PROGRAM YA KULINJI KU TIME- KUMVA MAGANIZO AWANTHU 4 September 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 15 сен 2024

Комментарии • 88

  • @ChifundoChiwanda-ru3pg
    @ChifundoChiwanda-ru3pg 10 дней назад +2

    Dr Mtumbuka is the best kutsogolera chipanichi, Kaliati akhalebe SG azichepetse ndipo pa SG Palibe angapikisane ndi Kaliati, Usi is not fit for any mpando anaonetsa kuti ndiwosakhazikika.

  • @brianjames211
    @brianjames211 8 дней назад +1

    Mery Chilima should come upon and lead the Party and stand for the Presidency, she's the only person who's going to destroy MCP and Lazuro chakwera with his goons.

  • @SayidiMisessa-x6y
    @SayidiMisessa-x6y 11 дней назад +5

    Ayi Akaliyati ndiwomwe angavale nsapato ya achirima ndipo akuwonesa kusapendekeka ayi koma ena onsewo musakopekenawo abwera ndimpeni kumphasa

  • @IreenMwachande
    @IreenMwachande 8 дней назад +1

    Apeseni mwai mai kaliati nawo aimed nawo tiyeseko azimai pa u presdent

  • @user-ww4ei5fb7d
    @user-ww4ei5fb7d 8 дней назад

    Mai Kaliati my vote, enawo ayimire zinazo

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v 10 дней назад +2

    Osazamuvotera Micheal Usi simunthu wabwino chipani achigulisa ku MCP Chikangawa party

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 11 дней назад +2

    Kaliati ayimire basi atumikira ndi malemu mosawazembera mwachilungamo .komanso achigwira chipani cha utm.koma a usi chipanichi chikhala cha mcp a usi akatenga ndipo adzachisintha zina siyizakhalanso utm .koma odya zake alibe mulandu plus chikangawa party

  • @shotsfired588
    @shotsfired588 8 дней назад

    I think Mary chilima and Brian Banda would be a breath of new air

  • @ChikuMatemba
    @ChikuMatemba 7 дней назад

    Merry Chilima My Vote

  • @emmanuelkhosa-ze6fl
    @emmanuelkhosa-ze6fl 10 дней назад +3

    I see merry chilima coming up wait and see

    • @BrianNowa
      @BrianNowa 10 дней назад +1

      I wish she could kuti angopitiliza kutitsogolera than anthu adyerawa, omwe amadikira a chilima apite Nde adzidzalowa chipani bwino, Ngati Yehova angawafulumizitse kutero, atero it can be hard koma yehova amapanga zose ndi cholinga, anthu atakhala ngati Mai kaliati chipani cha utm chidzalimba mpaka kale

  • @RodgerChaula-r5z
    @RodgerChaula-r5z 10 дней назад +2

    Mary Chilima be strong.we need you come on

  • @BrianNowa
    @BrianNowa 10 дней назад +1

    Sizose zonyezimira zili Gold, UTM ikhale maso pa utsogoleri wa president chifukwa kulipo kugulitsa munda wawo kenako mkumadzapangaso ganyu mmunda mwawo momwe, vuto la a usi samadziwika kuti Ali mbari iti chifukwa samakhala open pamikumano ya utm ndi zochitika zose amadzipatula muzambiri, anthu onse omwe alowa chipani chilima atamwalira sakufunika kuwakhulupilira mwachangu chifukwa mitima mwawo akungofuna mipando, we will regret sure, anthu 5 akalimbilane mpando umodzi afuna chani kwenikweni, apa Pali dyera osangoti matipate, nuona ngati kutsogolo kwa utm kuli kasavana ,

  • @user-ld8gb9xm7v
    @user-ld8gb9xm7v 11 дней назад +1

    Mayi kaliati my vote

  • @paundfeston
    @paundfeston 10 дней назад +1

    MANGANHA anapha chilima

  • @Sherrie-b5s
    @Sherrie-b5s 10 дней назад +2

    Mary Chilima tikumufuna ife

  • @ChimmsRichardOrden
    @ChimmsRichardOrden 11 дней назад +4

    Michael usi wakomedwa ndi Mcp so akhonza kuchigulitsa chipanichi bola akaliyati or Kabambe

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 10 дней назад +1

      @@ChimmsRichardOrden apa tipitire kaliat.zopatsa alendozi ayiii

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 10 дней назад

      ​@@henryphiri6100am with you

  • @TauraiBasa-vj4ci
    @TauraiBasa-vj4ci 10 дней назад +1

    mery is only one who have more flo utm open your eyers

  • @user-xc2zm9bu1i
    @user-xc2zm9bu1i 11 дней назад +1

    Ife anuwake a UTM tikudziwa president wanthu
    Iwe wa MCP izo ukufunazo singachitike

