Limpopo Ntanyiwa woyeee kufika nazo zomwe wapezaso chigawo chaku mmawa 19 July 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 14 окт 2024

Комментарии • 176

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 2 месяца назад +15

    I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa.

  • @OmegaKauya-i5y
    @OmegaKauya-i5y 2 месяца назад +22

    Kumvera mwachidwi limpopo with comrade nta

  • @EstherBonga
    @EstherBonga 2 месяца назад +9

    God will protect our country in Jesus name, Limpopo love ife

  • @AroushMussah
    @AroushMussah 2 месяца назад +14

    Inuyo Mr ntanyiwa mumatimilira ndipo enafe tikudziwa direction chifukwa cha inu ndipo popanda inu sibwenzi tikudziwa mene zinthu zikuyendera mdziko muno inuyo ndi nyali ndipo musadzafe mudzangosowa ngati elliya❤❤

    • @VungaQueen
      @VungaQueen 2 месяца назад

      Mwalakhula dzoona without Limpopo bwezi enafe tili chabe azasowedi Ngati Elijah wakumwamba🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 2 месяца назад +8

    I love you My brother Ntanyiwa mumakwana Mulungu ankhale Nanu nthawi zonse

  • @ImanRashidi-so4oo
    @ImanRashidi-so4oo 2 месяца назад +4

    Powerful massage ❤❤
    Live from south Africa Durban Pietermaritzburg

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto 2 месяца назад

    Live from Durban South Africa ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @RitaKainga
    @RitaKainga 2 месяца назад

    Sizingatheke Coomrade,kummwela Kuno kudzera pa Limpopo FM anthu achenjera,palibe angamvere zamamina zaozo, Salute Limpopo Staff

  • @MalvenDzonga-x7h
    @MalvenDzonga-x7h 2 месяца назад +19

    Umatha upitilidze ife dzikuti wawabe ndipo tsitiza iwara imfa

  • @ephraimphalawala4720
    @ephraimphalawala4720 2 месяца назад +1

    In Jesus name, Bon Kalindo will be protected.

  • @cosmasnkanda8193
    @cosmasnkanda8193 2 месяца назад

    We always pray for you comrade ntanyiwa❤❤❤

  • @Mirrium-h3l
    @Mirrium-h3l 2 месяца назад

    Mulungu akukute ndi chitetezo Chake mtanyiwa

  • @MalawianMediafm97
    @MalawianMediafm97 2 месяца назад +3

    This is Comred ntanyiwa on Lipompo FM kuzangoturikira ndi khanga zaona more 🔥🔥🔥

  • @happymumba2261
    @happymumba2261 2 месяца назад +10

    Ulemu wanu big mumakwana

  • @JessicaKatugwe
    @JessicaKatugwe 2 месяца назад

    ndilimphee kuvela limpompo tv and ikungong'alula

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 2 месяца назад

    Chikangawa boys on a Mission, Koma ziliko liko.
    Tchimo limazunza. Ngati akudziwa Kuti ndiabwino mchifukwa chani matukutuku akuchiluka .
    Macathy Chikangawa muyaluka . There is God out there who created heaven and Earth

  • @thomgondwe6594
    @thomgondwe6594 2 месяца назад

    Live from Canada

  • @EdnahShantell
    @EdnahShantell 2 месяца назад

    Ankolo mtanyiwa vumbutso la late grace chinga lundipezano , Chipani Cha Thukuta ndi mwadzi chija ichitu,, ankolo Bushiri ndi Mai Banda aja amati sazaonekera koma azakhala Ali momo SI izi kodi😢 Ambuye chitani nawo agaluwa

  • @AaronLilexMphangwe
    @AaronLilexMphangwe 2 месяца назад +1

    Wishing you more life our Malawian voice Comrade Mtanyiwa

  • @VungaQueen
    @VungaQueen 2 месяца назад

    Zikomo poti ziwitsa km mulungu akutimva anthufe kulira kwanthu kwa tsiku ndi tsiku atimenyere nkhondo iyi patekha sitintha 👏👏 ulem wanu fm ladio

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf 2 месяца назад

    Posowa masomphenya dziko limaonongeka.

