TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 106

Поделиться
HTML-код

Комментарии • 202

  • @GOEMENGONDWE
    @GOEMENGONDWE Месяц назад +7

    Congratulations to Mr. Zimveka for his great acting in these all episodes. He is doing an excellent job portraying his character and the difficult situation the way character should be acting and how he is going through. Mr. Zimveka's acting feels very REAL and GENUINE. He clearly working hard to understand the role deeply and bring the character to life in a believable way. His performances have been truly impressive and engaging for us to watch.
    Well done, Mr. Zimveka, for your outstanding acting skills and commitment to your craft. You have set a high standard with your powerful performances bringing the comedy to real life

  • @lovemorenaluso8965
    @lovemorenaluso8965 Месяц назад +2

    Farao and Chisomo ndiinu Madolo, iwe Zakhwima wati ayaya samasamala zithunzi zanu😂😂😂

  • @GodfreyChikwapulo
    @GodfreyChikwapulo Месяц назад +1

    Kodi osangomumasula kuti mimbayi ndiyako bwanji aaaa mwana wanzanu avutike chomcho😂😂

  • @rabsonkaunda4554
    @rabsonkaunda4554 Месяц назад +1

    Koma Faraoh. Akuzunzika eeeh. kuletsedwa kukwatira, kuchoka ayi koma adzikhala single. kkkkk
    Zimveka inuyo mmatha ndipo mmakhala serious bwana. I like your character

  • @zaithwachiwaya8885
    @zaithwachiwaya8885 Месяц назад +1

    😂kom farao ndi chisomo mumativesa kukoma🤣🤣🤣🤣

  • @user-ec7du2yf9d
    @user-ec7du2yf9d Месяц назад +1

    Farao waipasa fire,,, kumangowerengera madzi aphutsi😩🤭😅😂🤣🤣🤣🤣🤣

  • @LucasBetiasseJairosse
    @LucasBetiasseJairosse Месяц назад +3

    mimba ndiyake farao chisomo ndi ochenjera kwambiri anapatsana mimba ataledzera kachasu kkkk

  • @masasadannck4726
    @masasadannck4726 Месяц назад

    Kodi chisomo program ikuiyendesa bwanji kkkk 🔥🔥🔥🔥

  • @jrculdickson6629
    @jrculdickson6629 Месяц назад +2

    Koma tu serious ngati chisomo ungaione iyi comment chisomo u are so cute ilove u chisomo

  • @ZioneIssah
    @ZioneIssah Месяц назад +2

    Mumakwana frawo end chisomo ❤❤😂😂

  • @BlesskudaJunior
    @BlesskudaJunior Месяц назад +2

    Komatu chisomo akurakwisa apase adye kamoz 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🔥🔥💞

  • @user-pj7hn2ky5j
    @user-pj7hn2ky5j Месяц назад +8

    Faraoooooo more 🔥🔥🔥🔥

  • @justinenambazo6855
    @justinenambazo6855 Месяц назад

    Farao and Chisomo mukusewera bwino kwambiri keep it up

  • @user-nl5nk2wx1q
    @user-nl5nk2wx1q Месяц назад +7

    MR ZIMVEKA OSAMAZIVUTA MWANAYO NDI WATONDE 😂😂😂

    • @IssaMmadi-zh8un
      @IssaMmadi-zh8un Месяц назад

      😂😂😂 komaditu mwanayo amutenge mwiniwake tonde

    • @user-ng9mj2sb7f
      @user-ng9mj2sb7f Месяц назад

      Eeeh ali mkukakamira 😅😅😅

  • @ElickPhiri-bf2jt
    @ElickPhiri-bf2jt Месяц назад

    Chisomo sankha chimodzi farao azipita or else banja liyambikepo 😂😂😂

  • @RonaldGama-gz9ug
    @RonaldGama-gz9ug Месяц назад

    Faroooo kuponyera kwakuya ..kulowa ndi mutu 😂😂😂😂

  • @PeterMachaka-mn5di
    @PeterMachaka-mn5di Месяц назад

    Falao ndi one koma ndikudzuka khotsi Falao chiso ndi wanga kkkkkk

  • @JohnSmart-fg6ci
    @JohnSmart-fg6ci Месяц назад

    Farao very impressive man.

