ANTHU ADABWA NDIZOMWE WAYANKHULA MKULU WA NRB ATAMUKWENYA NAWO MAFUNSO PA ZOMWE ZAULULIKA LERO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 дек 2024

Комментарии • 330

  • @LivaneMsyamboza
    @LivaneMsyamboza 5 часов назад +22

    Iweyo mwasambo umudziwe yesu ndi ophunzira Ake ukapanda kumudziwa mulungu akulangira pansi pompano

  • @MayimunaZuber
    @MayimunaZuber 5 часов назад +17

    Nkulu uyuyu ndigalu akuona ngati ndife ana 😢😢 but why you don't even think about your on Children you only think about yourself's why nde tizizavutika kamba kadyela lanu😢😢😢😢 only Allah knows 😢😢😢

  • @ManzyBusy
    @ManzyBusy 5 часов назад +22

    Kodi palibe mwana apa zili ngati ma passport kupezeka Ku admarc kkkk

  • @YohaneMmorrah-k9d
    @YohaneMmorrah-k9d 5 часов назад +18

    Why chigawo cha ku mwera ndi ku mpoto komanso ku mmawa izi sizinachitike??

  • @CarolineLiabunya-j8k
    @CarolineLiabunya-j8k 47 минут назад +1

    Atola nkhani ndinu opilira, mumakwanisa bwanji? Enafe mafunso enawo bwezi tikufuna limodzi ndimambama😔

  • @JuweriaMussa
    @JuweriaMussa 5 часов назад +10

    Inuyo office mulibe musatinyase nde feteleza alikutiko ngati inuyo mwayikamo ma I'd aaaa mbelela

  • @IndoliNyirenda
    @IndoliNyirenda 4 часа назад +6

    Kodi ku Lilongwe office ya NRB kulibeko tiudzeni

  • @Kamwachale
    @Kamwachale Час назад +2

    Can the commission tell Malawians if in Blantyre we have similar warehouse

  • @JosephMakatha
    @JosephMakatha 4 часа назад +4

    Akuchita kudodoma kunyewa poyakhula komas khope yopanda manyaz ..munthu osanama sasowa amatamba pachipande lero wagwidwa ...chinveni amalawi aziwe chani apa anthu aziwa wokha

  • @MjombaMoosa
    @MjombaMoosa 5 часов назад +5

    Ukunama iweyo nkhani imeneyo ikathele ku Court

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 3 часа назад +2

    Ndiyekuti DPP ija imabelaso eti chifukwatu ndeakugwilana okhaokha DPP vs MCP anthu amenewa akuziwana bwino bwino 😂😂😂😂

    • @chimwemwechimwanza
      @chimwemwechimwanza 2 часа назад +1

      Nawe mbuli ukuona ngati moyo nyengo zinozo zikukoma

  • @MikeLodzi
    @MikeLodzi 4 часа назад +5

    ma office onsewa chomakabisaka Kuma warehouse osungila mbeu ndichani

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 5 часов назад +5

    Mizimu ya kwiya baba.

  • @RoseChimbwefu
    @RoseChimbwefu 2 часа назад +1

    Maboza awo winiko ndi ntanyiwa ananena kare kuti mkugura ma ID a anthu ku Lilongwe foseki

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 4 часа назад +2

    Inu uyuyu asatipusise akunama iyiyi ndi nkhokwe ya cimanga osati nkhokwe ya ma ID.Mec ndi nrb akugwilira ntcito mcp osati a malawi asatinamize oposition musalole kalembela uyuyu zonse dziwotchedwe, tiyambilenso mcp isatipusise za usilu basi.

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 5 часов назад +12

    Mwangwa nayo la 40 la kwana 😢😢😢 chimwendo ali madzi palimbe zoti boma ndi lomweli ayi mwayaluka bas😂😂😂😂😂

    • @DesireMoyo-y8x
      @DesireMoyo-y8x 4 часа назад +1

      Umbuli wakuvutani adpp

    • @MagretHassan
      @MagretHassan 3 часа назад +2

      Za umbuli ndizimene akuchita ambuyakowo Za ziiiiiiii

    • @MagretHassan
      @MagretHassan 3 часа назад +1

      Sindipanga nawo zandale ndili kuno kunja Koma MCP mmmmmmmmm mavuto okhaokha alipo kumalawi kulibe chabwino

    • @blessingsnyalo-rp9ko
      @blessingsnyalo-rp9ko Час назад

      Mbuli ndiweyo udakalibe ntulo ukuyenera kuzuka kape iwe​@@DesireMoyo-y8x

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye 29 минут назад

      ​@@MagretHassanineso zandalezi mmm ayi ndithu.Koma momwe tikuvela momwe ziliri kumalawiko palibepo chomwe chikuyenda.

