UKU NDIYE YALAKWA, ANTHU AKUCHILIMBA BLANTYRE ZOMWE ACHITA🙌🙌🙌

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 5 сен 2024

Комментарии • 563

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 Месяц назад +8

    Mfiti zopemphera Chakwera ndi mbale wake Usi ndipo anthu inuyo Mulungu akuyendelereni mwapadera ( SKC FOREVER IN OUR HEARTS 💔)

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Месяц назад +11

    Inu agaru yehova wake uti,kupusa ziwanda yehova wamoyo sakhala ndimbava akuba akumpha, mulungu azakulangani osapota zopusa ukule garu iwe chairman

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v Месяц назад +52

    Kodi ngongole imasitha dziko poti mukufuna mwaonjezere anthu mamvuto musise katundu osati ngongole

    • @ManganiStanley
      @ManganiStanley Месяц назад +1

      Ndipo live atsitse katundu

    • @CatherineDesire
      @CatherineDesire Месяц назад +1

      Ngongole pa campaign aoneke abwino

    • @prettytambala5687
      @prettytambala5687 Месяц назад +2

      God bless this thinking, ineso wad like why keeping poor malawians in a bandage yangongole mmalo mokaika mankhwala mzipatara, kutsitsa katundu, kuwaonjezera aziphuzitsi ma salaries kuti aliyese azifikira zinthu mosavuta. Izi zikungoperekaso mwayi kwa mbava za m,bomazo kuti ziziba ndalama in the name of kupereka ngongole kwa amalawi mxiiiii

    • @CatherineDesire
      @CatherineDesire Месяц назад

      @@user-hl3st3cc4v maona Ngati ndi thandidzo angobitsa Chichewa kodi NDI ngongore yangati ya fincca adzaole tidziwiya ,adzatenge timinda NDI tinyumba akalephera kubwedza

    • @Gautengstanzo
      @Gautengstanzo Месяц назад

      Zimayamba wez wez, sungapangile zinthu pakamodzi

  • @JasonMailos
    @JasonMailos Месяц назад +15

    Mwamchitq bwino munthu wakupha ameneyo angampeleke chilima zoona

    • @Henry-vw2cz
      @Henry-vw2cz Месяц назад +1

      Midzimu yakwiya😂😂😂😂😂😂

  • @Cathy-oc7vd
    @Cathy-oc7vd Месяц назад +8

    Anthu siyani kaduka.. mulungu simunthu..
    Mulungu anaziwa kale kuti Usi azakhalapo vice president wa dziko la Malawi. Tivomereze chifunilo cha yehova pa dziko lathu la Malawi.

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Месяц назад +16

    Awus mulibe nselu misimu yah andu 8 yinkukusatilani nkomaso awusseni amalawi ndege yinangwa bwanji osat samanyi munkunenaso mulungu ankuphasani matenda onyassa phamodsi ndi ashankwela mulungu anankuwonani 👌👌👌👌🙏

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад +1

      @@esaMoha-dm4kj inu mulungu????

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 Месяц назад

      @@esaMoha-dm4kj pelepa kuwecheta iseseni. Ambuje Mlungu akunde yakuti uchimbichimbi uyiche kwa mmwejo. Ajaliwe wakulungwa.

    • @user-qw3hj1hc7s
      @user-qw3hj1hc7s Месяц назад +1

      Mcp chipan chonunkha kwambiri 😢😢

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      @@user-qw3hj1hc7s chonunkhila ndichiti???

    • @JamesNgwaya-vz1ox
      @JamesNgwaya-vz1ox Месяц назад +1

      Kupha

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 Месяц назад +42

    Sewelo leni leni tikufelanji apapa pangosowa mulelemba

    • @LuundoJohnkabage
      @LuundoJohnkabage Месяц назад +2

      😂😂

    • @alicehananiya
      @alicehananiya Месяц назад +2

      Eya pakusowatso make sikono ndi winiko

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 Месяц назад +2

      Dramatising politics .this guy is useless

    • @lucianogeoffrey4275
      @lucianogeoffrey4275 Месяц назад

      Nde mwati ndinu a UTM? Muzivere chisoni bwana😢😢

    • @WitnessPhiri-zr9uf
      @WitnessPhiri-zr9uf Месяц назад

      Nde anthu mukuwona akakupasani ngongolezo mulemela mumene Zinthu zikudulilamu tsiku ndi tsiku ndalama ya ngongole siyingakupindulileni asise zinthu pandalama yanu yochepayo ikupindulilani 😢

