KODI MWAIMVA? ZAULULIKA CHIFUKWA CHOMWE MAYI AGNES NYALONJE ATULIRA PANSI UDINDO WAO MU BOMA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 дек 2024

Комментарии • 115

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 дня назад +10

    We need person like u mah , u ar such special for Malawians who suffering bcs of this government of mcp we love u mah for gd dissection

    • @brothermanjamkhosi1479
      @brothermanjamkhosi1479 2 дня назад

      A real man does the right thing because it is right and pleasing to God no matter what people say or write. So Malawians let's learn to be honest in making decisions.

  • @GideonNkosi-i4n
    @GideonNkosi-i4n 2 дня назад +4

    An excellent development. Life matters though, she only needs to be protected. If you are working with carnivals and cannibals, it is good to prepare your Armada.....

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 2 дня назад +9

    To me Agnes is a Hero in all ways. Umunthu alinawo kuposa enawa omwe sanaonetse kukhudzidwa ndi infa ya SKC.

  • @Chikulamayembe57
    @Chikulamayembe57 2 дня назад +6

    Jonah's analysis is brilliant!

  • @DavidPhiri-s6r
    @DavidPhiri-s6r 2 дня назад +1

    Wishing you a long life mama. You know the pain that the woman feels when giving birth. I want many of you in our country for the future Generations coming.

  • @DavidKanyemba-n2s
    @DavidKanyemba-n2s 2 дня назад +5

    Welcome development Agness
    Chikangawa party yatopetsa

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz День назад +2

    Manganyatu angovina uku chimwalilireni chilima 😂sikusija wapenga uku😢

  • @WilsonMalingamoyo-z5x
    @WilsonMalingamoyo-z5x 2 дня назад +8

    Mai Nyalonje ndi munthu wa ma principals ake ,ngati munthu siuli comfortable ndi Malo uli

  • @EmmanuelSimthole
    @EmmanuelSimthole 2 дня назад +6

    Mai oganiza bwno kwambili coz is same like pa banja ngati latha nkati mwaana ena mumakhala chkumbu mtima chamu2 yemwe mawakonda ngati anali bambo amapita kwa kwa bambo ngati analiso mai amapita kwamai ndgwlizane nao ao omwe anena kuti or kuxul kumakhala mphunzitsi wina oti akati akuchokapo pa xulpo ana ena amachokaso chilima anali mu2 yemwe wina aliyense sazamuiwala koma okonda a2 ake

  • @esthermafaiti3556
    @esthermafaiti3556 2 дня назад +7

    Amaiwo akukhudzidwa ndi imfa ya Chilima 😢
    Mzimu wa Chilima ukuwasowetsa mtendere

    • @AnorldKamponda
      @AnorldKamponda 2 дня назад

      Inutu ndopepera

    • @PrinceThom-pe6ie
      @PrinceThom-pe6ie 2 дня назад

      Kum'yini Kwa amako nyau iwe.kodi womwe adapha chilima siwukwaziwa iwe nakumtumbo

  • @TadalaMtipe
    @TadalaMtipe День назад

    Good idea mum

  • @EmmanuelChavulla
    @EmmanuelChavulla 2 дня назад +2

    Wachita bwino kusiya udindo, boma ladzigawenga, ndipo mmayiyu ndiwophunzila kwambiri kuposa galuyu Chikangawa

  • @DickinsonLikhoma
    @DickinsonLikhoma 2 дня назад +5

    aululana anapha chilima asala pang'ono

  • @hesbaluku7281
    @hesbaluku7281 2 дня назад +5

    Mai aja ndimuthu wakulu woganiza boo alibe dyere ngat nduna zinazi ma yudasi

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl День назад

    God bless Agnes🙏🙏🙏🙏

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 2 дня назад +3

    Maiyu akuopa kuti,pangapite nthawi ya italibwanji nayeso adzamupha ngati Dr chilima RIP wachita mantha ameneyu apite ndi mtendele kusiyana ndi kuti amwalire mukumudziwa chikangawa amamenya nkhondo ya pansi adzamusowetsa wachita bwino wachoka ndi moyo.

    • @DelubyMarko
      @DelubyMarko 2 дня назад

      She is telling us how hard it is in this government coz this is not what we are expected to this government according the promises we were told.