  • @AmaduMkwapatira
    @AmaduMkwapatira Месяц назад +2

    Koma farawooo ndi chisomo mmakwana inuyo😂😂😂🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-zd2ne1ic2v
    @user-zd2ne1ic2v Месяц назад

    😂😂😂😂😂 murore farawo apite watopa kunkhara singo

  • @BlessingsMakalani
    @BlessingsMakalani Месяц назад

    Ndizomwe ndimayembekezera kudzera kwachisomo and Farao

  • @edgarlastone
    @edgarlastone Месяц назад +6

    Farao wavutika 😅😂

  • @BlessingsMakalani
    @BlessingsMakalani Месяц назад +1

    Koma akhalango mukumatinvesa kukoma

  • @shakajudahTV
    @shakajudahTV Месяц назад

    KKKKKKKKK 😂😂😂😂 farah😂😂😂😂

  • @BentryKumwenda-ze2gn
    @BentryKumwenda-ze2gn Месяц назад +4

    Farao wayaka moto pilira m'bale mwina mimba ndiyako anakudyesa utaledzera kkkkkkk

  • @khumbophiri9006
    @khumbophiri9006 Месяц назад

    Chisomo ukumunzunzatu faraoyo
    Mmasuleni ayende akamwe madzi iiiiih

  • @GOEMENGONDWE
    @GOEMENGONDWE Месяц назад

    But zimveka congratulations 😂😂

  • @IbrahimSaid-hu1uf
    @IbrahimSaid-hu1uf Месяц назад

    Faraoh ❤❤ umatha Koma chisomo akumukhomelela faraoh srs

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos Месяц назад

    Pharaoh your number 1 😂😂😂

  • @LlopPitros
    @LlopPitros Месяц назад +1

    Bravo guys koma mwayamba kuchedwa heavy

  • @ShadreckMwija
    @ShadreckMwija Месяц назад

    Mumuyakhetu bwino bwino achisomo falauyo osatiso azikangona kumakasuko sanavesesetu ameneyo

  • @ZandileZuma-cb1sq
    @ZandileZuma-cb1sq Месяц назад

    Faraoo wavuta tuu kkkk next

  • @user-qq1uj7ct6n
    @user-qq1uj7ct6n Месяц назад

    bwanji osabweresa mwini mimbayo azizagwira mmalo mwa Farao? kuzunzanatu kumeneko chisomo. zoona munthu uzingomugoneka kumakasu?😂😂😂😂

  • @CalvinThomson-ys5zf
    @CalvinThomson-ys5zf Месяц назад

    Farawooooo naye ndimuthu amatopa 😂😂😂😂

  • @user-co8zf3px8v
    @user-co8zf3px8v Месяц назад

    Chisomo siyeni farao azipita ngati simukufuna zomwe afuna iye

  • @IbrahimAdam-pb7rn
    @IbrahimAdam-pb7rn Месяц назад

    Koma pharaoh yo tapangani zoti zimuthekere mwatani Kodi kkk

  • @violetnkhoma8535
    @violetnkhoma8535 24 дня назад

    Analimo mu epsode iyi mr chibiliti,,, Nkhani ya chisoni

  • @jrculdickson6629
    @jrculdickson6629 Месяц назад

    Kwaife ife amene school yanthu tinaphunzira pa dzenje taziwa kale kuti chisomo akumukonda pharao😂😂😂😂😂koma sakufuna kuoneka ophweka kutengeraso kuti mimba ilipo kale 😂😂😂😂 pharao my blood from mulanje wawina kale miaziyo mtima pansi man imwani kae msuzi wa nyembao nyemba zeni zeni muzipeza pansi😅😅😅😅

  • @dominicmphepo-jk8lk
    @dominicmphepo-jk8lk Месяц назад

    Farawoooo wayaka motooo kkkkkk

  • @gracechiumia7103
    @gracechiumia7103 Месяц назад

    Faraoooo ndiwe dolo😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @shibeymaliro
    @shibeymaliro Месяц назад

    😂😂😂 falaoo fire 🔥

  • @HameedahMasambuka
    @HameedahMasambuka Месяц назад

    Farao mooooo 🔥 🔥 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @AishaPanjira-od9hg
    @AishaPanjira-od9hg Месяц назад

    Faraooo akufuna banja km uli bho kwambiri

  • @benedictmaguda8799
    @benedictmaguda8799 Месяц назад +1

    I like this play kwabasi, plz kip it up!!!!!

