NJIRA ZINA ZOPEZERA UMBONI WA CHOMWE CHINAPANGITSA NGOZI YA NDEGE YOMWE INAPHA DR SAULOS CHILIMA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 13 июн 2024
  • NJIRA ZINA ZOPEZERA UMBONI WA CHOMWE CHINAPANGITSA NGOZI YA NDEGE YOMWE INAPHA DR. SAULOS CHILIMA NDI ANTHU ENA 8.
  • РазвлеченияРазвлечения

Комментарии • 270

  • @leonardngala6148
    @leonardngala6148 26 дней назад +22

    Kuyankhura koma kumeneku ithink ndinu munthu wowopa Mulungu. God bless you

    • @madalitsokalima8533
      @madalitsokalima8533 8 дней назад

      It's not all aircrafts that carry data and voice recorders because the equipment is very expensive in most developed countries only planes that carry above 16 passengers and they are commercial,all planes are mandated to have a transponder which sends a ping that to show position for the air craft.And this aircraft being military less hope it was carrying data and voice recorders and that they were recovered safely for engineers to analyse.On top of that service records, communication between pilots and traffic control also plays a big role in investigation.

  • @campbell8988
    @campbell8988 23 дня назад +7

    This is the type of wisdom we need, ndamva audio yanzeru since i started following this issue. Stay blessed

  • @evelynnzima1716
    @evelynnzima1716 26 дней назад +29

    My deepest condolences to our beloved sister country of Malawi. As a Zambian citizen I mourn with you. The Lord is your strength!😢

  • @user-ol1hf7ru1v
    @user-ol1hf7ru1v 26 дней назад +26

    Zikundiwawa kuchiona chichakwera pamwambo umenewu aaa amalawi please 🙏 munthu wationjeza uyu

    • @ChrissKaswaya
      @ChrissKaswaya 26 дней назад

      Ose anali kuja amaziwa siku lakwana inuyo mumaona ngati chilima azamfa imfa yodwala yokha kapena ndi wamuyaya mulungu uja mmamulila uja kuti zithu zikudula akumva mapemphelo aja

    • @yowasschitsosa5348
      @yowasschitsosa5348 26 дней назад +2

      Usapiteko tisie tiike maliro a president wathu mwaulemu

    • @user-lz5yv4vj6h
      @user-lz5yv4vj6h 26 дней назад +2

      He wasn't suppose to be there

    • @glorynkhata1185
      @glorynkhata1185 25 дней назад +1

      It's accident you never pridict or know if the pilot loss the control so what ? He was not God chilima

    • @LeendaDeborah2005
      @LeendaDeborah2005 25 дней назад +1

      @@glorynkhata1185the pilot never lost control. The villagers that live near that place said that the plane landed perfectly do not blame the pilot 😑😑

  • @AaronDungadunga-ff2ny
    @AaronDungadunga-ff2ny 26 дней назад +12

    Munthu amene anapanga kuti chilima ayende pa ndege akhale munthu oyamba kupereka umboni chifukwa iyeyo ndiamene ali ndi nkhani yonse ya imfa ya chilima ndipo akuziwa chilichose chomwe chinachitika ndipo ndiyemwe anapanga plan yonse ya mmene chilima amayenera kuyendera

  • @giftnyirenda5614
    @giftnyirenda5614 26 дней назад +5

    Bwana ndinu munthu wanzeru koopsya. Nkanakonda nkanakudziwani.
    Your are a matured person, civilized.

  • @speakwellgladys5569
    @speakwellgladys5569 22 дня назад +1

    May the Lord bless you brother for your wise and humane speech may the Lord give you abundant wisdom...

