ATSEKELEDWA KUMANDATU UKU🏃🏃...Ufumu umodzi kuukirana ..KANGAUDE 28/05/2024...MIBAWA TV content.

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 окт 2024

Комментарии • 37

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba 4 месяца назад +6

    Abweze changu tione zina mmudz muno

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 3 месяца назад +1

    All this is because of extreme poverty.

  • @AnnieNkhata-q9j
    @AnnieNkhata-q9j 3 месяца назад

    Ufumu apatseni anyamatawo😃😃 nanga ku gwilizila mpaka kutengelatu amatelo ndipo anawo akuwoneka anzeru

  • @frankmzomera2798
    @frankmzomera2798 4 месяца назад +1

    Koma Abel ati "ndinu amene mumasokoneza?"😂😂... nkhani ndiya straight iyi perekani ufumu kwa anthu oyenera basi

  • @TheresaKuluwemba
    @TheresaKuluwemba 4 месяца назад

    Amagasa ndi osokoneza kwambiru, ras dan ufumu munabwera nawo kuchoka ku chiladzulu kod? Koma guys 😅

  • @rashidsaid2232
    @rashidsaid2232 4 месяца назад +1

    Pachilungamo ufumu umampatsa mdzukulu wako means the child of your sister that's all nothing else gulu lachina Rastalo ndiye mwiniake ufumu enawo anango gwilitsira basi abweze kwainiake basi

  • @MathewsSande
    @MathewsSande 3 месяца назад

    Nthawi zonse a chipani Cha dpp amakhala osokoneza

  • @Mussa-s4g
    @Mussa-s4g 3 месяца назад

    Kkkk koma siyamasewelo

  • @HawaMamo-q2v
    @HawaMamo-q2v 4 месяца назад

    Umfumu ndi wazizukulu chifukwa zimenezi ifeyonso tinaziwona ndithu...kuyambira lero tiziwe kuti sizithu zabwino umfumu kumusiyira munthu oti simbali yake lero ndiye izi ongwirizila aja pamene apita ana akufuna kutenga umfumu ...sizabwino izi

  • @BlessingJohnas-hu7lj
    @BlessingJohnas-hu7lj 4 месяца назад

    This 2 guys are right. Ufumu umapita kwa zizukuru. Unless ngati akuwukana ndipomwe amapasano anthu wamba.

  • @ShallaPoolokera
    @ShallaPoolokera 14 дней назад

    Yooo

  • @RoseMbande
    @RoseMbande 4 месяца назад

    Hamayooo kwathu ku Chirimba kwasokonekera kunali kwa BATA mthawi ya Chatha tinali anthu omvera ,,chonde kambiranani

  • @BFWCPHIRI1978
    @BFWCPHIRI1978 4 месяца назад

    Mfumu udayenela kuti uchokere ku banja la mfumu kazi omwe adamwalira zaka zapitazo osati Asuyawo,,,,,,,,
    Uwo ndi ufumu ogula because T/A wadelalo ndi cash hunger

  • @DonaldPonda-p2q
    @DonaldPonda-p2q 4 месяца назад

    Pempho bata ndi yabwino kusiyana ndi kukangana gonjelanani ufumu upite koyenera kupita

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 4 месяца назад +1

    Kkkk zokanganira zake kkkkkkkk

  • @mackmawunde4857
    @mackmawunde4857 4 месяца назад

    A Ras awapatse ufumu bs akuoneka amzeru kwambiri

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py 4 месяца назад

    Umfumu wadziko lapansi Ndiomwe wamvuta abale 😂😂

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py 4 месяца назад

    Kodi gatelo aliseka ndi Loko ? Ngati gate lake iri ndi gate ya sunghwi osangothyola bwanji aaaaaah😂😂😂

  • @CardoJustin
    @CardoJustin 4 месяца назад

    Ine amayi anga panopa agwirizira ufumu koma si wawo ndi azibale awo azatong'ole ditso kuti ndi wawo

  • @YassonNavilembo
    @YassonNavilembo 4 месяца назад

    mmene zikanayenela kunkhalila ufumu upite kwa anawo

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 4 месяца назад

    Mkulu wa dpp yu ngosokonesa akufotokoza zinthu zomwe sakudzidziwa

  • @CosmasChikwindi
    @CosmasChikwindi 4 месяца назад

    Ufumu umakhala wa zidzukulu osati ana amfumu potengela ndimwambo wakumwela

  • @RabeccaGama-f7m
    @RabeccaGama-f7m 4 месяца назад

    Muzabweraso kwakameza nako zilikoliko

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 4 месяца назад

    Kkkkkkkkkkkkkkk😂😂😂😂😂😂 koma❤❤

  • @ChoopsyaLloyd
    @ChoopsyaLloyd 4 месяца назад

    Ana apasidwe ufumu awo zokangana sizabwino

  • @isaackaima890
    @isaackaima890 4 месяца назад

    Mpingo wanji uwu wokometsawu?

  • @JosephChitseko-ro9fv
    @JosephChitseko-ro9fv 4 месяца назад

    Wakuba ameneyu afumu ndi anyamatawo ndalama ndi udindo zosiyana

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 4 месяца назад

    Ufumu ndi wa anyamatawa ndalama ndi zawo osawanyengerela

  • @GennuhGangster
    @GennuhGangster 4 месяца назад

    Yaa umfumu ndi wadzizukulu osati ana obadwa ai

  • @FlorahBanda-fl4vf
    @FlorahBanda-fl4vf 4 месяца назад

    😂😂😂akut mwayamba ina nkhani ya kalaliki

  • @GeofflyDyton
    @GeofflyDyton 4 месяца назад

    Alindimpanda? Kkkkkk

  • @successm-vt3dx
    @successm-vt3dx 4 месяца назад

    ziliko ziliko

  • @LuwisKaigwaze-gr6cg
    @LuwisKaigwaze-gr6cg 4 месяца назад

    Ma raster amazitsatatu

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft 4 месяца назад

    Ufumu ndi wa adzukuluwo osati ma cousin

  • @clalesschisale3792
    @clalesschisale3792 4 месяца назад +1

    Kumalawi mkooma bola kukhala ndi bundle basi 😂😂😂😂

  • @YassonNavilembo
    @YassonNavilembo 4 месяца назад

    mmene zikanayenela kunkhalila ufumu upite kwa anawo