  • @PeterKaligomba
    @PeterKaligomba 4 часа назад +3

    Ndi zabodza zonsezo agwidwa basi ndipo ayaluka.

  • @ShareefKalima
    @ShareefKalima 32 минуты назад

    Kod I'd Amasungilana kwa nthawi yayitali bwanji? Komanso Ziko la Malawi lili ndi Ma district angat ? Bwanji Mwasankha Lilongwe yokha MA boma enawa musunga lit pamoz ndi enawo?

  • @JamesYusufu-l6d
    @JamesYusufu-l6d 4 часа назад +2

    agalu a NRB. muziona ndi chakwela waninuyo. mumuize. kuti amalawi .sitikufuna loko pang,ono sitikuopaso. mbuzi. imeneyo ichoke asitikakamile. komaso. galu wina wakazi. ananero .talimanja. mbuzi iweso sitikukufuna. uzilamula kulilongwekomweko. galu iwe nazikwanje...

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 4 часа назад +3

    Osamenya khofi bwanji

  • @BonfaceGeorge-t8d
    @BonfaceGeorge-t8d 10 минут назад

    Kwa amene sadziwa za mma office zimakhala chonchi office ina amatha kukapanga rent mu office ya ena even imene iliyosephana ndi zochita zawo so a NRB kukagwlira tchito ku kanengo NRFA sizachilendo amangofunako malo basi

  • @BazaarShaibu
    @BazaarShaibu 4 часа назад +2

    Uyu machende ake kodi NRB ilibe office? Kodi mmene mumalowa mmenemo munamuuza ndani? Nanga ndi chifukwa chani ma ID onsewo ndi a kulilongwe okhaokha kodi kapena Lilongwe yonse anthu alibe ma ID?

    • @EvansEgra
      @EvansEgra Час назад

      Iweyo ulibe machende? It just show kuti mwa iweyo mulibe chirinchonse

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye 26 минут назад

      ​@@EvansEgraiwe usamangoyankha ma text aanthu ngati kut iweyo ndiye wanzeru wava.Kapena ndiwe mneneli wa MCP iweyo?

    • @BazaarShaibu
      @BazaarShaibu 9 минут назад

      @@EvansEgra iweyo ndiye mbudzinso

  • @ShareefKalima
    @ShareefKalima 44 минуты назад

    Kod office yanu yili kut komanso ma lD amenewa Ain ake Mukawapasa lit?

  • @ketrinankhonjera901
    @ketrinankhonjera901 Час назад +1

    Komatu sakuoneka ngati mkulu wa NRB😂😂😂😂Akumugwiritsa ntchito motchipa

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya Час назад

      Ndiponso momvetsa chisonitu kkkkk

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye 32 минуты назад

      Aaa ineso pomava kuti ati ndinkulu wa NRB ngati kumunamiziratu,,,,munthu wake otuwatuwa komaso zosamuyanja bwanji aaaa 😂😂😂

  • @jeanbotomani9081
    @jeanbotomani9081 4 часа назад +1

    Kuputsa sambo ufera za ini , inu chifukwa munachotsa ma office ku Blantyre, munya muona

  • @PatrickKapendo
    @PatrickKapendo 2 часа назад +1

    Vito lili ku malawi kuno kwachuluka mbuli zoti zinapita kusukulu koma ndi mbuli ndipo zimalakalaka kuti mdziko muno muyambike nkhondo vuti sukulu yophuzirira ndalama yochesa kachaso eeeee iku

  • @WysonChilonga
    @WysonChilonga 4 часа назад +1

    Ameneyi ndi galu kwabasi,nde kungopezeka ndi ma ID a Lilongwe okha😢😢

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 4 часа назад +1

    NRB irindioffice zayo bwanji mwakabisara kukanengo??? Ndani amene munauza kuti mukujamburira kukanengo,????

  • @richardbanda9997
    @richardbanda9997 2 часа назад

    May I request Sangwani to speak, the guy is intelligent.