  • @dominicmphepo-jk8lk
    @dominicmphepo-jk8lk 25 дней назад +4

    God bless Malawi with wise and intelligent people like you bro.
    But such good ideas can't be welcomed now in Malawi we are amongst the weakest people.
    But you are talking well bro

  • @hendrickbanda5644
    @hendrickbanda5644 20 дней назад +1

    My heartfelt condolences from Zambia

  • @yahgoshen5815
    @yahgoshen5815 26 дней назад +7

    Thanks brother mwayankhula bwino

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e 26 дней назад +6

    This massage is open a Malawian eyes let work together to find what cost deaths of our peoples RIP

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l 17 дней назад

    Umbuli these record information no one can stop it... This man is talking something very sensible ❤❤

  • @ThomasMphande-f8d
    @ThomasMphande-f8d 8 дней назад

    Inu abwana mnapitadi ku school mnthu wa school amalankhula motelomo zikomo God bless you.

  • @user-kw7wr4kq9w
    @user-kw7wr4kq9w 25 дней назад +1

    We need people like u God bless you ❤❤❤❤❤

  • @BlendaMpinga-fy8dx
    @BlendaMpinga-fy8dx 23 дня назад +1

    We have lost our dearest father my your Saul Rest in Everlasting peace my the good lord provide love Mary

  • @Shereenmustapha
    @Shereenmustapha 26 дней назад +5

    Very true.
    Takumvan abwana

  • @loziSteven
    @loziSteven 26 дней назад +1

    Well said sir. It's my hope that the two devices were collected from wreckage site, are secure and will be made available during enquiry.
    May their souls rest in peace.

  • @YamikaniLoya
    @YamikaniLoya 26 дней назад +7

    This massage makes a lot of sense

  • @StiveriaChikonga
    @StiveriaChikonga 25 дней назад

    Thanks for this massage 🙏

  • @levisonchimseu2779
    @levisonchimseu2779 25 дней назад

    Kulakhula kwa wisdom brother

  • @tapiwakalako-pm1ty
    @tapiwakalako-pm1ty 26 дней назад

    Well said bravo may the souls of those who were in the plane rest well

  • @vascoholland3273
    @vascoholland3273 25 дней назад

    Well spoken, keep on giving better and good advice to the nation of Malawi, only God knows what really happened the day our beloved deputy president passed on, let only the investigation reveal the truth
    May the souls of the deceased rest in eternal peace 😭😭😭😭😭😭

  • @thomluciouss7360
    @thomluciouss7360 15 дней назад

    May the lord show his grace through our brothers and sisters who lost their lives due to this accident

  • @ArthurMzingeni
    @ArthurMzingeni 26 дней назад +2

    God bless upangili wabwino

  • @AnthonyPhiri-bm4vs
    @AnthonyPhiri-bm4vs 24 дня назад

    Thanks polangiza ndikuphuzisa komwe koma ino ndithawi yoti athu alakhule zakukhos kwao iyi ndi imfa yowawa so do pray with it

  • @kachisuzimwale5641
    @kachisuzimwale5641 26 дней назад +2

    Good message

  • @greenwellmponda2363
    @greenwellmponda2363 25 дней назад +2

    Malawi 🇲🇼 my country,mourning together here in Zambia 🇿🇲

  • @user-nv5bd4rn8f
    @user-nv5bd4rn8f 26 дней назад +1

    Ambuye akudalitseni. Thus strong word

  • @Okalekale
    @Okalekale 26 дней назад +2

    Kufotokozela bwino,nzika ya nzeru.Ambiri ndi okhudzidwa koma kulira ndikosiyana-siyana.Tiyeni tilireni,tiyike maliro,then kafukufuku achitidwe mosasiya kanthu mpaka zidziwike zeni-zeni zomwe zinachitika,inali ngozidi kapena umbanda.

  • @chifundomatumula1652
    @chifundomatumula1652 26 дней назад +3

    Well said but kwathu kuno chilungamo chimabisala when people in power, rich and highly trained and educated are involved coz they influence the outcome of the investigations

  • @EuniceKalambo
    @EuniceKalambo 26 дней назад +5

    God have mercy...

