KODI MWAMVA NKHANI YA MA DEMO? KWACHEMA NDIPO ANTHU ALI OLUSA AKUTI ZIKHALA CHONCHI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 11 дек 2024

Комментарии • 311

  • @SimonBanda-b1f
    @SimonBanda-b1f 8 дней назад +34

    1. Akukaniza mademo ndiye mademo ndi amenewo
    2. Anyamata anu azikwanje aku Lilongwe amatenga ngati Lilongwe ndiyawo wokha
    3. Smart matic siyofunika kuno KU malawi
    4. Anthu atopa NDI chakwera NDI MCP
    5.Anthu akufuna report la imfa ya Chilima
    6. Mafuta asowa
    7. Anthu Ali NDI njala
    8. Fertilizer NDI mbewu zakwera kwambiri
    9. A police akugwira ntchito NDI zigawenga NDI MCP

  • @OfwaMwambila
    @OfwaMwambila 8 дней назад +34

    The first caller has nailed it👌 👏 .do for others what you wish them to do for you

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 8 дней назад +12

    Musasiye program imeneyi you will be one of the best program in mmalawi take your flowers 🎉🎉🎉🎉😢

  • @yasiniKalonga
    @yasiniKalonga 8 дней назад +26

    Ntchito dzawo zikuwachitila umboni,kugendedwako nde kulipo ndithu😂😂😂😂

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 8 дней назад +9

    Mr maseko bravo full malawian 🎉🎉🎉

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 8 дней назад +13

    First caller from kasungu well done

  • @TachikoMwanamanga
    @TachikoMwanamanga 8 дней назад +8

    Luntha TV 🔥 best program ever. Tchito zamanja awo zikuwachitila umboni a chakwela. Angopanga zoti misokho itsike i hope zonse zizatsika mtengo ndipo azapasidwa ulemu. Athu andale kupanda kuwagenda samamva. Komaso zogendana anayambisa nd chakwela emweyi ndie nayeso awone kut zimawawa bwanj🎉😂

    • @BonMatemba
      @BonMatemba 8 дней назад +1

      Chakwela sangasise misonkho ai akuopa akhoza kuduka kkkkkkk ngati akumaoda 😂😂😂😂

  • @LameckGamah
    @LameckGamah 8 дней назад +4

    I Love this program 100%.

  • @oswardzenizeni1458
    @oswardzenizeni1458 8 дней назад +6

    Vuto ndi mtsogoreli chakwera tawonani peter anapanga msokhano mpaka usiku osagendedwa

  • @AndrewCosmasmpama
    @AndrewCosmasmpama 8 дней назад +18

    Zimenezi kt zithe a police ayenela kugwila ntchito yawo mwa ukadaulo osayang,anila chipani.

    • @stevenmwamadi3035
      @stevenmwamadi3035 8 дней назад +2

      Komaso mcp ature pansi udindo basi chakwera awauze amalawi kuti warephera kuyendesa dziko basi ature pansi udindo basi asakamire sakuziwa chilichonse iyeyo crocodile

    • @bridgetmajor3646
      @bridgetmajor3646 8 дней назад +2

      live

    • @ClementLufeyo
      @ClementLufeyo 8 дней назад +2

      Chakwera ulemu wadzichotsera ekha.
      Izi Chakwera akudziwa.

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 8 дней назад +9

    Mbambande maseko kuyankhula chilungamo ❤

    • @ebinazielkandomo7803
      @ebinazielkandomo7803 8 дней назад

      Ziwawa sizabwino chifukwa zimasithitsa kaganizilidwe kabwino. Pali anthu ena a ndale samakodwa ndi utsogoleri wa ena. Iwo amafuna mtsogoleri yemwe iwo akumfuna.
      Izi kuti zithe tisunge ngodya zinayi zomwe zimamanga dziko lino.

  • @FosterDouglas-u9u
    @FosterDouglas-u9u 8 дней назад +8

    Mwaiyamba bwinotu continue....

