Limpopo FM katswiri Ntanyiwa watiuza dzina la vice president watsopano uja tazidziwa nawo

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 июн 2024

Комментарии • 72

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Месяц назад +6

    Achakwera zeru mulibe ndani sakuziwa Kuti ndinu munapha achilima manyazi mulibe

  • @ChrispoGawani
    @ChrispoGawani Месяц назад

    😢 Malawi wavunda basi azisogoleri saganizanso nkomwe za anthu osauka onani kwacha pano momwe yathera Limpopo ndi massive keep it up we Love Limpopo fm

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y Месяц назад +1

    Keep it up broo. Chakwera munthu wakupha uyu.Wapha abale athu ngati agalu

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz Месяц назад +4

    Angosowa zochita a mcp wo

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Месяц назад +6

    We don't trust MDF and malawi Police for internal security ,
    As Malawians we will defend ourselves from this evil government of MCP .
    ALLAH will protect every malawian .

  • @user-jn2oc3cn3q
    @user-jn2oc3cn3q Месяц назад +1

    Kmatu chakwera manyazi akhare nawo akapita kuja ndikukonda ndege kwakekuja azikamusala azungu

  • @yasitafuphiri-nw2he
    @yasitafuphiri-nw2he Месяц назад +1

    Kodi limpopo fm nkhani zaku malawi basi 😮.?

  • @user-kw7wr4kq9w
    @user-kw7wr4kq9w Месяц назад +1

    That's why you mislead people from Ntcheu and they got killed, it's a shame

  • @GenialaChalera
    @GenialaChalera Месяц назад

    Mzosatheka zimenezo ukukamba zosaveka galu iwe noman akufuna mpando

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz Месяц назад +1

    Chakwela tulapansi udindo mwansanga

  • @SaidiMilaji-dk8sr
    @SaidiMilaji-dk8sr Месяц назад

    Tikulila CHILIMA ife misozi ilikugwela mmimba mmesa mumati olila samutseka pakamwa?

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Месяц назад +1

    Iwe ukati ntanyiwa chisiru wakulakwira chani cadet iwe, chirungamo akuyankhula

  • @ChrispoGawani
    @ChrispoGawani Месяц назад

    Congeresi ndiyokupha kuyambira kale koma pano Malawi wasukusula zivuta kwambiri

  • @EmmanuelMarko-lf1oz
    @EmmanuelMarko-lf1oz Месяц назад

    Wabodza iwe. Sitingakunvereso iwe.

  • @davidkayangemakala7957
    @davidkayangemakala7957 Месяц назад +1

    Enanu mukulipilidwa fees ndi MCP Ena mukudyesedya ndi MCP yomweyi chifukwachake yifa yachilima cmakukhuzani musadane ndi ntanyiwa

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 Месяц назад

    Azunguladi muthu mwazi wamuthu uwazunguza chakwera ndi mbuzi pamodzi ndinduna zake zonse

  • @user-wg8tp8in1v
    @user-wg8tp8in1v Месяц назад

    Apa zikugwirizana ndi zomwe zatuluka?

  • @Alliechamolie
    @Alliechamolie Месяц назад

    Kodi mukamadana ndi social media ,msikulomwe ndige inasowa social media inakambakut achilima amwalila pemene amboma amakana kenako mumamvomeledza Mawa wake , ndiye athu adzimvela dziti

  • @alimamandra7115
    @alimamandra7115 Месяц назад

    😊😊😊anhaino munthu amwalila sapanoyapa atha thathtu muakhaly osachithe mwafuna muina kuthy azakhale vc presidente a bala azaganizia chyani.

  • @HagEva1
    @HagEva1 Месяц назад

    Akuazunza ngati mmne anazunzila marefugie!!😢😢

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw Месяц назад

    Musileni mulungu aweluze monga mwantchito yake pali mwazi wamunthu sipanama ayi chilima ayakha yekha mulungu umboni akuwuziwa

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Месяц назад

    Chakwela you mast go

  • @ChawingaMwaseteza
    @ChawingaMwaseteza Месяц назад

    Olo utikwane chosangalasa ndichoti ukumusatila bwino ntanyuwa..zilibwino udziwadziwitsa anyapapi akowo zomwe akulankhula,,ntanyiwa emweyooooooo