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 месяца назад

    Ndipo ndikuona dziko lino likulowa nkhondodi tisamare AMALAWI ndithutu

  • @TijaChilembo
    @TijaChilembo 2 месяца назад

    Here in mfuwe zambia we are happy with you mntanyiwa, keep it up with your good job

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 2 месяца назад

    Ndipo amene samvera Limpopo FM ndi awa akumatamanda zigawengazi Lazarus Chakwera ndi zigawenga zimzake

  • @ArtherGondwe
    @ArtherGondwe 2 месяца назад

    Ntayiwa ndi boni karondo mumatiimilira murungu akudaliseni timakupephererani kwambir

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 2 месяца назад

    Limpopo ifetu tili ndi inu.akangoyelekeza kuphaso wina ,dziko lathu ndinkhondo basi

  • @MrThomas-j9d
    @MrThomas-j9d 2 месяца назад

    Kodi napatumbo ameneyu akufuna athe tundu wathu wa Malawi mulungu akuwone zonsezo

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 2 месяца назад +1

    Ndiyetu aombera Malawi yensetu.chifukwa amene atatsale mbiri ilipobe.

  • @esthermalixani2244
    @esthermalixani2244 2 месяца назад

    Umakwana iwe wa rimpopo

  • @TressLuka
    @TressLuka 2 месяца назад

    Ndiwe wekha Mtanyuwa 😅😅😅

  • @WinerdShadreck
    @WinerdShadreck 2 месяца назад +7

    Ntanyiwa umakwana

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 2 месяца назад +1

    Aaaaaa apolice amenewo ndi opusa ine sangandipange zamanyizo ndipo sindingaimbe, aphwanyeni agaluwo

  • @davidkadyakapita8836
    @davidkadyakapita8836 2 месяца назад

    Ulemu wanu Big

  • @RanaQari-py4bd
    @RanaQari-py4bd 2 месяца назад

    Koma zotsenzi amene ndi chifukwa cha Ife anthu ndi amene thikuphangitsa zotsenzi ndi Ife anthu osauka chifukwa MCP ayikha ndalama phatsogolo kwanyengelera

  • @WilliamChirambo-cp5dl
    @WilliamChirambo-cp5dl 2 месяца назад

    Tikuona chilichose chomwe chikuchitika tili mmaso

  • @FrankHaruni
    @FrankHaruni 2 месяца назад

    Ndichocho manganya ndi wakudzimbabwe apotende mwabaya mr tanyiwa

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 2 месяца назад +5

    Basi chikangawa chakwera akhalira yomweyo kupha iiii

  • @sulleahmnyimbili1362
    @sulleahmnyimbili1362 2 месяца назад

    May God intervene

  • @GomezganiChiwaka
    @GomezganiChiwaka 2 месяца назад +1

    Powerful message

  • @AlickOdala-v5g
    @AlickOdala-v5g 2 месяца назад

    Mutamuuza umatha big up

  • @MaggieBanda-ft5tu
    @MaggieBanda-ft5tu 2 месяца назад

    Zikupeleka sense ndithu,sikuveka zoona,chifukwa manganya akudabwitsa,wagundikilanji ndikumwela

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 2 месяца назад

    Comrade nta your the best with Limpopo fm❤❤❤❤

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 2 месяца назад

    Anthu amasegula mimba kamba ka tanyuwa Muona moto tanyuwa osaopa ana mwachepa inu Mcp atanyuwa kachakumwa bwaaaa

  • @AdamuAsani
    @AdamuAsani 2 месяца назад +11

    Ife pa 31 july tikukayatsa moto ma Demo anyooo

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim 2 месяца назад

    Chakwera this time sitikusiya try kupha modzi kwa amenewa

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 2 месяца назад

    Agwiridzanedi kuti achotse nyansizo

  • @PaulJelemani-rh6kl
    @PaulJelemani-rh6kl 2 месяца назад

    Mulungu wathu sakhala chete

  • @ephraimphalawala4720
    @ephraimphalawala4720 2 месяца назад

    Tiuzeni Bwana, musatope nafe iyayi

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 месяца назад

    Thank you ntanyiwa may Tha almighty God be with you always God is watching what is happening in Malawi, Mulungu kumwambako tetezerani wina aliyense wakonzekeredwa chiwembu chofuna kuti aphedwe afungatireni ndi mapiko anu yehova mchtitseni manyazi mdyerekezi musalore kuti apambane, tipulumutseni mu chimzimu cha imfa pakati pathu Mulungu