  • @TriceBeib-e6x
    @TriceBeib-e6x 2 дня назад +2

    Well done Ag

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 2 дня назад +1

    The downfall of Chikangawa party😂😂😂

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz День назад

    Amayenera kulandira chifukwa adauzidwa adikire kaye apule chifukwa adali ali mu system, that woman is smart and good

  • @MakabaBauleni-c2i
    @MakabaBauleni-c2i 2 дня назад +9

    Bola akhale otetedzedwa cz atha kumuphaxotu kufuna kusokoneza umboni ,Mai uyu akuonesa kt akudziwa china chake za imfa ya Chilima

    • @Angel-dt6oe
      @Angel-dt6oe 2 дня назад

      Ur true

    • @bridgetmajor3646
      @bridgetmajor3646 2 дня назад +1

      live. ......kma ...... aliyese.....amaziwa....kuti anthu anja....anachita kumphedwa.......fact

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 2 дня назад +2

    I was listening to a clp yesterday on RUclips where they were talking of the 10 most rich people in Malawi and our president LMC is the richest person in Malawi ( 300 million USD ) My concern is to know how much he had declared on taking the presidency .

    • @YohaneNthala-n9p
      @YohaneNthala-n9p 2 дня назад

      Anthu amapanga kungofuna kut ena aziganiza molakwika

    • @DavidMalewa
      @DavidMalewa День назад

      Kkkkkkkkk misonkho yathu imeneyo sizake

  • @EssauChimpango
    @EssauChimpango 8 часов назад

    Setting best example

  • @HenelyBaskolo
    @HenelyBaskolo 2 дня назад +4

    Maganizo abwino komanso anzeru enawonso atengelepo phunziro

  • @WhyteSmart
    @WhyteSmart 2 дня назад +1

    Good sound zikumveka

  • @CHARLESMSAMSON
    @CHARLESMSAMSON День назад

    Congratulations

  • @owenchikopa7266
    @owenchikopa7266 День назад

    She deserves to be called honorable osati enawa

  • @M.shukriAdams
    @M.shukriAdams 2 дня назад +1

    Ulemu wanu mayi ndiwochepa angapange dzimenezi mulungu akudalitseni

  • @SylvesterLikumba
    @SylvesterLikumba День назад

    Aulusi, m'zoona zomwe ayakhula mr wo

  • @RachealHarawa-xc9gs
    @RachealHarawa-xc9gs 2 дня назад +4

    Pena kungofika straight pankhaniyo ndibwino timakunyadirani

  • @JimmyMaster-l1x
    @JimmyMaster-l1x 2 дня назад

    P K umakwana iweyoooo pa mkulu more 🔥 gays

  • @moirngwira4748
    @moirngwira4748 День назад

    Roots asogoleli , dyela a tree die when roots are cut off, grafting kapena but grafting a mango to an orange roots I don't think it's possible.

  • @BenjaminNgwira-r4q
    @BenjaminNgwira-r4q День назад

    Akazi amasiyana kwambiri ndi amuna ,anakhumudawa zikuonetsa chonchi ndiye atulutse satanesatane kuti time bwino.Maganizo anga anene choona chenicheni.

  • @AlicksonMakata
    @AlicksonMakata 19 часов назад

    Kungoti a Dr Lazarus Chakwera amagwira ntchito ndi adani koma Mulungu akusefa yekha ndi kuima kumbali ya Chakwera.

  • @RobertMuyira
    @RobertMuyira 2 дня назад +1

    Agness mulungu akudaliseni

  • @DoYouKnow3838
    @DoYouKnow3838 2 дня назад +2

    Makosana ukuonjeza kwambiri, kuchuluka zoyankhura, zikubowa 😮

  • @josephymunthali
    @josephymunthali 8 часов назад

    Wakanika kugwira bwino ntchito,musaphatikize imfa ya chilima ndi unduna wa mayiyu.min of security ndi min of labour ,ndizosiyana kutali

    • @SwalleyScotch-n3y
      @SwalleyScotch-n3y 5 часов назад

      Tachoka iwe sakufuna kuptilira kugwra ntchito ndzigawenga

  • @SwalleyScotch-n3y
    @SwalleyScotch-n3y 5 часов назад

    Afufuzidwe coz akhoza kutipatsa ka umbon ka ngoz ija

  • @EmmanuelMkhumbi
    @EmmanuelMkhumbi 2 дня назад

    Kodi Ku parliament ko sangapange lamulo loti aliyense wammboma akakhala kuti akuganizilidwa pa mulandu ulionse azitula pansi udindo .nanga si ambiri angapnge zimenezi