  • @vanSefu
    @vanSefu 8 дней назад +5

    Ndipo kugendako angophelatu chakwela ndiwamanyi

  • @MadalitsoAction
    @MadalitsoAction 8 дней назад +1

    Very powerful message from kasungu and phalombe mulandire ulemu

  • @MagretPhiri-z3b
    @MagretPhiri-z3b 8 дней назад +5

    Kungowawu achakwelawo kt azikhala ku Lilongwe koko akapita outside agendedwe bas zichita bwino pamenepo osatengelaso kt ndi prisedent chifukwa u prisedent wawo akukondela mbali

  • @GraceKalombola
    @GraceKalombola 8 дней назад +2

    Amaseko mmanja mwanu kuti phwaphwaphwa .mwalakhula bwino kwabasi❤

  • @doreenKamwendo
    @doreenKamwendo 8 дней назад +1

    Umunthu ukusowa Ku utsogoleri wathu...anthu akufatu ndi njala kunjaku pamene Ife tikudya ma sausage ndi zina... God have Mercy

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 8 дней назад +6

    Miyala is only solution,, mademo akuletsa mesa

  • @prophetjacksonmakonda63
    @prophetjacksonmakonda63 8 дней назад +3

    Hello, kuno ku johanesburg, kuchokera lwa jackson,
    Chofunika kuchita ndi president akhale maso, akhale ndi malankhulidwe ngati leader / president wa dziko.
    Koma zonsezi eoyambitsa ndi mcp chipani chamulira boma.
    Achakweta anatenga boma ndi ma demos, koma iwowo akukaniza anthu osutsa boma kuchita match why. Thats why zinazi anthu atopa chifukwa chokanizidwa kuchita peaceful matching.
    Chakwera aime ngati president wadziko lonse, koma panopo akuchita ngati ndi president ea chipani cha mcp, so shaneful.

  • @jykstaan678
    @jykstaan678 8 дней назад +4

    Anthu akuchita bwino pokuwiza chakwera chifukwavakumukuwizawo ndi amene anamulemba ntchito and chifukwa chabodza la chakwera mabwana ake achakwera apsya mtima and this is the bigginig the man will feel the real outrage of people chifukwa cha bodza Luntha it up keep bola asayitsekenso yanuyi

  • @FaheemChipojola
    @FaheemChipojola 8 дней назад +6

    😂😂 akuchita bwino kumamkuwa chalakwe yo 😮😮😮

  • @StuartShabalala
    @StuartShabalala 8 дней назад +4

    Akuyambisa ndi chakwera

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di 8 дней назад +5

    Nyansi saphimba chakwela ndiye gwelo la ziwawa ku Malawi kulankhula kopandanzelu kwa chakwela kufikila a lankhule mowonetsela poyela a zikwanje awo amangidwe

  • @MacxwellStuarts-h9r
    @MacxwellStuarts-h9r 8 дней назад +3

    Sakukwanira PA usogoleri achakwera akanakhala ovomereza anganayenera kutura pansi udindo chifukwa palibe chikuonapo amalawi monga momwe ananenera okha kuti kazalephera kuyendesa ziko azatula pansi udindo after years

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 8 дней назад +6

    Amaseko kukasungu mwayakhula zazeru zoonadi chisilu ndichakwela asadabwe lelo

  • @EnockSankhylani
    @EnockSankhylani 8 дней назад +3

    Adazichotsera ulemu okha pothetsa ufulu aziyamba okha mademo azisenga

  • @ShabaniSelemani-f9b
    @ShabaniSelemani-f9b 8 дней назад +3

    Kugendedwaku ndi uthenga owauza kuti zinthu sizilibwino.ndimau okha anthu andale samanva maka akakhala pa maudindo

  • @georgechinangwa
    @georgechinangwa 8 дней назад +2

    The president must resign anthu atopa kwambiri

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 8 дней назад +4

    Kukuwiza sikulakwa,,anthu aziziwa kuti anthu andale asiye kupusa ,,aziziwa kuti anthu aboweka

  • @BeatrinceChanza
    @BeatrinceChanza 8 дней назад +4

    Kuteroko gwero lonseli ndi achakwera iwowo sakukhala ngati munthu wamkulu iyeyo alindi nkhanza chifukwa sakufuna kutsutsidwa or atachita cholakwika

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 8 дней назад +3

    Chakwera ndie mbatama chifukwa tsiku anayankhula kwa Malawi lija akanasindika kuipa kwa zipolowe. Ndinapedzapo bvuto ndi Chakwera.