  • @JenniferFyson
    @JenniferFyson Месяц назад +3

    Powerful prayer 🙏

  • @user-nr4mi7pt8g
    @user-nr4mi7pt8g Месяц назад +4

    Anthu owopa mulungu ngati abusa a chakwera

  • @stevenfrancism3638
    @stevenfrancism3638 Месяц назад +2

    Amalawi tichenjere😢 kwambiri. Timva zinthu.lets think and work together.Tiwunikilane. and love each other ❤

  • @trymhango1509
    @trymhango1509 Месяц назад +2

    Abale mundiuzireko a vp nzeru alibe chifukwa iwo amayenera asanayambe kulankhura kunkhalakaye cohete ose pasonkhanowo popereka ulemu kwa skc ndikunena zimu wawo uutse mtentere kenako kuwapepesa a malawi zaifa ya chilima kwinako mkumakamba mbwerera zakezo

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn Месяц назад +9

    Amalawi chonde osayelekeza kuvotela izi

  • @fumbomumba5016
    @fumbomumba5016 Месяц назад +8

    Palibeletu Fundo apa koma A vp awa he's only proud kuti ndi vice president

    • @madakabichi2251
      @madakabichi2251 Месяц назад +1

      Kape uyu

    • @GeraldChisamba
      @GeraldChisamba Месяц назад

      ​@@madakabichi2251kape umamudziwa koma 😂😂😂😂 mesa kape amakhala osauka ngat iweyo

  • @lameckmajiga5426
    @lameckmajiga5426 Месяц назад +2

    Bwana micle usi athu amakukondani kwambili!! Koma pa game yomwe mukusewela ndichakwelayi athu akutulukani chifukwa azindikila kuti inu muli under M.C.P mukanakhala kuti mukutengapo gawo muma program ama candle 🕯 komanso kuchita zomwe anthu ena a UTM akuchita mukanayenda moyela kwambili komanso zikuwoneka kuti mukufuna kuzutsa chipani chanu cho odya zake alibe mulandu!!! Ife tikanakuvotelani chifukwa cha chilima koma mwaluza basi!!! Pepani bwana usi!!!

  • @KizitoChikuni-dy9us
    @KizitoChikuni-dy9us Месяц назад +1

    Akuwa patipo anthuwo yogulisira kut tionere imeneyo? Zopoila

  • @user-pb7mn1kx4t
    @user-pb7mn1kx4t Месяц назад +4

    Blantyre inachulukadi mbuzi,am from by city koma delali ndi la nkhumba basi

  • @YatoRoy-kt4lh
    @YatoRoy-kt4lh Месяц назад +4

    The guy has a good heart

  • @WedsonZuzewatayamakina-rn8yp
    @WedsonZuzewatayamakina-rn8yp Месяц назад +4

    Ndiye mwati chani😂😂😂😂 ine sindinatolepo mfundo atah olo pang'ono

  • @geokah78
    @geokah78 Месяц назад

    We need a system that everyone fine support without being influenced by any political figure. Dr Usi reflect on this.

  • @user-qt7hx7hq4f
    @user-qt7hx7hq4f Месяц назад +1

    Nde munayenda basi nkumawauza anthu zoti ndinkavala ma kabudula awiri ..zitithandiza chani ngt a Malawi

  • @tiwongehojaney5873
    @tiwongehojaney5873 Месяц назад +2

    A chairman wo akalamba😂😂😂

  • @Cathy-oc7vd
    @Cathy-oc7vd Месяц назад +3

    Ndiye kukuwa mwalemba pa munthu wa nkhanipo akuwa pati reporter wa bodza iwe

    • @GeraldChisamba
      @GeraldChisamba Месяц назад

      😂😂😂😂 😂😂😂 always cadet amatero mix mizimu yama albino

  • @EmmanuelstoneyJere
    @EmmanuelstoneyJere Месяц назад +1

    Olo opepherayo akuona ngati akupanga sewero ndi manganya

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson Месяц назад +6

    Mizimu ya anthu 13 yayamba kuonesa unya nawo ayise kufupika ngt mchimba

  • @augustMag
    @augustMag Месяц назад +3

    Apa ndiye ndikufuna nyimbo ija anayimba Joseph mkasa anasankha olakwika

  • @randettaclaan
    @randettaclaan Месяц назад +4

    Kodi Dr. Micheal Usi ndiu wa DPP kapena wa UTM///////////////// Nanga slogun ya woyeee ndi ya UTM

