Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Kkkkk Kkkkk wagula matewera kuionera patali metre
Kkkkkk, komatu zimvekayu sadzatheka basi😂😂😂
Chiso zafikapa bas fewesan mtima mukhale mai falawo😂😂😂
Rip Mr Lester Aka Chibiliti,koma alamwanu zikuoneka kuti katundu adyesa kwa Dev kkkkk
Farao ma example 😂😂😂 ndi ma Exercise
😂😂😂😂😂😂 gaga nde ndidolo sopano
😂😂😂😂😅 kumapanga ma example koma Faraoh 😂😂😂😂
It is good
Eeee Mayi Phiri mkulongolola 😂😂
Farao zitheka ndithu, Zimveka naye yake ija akuti amunenela mwana ku Police zitamuvuta.
I'm proud of being a Malawian, mukundimvetsa kukoma inu a team ya Tonde wadula,, more fire.
Chisomo wayamba kukhwefuka Farao moto yasabe
😂😂😂😂😂😂aziveka kuzichinjiliza😂😂😂
I love you chisomo u are so beautiful
Gaga yake ija akufuna kudzigulira place uku naye farao wayamba kuguluriratu pa pampas 😂😂😂😂
Rest In peace A Chibiliti.
Farao amatha Koma next time zikuonetsa farao and chisomo likhala banja
basi chilamu chatheka gaga🙌🙌
Zimveka kuyitembenunza nkhani 😂😂😂
Rest in peace chibiliti😢😢
Gaga upited plz ituluke mmawa gaga ubwerese nkaz plz ❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉
Azivekawa ana amango berekerendwa ndi Tonde nanga bwanji amangosirira ana azao
Zimveka😂😂😂😂😂uhule mwafikapotu nawo mmmmhhhh
Ine sibambo wako kkkk
Gaga😅😅
Kkkkkkkk km ziveka eeeeeeee chidya makandaditu
RIP Mr Chibiliti anagumbo asala ndi ndani 😭😭😭
Komatu farao ndi husband material😂😂
Ali ndi chibwana. Kukakamira too much mkulu ameneyu.
Koma ZIMVEKA 😂🎉😂🎉😂
Chisomo a Nambewe ati fodya ndamene Ali pa phuno utinazoo bwaa I can't wait for 109 episode. Along side Gaga na mlamu kkkk zikiko😂😂😂
Gaga ndi mlamu wache😂
Zimveka😂😂😂😂eish
😂😂😂Koma kumeneko
gaga ndi kasupe kkkkk
Farawo osadandaura udya
koma zimveka kkkkkkkk
First to watch 😅😅😅🎉
Farao atenganso mkazi uja, Zimveka sazakula, Gaga akuzigulira malo😂😂😂😂
😂😂😂zimveka ndi chidya makanda bas
Rest in peace Mr Chibiliti tikusowani
Zimveka!!!😂😂😂😂😂
mbambande ma guys😂😂😂
Ni police case zimveka 😂😂😂
🎉🎉🎉 ndipo mumandisangatsa chiso & frawo ndi one pawokha
Farao kuganiza kwa thinking
Gaga machine akwanitsa zimenezo I can't wait mfundo zake
🤜🤝🤙
Koma gaga sazatheka
Look sharp 😂😂😂
A Anambewe asiyeni achimwene anu ndi anagumbo
Ma example omweo farao
Farao my number one fan ...😅😅😅😅 koma mpaka ma example
Mmm farao mwaonjesatu koma
Inu please tanenani bwino za achibikiti zikumvekazi ndizoona?
Kkkkk koma gaga sazatheka
Farao watola nkhwangwa ndi mpini omwe❤
Chisomo unisamale ohooo I love you and Dollah
First to comment and to view
😂😂😂😂😂tione kt gaga akafika ndi mbalumbe zanji
Falao oyeeee oyeeee oyeeee oyeeee oyeeee
Koma falao kkkkkkk
😂😂😂😂Achibiliti vesazi Anambewe
Ma guys mwayamba kutiyika zitendeni
😂😂😂 anambewe kumenya kampeni ya farao
Gaga ndi big man ameneyo zintheka nditu
Wakumana nazo Ziveka lero 😂😂😂
Jomba mukumaikwanisa srs ulemu wanu
Farao ma example omwewo😂😂
Kkkkkk wayaluka ziveka
Khetemu
Koma a zimveka ulehu unakupwetekani😂😂
Second to comment and fifth to view
Keep.fire burning guys
Farau ndimo
Aziveka shafa kwadolo😆😆😆😂
Kkk ma example ndofunika mukakhala odwala
Chiso ndi best actor
Ma example 😂😂😂😂 koma farawo
Can't wait for episode 109😂😂🥺❤️🩹❤️🩹❤️🩹
Makwale ndi katundu
Mlibhoo ma big
Mayankho a Farao sopano .
Kkkkk Kkkkk Fargo ma example
Faraoh yayamba kugwira
😂😂😂😂😂😂
Ma example omwewo 😅😅😅😅
Farao ndi katakwe😂😂
Falawo ❤❤❤❤
Gaga 😂😂😂
Man farao mwaionela patalitu 😂😂
Yachina tonde
Pano mtima uli ku ndege yosowa ya chilima
Zimveka ndi bilimankhwe
Gaga
❤
Tikumakunyadirani guys
Olo ka sounds kokhako umangodziwilatu kuti achina Chiso ali ground
Azimveka khalikani iya
Mbambande
Tonde
Faraó kkkkk !
Ma example omwewo farao