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 8 дней назад +2

    Dzuka Malawi Dzuka 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼

  • @charlesdaisi616
    @charlesdaisi616 8 дней назад +1

    Ulemu sumakhala opita mbali imozi yokha ai andale apereke ulemu kwa nzika muzaona kuti solution ndiyomweyo basi. Nzikanso sizingakuwize mdindo straight forward bwana!

  • @wisdomkamwendo2820
    @wisdomkamwendo2820 8 дней назад +1

    Maseko ku kasungu kuing'alula

  • @GeorgeSmoke-xf2ks
    @GeorgeSmoke-xf2ks 8 дней назад +2

    Izizi zinayamba mene tonse alliance imalakalaka kt ilowe boma. Peter ananthamangisidwa and ku Nkhoma same Peter anayenda want chire. Kuyambila nthawi imene ija mantha anthu alibe. The word osaopa muli unthenga. Nde pulezidenti kuyankhulana mosasatisa mbola.

  • @ChidaPhiri
    @ChidaPhiri 8 дней назад +4

    Anthu atopa ndi ulamuliro wa Chakwera ayenela kutula pansi udindo alephera ndithu. Tikufuna mademo ochotsa Chakwera ndi mcp pasanafike pa 2025. Achoke ndithu aononga dziko. Enough is enough tisamangoyang'anira ai.

  • @happybinali4673
    @happybinali4673 8 дней назад +1

    The first caller was 👌

  • @KettieNathaya
    @KettieNathaya 8 дней назад +3

    Ndikudikila wapa Lilongwe ayankhulepo chakwera alibe khalidwe ndiwokupha anapha anthu 9 Chilima analakwanji?

  • @GraciousKhulani
    @GraciousKhulani 8 дней назад +2

    Uyu muti president yu alira sanati kamba ka mfundo zomwe anapusitsa mtundu wa amalawi zisawawe lero paja nayeso wanzuza anthu mokwanila nayenso yakwana nthaw yake

  • @FractionMailosi-p3n
    @FractionMailosi-p3n 8 дней назад +3

    Good program

  • @DickisonyusufChiwalo2
    @DickisonyusufChiwalo2 8 дней назад +1

    Mawu ogwila mtima kuchokela kukasingu❤❤❤❤

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 8 дней назад +4

    Chakwera ndi chitsilu cz zonsezi zikumukhudza mchifukwa akudzipatula.Koma being president akuyenera kuchita monga overall.

  • @EnockMvula
    @EnockMvula 8 дней назад +1

    pachitonga atiti kakumariya kawawa bwanji Mr chikangawa sitikumufuna achoke ndiposo ndiwakumpha ndichigawenga ameneyo watimphera Mwana wakwathu skc chifukwa Choti aramurire yekha

  • @ThokozaniBondo-em9fr
    @ThokozaniBondo-em9fr 8 дней назад +1

    Ali chikangawa achoke, palibe chomwe akulakwisa anthu coz anachulusa zolonjedza wanthu ndye amene akuchita zimenezo atopa ndye akukuyidwayo akusagana ndi zintchito zake

  • @HenryMalikebu-i4g
    @HenryMalikebu-i4g 8 дней назад +1

    Ndipo sitisiya kugenda mpaka azachoke ameneyo

  • @MMADICHANDE
    @MMADICHANDE 7 дней назад

    Chakwela ndamene akupangtsa nde ndkumufna chakwelayu ndtakumana naye ndmmete mpala kt adznva😊😊😊