  • @angelmalawiofficial9172
    @angelmalawiofficial9172 23 дня назад

    Well impact information Leader

  • @ireentaombe
    @ireentaombe 25 дней назад

    Following with interest

  • @EliChitupe
    @EliChitupe 25 дней назад +1

    Thank you sir ❤❤

  • @CynthiaPatel.E.B
    @CynthiaPatel.E.B 22 дня назад

    A big respect to you sir

  • @aggieguda8660
    @aggieguda8660 26 дней назад

    God bless you Mr

  • @user-qs7nx7wi4j
    @user-qs7nx7wi4j 26 дней назад +8

    Loud and clear milandu sorted km funso tizinthu timeneto tilipo

  • @joaquegerman2250
    @joaquegerman2250 17 дней назад

    God bless you man

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 25 дней назад

    Thank you sir

  • @micheckphiri5447
    @micheckphiri5447 26 дней назад

    This is a good talk

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 25 дней назад +1

    Ambuye wakumwamba bwelesani nthenda yamisala pa mbeu yose ya chakwera ndi azake ose achiwembu😢😢😢

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos 25 дней назад +1

    Mavuto abwerakale pano Kaya atimanga. Atimange basi chakwera wapha chilima 😭😭😭😭

  • @benchilenje9856
    @benchilenje9856 26 дней назад

    Mwayakhula Mr

  • @Hellenistic109
    @Hellenistic109 22 дня назад

    God bless you sir

  • @bensawanga9662
    @bensawanga9662 26 дней назад

    Leader par excellence.MHSRIP 🙏

  • @innocentsathasteven4093
    @innocentsathasteven4093 26 дней назад +1

    Sad story to loosing anthu omwe amatipatsa chiyembekezo Pa malawi mizimu yawo iwuse mu myendele

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 26 дней назад +2

    aboma azifufuza chani aboma ndi amene apha anthuwa anachoseranji zimenezo nfusen kunkuyu 'chakwera 'zikhale ng'oma ' ndi asilikali ndi apolice achita kuphedwa ndi mcp umboni ndiwuti

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 26 дней назад +2

    Zikuwawa abale 😢😢😢😢😢 taluza anthu dziko Muno

  • @KenDuweh
    @KenDuweh 25 дней назад +1

    Kom Chilungamo chimaziwika nthawi ikakwana ndipo muzachita manyaz kut Amalawi aziwa chilungamo sopano akuteng step ina yot kuyikilaba kumbuyo sizagwira😢

  • @user-lg2ws2ki3d
    @user-lg2ws2ki3d 26 дней назад +9

    Respect Sir

  • @brightadam110
    @brightadam110 26 дней назад +4

    Awa ndimaganixo womwe ndimaganiza cox ndidavaposo zama devices amenewa kuchoka kwa bwana wanga wa chi China 🇨🇳

  • @user-ul7rb4bn5e
    @user-ul7rb4bn5e 25 дней назад

    Well said 👏👏

  • @John-to8gl
    @John-to8gl 26 дней назад +1

    Nice one 👍 bro message yamphamva imeneyi, maka potiziwitsa bwino lomwe dza tizida Tosunga information tamundegeti kuti timakhala malo olimba or Ndege itayaka moto komano tizida timeneti sitikhuzi ndi moto, I hope tizida timeneti tilipo, ambuye alemekezeke

  • @joaquegerman2250
    @joaquegerman2250 17 дней назад

    God bless you

  • @ImmedGerrard
    @ImmedGerrard 26 дней назад +1

    Respect🙏

  • @user-wd9yd1bg9n
    @user-wd9yd1bg9n 26 дней назад +2

    Komanso ma phone a ma passengers can also be used because amongest passengers one might think of recording or eri

  • @jamesjana
    @jamesjana 26 дней назад +2

    That's only way to find out the foult of the crach of our plan

  • @kayzeesambani7153
    @kayzeesambani7153 26 дней назад

    Respect,🙏

  • @ArchraphNkhoma
    @ArchraphNkhoma 26 дней назад +1

    Iwe Mbuz umafuma azibisa Kut anthu asazione azione kumene oro akanakhala malophyata akanatulutsa coz ngoz siingavule tayi,shat,jekete zose