  • @JohnMeleka-s1t
    @JohnMeleka-s1t 2 месяца назад

    Mulungu apitilize kukutetezela kt oipawo agwe mumatope

  • @HannockMesiwni
    @HannockMesiwni 2 месяца назад

    Kungofa munthu wina panopa ndinkhondo

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal 2 месяца назад

    Komatu akangoyelekeza kupha wakumwela aziwe kuti tsiku lomwelo iyeyo azachoka pamoando siku lomwelo

  • @JosephHill-fy1bb
    @JosephHill-fy1bb 2 месяца назад

    Olo atalanda ma galimoto,,, ife vote yathu palibe angayisokoneze
    UTM yamakandulo Boma!!!!
    🔥🔥🔥

  • @ephraimphalawala4720
    @ephraimphalawala4720 2 месяца назад

    Lero nde wayamba ndi mototu kkkkk😂

  • @EleosJari
    @EleosJari 2 месяца назад

    ❤❤❤

  • @EmmanuelMpalagule
    @EmmanuelMpalagule 2 месяца назад +1

    Lililililililimpopo fm, nd Comrade ntanyiwa u make me feel gud

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 2 месяца назад

    IFETU TIMANENA KUTI USI NDI GALU NYANI OPUSA KUYENDA AKUYENDERA ZIPATALA NDI MISIKA SIKUTI NDI NTENDERE ALINDI CHOLINGA , SIZIMENEZI KOMA SIZITHEKA MUKUNGU AKUONA

  • @CosimassKalula-x5t
    @CosimassKalula-x5t 2 месяца назад

    Akomred ntanyiwa ndinu nyale yathu mulungu azikutetezani kwa adani amenewa kuti mupitilize kutiuniila🔥🔥🔥

  • @moyo77777
    @moyo77777 2 месяца назад

    Mya God bless you brother for what your doing to Malawian's 🙏🙏

  • @MphatsoIshmaeladam
    @MphatsoIshmaeladam 2 месяца назад

    Ntanyiwa is talking true, anthu a MCP akudziwa kut kumwela kuzakhala kovuta kut apeze mavot ndichifukwa chake akulimbana kukopa anthu akumwela koma ife manso ali kuchikangawa munya muona

  • @louisemsowoya8235
    @louisemsowoya8235 2 месяца назад

    ❤ Bravo Limpopo 🔥🔥🔥 Malawi waopsa 🤔Kodi chilango chosemphana maganizo ndi kupha????💔💔😭😭😭👹👹👹

  • @Samtv627
    @Samtv627 2 месяца назад

    Koma kungoti timve kuti mulomwe aliyense waphedwa Malawi a zavuta kwambiri ifenso tizapha ochewa ✊✊✊✊✊✊✊ sitikuoopa

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 2 месяца назад

    Manganya sangamupeze munthu kumwera kuno ife zausilu kuno ayi

  • @giftmulima6615
    @giftmulima6615 2 месяца назад

    Live from Welkom Free state

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 2 месяца назад +3

    Our truth station radio more fire

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 2 месяца назад

    MCP ilinso ndi magalimoto a chipani tipemphe ACB afufuzenso ku Congress ngati alidi pa chilungamo

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 2 месяца назад

    Timamukond zedi Mr ntanyiwa ambuye azikupatsa chitetedzo chokwana ndi moyo wautali nose ku kustudio kwanu❤❤❤❤❤

  • @MebleNgulinga-hi6rg
    @MebleNgulinga-hi6rg 2 месяца назад +1

    Oh Zosakhala bwinotu mmmmmmm MCP WHY?
    Komatu chaona nzako chapita m'mawa chili kwaiweeee
    This is your time you can do what you want MCP and everything it is well now.....but wait your day for God's revenge for his People and usana mudzauwona ngati usiku kuli kuwawa ndi ululu wachilango

  • @SaidiAdamu-c6i
    @SaidiAdamu-c6i 2 месяца назад +5

    Ntanyiwa mumatiyimilila ndipo timakunyadilani kwambili

  • @FosterChinzimuBanda
    @FosterChinzimuBanda 2 месяца назад

    Mwela madzi, Ntanyiwa umatha umatiimilira.