  • @InnocentNitamanMilanzi
    @InnocentNitamanMilanzi 8 дней назад +1

    Auzeni ndipo mkhondoyi siyikutha chifukwa china chili chonse chomwe anthu angadandaule iwo amatseka makutu osamvera zokamba za anthu

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 8 дней назад +1

    Ulemu wanu a Maseko ku Kasungu. 🙏

  • @WellsKasuka
    @WellsKasuka 8 дней назад +3

    Izitu zikuchitika chifukwa cha kudzuzika kwawathu kutopa ndi mavutto amene ali zikomo

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 8 дней назад +4

    Dziko lilibe security , ngati anthu akukhapana ndi zikwanje apolice alipompo ndiye chani , anthu aziopa ndani ?

  • @ProspaDMitummba
    @ProspaDMitummba 8 дней назад +1

    Cakwera sakuiziwa tcito yake

  • @BawulenLuka
    @BawulenLuka 8 дней назад +1

    Vuto ndi chilima kupita ku khoti..... zitsankho Zija dpp inawina

  • @BusisiweMakhoba-d8o
    @BusisiweMakhoba-d8o 8 дней назад +1

    Bambo panyumba akamunamiza mwana wake kuti pobwela ndikugulila sweet koma sweet ija osabwelesa mwana amakwiya naye Bambo wake chifukwa ngoipa wabodza oipa

  • @francistonthola1101
    @francistonthola1101 8 дней назад +1

    Ankagrndedwa Peter muja munkasekelela,lelo akugendedwa awa nde ikhale vuto??nde poti sanati agendedwabe ndipo nde akuwidwa.inunso mukanapanga present programme musamakhale ndi mbali coz siku lina tizakutikwananinso

  • @MiladgeAli
    @MiladgeAli 8 дней назад +2

    sanathi aziona

  • @joebonface4443
    @joebonface4443 8 дней назад +1

    Ndakwera Maseko wa Kasunguyo ntchito zawo zikuwachitira umboni

  • @WillieLamwa
    @WillieLamwa 8 дней назад +2

    Atsgoleri andale alephera

  • @henryibrahimsailes4638
    @henryibrahimsailes4638 8 дней назад +1

    Mwachidule maganizo anga ndiwoti, chakwera wamukanika utsogoleri ,ndipo ngatdi ali munthu ayenera kutula pansi udindo,avomereze kuti zamukanika

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika 8 дней назад +1

    Even him akhoza kuzikuwa yenkha n kuzigenda yekha pafika malawipa.. Chakwera will vote for APM aswel... congratulations APM..bwanji APM akalumbiliretu before voting 😂

  • @HennockMpumulo
    @HennockMpumulo 8 дней назад +4

    Kms apolisi sakudziwa ntchito yawo oyambitsa ndi president kms apolisi

  • @IsaacSombani
    @IsaacSombani 8 дней назад +3

    Bravo to ﹰMr ﹰMatseko from kasungu ur the best

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 8 дней назад +1

    Utsogoleri sulibwino

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 8 дней назад +2

    Atule pansi udindo mr chikangawa......mcp out

  • @OwenKamfoloma-u3l
    @OwenKamfoloma-u3l 8 дней назад +2

    Politician asiye kugwiritsa Ntchito achinyamata molakwika ,kuwongola mtengo mpoyamba. .Owen masulani.Machinjiri BT

  • @MerienohawaiBro
    @MerienohawaiBro 8 дней назад

    The first caller mr maseko mbambande

  • @grinesskuyere
    @grinesskuyere 8 дней назад +1

    Kasungu woyeeee!

