Комментарии •

  • @danielkhinguirossejuliasse6106
    @danielkhinguirossejuliasse6106 4 месяца назад

    Mbiri zake zopepera bwanji agaga aribe mbili yoguira mtima

  • @dalisoulphiri3094
    @dalisoulphiri3094 4 месяца назад +2

    Koma ndiye nyimboyo munaifunatu kumayambiliroko,,, abale taziyesetsani kumapangako upgrade munthu ukufuna uwonele program ya 45 minutes koma 10 minutes yonse kutha ndi nyimbo yoyambila mpaka kutopa ahaaa

  • @CHRISTOPHERMMAKIWA-mu8wn
    @CHRISTOPHERMMAKIWA-mu8wn 3 месяца назад

    Mafunso akuvuta oyenenera akuvuta kwambiri pamenepo,mbiri ya Maphunziro ake sananene,zitsuzo anayamba bwanji ayi,

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 4 месяца назад

    Mchifukwa Chake gaga umandibyasa umbava wachikhalidwe kupita nawoso musewero

  • @LinoMatchado
    @LinoMatchado 4 месяца назад +1

    Jazila amuthamangitse mulesi uyo😂

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 4 месяца назад +1

    Kufusa mafuso adzeru akuvuta

  • @NELSONMULIMAH-fv6ub
    @NELSONMULIMAH-fv6ub 4 месяца назад

    Apatu zimasemphanapo

  • @MathpeterLemon-ls1ns
    @MathpeterLemon-ls1ns 4 месяца назад

    Nyimboyi nduyifuna pilizi

  • @giftblack7690
    @giftblack7690 4 месяца назад

    😂😂😂😂 gaga ulesi okhawo nde muli bodza alibeso malo okha uyu kkkkkkk umatha gaga iweyo umatiyimilila

  • @Maxwell-e2d
    @Maxwell-e2d 4 месяца назад

    Kod uyuyu akuti chani 😂😂😂😂

  • @ancientkantonasoja103
    @ancientkantonasoja103 4 месяца назад

    madeya muli bodza 😊

  • @Gifttembo1979
    @Gifttembo1979 4 месяца назад +1

    Timafuna timve za xool

    • @Maxwell-e2d
      @Maxwell-e2d 4 месяца назад

      STD 3 koma yakale 😂😂😂😂😂

  • @LitnessKaunda
    @LitnessKaunda 4 месяца назад

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @QassimuWassi
    @QassimuWassi 4 месяца назад

    Gaga 😂😂kaya madeya

  • @AliAli.aliheassim
    @AliAli.aliheassim 4 месяца назад

    Madeya ukunama nkhaniya waleti

  • @ladymart-mw723
    @ladymart-mw723 4 месяца назад

    😊

  • @adamusaidih8570
    @adamusaidih8570 4 месяца назад

    Athu ambili samatha kusiyanisa history ndi khani awa akukamba khani osati history 😂😂😂😂😂😂 ndichifukwa makolo amati kunva ndikunvesesa ndikosiyana ndiye amazati tabweleza zomwe ndanena cholinga aziwe kt wanvadi