KOMA INU HOT CURRENT YA LERO MPAKA KUFIKA POYANKHURA IZI? KODI NDIYE KUTI IWOWA SAMAOPA?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 дек 2024

Комментарии • 67

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 3 дня назад +22

    Ndi pephero ndi pembezero Langa Kut MCP ichoke m'boma azunza athi kwambiri

  • @MatthewKaliyati
    @MatthewKaliyati 3 дня назад +6

    Nankununkha samazimva yekha kuti ndikununkha, ndiyeno inu achimwendo ndi MCP anthu akukuwuzani kuti mukununkha koma mukupanga makani, kodi inu usatana wake ndiwotani, kalapeni basi

  • @MablesserMussah
    @MablesserMussah 3 дня назад +1

    Guys of course you are working but I appreciate for your kindness I know you are not perfect but for the moment you're working to the times redio you're straight straight to tell Malawians the truth

  • @RedsonMbewe-s2m
    @RedsonMbewe-s2m 3 дня назад +14

    Kumbali ya katangale bomala chakwelayu ndilokuba kuposa maboma onse m mbuyomu mbava chakwela

  • @NumeriChibowa
    @NumeriChibowa 2 дня назад +2

    Afrobalometer ikunena zoona zokha zokha chifukwa anthu ambiri akuvutika kusowa chakudya ngakhale fertilizer
    Inuyo mukutha kuswa kuswa basi mukutokota zomwe zili pa ground panopa zinthu sizikuyenda bwino ndipo umboni ndi aliyense Ali kumudzi awo anena kuti sitikusinthawo akulandra nawo kena kake mu ulamuliro umenewu

  • @LanceLance-mj4kc
    @LanceLance-mj4kc 3 дня назад +11

    Anyamata inu mumati imilira ,keep it up with your lovery plogram ❤

  • @Amina-gg5gr
    @Amina-gg5gr 2 дня назад +2

    Awope chiyani nanu

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 3 дня назад +4

    Akudalira smartmatic nkani akusunsana ndi zimene azofufuza apedza

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j 2 дня назад +1

    Chikuni chachikulu kusunga moto ,,Apm my vote

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 3 дня назад +3

    Boma la Chakwera ndilakuba komaso A Chakwera alephera kuthesa😂 katangale 😂😂😂😂😂

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu 2 дня назад +1

    They better accept it now before it is too late a mcp sazawina

  • @AmosAugustus
    @AmosAugustus 3 дня назад +2

    Palibe chifukwa chomangira mtolankhani ngati Ali pantchito yake ndiye kuti vuto ndi apolice amapanga chinyengo pantchito yawo oyenera kumangidwa ndiwowo chifukwa amaphwanya lamulo kumanga mtolankhani and mtolankhani alindiufuru ojambula chilichose or maiko aruya kunkhondo mtolankhani amakajambula no mulandu vuto ndi bomali chilungamo palibe

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 3 дня назад +5

    Jonah guys amaziwa kutambasula Khan moveka bwno keep it up good work 😇

  • @frankkalonga
    @frankkalonga 2 дня назад

    Inuso mmatukwana bwanji

  • @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb
    @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb 3 дня назад +1

    50+1 malamulo mulibemo achitsankho izi zinabwera ndi a khoti zomwe ndizodabwitsa kwambiritu kuti khoti likapange lamulo mmalo momasulira malamulo...a Parliament akachotse lamulo la 51+1 zomwe ndizosagwirizana ndi kayendetsedwe ka chitsankho

  • @FatsanZiwah
    @FatsanZiwah 2 дня назад

    Bwanji mwavala zofanana nonse😂😂😂

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 2 дня назад

    Bakili muluzi tv uja osazaimphwekesa

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 3 дня назад

    This appears to have a common source because for a corrupt deal to work it involves many corners

  • @MaryZgambo-p5m
    @MaryZgambo-p5m 2 дня назад

    More fire

  • @ecksonkaime2511
    @ecksonkaime2511 3 дня назад +1

    I want to concur with bwana Chunga to say that we don't have a country if that's the survey results by Afrobarometer

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 3 дня назад

    The best example is Ramaphosa in South Africa. He failed 50 +1

  • @credochakwira-zk1sq
    @credochakwira-zk1sq День назад

    koma weare all corrupted kuyambira mwana wankulu

  • @Saeed-r3z
    @Saeed-r3z 2 дня назад

    Ndizovetsa chisoni

  • @chisomotaika4479
    @chisomotaika4479 3 дня назад

    Kkk apolisi mpaka ma defending champions pa katangale😂🤣🤣😅😅

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 3 дня назад

    Kodi mukamati siwopa munthu ifeso itimakuwopani

  • @MadalitsoKatchomoza
    @MadalitsoKatchomoza 2 дня назад

    Mkumafuna chani inu. Boma lakuba inunso muli mbava. Remember usachotse chitsotso chili mdiso la mzako usanachotse chili mudiso lako. Olo zimene zikulankhula apazi zonse ndimbava izi. Osamanama mulankhulila anthu angati izi. kumangosunga anthu omangotchedwa akuti ma professor, ma doctor amangodikilila kulembedwa ntchito Basi. Anthu adzichoka ku mayiko akunja kumadzayambitsa zinthu kumalawi mkumakulembani ntchito. Mungalankhule chani Cha mzeru.