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson 2 месяца назад

    Akawombela mwa ena amaina antchulidwawa nafe tiyamba po uchifwamba nafe olimbana ndi atsogole a MCP kumawaphanso

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 2 месяца назад +1

    I love limpompo ❤.......more lv keep doing lv

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 2 месяца назад +2

    Oh Dziko lathu Abale

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em 2 месяца назад

    Mr Ntanyiwa mulungu azikudalitsani opanda inu ife tiri chabe

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 2 месяца назад

    Akunamidzana ife kumwera sitidzavotera MCP

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 месяца назад

    Anthu nonse mukukonzekera zopha anzanu nde ngt inuyo ndi amuyaya mutakafe ndi inuyo

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 2 месяца назад

    Atanyiwa munthu wofuna kupanga zimenezo sangalalikire angopanga zimenezo kuti payere payere basi wosati kulalikira angothana nawo ngati mankhwalawo alipodi

  • @EvanceLumeyo
    @EvanceLumeyo 2 месяца назад +2

    Jane Asah knew this 😭😭😭

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 2 месяца назад

    Ndikutitu anthu amenewa apenge misala ngati Nebuchadnezzar.
    Akufuna anthu ayankhule kuti awaphe. Ndege muli nazo zingati zophera anthu

  • @MariaNyamwera
    @MariaNyamwera 2 месяца назад +1

    Akulephere kuulutsa uthenga wa kuchikangawa anthu qkutulutsa ndalama mboma momo koma kungopha anthu what type of government is this may God help us

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 2 месяца назад

      Ndipo ndi chimfiti chimangonama kuti ndi M'busa Ali chigawenga cha chabe-chabe

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka 2 месяца назад +2

    Comrade Ntanyiwa limpopo 🎉❤

  • @owengulumba5189
    @owengulumba5189 2 месяца назад

    Big up Limpopo FM

  • @violetpotani
    @violetpotani 2 месяца назад

    Koma tili pa mavuto oopsya, ambuye titetezeleni ife ana anu tili chabe pa tokha sitithasititha😢😢😢

  • @AnaLourencokan
    @AnaLourencokan 2 месяца назад

    Antanyiwa..inuyo....zikomo..mulungu..akudalitseni ..inuyo ...aaa

  • @NaduMbewe-zz6iw
    @NaduMbewe-zz6iw 2 месяца назад

    Lelo nditapita ku limbe ndapeza azimai amabelo akumvela limpopo

  • @ChimwemweSuluma
    @ChimwemweSuluma 2 месяца назад

    My favorite ntanyiwa

  • @GeraldMustafa
    @GeraldMustafa 2 месяца назад +1

    Apaseni umboni akalindo akasume ku khoti or mtambo yo asanaphedwe abale 😢

  • @ShareefDouglas
    @ShareefDouglas 2 месяца назад

    Akuona ngat tikavota chifukwa cha mantha?

  • @Gmtmphats124gy
    @Gmtmphats124gy 2 месяца назад +2

    Moto kuti buuu pa 31 atitola amenewa

  • @AbrahamTembo-z5k
    @AbrahamTembo-z5k 2 месяца назад

    Kodi Limpopo FM ili pa frequency yanji?

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 2 месяца назад

    Ntanyiwa pasavute apa ndiyekuti mulungu akutipatsira zigawenga zinja manja mwanthu wina atelekeze kuwomba mfuti ndikudziwa kuti kwawobedwa mfuti uku haaaa auzana chikangawa yose chifukwa nde tipha mokanyanga ndimanja anthu atipata mokwanira zingawenga za chikangawazi aaa ayelekeze ankhubira mulungu kubwera kudzawalanditsa ayese awone zachibwana eti

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 2 месяца назад

    Ife tili ku overseas tikukuvelanso ndipo iweyo umakamba zoona.

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 2 месяца назад +1

    God protect malawians.

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere 2 месяца назад +2

    Mtanyiwa❤

  • @ThandiBinali
    @ThandiBinali 2 месяца назад

    Mulungu akufungatileni Atanyiwa

  • @RafickMbwana-l6f
    @RafickMbwana-l6f 2 месяца назад

    Udzingot ntiko osat wa utm

  • @PaulMwachande
    @PaulMwachande 2 месяца назад

    Ndiye aombele anthu onsewa ndiye dzikoli likhalapo koma mmmmmmmmmm

  • @HoseKatsekera
    @HoseKatsekera 2 месяца назад

    ulemu wanu

  • @AlfredSteven-v9m
    @AlfredSteven-v9m 2 месяца назад +1

    Wabwera iweyo❤

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 2 месяца назад +1

    Ife athu akumwela ngakhale atimane kuti atikope ife sitikukopeka misozi sinathe maso mwathu