COMRADE MTANYIWA PA LIMPOMPO FM

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 15 сен 2024

Комментарии • 62

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 9 дней назад +8

    The Truth will set u free
    The best Radio station

  • @ClaudiaarmandoMafunga
    @ClaudiaarmandoMafunga 9 дней назад +7

    Yah kumalawi kuchitika zinthu

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 9 дней назад +5

    Comrade amayankhula Zowona enanu musatsutse

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 9 дней назад +4

    Koma amalawi akugona bwanji, kumene kumachitidwa print ma ballot paper kumayenela kukaotchedwa period. Kenaka ndikupanga ma demo kuposelanso a ku Kenya.

  • @EstherMbisa
    @EstherMbisa 9 дней назад +5

    Koma chikangawa or atalapa kumwamba sakalowa🙄🙄🙄

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 9 дней назад +4

    Ana achepa kwambiri, sangabere chisankho.

  • @AnthonyChirwa-t4g
    @AnthonyChirwa-t4g 9 дней назад +3

    panyapanu pamutumbo panu mcp patako panu ndinu agaru kwambili agaru a mcp ndipo inu a mcp inu mkuchoka muboma inu apa wina akathela kundende inu aphaka kwambili

  • @AngelaMphinji
    @AngelaMphinji 9 дней назад +2

    Paja. Ananena. Kuti. Ndale. Zawo. Amapanga. Usiku!! Mulungu. Salola. Akunva. Kulira. Kwa. Amalawi.

  • @CharityMkandawire-t8u
    @CharityMkandawire-t8u 3 дня назад

    Eeeh koma kuli zinthu yhooo

  • @MercyKatongo-p9b
    @MercyKatongo-p9b 9 дней назад +2

    Pepani mai chilima Zambia behind you Malawi

  • @HamzaMkwanda-bh8dc
    @HamzaMkwanda-bh8dc 9 дней назад +6

    Agalu mcp machende anu

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 9 дней назад +3

    AKHALE SIZIMUTHELA AMENEYU 😂😂😂😂

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 7 дней назад

    Tionana 2025 kulengezedwa kuti Chakwela wa wina ,tidzaotcha Malawi yonse, chifukwa tidzadziwa kut payenda chinyengo, tidzalira.

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya 8 дней назад

    Chikangawa koma akhale sinzinthera bwaaa

  • @sabinaphili
    @sabinaphili 8 дней назад

    mmmmmm koma boma limeneli lilamulila ndani avomeleze alephela basi , antanyiwa woyeeee!!!!!!!

  • @MercyKatongo-p9b
    @MercyKatongo-p9b 9 дней назад +2

    Thanks Mr mantanyiwa

  • @CatherineNkhala
    @CatherineNkhala 9 дней назад +2

    Zomveka ndiye ziti

  • @Malani41
    @Malani41 9 дней назад +2

    Za Chamba!

  • @RichardMatumbo
    @RichardMatumbo 9 дней назад +2

    Eeee panyopano a ,mcp mboleyano zodura kapena za shart😂

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d 9 дней назад +2

    Kkkkk akuti kantikana lodyela

  • @ChikumbutsoMaluwa
    @ChikumbutsoMaluwa 9 дней назад +3

    Inutu mukupenga koma smukudziwa tazilakhulani khani zot zitithandizee ife amalawi

    • @blandinabonaventure
      @blandinabonaventure 9 дней назад +1

      Nanu sakakamiza kumvera kwaife mzazeru

    • @MoosaBanda-su3zp
      @MoosaBanda-su3zp 9 дней назад +1

      tayakhulani inu adzelu inu koma ife tili pambuyo pa mlipopo ❤

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 9 дней назад +2

      Iwe wakuitana pano ndindani pamtumbo pamako wamko uchite nkhope ngati kuthako kwa Chakwera

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 9 дней назад +1

    Kunkuyu nkhope yayamba kusintha kkkkk akuopysatu

  • @ElisaNyirongo
    @ElisaNyirongo 9 дней назад +2

    Asizimpita amenewo, wakuba wamkulu wa mcp

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 9 дней назад +1

    Guys koma chakwera anatitayitsa nthawi, what a devil is this.