  • @Jamilahchinyama-y9b
    @Jamilahchinyama-y9b День назад

    Amanganya akukanika kutura pansi udindo chifukwa akudziwa kuti iyeyo ndi chakwera ndiamene anapereka chilima

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 2 дня назад +2

    Aggie wacita bwino moto sufuka popanda usi. Cilipo comwe cikangawa ndi azake a mcp amafuna kuwapanga apa ticedwepo.

    • @mwai19
      @mwai19 22 часа назад

      Utsi sufuka popanda moto rather

  • @Alexanderdzungu-i5o
    @Alexanderdzungu-i5o 2 дня назад

    A wonder Msiska mwafikapo plus yrs friends

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuli День назад

    Plz plz 😭😭 dziwani Kuti Mai uyu
    Amupha ,bcz akudziwa kanthu pa
    Zainfa ya Anthu 9 osalakwa Aja ndiye asamale ndithu plz

  • @AnorldKamponda
    @AnorldKamponda 2 дня назад +1

    Tax money from July ngati amamupatsabe simkufuna Kwake,,, iyoyo si nkhani iwe Kaya akukuti ndani ukuyankhula ukowe. Not Phiri

  • @chawanangwamkandawire5850
    @chawanangwamkandawire5850 2 дня назад

    Honestly speaking unlike Kamtukule, Nyalonje was a non performa if anything she might have been keept just to balance up representation in the alliance.

  • @InessSalimu
    @InessSalimu День назад

    achina usi gulu la anthu adyela ali kakaka

  • @KelsonThom
    @KelsonThom 2 дня назад

    President analakwitsa kuchedwa kuvomeleza chifukwa,chomwe mayiwa ankasiila udindi zilingati anawa tsekeleza zomwe ankafuna atanena mu nthawi yake

  • @ChalembecaDalitsoMughogho
    @ChalembecaDalitsoMughogho День назад

    Mulungu aludalitseni mama podzisungila ulemu komanso kulemekeza s k c

  • @EmmanuelSteve-q7b
    @EmmanuelSteve-q7b 2 дня назад

    Malawi akufuna anthu ngt awa koma akusowa,, ambir ndiawa analonjeza kwamalawi koma palibe chimene akupangapo or chimodzi

  • @blessingsthom5643
    @blessingsthom5643 2 дня назад

    Pajatu maiwa, bambo akunyumba kwawo ndi mzungu, so maganizidwe awo nchizungu kale

  • @petrooverton6643
    @petrooverton6643 10 часов назад

    kalelo analikuti kuusia udindoo zoonadi wava kutetha chifukwa waziwa kuti balibe chake kukusonyeza kuti wathawa kulandindwa mpando

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 дня назад +2

    Something is fishy in this government that we don't know.

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 2 дня назад

    Amalipidwadwe maripiro ache chifukwa sadayankhidwe pempho lake losiya ntchito . Bvuto ndiolemba ntchitoyo .

  • @KazembeGwedeza-b9u
    @KazembeGwedeza-b9u 2 дня назад

    Komanso malemu Chiwaya anatula pansi Unduna.

  • @WhyteSmart
    @WhyteSmart 2 дня назад +1

    Sound ikumasokoneza chifukwa ikumakwera

  • @SwalleyScotch-n3y
    @SwalleyScotch-n3y 5 часов назад

    Tiuzen zambr mam

  • @Lindamambiya
    @Lindamambiya 2 дня назад

    😊

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 2 дня назад

    Watinso membala wa chipani cha UDF inspector general akuyenera kusiya ntchito chifukwa cholora zigawenga kuopseza nzika.

  • @Stretor
    @Stretor 2 дня назад +1

    Nkazi woganiza kwambili komanso kuganiza mwakuya

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda День назад

    Amayi ndinu chisanzo chabwino

  • @AnorldKamponda
    @AnorldKamponda 2 дня назад +3

    Moni kwa mlongo wanga Mvera ka mtukule.......