  • @PreciousSteven-e5s
    @PreciousSteven-e5s 48 минут назад

    Akupanga chibwibwi uyo athiridwe unyolo

  • @PhiriChiyambi
    @PhiriChiyambi 4 часа назад +2

    Mulungu si munthu kugwidwa kochititsa manyazi kosungila chimanga kupezeka bwanji ziphaso

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya Час назад

      Ndizija feteleza amakagulidwa Kuma shop anyama...ziyalu hahahahhhaha

  • @EmsAdam-c1i
    @EmsAdam-c1i 5 часов назад +2

    Kukamwa ngat lichero galu iwe ukut Chan amalawi sangamvesetse

  • @BlessingsTomoka
    @BlessingsTomoka 52 минуты назад

    Anthu alembetsa bwanji ma ID alikunkhokwe?simuli serious

  • @ElizabethMwale-z3s
    @ElizabethMwale-z3s 29 минут назад

    Suleman munatani osawaomba makofi, kodi akufuna azibera mcp itengenso boma momwe likuzunzira anthumu, tibwererenso ku igupto kophula njerwa za moto.

  • @Patrickkaunda-me8it
    @Patrickkaunda-me8it Час назад

    Koma nkulu ameneyu ali ndi nxelu? kod alibe ma office opangla ximenexo? Tamachitankon manyaz

  • @ChisomocaxstonStima
    @ChisomocaxstonStima 5 часов назад +1

    Akulu tangotulani pansi udindo

  • @HenryChapweteka
    @HenryChapweteka 5 часов назад +1

    Kuyaluka kwenikweni zitsiru

  • @HappyBirchForest-zy8nq
    @HappyBirchForest-zy8nq 4 часа назад +1

    Aaaaaaa inu pano pankholoko panu asambo ma office mulibe kuti muzipangila kosungila chakudya? Ndipo munazuwitsa mtundu wa malawi kuwauza kuti mukhala ndi secret registration? Panyero pamanu pano wabodza iwe panyero Pako ine wamulilongwe momuno

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 4 часа назад +1

    Akulu sizomveka chito yanji mukugwirira Amalawi????

  • @JohnKayila
    @JohnKayila 4 часа назад +1

    Zimene akuyankha zikusiyana ndi afunsidwa

  • @nangaibraheem1758
    @nangaibraheem1758 2 часа назад

    Ningopejo yoo sau mungulugulu mwachimbusi, mweeee khola ja ngumba mpakana mupatikane achikalunga chatocheleje kwaaaa, mu mbwesese syenusyo

  • @BactonJasten
    @BactonJasten 4 часа назад +1

    Zosamveka zomwe ukuyankhula ukuchita chibwibwi iwe

  • @ThomasJohn-qt2jn
    @ThomasJohn-qt2jn 5 часов назад +1

    Ma ID onsewa alilongwe yokha mulilongwe muli anthu angati

  • @KaitanoMafuli-t5v
    @KaitanoMafuli-t5v 38 минут назад

    Nrb ndi mec mabungwe awa avunda. Kodi akumugwirira ntchito ndani,?

  • @LameckBanda-gk6ri
    @LameckBanda-gk6ri 3 часа назад +1

    DPP ndi ya mbava zokhazokha zikukumbukira m'mene tipex adabwera ,Akhara akulira mayo MCP ili kotsutsa nde ikulamura akudziwa kuti mwayi palibe nkharamba izikapuma kudikira nthawi yokadzara chinangwa

    • @EvansEgra
      @EvansEgra Час назад

      Ndizisiru, anyani a DPP ,mbava zinangozolowera basi

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye 28 минут назад

      Eeee kodi mwati kuyankhula inuyo kumenekoko 😂😂😂

  • @McfordKaunda
    @McfordKaunda 51 минуту назад

    Nanga bwanji athu afika kumeneko Inu ndi a MCP mukuziwana

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq Час назад

    We need auditors guys

  • @DicksonChibisa-w1v
    @DicksonChibisa-w1v 2 часа назад

    Smartmartc ichoke mugwa chogadama ndipo ikachoka olo half ya anthu simudzaipeza

  • @EsnartNkhoma-m2c
    @EsnartNkhoma-m2c 5 часов назад +2

    Kodi iwowo ziphasozo azitenga kuti poti aliyese amasunga yekha

  • @JacquereenPereira
    @JacquereenPereira 5 часов назад +1

    Muyaluka simunati musatinamize

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 4 часа назад

    Zoonama galuwe machende ako , bodza rako nenani chirungamo , NRB sipita kuware house , askupeperetseni AWA chonde . Bwanji sizinalengezedwe, palibe chimachitika dziko losalengeza.

