    • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
      @AbdulmajeedJbanda-oz3jv 5 дней назад

      Alibenzeru uyu

  • @user-fm7yg5yc2c
    @user-fm7yg5yc2c 5 дней назад

    Walaikum salaam warahmatullah wabarakatuh... Innalillah wainna illaih rajiun

  • @AliSinoya
    @AliSinoya 4 дня назад

    Sheikh uyu manyakwa

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 4 дня назад

    Shehee wadya chamba chanji chakwera Mutu Ngati gwafa😂

  • @CHIFUNDOCHINA-lp9lg
    @CHIFUNDOCHINA-lp9lg 3 дня назад

    Mashallah

  • @user-qs7xw4ph7z
    @user-qs7xw4ph7z 4 дня назад

    Amen

  • @MussaAndreQuenessi
    @MussaAndreQuenessi 4 дня назад

    Chakwera anapha chilima😊

  • @SolomonShaibuh
    @SolomonShaibuh 5 дней назад

    Live from Gaza city

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv 5 дней назад

    Palibe amene angakutameni yinu bodza zidyani ndalamazo msilamu weni weni akuonani Kuti mwanama akulu ndinu adyela

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 4 дня назад

    Achina chimoto ndi a MCP ndiwe shehe😂

  • @moosakananji1879
    @moosakananji1879 4 дня назад

    Sheikh awa Malo ngt awa kumafunika Sheikh ayyub azipita kumeneku not awa

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 5 дней назад

    Ndiye ulaliki otaninso uwu, mukulalikila ngati simukumva kuwawa bwanji, odya banzi sasowa.

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y 5 дней назад +1

    Ndalama Za mcp zikuyakhula

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 4 дня назад

    Iwe undithera nthawi ukuwoneka kuti walandila brown envelope

  • @abbasdamsonamini4888
    @abbasdamsonamini4888 4 дня назад

    Naam Ameen thumma Ameen

  • @user-ky8eq5ek1p
    @user-ky8eq5ek1p 5 дней назад

    Bodza pakadalipano akuliyamba ndi Chakwelayo

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 5 дней назад

    Ameen

  • @shadrackdrums3536
    @shadrackdrums3536 4 дня назад

    Ulaliki oti sungatingele kumoyo wosatha komaso sungasithe kalikose. Koma anthu akuwombela mmanja. Ulaliki oti mukupanga taget Boni kalindo, Bakili muluzi tv komaso limpopo FM. Ife we are not going to support any usiles speach or teaching like this wadya bamzi shehe.

  • @user-xd1cm7tm7t
    @user-xd1cm7tm7t 4 дня назад

    Chemoto ndinu mwandila ma unforp

  • @HallimaMakwinja
    @HallimaMakwinja 4 дня назад

    Kodi munthu ameyu ndani alinaye number yake sheikh ameneyo ndimuuze kuipa koononga chipembezo chifukwa chandalama

  • @HallimaMakwinja
    @HallimaMakwinja 4 дня назад

    Inu sheikh watu ndithudi si mslamu weniweni awa akuononga chipembezo cha chislamu ndi mbunzi yamunthu

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 5 дней назад

    Iwenso waikila kumbuyo asatana mmalo mowalesa zoipa which means ndiwe kafiir

  • @JumaMboneka
    @JumaMboneka 4 дня назад

    Aise kaya ukumati mwiniwakowe Malawi chani kuyambila lelo ndakutuluka ndakuona kut ndiwe wamanyi ukuchwmelela zimenezi kut sheh walalikila mwamphavu mphavuzake zilikut machende ako aise pamoz ndisheh akowo iwe wamanyi kwabas

  • @MussaAndreQuenessi
    @MussaAndreQuenessi 4 дня назад

    Awapasa ndalama 😮 awa

  • @NchocitoTuaibo
    @NchocitoTuaibo 5 дней назад

    Naam sheh

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 5 дней назад

    Uyu anadya kale ndalama uyu komaso ndi wa mcp uyu

  • @abdulllahanubieimran06comanubi
    @abdulllahanubieimran06comanubi 5 дней назад

    Jazackah alla

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f 2 дня назад

    Shehe my foot 😅😅😅

  • @EmanuelPaul-io2hk
    @EmanuelPaul-io2hk 3 дня назад

    Shehe akufuna chuma chamagazichi eti?