  • @NenaniMwamadi
    @NenaniMwamadi Месяц назад +2

    Zasewerooo bas usiì

  • @RachelKamanga-vt3fp
    @RachelKamanga-vt3fp Месяц назад

    Ambuye akupaseni moyo wautali me utsi muzina loti musinthe malawi wathu
    Ufumu unasata Daved kuubus chifukwa choti mulungu sakuva zaanthu

  • @user-vw7tj2ss3l
    @user-vw7tj2ss3l Месяц назад +1

    Fundo pa line katundu anali azanu anja inu ndi achimulilenji sakusiyan

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Месяц назад +6

    Mbuzi iyi ya MCP. Usi usanamize anthu ndiwe wa MCP. Wavala za MCP osati UTM. Ukunamiza ndani nyani iwe. Pamtumbo pako Usiku.

    • @ManganiStanley
      @ManganiStanley Месяц назад +1

      Galu kwambiri ndipo akundinyansa kwambiri

    • @omardyman8083
      @omardyman8083 Месяц назад +1

      Osaiwalatu ndimazimbabwe awaa​@@ManganiStanley

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y Месяц назад +3

    *wayankhulapotu .. Koma ndege inagwa chifukwa chani bwana*??

  • @LovenessShugar
    @LovenessShugar 2 дня назад

    Ine ndikufuna Dr usi ife tikufuna thandizo lawo ngongole atipase

  • @JohnKanjete
    @JohnKanjete Месяц назад

    🤗🤗🤗🤗anthu sakukufunani bamboo asikono mwakhalila mpando wamagazi 😊

  • @user-nv3rf7bl7r
    @user-nv3rf7bl7r Месяц назад +5

    Inuso ndinu a boza pena nanga akuwa pati apa chimutima cha nyawu icho

  • @HappyBirchForest-zy8nq
    @HappyBirchForest-zy8nq Месяц назад +5

    Ngongole muyambe mwaona tikuyandikila mavoti 4 years munalikuti kuti muwapase ngongole mwabwera nthawi yochedwa inu mwapha chilima nde mukuona kumene ali chilima akusangalala muvutikapo apa panya panu ana anjoka inu

    • @user-hr6dj4xc8l
      @user-hr6dj4xc8l Месяц назад

      Ngongole ilibe nthawi , utha kutenga olo tsiku lovota

    • @prettytambala5687
      @prettytambala5687 Месяц назад

      You can say this again, anthu tavutika all these years iwowa qnali pheee ,kumangokweza zinthu ndalama akusungira campaign? Rubbish

    • @HappyBirchForest-zy8nq
      @HappyBirchForest-zy8nq Месяц назад

      @@prettytambala5687 eti nde panopa akimalubwa zausilu aba ndalama za amalawi ena agwidwa nazo zana

    • @HappyBirchForest-zy8nq
      @HappyBirchForest-zy8nq Месяц назад

      @@user-hr6dj4xc8l khalani ndi umunthu inu nde ubwino wakuba ndalama ndi uti? Mesa kumangophelatu dziko chithyola anamupeza nazo zana president nkumati musiyeni azipita what doesn't mean you're rubbish

  • @patesnkajenda4258
    @patesnkajenda4258 Месяц назад +2

    Fundo palibe bwana ingodyelanitu basssssss😂😂😂😂😂😂

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Месяц назад +1

    Uyudi ndi manganya srs ,masewero paliponse

  • @RatifMakiyi
    @RatifMakiyi 6 дней назад

    Usi Khala serious ukulongosola zithu zisamveka kutundu wa malawi

  • @HarrisMathew-ve5ib
    @HarrisMathew-ve5ib Месяц назад +2

    Akuti kukhalatu ma Team ampira uku 😂 😂

  • @alfredbamusi1093
    @alfredbamusi1093 Месяц назад

    Ndi ntchito yabwino kuti akuzipanga available to the public anthu apempha ngongole kuti upange boost capital chomwe ndi chabwino koma zimafunika kuti ayambile kukonza moyo wa ma customer amene ali anthu ogwila ntchito m'boma ndinso ma labour onse azipasidwa ma salaries omwe atazipanga match kukwera kwa mitengo ya zinthu omwe ndi ma buyer ama businesses amene akuvuta kupita pa tsogolo

