I have been following you guys since day one,,,, you're doing a very great job,,,,you're teaching achinyamatafe chikhalidwe chabwino,,, relationship issues are great deal as far as youths are concerned,,,,zinthu zachikondi ndizovuta,,,,,thanks for uncovering critical issues and at the same time,,,you're intertwining us,,,,may God bless your all❤
Madolo tisayambane iyiyi muziitulusa pa week katatu ma days musakha nokha Koma ikumachedwa kutuka Ina aaaa zinthu zikukoma izi. Uncle KY mfundu nanu mulibe kkkkkk
Aucle k apopo ndiye mwaiponya kutali 💪
Ulem wanu ma guys uncle k mumatimilila ❤
Iyiy yabwera
I have been following you guys since day one,,,, you're doing a very great job,,,,you're teaching achinyamatafe chikhalidwe chabwino,,, relationship issues are great deal as far as youths are concerned,,,,zinthu zachikondi ndizovuta,,,,,thanks for uncovering critical issues and at the same time,,,you're intertwining us,,,,may God bless your all❤
Mphweteka mwana shasha,kantande ndi mfumu
Noxy ndiwachikape ndipo ndiwotsokoneza.
G Man waziona kkkkk
Auncle K azambatuka tsono.
mumatimvesa kukoma🎉
Kumalawiko ngat kuli best series panopa nde ndi inuyo maguyz mwatinyamula hvy mmmmmm
Koma ghetto rhythms mumativetsa kukoma guys ,i tel you what u are the best ❤️, and i wish u nothing but all the Best 💕💕💕
Munye ndi dolo,g man mwana dolo,nzake wa g man mphweteka dolo,noxy ine sandiwaza in my living God,samatha
More fyre guys mmandivesa kukoma nsaname 😂😂
Nde mpaka kulemba otenga thuli ziwiri ziwiri😂😂😂
Keep it up
Uncle kay,,,,eeeeh apa nde zilibho,,,tione ma dating a uncle k
Moto 🔥
A prophet adabwa mmene Jah man anaphatikizira ma Speaker akuluakulu 😂😂😂😂😂
Ghetto ndi Nyatwa🎉😂❤
Uncle k mwayambatu mukufuna mukare ngati nox
More fire 🔥🔥 guys mukutimvesa kukoma 😅
Madolo tisayambane iyiyi muziitulusa pa week katatu ma days musakha nokha Koma ikumachedwa kutuka Ina aaaa zinthu zikukoma izi. Uncle KY mfundu nanu mulibe kkkkkk
Umu muli funs iwiri inayi,sindiwaza
Jah man kungomenyedwedwa ghetto ilowa mbola kwambir munaganiza buanji
Probably one of the best series in the country 🔥 but pliz try to promote this in different social media platforms yhu guys deserve more views 🙏
Best series ever from malawi❤❤❤❤keep going guys 😊😊
🔥🔥 unandi mumakwana ma boys
Zomaphwekesa Jahman mu ghetto Moo ghetto ilowa mbola.. Jah man azingolanga Ana basi mix Ana asamadelele
Mpweteka mungopwetekedwa za eniwake kķ
❤take me one day guys i may be a good actor 🎉😊
Umakwana kantande muonetse Jahman
Kod simumakhla ndi nthawi yoponya eti??mumangoponya mene mwalotela....komabe keep it up mumatimvetsa illovo
Knoxy ah akupanga zobhowa💔💔
Naknak and Lizie welcome back magayezi, Kantande uzitenge bwino coz Jahman zimene angakupangezo upola moto ukuzitenga ngati wafikapo eti ife timaziwa kuti ghetto ndiya Jahman AKA Mandela
Ati chamba man😂😂😂,,,a prophet mumandiwaza,,,
Za ghetto🔥
Kkkk kantande wapanatu mesa wamanyaz uja iwe
Uncle k cheucheu kkkkkk😂😂😂😂
A Jah man takonzeni kamtande a kusaiza hvy aaa
Kd uncle kay inuso mwapeza wanu😂😂😂
Kma anthu alipachangu nawo uncle k akut akapanda kuyakha ndimapita kwawo konko😂😂😂😂
Abweze thirasipoti basi 😂😂😂
Mumuuze Noxy yo akundikwana ine otherwise mulibooo guys
ankolo K tandisakileni kumene kuli Ruth........
Kma kwayaka moto😂😂😂😂 EEE🔥🔥🔥🔥
Km thawi imatichepera gyz
Kma ngati kantande wawina ndeu kma zakhala bho coz ghetto simukhala dolo mmozi
I like character ya Rasta amayitha kwambiri please Rasta keep it up
Muthu wakulu kwambir nyamata wazamalamulo
Ghetto lectrurer
Ati ndi mkango koma wopanda mano
Ati sagwirira mankhwala😂😂,,,Ghetto rhythm moto kuti buu🔥🔥🔥
More 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 i
Lucy amandivetsa chisoni kwambiri, samakhala osangalala nthawi zose akakumana ndi Noxy,
Mumakwana ma gyz tiyeni naso
Massive series......ghettoh rhymes on fire🔥🔥
Kd uncle kay inuso mwapeza ka mkaz kanu😂😂😂😂😂
Nake nake akuopa zomwe kantande wa phwesa
kodi madala kwitapwani bwanji kodi,,,,, ndikukuwonanitu,,,,, big up......
😅😅😅😅😅😅
My favorite show❤
Zili bho kwambiri ma guy❤🔥
Ka ntande wabwera🤣🤣
Aaah street Lecturer naye akumazauma😂😂😂😂
Koma pweteka amandiwaza hevy😂😂😂😂
Uncle K makwana mwatiphunzitsa😂😂😂
Ndinachita kusunga nthawi moti sinayende ayi mpaka nditaonela magettohs😊
Duu kuonela kaye
Kkkkk kantande lelo nd shasha kkkk mulandu wa ndrama tikakambile pa ded
Jah man kufuna kuwabonesa a prophet 😂 koma
Nde mwat uncle k
Mumatimvesa kukoma guys
Knoxy ndihule❤❤❤
Kma guys osanama mukuyitha serious
Lecture mukupanga chidodotu kaya kkkk
Guys muli chenene kma keep on improving guys like kumbali ya shooting and video editing
Zoonadi kma amayuza ndalama ndiye zifunika kwapanga sponsor sinanga amajambula okha
More 🔥🔥🔥
Ngati mkotheka ndimafuna number ya Lucy
More fire
Kod mku machinjiri? Nyc guys
Umumu muli ma dolo heavy
Koma uncle k akumatchulukitsa kunong'ona
Kkkkkk Jah man alape 😅😅😅😅😅😅
Kkkk😂😂 koma uhule wa noxy 😂😂😂 aahh waonjeza
❤
Iney munyeyu amangondiwaza basi😂😂
Km katande aaaaaaa alibe mfundo uyu
Ankolo K akut ti date ? 😂😂😂😂😂😂
Kkkkkk koma yaaaa
Ndizowona kuti a pulo amatenga nthawi koma sabowa😅😅, muli nfundo
Eeh ndekuti mmaghetto nkhani ndi akazi basi lol
Linda ❤
Uncle k ndi one😅
Ghetto ili hot 🎉
Creative mbambande pakufunika kuthandiza ma camera
Kwambiri
Chamba man
Atiii kapakhonde mu Limbe mu 😅😅😅😅😅
Koma aprophet😂
💥💥💥💥😣😣
🙏🙏🙏🙏
ndati ya phone tu
Kkkkk chamba mn et
😂😂❤❤❤
Mumakwana mitchana
Noxy😁😁
Noxy boring 😠😠
Chamba man