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye 2 дня назад

      Kkkk chamawu ngat mamuna chija eeee Chikamtukule ndichadyera mmmm

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 2 дня назад

      ​@TysonM😂😂😂😂😂😂wenye

  • @CliveMhango-e9m
    @CliveMhango-e9m День назад

    Nyalonje ntchito wa kutondeka. Lutanga kapumule na kutondeka kwako.

  • @BERNARDSIKWESE
    @BERNARDSIKWESE 2 дня назад +1

    Ya

  • @aubreyhills
    @aubreyhills 2 дня назад +3

    Izi zikuwonetsa kuti zizili bwino m'boma limeneli

    • @FracksonMadani
      @FracksonMadani 2 дня назад +1

      Boma ndilomweri tingosintha utsogoleri 😂😂😂😂

  • @EmmanuelMalikita
    @EmmanuelMalikita День назад

    No need to work with olephera

  • @EllenJimmy-f9l
    @EllenJimmy-f9l День назад

    Zabwino chinsinsi sapanga gulu

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 2 дня назад

    There is smoke without fire. Timva zambiri.

    • @joegibsonzulu2599
      @joegibsonzulu2599 2 дня назад

      🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @GiftLambati
    @GiftLambati 2 дня назад +2

    Alexander ndi inu a MCP mukukamba zopanda nzeru ndi zoduka mutu zomwe mukulemba apazi fotseck

  • @EsimeMamama
    @EsimeMamama 2 дня назад

    Congratulations mom potula pansi udindo, moyo ndi mpamba, we don't know who's next after Chilima

  • @YohaneNthala-n9p
    @YohaneNthala-n9p 2 дня назад

    Zangomukwana ndarama

  • @ChikumbutsoTsalangu
    @ChikumbutsoTsalangu 2 дня назад

    Uyu chi khale chi sazo

  • @Alexanderdzungu-i5o
    @Alexanderdzungu-i5o 2 дня назад +1

    Wafuna yekha kutula pasi udindo azimayi ndi ambiri ophuzira kuposaso iyeyo

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye 2 дня назад

      Aaa inutu nkhaniyi simukuitsatira ndi chidwitu bro 😂😂

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 2 дня назад

      ​@@TysonMwenyeawo ndi achikangawa inu

  • @Alexanderdzungu-i5o
    @Alexanderdzungu-i5o 2 дня назад

    Kodi Chilima anali wamuyaya
    Ngawunju ali kuti and Chasowa mati chilima chilima bwanji pangani zanu

    • @dinchisale
      @dinchisale 2 дня назад

      Ndiwe chitsiru eti?

    • @Alexanderdzungu-i5o
      @Alexanderdzungu-i5o 2 дня назад

      Chitsilu ndiwe wapulika fumba awo nganya

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye 2 дня назад

      Ineyo sindimatukwana koma ndiphunzilira paiwe moti pamnyero pako ndithu.Mtumbuka osasamba iwee

    • @CharlieChirwa
      @CharlieChirwa 2 дня назад

      Mboli yako wava

    • @GeofreyBandah
      @GeofreyBandah 2 дня назад

      Pamtumbo pa mai wako wandikwiyitsa ndiwe chitsiru

  • @Trishamanda-b5z
    @Trishamanda-b5z 2 дня назад

    Mmmmmmm

  • @Alexanderdzungu-i5o
    @Alexanderdzungu-i5o 2 дня назад

    Atola khani achi Malawi kukonda kukokomeza basi

  • @Alexanderdzungu-i5o
    @Alexanderdzungu-i5o 2 дня назад

    Nyalonje si wa MCP tiyeni nayo uko olo u MP sadzawina

    • @GodfreyWhayo-hh1dm
      @GodfreyWhayo-hh1dm 2 дня назад

      Maiyu adasankhidwa ndi anthu a dera lakwao osati ndi Malawi yense .

    • @Alexanderdzungu-i5o
      @Alexanderdzungu-i5o 2 дня назад

      Zake izo amadya ndi ife ngati na ine nono ati wodziwa koma zaziiiiiiiii

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye 2 дня назад

      Kodi iweyo ukudziva kutchuka chaniii?

    • @FloraBanda-w7t
      @FloraBanda-w7t День назад

      Macadet

    • @TysonMwenye
      @TysonMwenye День назад

      Ucadet winawu mmmm umangosavuka nawotu