  • @CathrineBizza
    @CathrineBizza Месяц назад +4

    Mfundolesi usawi kkkk

  • @ShepherdChisale
    @ShepherdChisale Месяц назад

    Musamatichotse feel nanu......penapake muzingodula pofunikila pokhapo.
    Ma Bandle akuvuta kale awa😢😢😢😢

  • @JumaGadaff
    @JumaGadaff Месяц назад +6

    Mwayankhula bwana koma ndege inagwa bwanji boss 😂inuyo bwana ndinu opanda mnzelu mulungu akukantheni chisanathe chaka muyankha mulandu

    • @HappyBirchForest-zy8nq
      @HappyBirchForest-zy8nq Месяц назад

      Umayankhula bho heavy

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Месяц назад

      @@JumaGadaff kafuseni mulungu kuti ndege inagwa bwanji chifukwa ndamene amadziwa chilichose

    • @IanChidothe
      @IanChidothe Месяц назад

      Ndipo akudziwapo kanthu uyu

  • @rasnocuss4183
    @rasnocuss4183 Месяц назад

    Chirimba one love!!!!!🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤🎉 mwana wapaden Manganya

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 28 дней назад

    Zopepela zakozo osamantchula mulungu ukuwona ngati mulungu ndiwosewela naye

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Месяц назад +1

    Tengani ndalamazo or musazabweze Ayi ndi misonkho anu atuzuza thawi yayitali tengani zaulere

  • @lawrencekayona9247
    @lawrencekayona9247 Месяц назад

    Ndinaonela atapanga comedy as a president of the republic of Malawi lelo izo

  • @LucyTatianahChikwekwe
    @LucyTatianahChikwekwe Месяц назад

    Usi mu ma speech akewa mmmm chikondi chikupelewera bwenzi ali mu chisoni 🙏

  • @prettytambala5687
    @prettytambala5687 Месяц назад +1

    Bambo asikono woyeeee😅😅😅

  • @DevisonHala
    @DevisonHala Месяц назад

    Monga muja mudamukondera chilima kuchikangawa pomupereka kuti aphedwe koma inuso mudzafa kulibe wa mbewu

  • @wotchidawood
    @wotchidawood Месяц назад +1

    😂😂😂😂 yakwiya ndi midzimu bambo uwona wamphesa chilima garu iwe

  • @FrankMasamba-uk6mc
    @FrankMasamba-uk6mc Месяц назад +1

    Iweyo Usi ukamalankhula kumatchula dzina la chakwela , panyapako kwambir

    • @mishecksipolo7153
      @mishecksipolo7153 Месяц назад

      😂😂😂😂😂😂😂akutopetsadi bwanji ameneyu

  • @AlexZanda-e5i
    @AlexZanda-e5i Месяц назад

    Ndakunyadilaniii amalawi welocom to Tanzania

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Месяц назад

    Apapa yalakwa , Mr Usi mwakwiyisa anthu kwabasi shaaa

  • @johnmpatama1461
    @johnmpatama1461 Месяц назад +2

    Mzimu wa Chilima waononga microphone 😂😂😂

  • @arthurkayuza
    @arthurkayuza Месяц назад +1

    Is that soccer player from chirimba?

  • @user-bp6cq5pe3c
    @user-bp6cq5pe3c Месяц назад

    Za ndale doest require presence of God. Ndale nzasatana who rules

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l Месяц назад

    My vote only for USI, I president of my heart

  • @user-oc6xd4tv9l
    @user-oc6xd4tv9l Месяц назад +1

    ,😂,😂😂 akuti lathulija manganya woyeeee

    • @user-px9gd6fc6w
      @user-px9gd6fc6w Месяц назад +1

      😮e paka manganya oweeeee mmmmmmhhhhhhh

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Месяц назад

      Mpaka bambo asikono woyeee😂😂😂😂

  • @IssahAluba
    @IssahAluba Месяц назад

    Zomwe akulimbana nazo athu awa zaziiii, noe mukuyenera kutsitsa zithu mtego komaso mudziwe kt kugwa kwandarama yathu yakwacha mukuyenera kuganiza kwambili mukapanda kutelo zithu zizativuta mpakana kale

    • @JaneMhango-zl6pt
      @JaneMhango-zl6pt Месяц назад

      Kujaila kungongola ndiye mulephere kubweza ndalamazo.
      Dziko la malawi latha ili. Ma president ake ndi akuba onse.