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 11 дней назад +2

    Dr usi akuyenera kuyimira u president ku UTM

    • @billymhoni9527
      @billymhoni9527 11 дней назад +1

      Ndinu a mcp ndipo mumutengatu ameneyo

    • @KondwaniBanda-ul8sj
      @KondwaniBanda-ul8sj 10 дней назад

      @@billymhoni9527 manganya ndikape

    • @Henry-vw2cz
      @Henry-vw2cz 10 дней назад

      Usi ndiwa chikangawa😂😂😂😂

    • @GiftKananji
      @GiftKananji 10 дней назад

      Utsi ayi wa chikangawa

    • @PaulKachule
      @PaulKachule 10 дней назад

      Mfiti ya munthu kufuna kudzamaliza mtundu eti

  • @xinalungu9616
    @xinalungu9616 11 дней назад +3

    Mwawi uli ndi awiriwa Utsi ndi Kaliati.
    Utsi akawina chipani chilimba monga mmene Chilima adasankhila. Sadasankhe kulalata ayi..
    Atakatenga Kaliati, chipani chikhala under DPP ndi kutha ngati makatani

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 11 дней назад

      😂😂😂. Paja chikangawa party mukusapota usi cholinga atenge chipani kupitaso ku MCP, nde bola atapita komwe anachokera than ku MCP azingophedwak ngt mmene mwaphera chilima 😢

    • @user-vm7iz6oz6r
      @user-vm7iz6oz6r 11 дней назад

      Khani ilipan ndi ya utm not MCP kodi walowera pat iwe

    • @billymhoni9527
      @billymhoni9527 11 дней назад

      Ndinu a mcp

    • @NizigiyimanaChantal-c2p
      @NizigiyimanaChantal-c2p 10 дней назад

      Ndiwe oipa using wake utiyo

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c 11 дней назад +3

    Utsi amuchose nga mcp awo

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 10 дней назад +2

    Manganya si wa UTM.

  • @Jacksonmuhackeya
    @Jacksonmuhackeya 11 дней назад +2

    Okuphayo musayelekeze mutha nonseeeeee

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg 10 дней назад +1

    Usi azawine Ali ndi usogoleri chilima anasiyilanji kuwasankha inawo bwanji

  • @KennedyPhiri-c7g
    @KennedyPhiri-c7g 8 дней назад

    Kopanda Usi Ku UTM singawine kozi akupanga kamupeni ndi Boma Popano anthu akumuziwa

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 11 дней назад +1

    Usi ndi wa MCP mapeto ake UTM itha koma ena okay apikisane tikudziwa kt enao akupikisana cholinga a usi achoke pa mpando

  • @abumatupholstery
    @abumatupholstery 10 дней назад

    Dr manganya usi ayimile
    Ndi amene anasakhidwa ndi chilima komanso amaye ndesela limodzi munthawi yawo sanga gulise chipani ndi munthu wina ayi

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l 10 дней назад +1

    Why do you hurt running of Chilima, honestly Chilima was not stupid to choose Usi. Kaliati ndinu chitsiru 0:00

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 11 дней назад +1

    Usi ali ndi chipani chake ndi gulu lachina masangwi.dikirani munva kuti odya zake wabweranso ndipo ali ndi boma mgwirizano

  • @ruthmpunga6331
    @ruthmpunga6331 11 дней назад +1

    Dr Usi akuyenela kutenga enawo amuthandize MAI mkulu ulemu wao ku SG chair

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v 10 дней назад

    Manganya Siwa Utm iyeyu ndiwa Odya Zake alibe mulandu

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 10 дней назад

    Ine isupport usi koma achoke aliko plzzz for malawi to ❤ him basi

  • @BMDMasulani
    @BMDMasulani 11 дней назад +3

    Manganyao ndikatundu mpatseni mwayi

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k 6 дней назад

    Manganya anapha chilima

  • @MveraNambala
    @MveraNambala 10 дней назад

    Mmmm utsi Nd wa chikangawa party

  • @UlemuKamanga-yn4jk
    @UlemuKamanga-yn4jk 10 дней назад

    No leadership qualities in Patricia kaliati,UTM please open your eyes, Incase you partner with DPP in 2025 with KABAMBE ,just know that the end of UTM , DPP should also mindful of APM leaving the power to KABAMBE due to age , which also will mark the downfall of DPP ,SO both UTM &DPP should open their eyes

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 10 дней назад

    Nkhani ndi Mary Chilima muona Ena onse athawamo

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 11 дней назад +1

    Ausi atha kukhala upule not kaliyat kulalata sangasogolele

  • @MateusEliasluciano
    @MateusEliasluciano 7 дней назад

    Obera kutsogolera utm: usi...