  • @Maxielyies
    @Maxielyies 2 часа назад

    Even chinkhope chakecho chikuoneka kuti ndichimbava ichi chikufuna kuthandiza a MCP kubela zisankho

  • @elidajuma5207
    @elidajuma5207 3 часа назад

    Nsamboyu nditsilu kobasi izi sizinayambe zachitikako olo nde angasamuke ku area 3 kukafika kukanengo nzika asanazidziwitse zowona ndinu achitsilu ndithu mbuzi ya munthu

  • @MphatsoKaputa
    @MphatsoKaputa 18 минут назад

    Kodi atolankhani samatha kumumenya munthu chimbama akakhala kuti akuyankhula zopusa?

  • @Malawiofwanga
    @Malawiofwanga 2 часа назад

    Amenewa ndiagalu kwambiri kungot mbudzi zimenezi zikufunika kuphedwa

  • @AronChawinga
    @AronChawinga 4 часа назад +1

    Malo ose amene mumagwilila ntchito mumawauza amalawi nanga zaizi munawawuza?

  • @RawrenSonga
    @RawrenSonga 4 часа назад +2

    Opposition akukura ndi mamtha ndimthu 😂😂😂

  • @InacioCement-t7n
    @InacioCement-t7n 2 часа назад

    Palibe angathe kutembelera nkulu ameni atsogole tikampeza ,mmene zikuyenderamu wina nkumapanga zopusa

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 3 часа назад

    NRB ndi Electral Commission mwakayikiridwa kuyambira pachiyambi pa ntchito imeneyi chifukwa choonetsera mbali imene mukutsamira .

  • @HappySiyame
    @HappySiyame Час назад

    Musaipitse mbiri ya where house yanga cotsan ma card anu ndikubweretsera cimanga

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 3 часа назад

    Fotsek kumalawi kulibeko human rights iyaaaa

  • @Kamwachale
    @Kamwachale Час назад

    Ndizodabwisa usakhwekese zinthu, you mean medical equipment, or passport or any other item must be found in any warehouse ? So it shouldn't be a surprise to Malawians to see passports in ADMARC Depots. Can you also give any similar warehouse in any district where you are sorting out ID Cards

  • @MMK-p3y
    @MMK-p3y 2 часа назад

    Chavuta apa ndi transparency from NRB...

  • @noelliwonde8661
    @noelliwonde8661 3 часа назад

    ... zanu a NRB, ife siana kuti mungamatinamize

  • @ChembeKasinje-s2p
    @ChembeKasinje-s2p 3 часа назад

    Kod nrb ilibe ma office okhazikika amene amsungilako ma id

  • @JamesMachunga
    @JamesMachunga Час назад

    Iwe usaone ngati zikomo lamawi ndilamayi ako ukuyibeleka MCP iweyo ukugwila ntchito ya MCP usanamize anthu apa

  • @JerieWytonTengani
    @JerieWytonTengani 3 часа назад

    Bwanji osatenga a zipani zonse kuti akhale mboni ya zipani zawo.Apolice alibe ntchito pa nkhaniyi.

  • @JustinLipipa
    @JustinLipipa Час назад

    Mmmmmm mpovuta kukhulupulilira kwake, bwanji otsutsa samadziwa za malowa? Coz ngati madziwa bwanji amadabwa?

  • @JerieWytonTengani
    @JerieWytonTengani 3 часа назад

    Iwe ukunama a mcp akumaulula zimene mukupanga.Komatu musathawe

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 5 часов назад +2

    MUMUWUZE CHAKWERA BOLO YAKE ANTHU OYIPA INU

    • @EvansEgra
      @EvansEgra Час назад

      Mukhalira zomwezo, bwanji wosapeza zina zochita? Than kutukwana.

    • @PaulChauluka
      @PaulChauluka Час назад

      Pompano mulungu ayambe kuchita nawe kufikila uzadzindikile kuti unalankhula mopusa,bwanji ukutukwana munthu oti sanakulakwire?anthutu mukuputa tsoka

  • @SedoMissi-m3c
    @SedoMissi-m3c 5 минут назад

    HRDC yawulendo uno akuzidziwa ndi a boma

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 3 часа назад

    Koma ndiwe chitsiru ukunama kukhala ngati ukuuza ana bwanji?

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 3 часа назад

    No wonder Boma iliri limakagura fertilizer ku Butchery😂😂
    Moti pamenepo a Opposition mwakhutira ndi bodza limeneri.
    NRB ndi bungwe lokhazikika,anaenera kukhala ndi malo awo.
    Sangakasunge ziphaso ku NFRA.