  • @user-lk8kj9zv6x
    @user-lk8kj9zv6x Месяц назад +2

    Komano za ndege ya kuchikangawa zinayenda bwanji

    • @Extratremendouszeus
      @Extratremendouszeus Месяц назад

      Sangayankhe ..ndi yudasi iscariot

    • @tamalangoma2765
      @tamalangoma2765 Месяц назад

      I thought kafukufuku adakali kuchitikabe?

    • @Extratremendouszeus
      @Extratremendouszeus Месяц назад

      @@tamalangoma2765 look sharp..use common sense. Pakamwa pa usi sipanalankhule zachilima mpaka lero

  • @elbeys783
    @elbeys783 Месяц назад

    Awaso nde ayi, athu akuvutika osamuuza za umphawi wanu muli ndalama osamatipusitsa

  • @RhodaBandah-sh1ir
    @RhodaBandah-sh1ir Месяц назад

    Chakwela satipasaso nsimayo
    Ukuyakhulabwanji iwe manganya

  • @JackNagoli
    @JackNagoli Месяц назад +1

    Koma ma comment wa abwana mukuwaona? 😂😂 timaganiza kaye zokalakhula sitikufelanjitu iyi iya

  • @Gautengstanzo
    @Gautengstanzo Месяц назад

    Zimayamba wez wez am sure manganya akonza zinthu, very soon katundu atsikaso

  • @RhodaBandah-sh1ir
    @RhodaBandah-sh1ir Месяц назад

    Ngongole sisitha zithu bwana ..mungowawonjezela mavuto
    Kasiseni zithu kuma shop full stop

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO Месяц назад

    Bambo asikono ife sitikufuna ngongole ai, coz ngongole yo ndiye mavuto oooopsa Kwa ana anthu. Koma pangani zoti zinthu zisike pansinka kuti aliyese athe kufikira mtengo wakatundu osiyana siyana emwe mtengo wake wachita kuopsa ngati muja uchitila mkango

  • @GIFTEDWARDCHIGUMULA
    @GIFTEDWARDCHIGUMULA Месяц назад

    MP wachinyamata and chi player mbambande🤜🤜🤜, msikawo akonzedi eee

  • @user-mf5ce9wj4m
    @user-mf5ce9wj4m Месяц назад

    It's so sad to see Malawian are still fooled by MCP.what a hell

  • @EdwinHowardmkandawire
    @EdwinHowardmkandawire Месяц назад

    Bola Ali vice president basi olo anthu atakuwa

  • @user-kr1tf2tu7s
    @user-kr1tf2tu7s Месяц назад

    Iweyo ukati kumdula kwa zithu,,Ausi amapanga zithu usakafunsa ama factotry bwanji za umburi

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya Месяц назад +1

    Musanayambe kukamba zasewerozo mutatiyankhako kaye funso likumatisowesa mtendereri, Kodi ndege inayenda bwanji ku chikangawa? Zangongole zanuzo ifeyo ayi, munali kuti ndi chakwera wanuyo? Nkhani ndikusisa katundu, zinazo mukakambirane ku state house

    • @AbdulhameedWyson
      @AbdulhameedWyson Месяц назад

      Chisilu iwe

    • @DeliaKaduya
      @DeliaKaduya Месяц назад

      @@AbdulhameedWyson tangopita ukalandire nawo ngongoleyo munthu iwe

  • @SurprisedFlamingoBirds-ko1dw
    @SurprisedFlamingoBirds-ko1dw Месяц назад

    Uyu SI wa UTM ayi,asagawanise chipani,ingoimilani indipendent yo basi

  • @manfredzalirabetha2440
    @manfredzalirabetha2440 Месяц назад

    Galu wamuthu uyu yudas scariot wamuphetsa chilima iwe sizikupindulira zimenezo mzimu wa chilima ukuzunzani nonse ku chikangawako

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Месяц назад

    Musapusitsike Chakwera anabweranso modzichepetsa

  • @EnockMaluwa
    @EnockMaluwa Месяц назад

    Wise words Dr utsi

  • @user-vq5fe6mo6o
    @user-vq5fe6mo6o Месяц назад

    Koma abale osapha wanthu mlungu azakulangan inu ife kumuz timavutika timasowa chakudya kamba inu atsogoleri kukweza katundu tikhulupilirapo chan apa

