Limpopo woyee kufika ndi breaking news yomwe wabweletsa ndi Mr Don’t Trust Uja sakusewela nawo

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 14 окт 2024

Комментарии • 78

  • @jamiajafali6619
    @jamiajafali6619 2 месяца назад +6

    Mangochi Wooooyyyeeeee!!!!

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 2 месяца назад +7

    Agalu amenewa achoke ndipo asadzalowenso m"boma m"dziko la Malawi

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 2 месяца назад +6

    Katundu bambo more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @spargomw
    @spargomw 2 месяца назад +4

    Program iyi ikadabwera nd Ntanyiwa kukadakhala Phweteee osati masewera😂😂😂😂😂😂 takunyadira Mr Don't Trust🎉🎉🎉

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 2 месяца назад

      😂😂😂😂😂 mukunena zoonadi bwenzi tikuseka kwabasi

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 2 месяца назад +2

    Yadula kooda iyi ya chakwera zopusa adyeleni ndipo kaguleni nkhuku mudyele mpungu ndalama za super bet zimenezo

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 месяца назад +3

    Mangochi woyeeeeeeee, Mangochi palibenso safuna zachibwana adyereni ndlamazo bvoti ili mumtima

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 2 месяца назад

      @@MiddayDeleza ndipo chaka cha mawa tonse tidzatero ngati zomwe achita amzathu ku Mangochi.

  • @ZioneMkwanda-y6i
    @ZioneMkwanda-y6i 2 месяца назад +1

    Trust ino ndi Mangochi sitigawatu masweet paja , ife kuno kutifupa ndalama Achikangawa Party kulandira mkwadyera koma vote osapatsa ndagwilizana choncho ndipo atimva Mangochi woooooyeee😅😅😅😅😅

  • @MexcoJepter-p5f
    @MexcoJepter-p5f 2 месяца назад

    Abale munena zoona kuti mcp Yaluza???? Ndamva kukoma osati masewera ,awonetseni asatana amenewa mwabwera ngati coming 💃💃

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 2 месяца назад

      Ndipo m'mene tikumvera mu mtimamu tikuchita kumva kukoma

  • @AbdirashidMohamedIbrahim-ib9uy
    @AbdirashidMohamedIbrahim-ib9uy 2 месяца назад

    Yes mark💯💥💥💥💥💥🔥🔥🔥

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere 2 месяца назад

    Bwana don't trust ndanva Ben longwe akutukwana sindikudziwa Ngati mwamunvako?😂
    Lipopo on fire 🔥🔥🔥

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 месяца назад +4

    😂😂😂😂😂 yomweo chikangawa wagwa nayo atakhala kuti ndi plesdent wa umuthu angamatenge ndrama zambili chocho kumagawa chimwecho athu akufa Ndi njala uphawi wadzaoneni makhwala m zipatala mulibe koma kumaononga ndrama Chocho akamachoka ali zithu zavuta ziko lose galu wachabe chabe chikangawa

  • @MphatsoIshmaeladam
    @MphatsoIshmaeladam 2 месяца назад +2

    Ndalama tidya ndithu popeza zaphweka koma manso athu ali kuchikangawa ndipo mcp siinathi mzimu wa chilima ukufwafwanda

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n 2 месяца назад +2

    ndipo sazakhalaso nambala ya bwino azakhala kutali kwenkwen.. ndipo ngat Pali chipan chomwe chizasalire ndi ma vote nde ndi mcp. ndimwana yemwe akuziwa kut, MCP ndi yakupha,kuba,kuwononga ndi kusasamala miyoyo ya Amalawi. Chikangawa Shem on you

  • @TonyMpate-by9gp
    @TonyMpate-by9gp 2 месяца назад +1

    Wasala wagwilizila nthiko uja Ife ndiomwe tatenga mapoto mafuwa madzi Ufa machesi tiona Kuti akathyakulila Kuti ndi Nthiko wakewo 😅😅😅😅😅 aMalawi akanyimbiwa akabwela ndi mamilion awowo tiyen tilandile mulungu sapatsa pamanja what ever chomwe angabwele nacho kwende tupochele tisakanei ndipo tiwalimbitse mtima kuwopa kutikayikila koma patsikulo kudzawona dzochita