  • @mafukenimasangwi5487
    @mafukenimasangwi5487 Месяц назад

    Farawo mukanango fusila basi zika kanika nkumapita

  • @RAZAQJAMES
    @RAZAQJAMES Месяц назад

    Kkkkkkkkkk falawooooooo umakwana kkkkkkkkkkk

  • @IssaMmadi-zh8un
    @IssaMmadi-zh8un Месяц назад

    Atonde NSO no mutende mkhazi amene munabalekera mutengane ndi amayi akeabora
    Komaso chisomo amurore faraow watopaso no
    Komaso David abwererane ndimkhaziwake

  • @AfickDaud
    @AfickDaud Месяц назад

    Pharaoh2 ukuonda ase nkhan yake ndi chiso yemweyu?
    Chiso aona plan don't worry kkkk

  • @user-jk4ew3pm6l
    @user-jk4ew3pm6l Месяц назад

    Mayi phili mukungofuna kusokoneza banja lazanu

  • @ellenkanyenda3211
    @ellenkanyenda3211 Месяц назад

    Chisomo ndi Farao Kkkkk ayi zikomo

  • @chewejeali1059
    @chewejeali1059 Месяц назад

    Following...

  • @BenjaminGondwe-po5dq
    @BenjaminGondwe-po5dq Месяц назад

    Faraoh 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @petrosmunthali5562
    @petrosmunthali5562 Месяц назад

    Farao ayiphula basi😂😂😂

  • @duncankamthemba1100
    @duncankamthemba1100 Месяц назад

    Ukunamatu pharaoh pakhomopa sukuchoka mpaka ulera mwana

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg Месяц назад +1

    Koma falawo ndi chisomo yafika po beba 😂😂

  • @mosewallace9717
    @mosewallace9717 Месяц назад

    l can't wait to see falawo kusatira chifukwa nyumba ,mumakwana guys siku langa layenda bwino 😂😂

