TIMOTHY MTAMBO KULANKHULA MOSAOPA PAMASO PA CHIMWENDO BANDA | NDIPO ACHIMWENDO ANAYANKHULA IZI |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 13 окт 2024

Комментарии • 48

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 2 месяца назад +15

    sanamwalile pa ngozi ya ndege muziti amene anaphedwa ndi chakwera pamozi ndi yudasi ali pompoyo boma la zigawenga zokha zokha

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 2 месяца назад +5

    ❤❤❤ chakwela watikwana

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 2 месяца назад

    Chimwendo kulakhula koputsa dzimenedzi waziziwa liti

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 месяца назад +1

    Inde Mtambo

  • @manfredzalirabetha2440
    @manfredzalirabetha2440 2 месяца назад

    Osamalakhula mozembaitsa chilumgaamo chimamasula kumanena bwino bwino kuti yemwe anaphedwa mu chikangawa ndi boma la mcp ndi tsogoleri wake chakwera continue resting in eternal peace bwana chilima anakupherani njiru

  • @OscarKJekapu
    @OscarKJekapu 2 месяца назад +1

    Akunama a NRB chilungamo alibe

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi 2 месяца назад +1

    Kodi inu Anrb mukukalila zinthu zoti zili be sogolo bwanji mapana chibaanzi mungolamula kuti wina aliyese amene Ali ndi khadi lakuchipatala. Laicesi passport ndizinva aka vote chifukwa onsewa ndi amalawi zauchisuru basi mitu yanu yapanda nzeruyo ngati chakwera

  • @SafariBvumbwe
    @SafariBvumbwe 2 месяца назад +1

    Chimwendo zopusa ayi ifetu sitikuwopano

  • @UsenLashid
    @UsenLashid 2 месяца назад

    Iwe Muthu wakuba galu iwe

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 2 месяца назад +1

    Chakwera anapha chilima

  • @PetrosMunthali
    @PetrosMunthali 2 месяца назад +2

    NRB yankhulani chilungamo it was very difficult for my son and daughter to get the registration forms. Let people be well informed by conducting enough sensitization and provide the forms once someone has come at the centre otherwise most people become discouraged if they come across hardships to get a form as was the case at Nkolokoti.

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 месяца назад

    Amene anaphedwa ndi bingu wamthalika ndi chipani Cha dpp kupha anthu 22

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 месяца назад

    Katangale pamalawi wafikapo.

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 2 месяца назад +3

    Iwe chimwendo, unamunyoza chihana pano ukut zonyozana ay ukutanthauza chan.

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v 2 месяца назад +1

    Achinyamata sitikhala chete agalu Inu pamene matenga Boma munagwilitsanso ntchito achinyamata

  • @BMDMasulani
    @BMDMasulani 2 месяца назад +1

    Chimwendo chitsilu chigawenga

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 месяца назад +1

    Chimwendo suja unkanyoza peter muthalika kumamuyelekeza mmene amayankhulira shame on you

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 2 месяца назад +3

    Iwegalu chimwendo banda

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 2 месяца назад +1

    Gulani Zinkudza mawu baba. Aliyense uthenga umufikire

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 2 месяца назад +1

    Muli Ndi mantha,zowonadi simunga khumbire kulowa ndale,m'bale wanu waphedwa pompano khalani muzilira, MCP Yachita zoipa kwambiri kumupha Chilima

  • @wittinessnkhokwe
    @wittinessnkhokwe 2 месяца назад

    A dziwe TV ndiye mumangomatulatu zinthu

  • @ShayibuJames-xc8il
    @ShayibuJames-xc8il 2 месяца назад +1

    One day malawi idzakhala pa ufulu apapa ndi akambere mbere okha okha

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 месяца назад +1

    Sindimafuna kuyakhapo komwe chimwemdo wayambe iyeyo kulakhula zonyoza nduna yotani kukonda kunyoza amalawi azake

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 2 месяца назад +4

    chigawenga iwe chimwendo chitdiru

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 2 месяца назад

    Chimwendo Banda mphuno ngati tomato😂

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 месяца назад +1

    Achimwendo banda mulibe nzeru mukamayankhula ku msonkhano Kuja simumanyoza? Komanso nkhani yosankhana mitundu mmayesa mumayambitsa ndi inuyo a Mcp anthu adzisankhana

  • @MolosonMisitala
    @MolosonMisitala 2 месяца назад +1

    Aaaaa panyapanu inu bwanji chitchola adamugwila ndi ndalama ku airport mudamusiya fokofo

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 месяца назад +1

    Machende ako iwe chimwendo mbuzi ya kupha

  • @hopembendela
    @hopembendela 2 месяца назад

    Kupha nkatolika m'modzi munakhalangati mwapha onse 2025 mukuchoka inu a mcp mudziwe zimenezo majority ya anthu kuno ku malawi ndi akatolika

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 2 месяца назад

    Chokani achilundi, mau osasawo ngati omwa kachasu

  • @EmmanuelNkosi-ts8bn
    @EmmanuelNkosi-ts8bn 2 месяца назад +1

    Amalawi ndife zitsiru za anthu why kumaimba phone ku banja nkumawafuza za ndale , stupid questions

  • @CvgGgbnb
    @CvgGgbnb 2 месяца назад +1

    Akakhala paudindo amayiwala Kuti ena azakhalaponso 😂

  • @johnnyirenda5848
    @johnnyirenda5848 2 месяца назад

    Mtendele It's our prioliy koma Ukunenedwa pakamwa zochita Zamtopola zokha zoka ayi zatopetsa Njanji Yadulidwa payioa basi

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 2 месяца назад

    Inu inu inu musati anamwalira pangozi ya ndege, ndege yake iti, lankhulani zazooona.

  • @BonfaceMajawa
    @BonfaceMajawa 2 месяца назад +1

    Achimwendowa sa xul bwanji

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 2 месяца назад +1

    Chimwendo Banda ndiwe Galu ndi MCP yako

  • @OweniMolokooweni
    @OweniMolokooweni 2 месяца назад

    Chifukwa chani mukuwulusa inzi musaulusa za ku gwendwa kwa chithyora ndirama zakhanikhani

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 2 месяца назад

    chimwendo is ontop ndi akatundu osati za alomwezi ayi

  • @CvgGgbnb
    @CvgGgbnb 2 месяца назад

    Andale Ku Malawi ambiri akukonda kutukwanizana Ife timawona kulemphela kwawo basi chifukwa Boma ndi Boma mpaka Kale azalamulanso ndi ena

  • @OscarKJekapu
    @OscarKJekapu 2 месяца назад

    Zitsilu

  • @IdahMoyo-no3pe
    @IdahMoyo-no3pe 2 месяца назад

    Nrb mabii 😅😅😅😅😅😅

  • @DysonKamama-yh7hq
    @DysonKamama-yh7hq 2 месяца назад +1

    MCP chipani chamavampaya

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td 2 месяца назад

      Nyani iwe DPP inapha anthu okwana 20 kumzuzu ufuna utiuze chani anaphedwawo siwanthu ameneo sitikuwelenga malubino DPP kupha

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo 2 месяца назад

    Zolembetsa za unzika sizingaende bwino jamba ka vuto la kusalengeza pa zifukwa zao

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 2 месяца назад +2

    mcp ndi chipan cha zigawengs ndi umbava

    • @tasmania527
      @tasmania527 2 месяца назад

      DPP itapha anthu 20 ku mpoto mu 2011?

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki 2 месяца назад +1

    Iwe chimwendo banda ndiwe mbuzi yeniyeni