  • @AnitaChakwana
    @AnitaChakwana Месяц назад

    Ati olo magalimoto apange ng'wing'wing'wii uyu anazolowela sewelo 😂😂😂

  • @kelvindickson
    @kelvindickson Месяц назад

    Kkkkkkk munafulumila kumusogoza nzanu ndichifukwa zambili zikungooneka zopelewela

  • @earnestchapita2194
    @earnestchapita2194 Месяц назад

    Nanga bwanji asilikari sadaseke maso popemphera bwanji

  • @MeshackLondwa
    @MeshackLondwa Месяц назад

    I don't think bodyguards closed their eyes 😂😂😂😂😂 , Amen.

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm Месяц назад

    Ife àngon tikulira mwana wakwathu kuntcheu kapolo iwe galu iwe olo mcp sitikuifuna ukulankhura zapambolo pako

  • @KestenMukhwapa-qp2gj
    @KestenMukhwapa-qp2gj Месяц назад

    Za ziii zeni zeni zopanda ndi Schererville womwe

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Месяц назад

    Iwe ukati kaduka ukutanthauza chani nawe zausiru , MULUNGU wake utiyo amene anaziwakuti mfiti usi adzakhala vp, u vp ochita kupherau ndiye ukamutchule MULUNGU usatchule dzina la MULUNGU pachabe akukwapula , us si MULUNGU koma anapangana ndi chakwera kuti aphe chirima kenako ampase u vp ngati akutuma kuti uziwaikirakumbuyo agalu amenewa ndiye wauponda awa palibe chao afiti opemphera

  • @user-qh4dd6nq3k
    @user-qh4dd6nq3k Месяц назад

    Kma chilimba 😂😂 zoti anthu aliokwiya ndi ifa yachilima ndiye aziti ndiambuye

  • @EscoChingayipe99
    @EscoChingayipe99 Месяц назад

    Amen powerful player

  • @DarlingtonChinyamunyamu
    @DarlingtonChinyamunyamu 3 дня назад

    Chinyamu50

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Месяц назад

    Koma manganya ndi udindo wa VP sidzikugwilidzana guy's 😂😂 iyi ndi minyama

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem Месяц назад

    Zamakabudula akowo anthu apindula nazo chani pomwe anthu akugona ndinjala. Dzuno pamenepo panali ena lelo ndiwe ndipo mawa ndi ena samala osatenga Malawi kusowa zochita.

  • @PetrosGere
    @PetrosGere Месяц назад

    Kķkķkkk Koma nde kunabebatu

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 Месяц назад

    Ndikuon ngat Anthu anu okuthandiziran sadakuthandizen
    Kungokhal ngat sewer sinthan okuthandiziranio

  • @user-xr9mc5hg5t
    @user-xr9mc5hg5t Месяц назад

    Munthu ukamangitse okusakira mtchele

  • @SylvesterMoyowinah
    @SylvesterMoyowinah Месяц назад

    Kodi muli pa campaign 😢😢 kodi

  • @umboneyusufu4499
    @umboneyusufu4499 Месяц назад

    Aka manganya ngati adalephela mayeso awumphunzitsa nde lelo angatukule Malawi

  • @IbrahimkDyman
    @IbrahimkDyman Месяц назад

    Kodi uyuyo akuona ngati ndioziwa tchito 4year yathayi anali kuti (manganya ayenera kubwerera ku tikuferanji)

  • @vincentkhunsanama584
    @vincentkhunsanama584 Месяц назад

    Ngongole mumupatse munthu ogulitsa zitumbuwa mwati

  • @IdahCharles
    @IdahCharles Месяц назад

    Ukudabwa mmesa uli pamenepo kamba ka imfa😢

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh Месяц назад +1

    Tamangodyani ndalamazo bas,uku tikudikira report la kuchikangawa,koyenda ndege ma hours 3800, ngati imayenda wapansi

  • @user-su2dq5lr1h
    @user-su2dq5lr1h Месяц назад

    Amalawi azanga Pena mukamalakhula muziganiza osamangokamba zithu zopanda umboni musiyeni usi ndi thawi Yake iyi yakwana

  • @FrankHaruni
    @FrankHaruni Месяц назад

    Akuluwa alindifundo dxopusa kobasi adximuudxa Chakwela dxoti mulungu simuthu amasithadi kom osati kwaife ndiwe galu kobasi