  • @MikeGomani-tb9np
    @MikeGomani-tb9np 2 месяца назад +1

    Zikungovuta kuti malamulo aku Malawi kuno samagwira ntchito, bwezi amphungu omwe athawa zipani zao ataona nyekhwe

  • @OrackPhili
    @OrackPhili 2 месяца назад

    Timasangalala nanu a muthanyiwa

  • @MelissaMondey
    @MelissaMondey 2 месяца назад

    Sanati tiyeni tione kuti mulungu panga zotani, Kodi anthu ambiri azidandaula mu dziko muno?chonde ambuye mulowelerepo ife anthu tatopa ndikunamizidwa🙏🙏🙏🙏🙏🙏God plz for give help us

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 2 месяца назад +5

    Ngakhale ma MP a Mcp azawina kwa chakwera basi agalu amene aziona sanati aliradi ndithu

  • @UsenLashid
    @UsenLashid 2 месяца назад +1

    Pamenepo ndipamene angadziwe chakwela Kuti ndalama sizidzavotela Ayi amalawi anapenya pano ndipo Amalawi akudziwa Kuti ndalama zimene akupeleka ndi Za amalawi

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 2 месяца назад

    Kuli Limpopo Woyeeeeeee yomweyo Chikangawayooooo

  • @HalimaMussa-j6t
    @HalimaMussa-j6t 2 месяца назад

    ❤❤❤

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 2 месяца назад

    ❤❤❤❤❤ ife akumangochi sitimagawa kamba ayi ❤❤❤❤

  • @emilynthite6545
    @emilynthite6545 2 месяца назад

    Tiyamike anthu onse akumangochi pazomwe mwachita

  • @johnnyirenda5848
    @johnnyirenda5848 2 месяца назад

    Go ahead with Chilungamo
    Amalawi tinakhulupilila Tonse alliance Move Kona Kudabwisa ndi uku, Chipani chomodzi chikuzikweza kuti ndichocho chokha kuzitsogoza KU fufuta u Tonse mmmmm Mchitidwe wowopsa zedi mmmm 2025 Topanga Zina no Reverse

  • @BadzuzenbiliatBiliat
    @BadzuzenbiliatBiliat 2 месяца назад +1

    Zabwino zonse mango hi tchito mwagwira Madera ones tione zimene mango hi ya chita akabweresa ndarama tilandile koma voti Ili mumtima

  • @BysonPhiri-gu4io
    @BysonPhiri-gu4io 2 месяца назад

    Mbambande mbambande

  • @MolosonMisitala
    @MolosonMisitala 2 месяца назад

    Kd achakwela ndalama mumwazazo simungaponye mmacompany kt zinthu zitsike? Kuyambila lelo muve kt nyini yamanu yamagaziyo

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi 2 месяца назад

    Chikangawa tipaseni ndalama koma voti 0 simudzaiona mwati khaulisa kwabili tikufuna kubwezela sopano

  • @beatricenkhoma1109
    @beatricenkhoma1109 2 месяца назад

    Yomweyoo cikangawa

  • @bornface4786
    @bornface4786 2 месяца назад

    Zimenezi ndizimene tikufuna . Osamangowombera m,manja gule asakuvina bwino. Gule kwawo kkkkkkk

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 2 месяца назад

    Auze a chimwendo

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 2 месяца назад

    MBAMBANDE MALAWI WAKE SI WALERO MANGOCHI IMAKANA ZAUCHITSIRU ISYENE WACHIYAO WANGALUSA MBAMBANDE

  • @MarriamMatola
    @MarriamMatola 2 месяца назад

    Akapuku a mcp aziona zosaona,azatulu m'boma kwamuyaya titidzaonanso amcp alim'boma agalu make mbuuu mwananso mbuuu

  • @courageouslondo1986
    @courageouslondo1986 2 месяца назад

    Kd ausiwa ine sindikuwanvetsa akudziika pati?nanga 2025 akudziika pati

  • @ChancyJere-pz5sv
    @ChancyJere-pz5sv 2 месяца назад +2

    MUlUNGU NGATI KUMWAMBA UKO MULIKO VANI KULILA KWA ANA ANU AMALAWI CHOSANI NYASI IS

  • @williamyusuf259
    @williamyusuf259 2 месяца назад

    Owinayo ndiwachipani chanji?