  • @user-dx5dc4sm5v
    @user-dx5dc4sm5v Месяц назад

    Farao ndakatundu😂😂😂😂

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Месяц назад

    Nyc

  • @SleepyHarmonica-rg4ic
    @SleepyHarmonica-rg4ic Месяц назад

    Koma inuyo afalaho ndi chiso mmmm mavuto kwabasi

  • @chimTchausi-wh9yf
    @chimTchausi-wh9yf Месяц назад

    Farao fire

  • @IshmaelChimera
    @IshmaelChimera Месяц назад

    Falao wayaka moto😂

  • @GeoffreyMajawa-fw2lk
    @GeoffreyMajawa-fw2lk Месяц назад

    Iyiyi Pharaoh waipha

  • @WilliamBauren-nm8lb
    @WilliamBauren-nm8lb Месяц назад

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣Faraoh

  • @user-ng9mj2sb7f
    @user-ng9mj2sb7f Месяц назад

    Eeeh naye Faraoh ndi muthu 😂😂😂

  • @AfickDaud
    @AfickDaud Месяц назад

    Question to Ans, farao wakuliramo akut azakwatira litino kkk

  • @user-kp1wr4ql5d
    @user-kp1wr4ql5d 29 дней назад

    😅😅 pharaoh 😂😂

  • @user-bg7lk9sx7n
    @user-bg7lk9sx7n Месяц назад

    Zikuoneka ngat tonde ali limodz ndi madola coz asowera limodz

  • @user-hj8wr7zb2m
    @user-hj8wr7zb2m Месяц назад

    Kkkk kma farao umatha

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos Месяц назад

    Aziveka mwaganibho samalani mwana wanu

  • @user-ip6pt3rw7f
    @user-ip6pt3rw7f Месяц назад

    faraoooo waiphula

  • @marynjanji985
    @marynjanji985 Месяц назад

    Kkkk faraoh

  • @gracechiumia7103
    @gracechiumia7103 Месяц назад

    Faraoooo muzimiika kumayambililo plz 😢

  • @MacErnest-se1xm
    @MacErnest-se1xm Месяц назад +1

    Party ya farao. Imandisangalasa heavy

  • @user-sm3vj3uu8u
    @user-sm3vj3uu8u Месяц назад

    Chiso uli na sambi😂😂

  • @mailosyasin3110
    @mailosyasin3110 Месяц назад

    Kkkkkk koma ma actors ndi ma actress inuyo mumatha

  • @PrincehrnNgombayela-rq3gi
    @PrincehrnNgombayela-rq3gi Месяц назад

    Watutiratu farao sakuimva

  • @user-rj6ry7pr3l
    @user-rj6ry7pr3l Месяц назад

    Achisomo mupaseni mwayi falawo

  • @bonifasthemba9624
    @bonifasthemba9624 Месяц назад

    Faraoooo uja kunoooo

  • @user-df7yx8fw3v
    @user-df7yx8fw3v Месяц назад

    Zinveka sawumila mawu😂

  • @gidyonmshani5259
    @gidyonmshani5259 Месяц назад

    Farao walimba ntima akhufunitsisa banja

  • @patrickzembani4315
    @patrickzembani4315 Месяц назад

    Chisomo ukumudzunzatu munthu mmene wakuliramo basi azingokhala singo🤣🤣🤣🤣🤣🤣🔥🔥🔥

  • @VictorLatchana-lk3iw
    @VictorLatchana-lk3iw Месяц назад

    Nayeso farao watopa

  • @mcdontonchida4761
    @mcdontonchida4761 Месяц назад +1

    pharaoh at his best good drama

  • @atom3492
    @atom3492 Месяц назад

    Kumachita kudikira 2weeks for next episode

  • @nonhlanhlanhlanhlo3907
    @nonhlanhlanhlanhlo3907 Месяц назад

    Maitha madolo😅

  • @cananmwale4313
    @cananmwale4313 Месяц назад

    Next please

  • @bonifacebwanali9815
    @bonifacebwanali9815 Месяц назад

    Pharao tangomipatsani metre basi kkkkk

  • @thomaschipinda6952
    @thomaschipinda6952 Месяц назад +1

    Kodi mai phiri mkazi uja pali cholowa, mulitu serious. Farao udya dekha 😂😂😂

  • @SungeniChabwera-xv9td
    @SungeniChabwera-xv9td Месяц назад

    Faraoooooooo eeeee ndi nkhani Zina ndithu

  • @frankkachigumba187
    @frankkachigumba187 Месяц назад

    kkkkkkkkk chiso akanangomasuka basiiii coz there is something behind ..........why faraoh

  • @GOEMENGONDWE
    @GOEMENGONDWE Месяц назад

    Farahooo palije chimene alakwa iye

  • @SleepyHarmonica-rg4ic
    @SleepyHarmonica-rg4ic Месяц назад

    Mmmmm kwavuta uku nditu

  • @VanMak-ry9mm
    @VanMak-ry9mm Месяц назад

    Any way I love Dollah but chisomo wayamba kundifikaposo ndingophatikiza

  • @storytambala6088
    @storytambala6088 Месяц назад

    Eeh koma Farawo, nkazi oyembekezerayo ngati ndi wako?

  • @SurprisedDriftwood-ef3lc
    @SurprisedDriftwood-ef3lc Месяц назад

    23:30 farao siwukuchoka udyesele mimba

  • @KennedyMakonda
    @KennedyMakonda Месяц назад

    Waiting next faraoh ndi chisomo banja kapena ayi !?

  • @wilsonfelix6559
    @wilsonfelix6559 Месяц назад

    Koma ndaseka farao mmmmmm anakonza

  • @user-nl5nk2wx1q
    @user-nl5nk2wx1q Месяц назад +1

    TONDE WAPITA KUMUZI KWAO 😂😂😂

  • @MacksonTchovaNkwinika
    @MacksonTchovaNkwinika Месяц назад

    😂😂😂 Farawo mlenji apite metsa chakudya akumunama munthu apite kumkadzu wake Farawo adzikadya bho bho

  • @AgriwhatMW
    @AgriwhatMW Месяц назад

    Farao nde watopadi ndi munthu iyeyo naye amatopa😂😂😂 😂😂😂😂