  • @allanmvuma1891
    @allanmvuma1891 8 дней назад +1

    A president chakwela anati namiza pazinthu zambiri zedi
    Iwo panthawi ya campeni anati azasitsa zinthu zonse monga feteleza chjmanga
    Ndichifukwa amagenda akamayenda pa nseu
    Asitse zinthu tizasiya kugenda kugwesa ndalama ya KWACHA

  • @AnusaChiwale
    @AnusaChiwale 8 дней назад +1

    Zoonad akanapanga raisin osatiso kumatuma anthu ndizokwanje kuopseza anthu ai ndie kumati ndi nsogoleri

  • @kimukamawe1591
    @kimukamawe1591 8 дней назад +1

    Kod nanunso mukamati inu otsutsa ndamene mukutuma anthu kuti azigenda, zikungoonekeratu namwenso nzeru mulibe inuyo muganizakuti kukhutakwanu kwa inuyo pakubera misongo amalawi azingokusekelerani zopusazo, Achakwera ananena okha kuti Nyasi sapimpha ndiye inu mukufuna kuvindikila manyiwo sizitheka mukhaula muona amalawi atopa basi.

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 8 дней назад +1

    Ndigalu Chakwera wosati vachizungu koma galu vamumidzi uja vamakutu mwamba

  • @Martinmkapangakapanga
    @Martinmkapangakapanga 8 дней назад +1

    zikugwilizana chifukwa iyeyo akuzudza miyoyo ya anthu a president akuyambisa ndi iyeyo mtundu wa anthu wafa chifukwa cha iyeyo wafinya zonse kuti zikhale zake

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 8 дней назад +1

    Palibe zaulemu Chakwera akuzuzitsa Kalamba mumidzimu ndiulemu?????? Chonde musatiyakhulitse zoipa

  • @RuthChaola
    @RuthChaola 8 дней назад +2

    Amaseko ulemu wanu

  • @InnocentNitamanMilanzi
    @InnocentNitamanMilanzi 8 дней назад +1

    Ichoke smart matic kaye ndiye kunyozedwa kutha

  • @MiladgeAli
    @MiladgeAli 8 дней назад +1

    kodi anthu ogendawo akumalankhula mau chimenecho ndifukwa chothesera😅😅😅😅

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 8 дней назад +1

    Azikuwidwa kumene coz palibe chomwe akupanga mdziko muno achoke tatopa naye

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 8 дней назад +3

    Andale azigendedwa or kuphedwa kumene chifukwa ndamene akuononga malawi yi

  • @InnocentNitamanMilanzi
    @InnocentNitamanMilanzi 8 дней назад +1

    Nyapapi chakwera nthawi yomulemekeza inatha chifukwa iyeyo alibe umunthu olemekeza anthu

  • @LipengaPhillip-u5l
    @LipengaPhillip-u5l 8 дней назад +3

    Angotula pasi udindo chakwera

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr 8 дней назад +2

    Mchewa oyambilira saku Kasungu bambo Maseko mulandile ulemu wanu ndipo komwe muliko mumve kukoma. Chakwera wagwa nayo ndipo zomwe mwalankhulazi ndizomwe nkaziturutsa nane, komanso reporter simunandikomeleyi mukubabaika bwanji? Mukufunika mudzakumane ndi Brian Banda bambo maseko kuti mudzamukhuthulire nkhawa zanu ndiwauza a president osamvawa kuti sitikuwafuna ife 😅😅😅

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr 8 дней назад

      I meant kuti aku Kasungu not saku sorry about that. Bravo kasungu ❤

  • @Enock-c9l
    @Enock-c9l 8 дней назад +1

    Asogoleli akasiya kuba

  • @bornface4786
    @bornface4786 8 дней назад +1

    Vuto ndiloti ochakwera sakukwanitsa zomwe analongeza ku mtundu wa Malawi. Komanso aiwala kuti nditsogoleri wadziko osati wachipani

  • @Ericmalimelo
    @Ericmalimelo 8 дней назад +1

    mukazaona izi ndekut usongoliri wanthawi imeneo suli bwino anthu atopanazo nde izi zipitilire bas