  • @HappyMmenyanga
    @HappyMmenyanga 3 часа назад

    Kubulamtaya apangacampukuti a
    Nrb.

  • @LloydChiposa
    @LloydChiposa 3 часа назад

    Pena kuvomeleza kulakwisa ndi bwino akulu sizomatipaka zitosi maso

  • @DominiqueChitimbe
    @DominiqueChitimbe 4 часа назад +1

    wagwidwa bas ra 40 ramukwanira

  • @finchiadriano
    @finchiadriano Час назад

    Umbuli wa anthu otsutsa

  • @SydneyNyasuli
    @SydneyNyasuli 3 часа назад

    Opposition mwanyanya matha munaba moipa mukuganizaso ngati azanu ndi akuba mbuzi Inu mulibe manyazi

  • @SalimGrey
    @SalimGrey 7 минут назад

    Mbuli iwe ma LD afake amenewo system take iti

  • @ChipMkombezi
    @ChipMkombezi Час назад

    Asatinamize ameneyooooo Kodi chifukwa chani amaleka kupeleka thawi yoseyii maboma enaaa

  • @McshonWilliam
    @McshonWilliam 3 часа назад +1

    Tamuswen mbama kapeyo asawononge dziko LA Malawi

  • @JustinMakoka
    @JustinMakoka Час назад

    Anthu akuba inu

  • @AishaSanudia
    @AishaSanudia 3 часа назад

    Kodi ukalembetsa akumafuna fon number ndiyachani zinayamba zachitikako zisankho zonse za mbuyomu

  • @binosjoseph142
    @binosjoseph142 3 часа назад

    Palibe chomwe chikumveka, bwanji ankanena kuti munthu azikalembetsera ku ma office kwawo kokha osati ku ma voting centres angosiya udindo anthu amenewa ndi mbamva

  • @PreciousSteven-e5s
    @PreciousSteven-e5s 50 минут назад

    Asaname wakuba ameneyo amangidwe basi anthu aonjeza awa

  • @rabsonwisky4840
    @rabsonwisky4840 3 часа назад

    Funso mkumati bwanji kuli ma ID a lilongwe okha coz anthu amene alibe ma Id ndi ambiri ,tsono bwanji kuli a lilongwe òkha?

  • @LizzieBullah
    @LizzieBullah 2 часа назад

    Inuyo muli ndi ma office anu bwanji simunapite ku office kwanu musatitenge ngati ndife Ana wava takugwilani palibe wasangalala nawee

  • @ChisomoKalimira
    @ChisomoKalimira Час назад

    Muwononga dziko anthu inu 😢

  • @abduljabu8709
    @abduljabu8709 2 часа назад

    Zija amanena Bon Kalindo ndi zoona kuti ifeyo a Malawi tidapusa mopusa apapa onse a NRB amafunika kumenyedwa

    • @EvansEgra
      @EvansEgra Час назад

      Pita kamenye, Bola wadziwa komwe ali

  • @georgeaiwa8661
    @georgeaiwa8661 2 часа назад

    Osamukhwapula ndi khofi bwanji

  • @YunusuMaulidi
    @YunusuMaulidi 4 часа назад +1

    Bwanji ma birth certificate sanapezekeko kumeneko

  • @wezzieneba9238
    @wezzieneba9238 5 часов назад

    Just to add…..NRB man imwe umudziwe Yesu ndi ophunzira ake

  • @MathewsMandutu-q9l
    @MathewsMandutu-q9l 7 минут назад

    Wagwidwa iwe basi koma ndi ochenjela mopusa.

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 4 часа назад +1

    Akunama ameneyo.

  • @SylviaBulla
    @SylviaBulla Час назад

    Nkhope yokamba zoona sisowa

  • @ChikondiMzika
    @ChikondiMzika 2 часа назад

    Chimutu changokula alibe mzelu mbela mpaka liti anthu sakukufunani basi agalu opanda nzelu

  • @peterbyson6269
    @peterbyson6269 4 часа назад

    Office mulibe?

  • @LameckBanda-gk6ri
    @LameckBanda-gk6ri 3 часа назад

    DPP I Akhara ndi mphuri zokhazokha maburutu adazorowera kubera akhaura Chaka Chama

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 3 часа назад

    Mbamva....zeni zeni mcp ndi gulu lako

  • @SylvesterMachira
    @SylvesterMachira 3 часа назад +1

    Khumalo aboma kwapezekaso zinthu za boma vuto nchani ma mps ndi mburidi zophuzira aaaaaa zamanyazi