NKHANI YA IMFA YA EDSON CHILEMBA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 26 май 2024
  • Chonde mvetserani mwachidwi nkhaniyi ndi kuwathandiza kuti chilungamo chichitike - NKHANI YA IMFA YA EDSON CHILEMBA
  • РазвлеченияРазвлечения

Комментарии • 36

  • @user-qk1mp9qc5r
    @user-qk1mp9qc5r Месяц назад +2

    Mmmm shame 😢😢😢😢😢zovesa chisoni abale Mzimu wawo uwuse mu mtendele sure munthu anamfa imfa yowawa

  • @PangananiChikaoneka
    @PangananiChikaoneka Месяц назад +2

    Limbani mtima chemwali. Mlandu sumaora. Mudzasuma boma likadzasintha. Yembekezerani pa Yeheva basi. Pepani 😢😢😢

  • @ShadreckMwija
    @ShadreckMwija 12 дней назад

    Ipakaso okupha kumachalenja ondandaula Malawi wakaka ndiuchi unja akupita kuti wasanduka wamangazi ndi misuzi?
    Zikomo Mulungu ndiamene akuziwa akuthandizani akumbanja sizinaenereke kutero ause mutndere chimwene waifeyo pooezaso amapita kukapanga zachalichi muyembekezere kuona zachilendo kwaoseo amen

  • @OlivaKambelembele
    @OlivaKambelembele Месяц назад +3

    Eish chilungamo chikuyenera chiyende ngati madzi apa amqbungwe pls athandizeni nkhani yokhuza iyi😢😢

    • @JAMESSAIZI
      @JAMESSAIZI 15 дней назад

      Ndipo ndizooba 😢😢

  • @GladysChiwanga-vd9zp
    @GladysChiwanga-vd9zp Месяц назад +2

    Mulungu oziwa chilulungamo akukhuzeni ndi dzanja lake pemphero langa ndi kuthekera kwachofuna chanu (justice)

  • @chrispahuwa
    @chrispahuwa Месяц назад +1

    Mmm yandikhuza komanso kundililitsa Mulungu akukimbitseni mitima yanu nonse akubanja

  • @user-jk4ew3pm6l
    @user-jk4ew3pm6l Месяц назад +1

    Achakwela mungotipha amalawi tonse mutchuke ndinu,,, pepani akubanja.

  • @LucyKasengwa
    @LucyKasengwa Месяц назад +2

    Very sad 😭😭

  • @ThokoKamvuma
    @ThokoKamvuma 21 день назад +1

    Zomvesa, chisoni pepani ndithu.

  • @joelkatembe9198
    @joelkatembe9198 Месяц назад +1

    ine ndingakaibwenze live imeneyo ndipo eish angamve kunyuunguunya

  • @LM-gz5pk
    @LM-gz5pk Месяц назад

    Ku police kunalowa chinyengo pano... Kumwamba kuli Mulungu onse apanga izi komaso akubisa chilungamo Mulungu akukatheni

  • @starlonJames-qr4xl
    @starlonJames-qr4xl Месяц назад

    Aeee zosankhala bwino hey km dziko kd likupitakuti😭😭😭 pepani pepani akubanja

  • @MathpeterLemon-ls1ns
    @MathpeterLemon-ls1ns Месяц назад

    Kodi mulibe anyamata oti atha kungobwezera okha zachambazi inuyo musadandauleyi ingobwezerani basi

  • @EstherKanjanga
    @EstherKanjanga 6 дней назад

    Pepani ambuye alowelele

  • @JamesPaul-rg6tj
    @JamesPaul-rg6tj Месяц назад

    Farawo kkkkk mbambanfe

  • @user-dc3bo2ey8t
    @user-dc3bo2ey8t Месяц назад

    Zovetsa chisoni ndithu

  • @juliusnjerengo2610
    @juliusnjerengo2610 Месяц назад

    This is very bad, I hope people in authority can help this family.
    Mr Mgombe why?

  • @MathpeterLemon-ls1ns
    @MathpeterLemon-ls1ns Месяц назад

    Ineyo vuto ndi mm'ang'anja ingotumani munthu akatape phazi basi tilange

  • @EsnartMateuchi-bz7bo
    @EsnartMateuchi-bz7bo 12 дней назад

    Rest in peace

  • @robenmatchilinga604
    @robenmatchilinga604 Месяц назад

    Ambuye akhururukre pepan akubanja

  • @user-kv1ik8tj6k
    @user-kv1ik8tj6k Месяц назад

    Sizoona ulamulilo uwuwu siulibwinoayi guys chakwela atimaliza guys tiyenitimpephelelechakwela amwalile guys atiphatuuyu

  • @user-lj3dx7wz9t
    @user-lj3dx7wz9t Месяц назад

    Anthufe koma chikondi chimatisowa kwambiri ambuye yekha ndiamene akuziwa koma

  • @hanneckkadyampaken2197
    @hanneckkadyampaken2197 Месяц назад

    Too bad

  • @lingstonenagoli7729
    @lingstonenagoli7729 Месяц назад

    Koma dziko iliri limakonderad anthu alemera komanso andale omwe akulamula pa nthaw imeneyoyo,,kumupha munthu opanda chifukwa aaah

  • @nadiahPhiri
    @nadiahPhiri Месяц назад

    Anthu kuyipa kuposa Satan 😭

  • @OmarSalim-jo4ne
    @OmarSalim-jo4ne 26 дней назад

    Chipani cha mcp

  • @angellahmuwowo9413
    @angellahmuwowo9413 Месяц назад

    Pepani akubanja very sad

  • @BentryThupa
    @BentryThupa 22 дня назад

    Pepani

  • @ChrispinChikagwa
    @ChrispinChikagwa Месяц назад

    Mulungu amabweretsa zinthu poyera ndipo choonadi chidziwika komanso munthu umakolora chomwe wabzala. Mu mtima mwanga mukuwawa ndipo mulungu chitani mukuweruza kwanu

  • @KavisikaMaria
    @KavisikaMaria Месяц назад

    Sorry

  • @OliverNkhoma
    @OliverNkhoma Месяц назад

    Uyuyu kungomuphanso pogwiritsa ntchito gulu

  • @elias.m.chunga
    @elias.m.chunga Месяц назад

    Very bad

  • @ThokoKamvuma
    @ThokoKamvuma 21 день назад

    Zomvesa, chisoni pepani ndithu.