    • @user-sz6bi3tw5y
      @user-sz6bi3tw5y 26 дней назад

      Bambo uyu ali mbali yachakwera angoyenda mbali apa

  • @user-nb1ns6ye1v
    @user-nb1ns6ye1v 26 дней назад

    Perfect said 😢

  • @lucassakala3352
    @lucassakala3352 26 дней назад

    Too sad rip our brothers and sisters we believe almighty is with your souls Amen

  • @bennyfuratiro8617
    @bennyfuratiro8617 26 дней назад

    Eish ndiri kudandaura ini why why mara, forever in our hearts

  • @wilsonnoahkadyamaliro1358
    @wilsonnoahkadyamaliro1358 25 дней назад

    Well Spoken

  • @NedsonKanjira-qj2ig
    @NedsonKanjira-qj2ig 26 дней назад +2

    Zimenezo zili Ngati macamera anthu amatha kuzimitsa magesi Chocho camera singajambure Chocho musawanamize anthu , zimenezo kutheka Kuti anazipanga off ndizipanga anthu

    • @LeendaDeborah2005
      @LeendaDeborah2005 26 дней назад

      Zidakakhala izizi zachitika ku America bwezi zitapezeka ndithu

  • @Musafiri529
    @Musafiri529 23 дня назад

    Mukamati legend mukutanthauza chani

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 24 дня назад

    This doesn’t need a forensic expert to unearth the truth of the demise of Chilima.
    There are only few questions to be asked.
    1. Not a question as per se BUT just follow the sequence of things that have happened around Chilima the past two months.
    2. Who can stand to benefit from Chilima’s demise?
    3. Those that can benefit from Chilima’s passing, what strange things did they say or do in the past two months or so????
    These are just some of the few questions that if correctly answered, we can have a pointer to what really has happened to Chilima and who is or are behind the so called accident.

  • @georgetwayibu7240
    @georgetwayibu7240 26 дней назад +1

    Live from rustenburge

  • @user-rm2hr8ps1q
    @user-rm2hr8ps1q 24 дня назад

    Lord have mercy on us

  • @SinsamalaWazuwala
    @SinsamalaWazuwala 23 дня назад

    Kulankhula kwa mkhalapakati❤

  • @patchipanga8445
    @patchipanga8445 25 дней назад

    Amen

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 26 дней назад +3

    Good Messnge koma Chakwela you mast go

  • @eskrecordstv7585
    @eskrecordstv7585 26 дней назад

    Its hard

  • @JamesIngeni-ku3qj
    @JamesIngeni-ku3qj 26 дней назад +1

    Wich radio station onse ndi anomaly palibe, umboni uziwike maliro asanaikidwe

  • @HusseinAdamLidezo
    @HusseinAdamLidezo 26 дней назад

    Never give up

  • @user-yb5xh1ry7d
    @user-yb5xh1ry7d 26 дней назад +5

    Kuyankhula uku ndi kwa umunthu koma pakakhala kuti kafukufuku watha anthu izi amaziona, monga momwe anali public figure? Za enawo tiribe nawo ntchito koma chilima. Pali mau ngati mukuona kuti chilungamo chidzavuta gwiritsani u salvage. Usaone ngati pali umbuli

  • @SuperStuart1999
    @SuperStuart1999 26 дней назад +1

    Mulungu lowreranipo, tiziwe zoona za ngozi yimeneyi.