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO 8 дней назад +1

    A president Ali dull 😱 kwambiri. Kumkuyu, Chimwendo ndi Kabwila ndi anthu opanda mzeru amamupotoza president. Sindinaone president odikila anyamata ake amuuze cholankhura. No wonder sanafune kuti apikisane ndi wina ku convention. Chifukwa ndi munthu amalamulidwa ndi anyamata

  • @usherjamson174
    @usherjamson174 8 дней назад +1

    Maseko 100% said

  • @Khalidwearthouse2003
    @Khalidwearthouse2003 8 дней назад +5

    First to comment

  • @IbrahimIsmael-h2w
    @IbrahimIsmael-h2w 8 дней назад +1

    Nkhani ndi usogoleri ndimanyakà

  • @VenançioZocueza
    @VenançioZocueza 8 дней назад +2

    A maseko anena chamuna zosezi ndi chakwera.tsankho 2 much.amfumu opusa amagawanitsa mtundu.

  • @innocentjackson2003
    @innocentjackson2003 8 дней назад +1

    Ife tizisunga chikhalidwe ena akusunga ndalama?

  • @WilsonMalingamoyo-z5x
    @WilsonMalingamoyo-z5x 8 дней назад +1

    Apapa ife ngati amalawi tikutaya chikhalidwe chathu chimene chimene timatchuka nacho ,kachiwiri atsogoleriwa apapa Kwa iwowo andale ndi chidziwirso kuti usogoleri ukuvuta kwambiri , ngati iwe kholo ukuyang'anira ana akupanga zoipa siku lina mwana yemweyo azakupweta chifukwa amaona ngati ndi chikhalidwe chabwino ,chachitatu mavuto amene anthu akukomana nawo umphawi kusowa kwa ntchito anthu akusiwa pogwira
    Pofuna kuthana ndi vutoli atsogoleri akhale pansi ndikukambirana ndikuona kuti chisogolo tiyende bwanji , chachiwiri atsogoleri amipingo akugona onse akumwa fanta ndi ma bazi amene akuononga dzikoli ,mmbuyo muja amipingo amazuzula pompo zithu zimasintha amipingo akalankhula lero amipingo ali ndi mbali zimenezi zaonongetsa dziko amipingo adzuke ndikudzudzula mopanda kutenga mbali

  • @JosephyChithope
    @JosephyChithope 8 дней назад +3

    Kwacha yagwaso lero😂😂😂😂😂

  • @CollinsJustinchinguwo
    @CollinsJustinchinguwo 8 дней назад +3

    Ng at I akuletsa ma Demo zotsatila ndizimenezo

  • @JamayakoJamayako-rv2he
    @JamayakoJamayako-rv2he 8 дней назад +1

    Following with patient

  • @ModestaMlamba
    @ModestaMlamba 8 дней назад +2

    Anya manyitu ameneyo tidakakuwabe

  • @ElizaKanyama-fq8jy
    @ElizaKanyama-fq8jy 8 дней назад +1

    Choipa chisata mwini pochita zithu muziganiza ,tchimo limazuzuza olo. Lichita iyaaa

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer 7 дней назад

    Vuto ndilakut chakwera adaiwara malonjezo ak poyambilir coz anthu atopa nay, mfumu Solomon idapepha zelu kwambili mulungu chifukwa idaona kut udindo wamukurir apapa mulungu walola dala kut eliko agwetsedwe bas no matter what, 😢😢😢

  • @vanSefu
    @vanSefu 8 дней назад +1

    Mr Maseko,pali mwambi oti,umakolola zomwe wadzala,so achakwela akukolola zomwe anabzala

  • @FelixMachika
    @FelixMachika 8 дней назад +2

    Mademo a mtendere ndiye titaniii? Mademo ndi omwewo basi😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣😣

  • @tensonsitiyanjana5385
    @tensonsitiyanjana5385 8 дней назад

    The anchor's demeanor is telling stories.

  • @SadickAdam-x8j
    @SadickAdam-x8j 8 дней назад +1

    Ayambe ndiwo achakwera kulankhula nkhani zimenezo kmso zikwanje ndizawo