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi 9 дней назад +2

    Zitsilu za wathu ndipo ufiti akupangawo sakwanitsa

  • @EuniceKalilombe
    @EuniceKalilombe 6 дней назад

    Koma ya asitikali momwe amabvitikila munja kumalola izi zosayenda komanso za manyazi

  • @ThokoGomeza
    @ThokoGomeza 8 дней назад

    Sitikuifuna ZANU amene mukt zabodza Inu mudya manyi Chaka chamawa

  • @MercyKatongo-p9b
    @MercyKatongo-p9b 9 дней назад +1

    Sorry dear it's heartly broken

  • @ZarihunAyele
    @ZarihunAyele 8 дней назад

    Tasiya kuvota adzakuvotera namanu tikavota mukuphana zachamba

  • @etomansailes4932
    @etomansailes4932 9 дней назад

    ulemu wanu ntanyowa mumatiyimirira km zoika imfa ya chilima mmmm timusiye kaye kaye mkaz wake apumeko plz 😢😢

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 8 дней назад

    Nyau party 2025 out

  • @lazaruschitsamba8394
    @lazaruschitsamba8394 8 дней назад

    ummm uyu wabodza amanena kuti black box inapezeka ku state house koma report ukuti sianapezeka

  • @MajeedMaulana
    @MajeedMaulana 9 дней назад +2

    Warykum Salaam

  • @ADHASAPONYILENDA
    @ADHASAPONYILENDA 9 дней назад +2

    Wabiza iwe

  • @JanaJovian
    @JanaJovian 8 дней назад

    A mcp tikumana pa 2025

  • @HopeChikopa
    @HopeChikopa 8 дней назад

    koma kumalaw kukuchitika zinthu

  • @georgedzimbiri8383
    @georgedzimbiri8383 9 дней назад +2

    Mmmmm, mmmmmm

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 9 дней назад +1

    Inutu ndinu abodza inu ,I don't think MCP is that desperate chokani apa aaaaaa

    • @FannyWadson-zg4oj
      @FannyWadson-zg4oj 9 дней назад +2

      Muziona sitikusiyani tithana nanu athu oipa inu

    • @blandinabonaventure
      @blandinabonaventure 9 дней назад +1

      Awatuma awa sakakamiza ife zimatikomera

    • @spargomw
      @spargomw 9 дней назад

      Musatiyankhulitse pambali chifukwa Magazi a anthu 9 aja sadaume ku Chikangawa uko😢😢

  • @MatronOsiten
    @MatronOsiten 9 дней назад +2

    Welcome

  • @aminambaya6387
    @aminambaya6387 8 дней назад

    Ndiwe wabodza Mtonyiwa ine ndilibe chipan koma ndiwe attention seeker oipA

  • @KanyozaMatope
    @KanyozaMatope 9 дней назад +2

    Zosamveka..izi,, evidence.. ilipo?

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 9 дней назад +2

    Hahahahahah eeee koma yeaaaaa🙌🙌🙌

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 8 дней назад

    Mmmm

  • @wantwamwangomba
    @wantwamwangomba 9 дней назад +2

    Ah zopanda mutu izi

    • @chifundomatumula1652
      @chifundomatumula1652 9 дней назад +2

      Zamutu zilikuti

    • @user-ww9rj2wx8d
      @user-ww9rj2wx8d 9 дней назад +2

      Anakutuma ndani kuti uzimvela za mtanyiwa galu iwe kwabasi usalimbane ndi mtanyiwa

    • @wantwamwangomba
      @wantwamwangomba 9 дней назад +1

      ​​@@user-ww9rj2wx8dnzoduka mutu izi inu, let me even unsubscribe immediately. I hate nonsense

    • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
      @HappyAbyssinianCat-xt2bm 9 дней назад +1

      Iweyo ndiye ukulankhura zoduka mutu chisiru iwe

    • @Grenamawerenga
      @Grenamawerenga 9 дней назад +1

      Bweresani zanu zamutuzo timvere

  • @nessymwakitalu
    @nessymwakitalu 9 дней назад +1

    No this cheat

  • @MATTHEWSGPHIRI-ho7ud
    @MATTHEWSGPHIRI-ho7ud 9 дней назад

    😂😂😂 Malawi