  • @LeoLongwe
    @LeoLongwe 2 дня назад

    Apolice ambili ndimbuli zitsilu

  • @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb
    @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb 3 дня назад

    Times TV mmanja mwanu mukugwira bwino ntchito yabwino kwambiri

  • @TamaraSamidu
    @TamaraSamidu 2 дня назад

    Afro barometer,,,,, inetu olo atangoti lero tivote mmmmmh Afro barometer yalondola

  • @FrankMwadzaonga
    @FrankMwadzaonga 7 часов назад

    Live

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j 2 дня назад

    Afriobarrometer imadana ndi a bima ma resuts ake

  • @DelipherMtekateka
    @DelipherMtekateka 3 дня назад

    🎉🎉🎉❤❤

  • @AnnaMarverous
    @AnnaMarverous 2 дня назад

    Chakwera has failed us

  • @ChikumbutsoMahayah
    @ChikumbutsoMahayah 3 дня назад

    Matsku ano akukonda mimba zao mmalo mokonda amene adawavotera alibe nazo ntchito kma ovota ndife

  • @jameshend9453
    @jameshend9453 2 дня назад

    Mipando yanuyo munayandikisa pena ndimazaona ngati mumathilana mate polankhula koma program mumakwapula gyz

  • @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb
    @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb 3 дня назад

    DPP woyeeee APM woyeeee Times TV woyeeee zamphamvu atsukuluzi

  • @HarryMsudzula
    @HarryMsudzula 3 дня назад +1

    Kkkkkkkkkk koms pa apolice po ndiye sindimamvesa cos apolice ambiri ndiosauka kwambiri mosogozedwa ndi aziphunzinsi koma eeeee afrob akunama kwambiri

    • @sellahlonjezoprecious9159
      @sellahlonjezoprecious9159 2 дня назад

      Ndalama yoti munthu wina akuyidandaulira si yigwira Ntchito molongosoka Chifukwa sunayinkhesere thukuta ngati mulungu anati aliyense azadya nthukuta lake sanama

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u 2 дня назад

      Mwanena bwino kuti Ena ndi osawuka nde kuti Enanso ndiwochita bwino that's why u can see that is not 100%, ikadati ikhale 100% mukadanenanso kuti onse ndiwolemela😂

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 2 дня назад

    Bvuto la miigwirizano ya dzipani ndiloti amakulirina mtima . Amafuna kuti oyimira chipani chao ndiye oyenera kukhala presidential candidate .

  • @AdamAhamad-k2i
    @AdamAhamad-k2i 3 дня назад

    Chimwendo banda ndi mbolo yopanda mzeru kumtumbo kwake konunkhako galu ameneyu

  • @Dalsonchimlomo
    @Dalsonchimlomo 3 дня назад +2

    Atat apangaso kafukufuku waoyo today ,percentage UTM itha kukwera coz survey imeneyo idachitika UTM isanapange convention yake isadapeze mtsogoleri wake.

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 3 дня назад

    boma la chakwera onse ndi mbuzi zokha zokha

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 3 дня назад

    boma la zigawenga zokha zokha ili chakwera ndi chitsiru cha munthu

  • @DippedJob
    @DippedJob 3 дня назад

    Mathainuyo

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 2 дня назад

    Malawi wathapo basi chifukwa cha MCP ya CHAKWELA KUBA NGATI ACHITA KUWALEDZA IIIII AMALAWI TIWONE DZINA AYATIPHA AMALAWI

  • @CorneliusSande
    @CorneliusSande 3 дня назад +1

    Palibe olungama padziko pano ngakhaleso inuyo atola nkhani ndinu akatangale .

    • @EidPaseli
      @EidPaseli 3 дня назад

      Ndiyeno??

    • @liz9425
      @liz9425 3 дня назад +1

      Awa anyanya katangale ndi kupha komwe komaso akuba zonse enawa amaba koma osati zonse

    • @MatthewKaliyati
      @MatthewKaliyati 3 дня назад

      Izi ndi mbava zeni zeni and they are doing it out of ignorance

    • @christophermukaka7403
      @christophermukaka7403 3 дня назад +2

      Bolako kuba Kwa DPP zinthu zinali fair komanso anthu akathamanga-thamanga zao zimatheka osati m'mene zikukhaliramu.

    • @bridgetmajor3646
      @bridgetmajor3646 2 дня назад

      Khani ndiyoti mcp yawonjezatu

  • @JacynthaMisomali
    @JacynthaMisomali 3 дня назад

    Awa anafa kale aope chaninso kkkkk

  • @AlfredTengani
    @AlfredTengani 3 дня назад

    Zoonadi auzeni amenewa

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j 2 дня назад

    Musangoti muthu wa kumudzi kuro ndamene aku m'mabvuto komanso townmu mulimabvuto oooophsyaaaaa!!!!!!??

  • @BensonPiasi
    @BensonPiasi 3 дня назад +2

    Achimwendo ziwani kuti izi muku tsutsazi sizowona inuyo sikuti ndinu anzeru kuposa aliyense musazatigwilitse mpweya ndare zanuzo achimwendo ndinu munthu wosafuna kumvera konzani zinthu akukondeni

  • @andrewnkhoma3566
    @andrewnkhoma3566 3 дня назад

    Aope chani kuswa kuswa baxi pade pade iyaaaaa!!!!!

  • @NishaatCornelius-r2i
    @NishaatCornelius-r2i 3 дня назад

    Ziuzeni mbava zakuba izooooo😂

  • @nelsonsikwese5952
    @nelsonsikwese5952 3 дня назад

    Eish

  • @PrescottSMART
    @PrescottSMART 3 дня назад +1

    zativuta basi