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o Месяц назад +2

    Ayenera amangidwe

  • @charlesbanda7594
    @charlesbanda7594 Месяц назад

    Kodi anthu mudana ndi chilungamo bwanji isiyeni Limpopo FM a lone

  • @user-is3jt9el8l
    @user-is3jt9el8l Месяц назад

    Tifufuzireniko za magalimoto alowa munowa

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Месяц назад

    Koma aganyu achakwera muli mmabvuto amakutumani ndani kuti mudzvera limpompo

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 Месяц назад

    Mulungu akuona misozi yathu

  • @MercyNyachi
    @MercyNyachi Месяц назад

    Mcp is 😈 👿 indeed I hate this party with my soul😢

  • @user-yv3jp3it2t
    @user-yv3jp3it2t Месяц назад

    Nonse amene akuyikila MCP kumbuyo ndinu athu opanda nzelu mukuvuti zomwe akubazo simudya nawo musiyeni Ntanyiwa alakhule zomwe akudziwa mukati umboni mukufunatso umboni wina Musamakhale athu opepela wake up guys dziko ndi lathu ili

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Месяц назад

    Mabodzatu awa

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Месяц назад

    Anthu akucheu mukaona anthu akubwera kuzamanga mp wanu uko.muzawagendeso musawasekerere ayi koma chakwera niusataniki wake osazamuvoteraso ayi nimunthu oyipa chakwerayo bwanji iyeyu osamumanga boni karindo akurephera kumumanga bwanji

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no Месяц назад

    Uyambe ndiwe ukolozera motowe, adakulakwira chian a president ?

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Месяц назад

    Usatana wa chakwera wafika popenga nawo

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no Месяц назад

    Uyambe ndiwe

  • @zebronchipate7297
    @zebronchipate7297 28 дней назад

    Wapala

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela Месяц назад

    Malawi kuimba kwa late matafale

  • @PetroMatias
    @PetroMatias Месяц назад

    Sizigwilizana zimenedzo

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Месяц назад

    Chisilu chamunthu mmalo moti mzigwira ntchito ku o ku sa nfiwe chisilu kwabasi

  • @alfredchigwankhu7355
    @alfredchigwankhu7355 Месяц назад

    iwetu uimbidwa mulandu obweretsa chisoko ezo mdziko

  • @AticksonRevesonSemele-lk3du
    @AticksonRevesonSemele-lk3du Месяц назад

    Mmmmmmmmmmmmmmmmmm koma Nde malodzatu

  • @ChaloseMoyenda
    @ChaloseMoyenda Месяц назад

    Changu udindo pansi😂😂😂

  • @Stewartchikoja
    @Stewartchikoja Месяц назад

    Atiputa angoni dala

  • @alimamandra7115
    @alimamandra7115 Месяц назад

    Iweo simulila simukhaiankhula chonchi?

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz Месяц назад +1

    Adad oyeeeeeeeeee❤❤❤❤❤

  • @Alliechamolie
    @Alliechamolie Месяц назад

    Agalu awa mcp

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO Месяц назад

    Mmmmm

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz Месяц назад

    Chakwela galu iwe

  • @user-uz2wm9uq4g
    @user-uz2wm9uq4g Месяц назад

    Apenga zenizeni sanati avula

  • @FrancisDinala
    @FrancisDinala Месяц назад

    Nde mwat azunguso akuziwa eti ine ndikuona kut mwapanga edit za mzunguzo sure ndi Edit iyi

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Месяц назад

    Mmmmm ,masiku ano kulibe zomangana chisawawa ABUSA mwatni ?? ADAD sadaphepo MUNTHU ,muziwona a MCP, anthu amakonda MUNTHU wabwino 😂😂😂😂

  • @JhdaLifi-vu9sd
    @JhdaLifi-vu9sd Месяц назад

    Limpompo fm

  • @user-tu8sv2pu9z
    @user-tu8sv2pu9z Месяц назад

    😂😂😂

  • @isaacedsonmabulesi
    @isaacedsonmabulesi Месяц назад

    asamangidwe alakwachani

  • @PreciousChiphwanya
    @PreciousChiphwanya Месяц назад

    Asiyeni awamange, sadzaluza okha mlanduwo, ndi nkhani yopanda umboni imeneyo, chifukwa adzawauaza kut ndikufuna mundipatse umboni kut ndine amene ndinawatuma give me umboni ogwirika video yake y tione kut ndinawauza anthu kut adzikuwa, at the end Boma lidzapezeka kuti likuluza ndalama zankhani nkhani kulipira.

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад

    Wachamba iweti mesa wenkha umati avotela bushiri anapikisana ndinankhumwa lero ukuti chidati malunga wankhuta batata eti

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no Месяц назад

    Eyaa apanga bwino chifukwa zikuonjeza , kunyoza , kutukwana , si zooona , malo mopempherela wakufayo , pano mwapanga zomangotukwana , ayi zaonjeza koma ,

  • @YusufuUsumani
    @YusufuUsumani Месяц назад +1

    adadi❤❤❤❤❤❤

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o Месяц назад +1

    Chitsiru Cha munthu ntanyiwa

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y Месяц назад

    Keep it up broo. Chakwera munthu wakupha uyu.Wapha abale athu ngati agalu