  • @feehasaidid.r.d
    @feehasaidid.r.d 26 дней назад +1

    Nkhani ndiyoti zimenezo aboma azibwelese kuti azipange cleare okha

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g 26 дней назад

    Okay following 😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @gracemusuku6645
    @gracemusuku6645 26 дней назад

    🙏

  • @DianaNakazwe-bl6oz
    @DianaNakazwe-bl6oz 22 дня назад

    May their souls rest in peace what a tragic

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 25 дней назад

    God please give big disease family for chakwera 😢😢😢 mukantheni chonde mulungu wanga napota nanu

  • @KomaniMvula
    @KomaniMvula 25 дней назад

    Not only Malawi but all maneba mu africa

  • @ElinaDuncan
    @ElinaDuncan 22 дня назад

    Zomvesa chison rest in peace Mr chilima

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b 26 дней назад +2

    Kachiduloko nkutheka chakwera anatuma wanthu kuti akachoseko

  • @DianaMbewe-sj5qb
    @DianaMbewe-sj5qb 11 дней назад

    😢😢😢 Amen 👏👏👏👏

  • @MichaelWilliamsNyirenda
    @MichaelWilliamsNyirenda 26 дней назад

    Good message But impeachment process go ahead

  • @Furnituremaker-vt8ku
    @Furnituremaker-vt8ku 25 дней назад

    Rest well ❣️❣️❣️

  • @MarcosBanda-su1fb
    @MarcosBanda-su1fb 23 дня назад

    kupepesa ndikomweko koma ndizomvesa chison kwambiri chifukwa mpungwepungwe ulipowu ndi chifukwa cha zithunzi zake zomwezo

  • @roderickmwamondwe5938
    @roderickmwamondwe5938 22 дня назад

    They must not remove these devices from

  • @WitnessPhiri-zr9uf
    @WitnessPhiri-zr9uf 26 дней назад +2

    Kutheka titapezeka timeneto umboni ungapezeke pakugwa kwa ndenge mmm ambuye ayendelepo ndithu

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu 26 дней назад +1

    Bro lnuyo msg yanu munayamba bwino kenako kulakwisa ndinu achitsiru abise zinthuz chifukwa chani zikukusangalasa lwe ndege lri ndimanja kutu lkavure zovara munthu nanga ma4n a Dr chilima ndi anthu ose alikt lweso kape information lkunenayo palibe chazeru atapangepo chakwera apa umboni owona uli muanthu

    • @CatherineChalema
      @CatherineChalema 17 дней назад

      koma phone ikakhale moyo pangozi yoopsayi!!! Malawi tidzuka liti ku umbuli

  • @MosesSolomoni
    @MosesSolomoni 26 дней назад +2

    Akutuma kt utikhazike chete ifeyo

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 26 дней назад

    Tikumva kuwawa my brother koma zikomo mwayankhula bwino pitilizani kutilimbikisa

  • @user-ym4kf9it2d
    @user-ym4kf9it2d 24 дня назад

    chomwe chasarapo ndi holiday basi mumuona chakwela azayika holiday yoti ndege inagwa kumalawi chosecho wapha anthu ndi iyeyo

  • @chekiamaabdul5083
    @chekiamaabdul5083 25 дней назад

    Zokayikitsa ngati zida zimenezo zingapedzeke mu ndege imeneyi ndakqyikila kwambili

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 26 дней назад

    muziti amene amapezeka kumeneko ndi zigawenga zokha zokha zimene zimatumizidwa ndi chakweta ' kunkuyu 'zikhale 'ndi army mosaopa

  • @IsaacDailes
    @IsaacDailes 26 дней назад

    Mr.. Mulungu akudalitseni poyankhula bwino chonchi no mistake 😢😢

  • @FletcherMkwailaMkwaila
    @FletcherMkwailaMkwaila 26 дней назад

    Technology

  • @lottiemcdonaldsoko8589
    @lottiemcdonaldsoko8589 25 дней назад

    I see the same happenings of 1986 when Samora Machel died in the same act

  • @IdiWilliam-uo8tw
    @IdiWilliam-uo8tw 26 дней назад

    Onse omwe atisiya mizimu yawo iuse mumtendere zoyakhula ziziyakhulidwa koma answer yeniyeni ndiyokut Malawi waluza anthu ofunikila Basi.