  • @JummaRattik
    @JummaRattik 11 дней назад +1

    Manganya is a president of UTM ,, don't give female

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 10 дней назад

    Usi basi anamsankha yekha malemu. anasiyilanji kusankha enawo ndipo potsankha usi anawonamo mwini wake

  • @AliceGeorge-il6ig
    @AliceGeorge-il6ig 10 дней назад

    Manganya akungofuna kugulisa chipani

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e 10 дней назад

    Kaliati ❤❤

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 10 дней назад

    Kaliati boma

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r 11 дней назад

    Uyo maiko usi ndi wa kongeresi mm paka achigulisa Ku MCP simuthu wabwin

  • @BillyChisale-m1z
    @BillyChisale-m1z 9 дней назад

    Kaliyati vuto alibe ulemu ndi anthu

  • @WinnieNkosi-f6p
    @WinnieNkosi-f6p 10 дней назад

    Manganya chipani chache cha NTHIKO nchimozimozi ndi MCP NG'ONA PARTY, dzimbalangondo

  • @TiwongeChikhoza
    @TiwongeChikhoza 10 дней назад

    Vuto la usi si wa utm coz akipanga zimezizo coz adzagulitse athu ku mcp zomwe sizili zoyenera

  • @RashidKusum
    @RashidKusum 10 дней назад

    Imeneyo ndiye democracy

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 11 дней назад

    Usi ndi wa mcp kumpasa mpando ndiye kuti chipani chathapo basi nonse mukhala a Congress party utm be careful

  • @Brihippo
    @Brihippo 11 дней назад

    Kaliati ai pau presedent iwe ndi SG basi

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k 6 дней назад

    Usi ndi galu kwabasi

  • @IbuAli-u3f
    @IbuAli-u3f 10 дней назад

    Manganya ndiwa chikangawa part

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 10 дней назад

    Kodi angamvotere usi ndi ndani yudasi ameneyu koma ine musatiyese mwamva

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j 10 дней назад

    Kukanakhala kobvuta kuti ausi azionesere kwambiri kuti akusapota utm pamene akugwira ntchito ku boma zambiri zimaoneka kampeni ikayambika panopa ndikobvuta kuti ausi anganene zolakwika aboma akweni akapusa aluza mbali zonse akayerekeza kuimilira uprezident

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 11 дней назад

    Manga samakhala serious ku chipani cha utm komanso ndale adziwika momwe asakhidwa u vice

  • @AbgirlChinheya
    @AbgirlChinheya 9 дней назад

    Usi ndi galu

  • @souzajoaquim571
    @souzajoaquim571 10 дней назад

    Kodi amanganya alikuti mesa paja Yao sinatuluke

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v 10 дней назад

    Manganya ayi mapeto ake apitisa chipanichi ku Mcp

  • @user-eu6ox1nx2s
    @user-eu6ox1nx2s 11 дней назад

    Mpakana kaliati kufuna u president? Aaaah koma Malawi Malawi ai ndithu

  • @jelsonmlowoka8611
    @jelsonmlowoka8611 11 дней назад

    Kaliati kukhala mtsogoleri wa chipani, are you serious 🤔

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 11 дней назад

    Akufuna usi woo ndi a mcp

  • @JummaRattik
    @JummaRattik 11 дней назад

    Hi

  • @MariaGatoma
    @MariaGatoma 10 дней назад

    Osaopa usi agulisa chipani

  • @benjaminmvuma-rk6mu
    @benjaminmvuma-rk6mu 10 дней назад

    Forget a bout utm

  • @JulianaMkonda-k2n
    @JulianaMkonda-k2n 11 дней назад +1

    Maiko usi ayi ndi wamcp

  • @AishaChipande
    @AishaChipande 11 дней назад

    Inu usi ndi wa mcp bwanji mumasokoneza zinthu

  • @AdamChamveka
    @AdamChamveka 11 дней назад +1

    katunthu ndikaliyat maiko usi agulisa ku ng'ona kaliyati chilimba

  • @AlbunoCement
    @AlbunoCement 11 дней назад +1

    Us basi

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 11 дней назад +2

    Dr usi akuyenera kuyimira u president ku UTM