  • @DavieKalonga-y5j
    @DavieKalonga-y5j 2 месяца назад

    Mr Don't Trust mumakwana kwambiri

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 2 месяца назад

    Tsiku lofa NYANI mitengo imangotelera

  • @shanlaljith5389
    @shanlaljith5389 2 месяца назад +1

    Ndalamazo tizilandira kumazidya ndithu koma osawavotera 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

    • @VungaQueen
      @VungaQueen 2 месяца назад

      Ndenkhani zikakufikani dyani osaopa osafooka 😂😂😂 km voti njee Ku MCP 😢😢

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa 2 месяца назад

      koma ndaseka kumangodya bas ndlamazo

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 2 месяца назад

    Mbambande mangochi mumatiyimilira

  • @FaheemChipojola
    @FaheemChipojola 2 месяца назад

    Kkkkk mangochi oyeeeeee ndipo kumangochi sangawine anthu amenewo

  • @ErickTym-u2m
    @ErickTym-u2m 2 месяца назад

    Tambala wafa chibudu

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem 2 месяца назад

    Tiyeni tiyeni ndalamazo tikudya ndizathuzomwe

  • @SaidiAdamu-c6i
    @SaidiAdamu-c6i 2 месяца назад

    Ifeso a limpopo fm tiimakunyadilani kwambili

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 2 месяца назад

    Ife sitimafoira big mangochi ndi more

  • @WilliamMasauko-su1wx
    @WilliamMasauko-su1wx 2 месяца назад +3

    Kuyipatsa Moto Mr don't trust

  • @ChanguMbozi
    @ChanguMbozi 2 месяца назад

    Chakwela sawina 😂😂😂😂

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 2 месяца назад

    Ndalamazo idyani koma asawavotela afiti obadwira muchikangawa😅😅😅😂😂😂,ngongole landilani koma musazabweze

    • @zimmekapachika6784
      @zimmekapachika6784 2 месяца назад

      Ndiwolotse nkakupange kanyenya😂😂😂😂😂😅😅😅😅 yomweyo mr Chikangawa 😅😅😅😅😅😅😂😂😂

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 2 месяца назад

    Mangochi woyeeeeeeee mcp yizipita basi

  • @jonas-xh4hz
    @jonas-xh4hz 2 месяца назад

    real story we cannot laughing with such kind of silly things like this

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 2 месяца назад

    Chiyambi ichi mcp ulendo bs

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw 2 месяца назад +1

    Zipitilile asapeze mpata a m c p zisilu zimezi zichoke

  • @DouglasNjerenga
    @DouglasNjerenga 2 месяца назад

    Wina aziona agalu a yemusipi

  • @LaynaAdam
    @LaynaAdam 2 месяца назад

    Mangochi woyeeeeeee

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli 2 месяца назад

    Kkkkkkk Angela galu ameneyu

  • @DoreenKhemusani-v7m
    @DoreenKhemusani-v7m 2 месяца назад

    🎉🎉🎉

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 2 месяца назад

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @robenallie6985
    @robenallie6985 2 месяца назад +2

    Timagawa zambo

  • @Creslevison-vj2sl
    @Creslevison-vj2sl 2 месяца назад

    Mcp out out out out tatopa nayo iyaaaaaaaaaaaaaa fire fire fire unandiiii kut buuuuuu mangochi oooooooyeeeeeeeee

  • @RitaKainga
    @RitaKainga 2 месяца назад

    😂😂 yakwiya ndimizimu bas

  • @ChristianMtambalika
    @ChristianMtambalika 2 месяца назад

    Mwaonatu zayambika onkha mcp out

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 2 месяца назад

    Akhaula kkkkk

  • @DonexNasenga
    @DonexNasenga 2 месяца назад

    😂kkkkkkk akulila amcp