Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
My view ......pharaoh is being deceived that mamuna has gone ku jon with the aim behind to hold him still😂
Kulankhula uku akudalira kuulurazinsisi zawo
😂😂😂😂 achiswa nthaka amafuna nsima yowuma osati Phala 😂😂😂
Tayamika...taziponyani mowirikiza timakusowani
taponyani
Koma molley vest ndi wiscot 🤣🤣🤣🤣
zmveka perekan kwene fon mwana aone number mufon yanu 😂😂😂😂😂
yomweyo chisomo ndi farawo you make my day guys musazafe😂🔥🔥🔥
Koma Dora nzako sungamusiye choncho atabwela kwanu😢
nde mwati za number zataniiiiiii kkkkkkkk zimveka smuthu wamba
Kkkkkkkk kma chisomo ndi pharaoh mumakwana😂😂😂
Mwakwana inuo
Zimveka Man of the match 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Farao wamphula Kaz uja baa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅
ma guys mwauswa kwambili muthinda azimai adya wachinto wakwe ,kms zimveka ana samanyengelera ,km mai zimveka asowa
Farao wayiphula basi🎉🎉
Zimveka eeeee nd dolo hvy
Dave kudabwa kwakeko😅😅
Azimveka uhule wakeso mmmmm
Koma mayi phiri mumakwana
Muthinda 😂😂😂😂
Zimveka my man, keep it up ❤
Conversation ya mole ndi zimveka ngat ingapitilile
Zimveka ❤❤
Farao is a great man! Very resilient and loving.
Falao mutuwo akumauvalila nkati pena
Koma auntie Davie ngooneka bwino 😅
Kod pharaoh ali ndi mitu ingati❤
Rest in peace Achibiliti tikusowani
Km falao ndoifela man😂😂😂😂
Falao pena awoneke ndi mpala pena ndi tsitsi zikukhala bwanji Kodi 😂
Anut Davin jonz inaphweteka
Kkkk pharaoh and chisomo mwadya one
Madala ndi okonda ndalama eti mmmmm mkona anakuthamangisani eti kkkkk komatu mumatha gaez
Farao akuti kalatayi ayilemba mchizungu kapena mchichewa?
Farao ndi one 2 palibeso 😂😂😂😂😂
🤣Akulephera kusiyanitsa😂
Chisomo ndi pharao 😂😂😂😂😂
😂😂😂eeeehh
We can't wait
aaaaa kd mwatop kuchit masewero zoon kudikir kosekujaa sewero lakee la half aaa zandibowaa sindidyaso msim
Inu poyamba mmaonera yaital bwanji mukat aika half mesa ndi momwe amaikira.
Iiii kkk nde mpaka musadye nsima 😅😅
@@estherkamwendo7971 kkkkkkkk
@@estherkamwendo7971 eyaaa aaa kkkk
Wantchito wa mthinda ndi nkazi wa ulemu wake
😂 kwambiritu
Farao ndi nyamata okonda osanama
Farao ndi okonda nyengo zonse
Mumatha
Kkkkkk farao ndisamalire mimba yangayo
😂😂😂😂😂😂 zilliko a Faraoh atola nkhwangwa ndi mpini omwe
Muthinda wapeza mkazi wantchito iwe😂
Time for farao to marry chiso😂
Kkkkkk chisomo walira kuno , bwelani muwone
Koma camera yimene najamburirayi ndiya bwino kwa mbiri
Shamira kugwada mpaka 3hrs
Koma farawo kkkkkkkkkkkk zopsa kwabasi 😂
Kkkkkk love you Dollah and chisomo
Pharaoh apa banja letheka kkkkkk ati waithawa ife tisamala kkkkkkk iweo ndi one
Ma Cheque azimveka,
Kkkkk farao is the winner man ❤❤❤❤
Zinveka amakonda kudya amnzake a Dollah kkkk wainyumwa Dollah
Mmmmm ngati isanthe kukoma kumvela bwanji
🎉kkkkkkk koma farao. Ndi moto😂😂😂😂😂😂
Panopo mukumachedwatu
More kod wamvarazo ndi chan kod 😂😂😂😂😂😂
Koma zimveka ndi Dolo uyu 😅😅😅😅😅 uhure ukuchita kukukhaloa a zimveka
Azimveka khalikani iya Naweso muthinda uti diso mphinyimphinyi kwa mtsikana wa ntchito bwanji
Falao waiphula bs apo banja latheka😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 koma aziveka 😂😂😂😂 amatha
Akuti mamuna uja Wapitha kujon 😂😂😂
Farao woyeeeeee
Tiyen nazoñ maguyz
Koma a zimveka amazichemelera ndalama
farao uyu siwa Bible uja ayi uyu ndiwina wabwino 😆😆😆
😂😂Asamala mimba kkk
Pharaoh wachena
Dollar bambo ako ndi hure😂😂
Good but you guys are late yesesani kumatulusa fast
Zimveka akamuna kkkkkkk
More 🔥
King Farao mmmmm kkkkkkk hahahaha
😂😂😂😂Koma Farao pachoka mzako Pali malo
Waiting
Mole waphya uyo muganizileni bas anagwila ntchito ameneyo
Zikuoneka kut muthinda uli watnchto waulemutu eeee nde ndzako zija wayamba kuionamonso kkkk
Aunt davie😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Aziveka sazatheka kodi mfumu William ndi Gaga alikuti
Kkkkkk koma zaveka ndi hure
Pharaoh the hero
Zimveka ndiwe psyuta otheratu
😅😅😅 mwa Farao muli luso
Ziveka sazantheka😂😂
Aunt Davie 😅😅😅
Kd moleni naye wavala chani😂😂😂😂
Farso amakwana km ........
My number one gayz
Farao wawina chigayo sopano kkkkkkkk
😂😂😂😂😂aunt Davie
Mai phiri ma hope anga 😂😂😂
Kkkkkk koma farao akuti kalatayi ailemba mchizungu mchichewa?
Chisoh and farao
❤❤❤
Mukumachedwa koma pano aaaaaaa tumaiwala ife
Koma ziliko kkkkkkk mumatha inuyo
Hello Farao ❤❤❤❤❤
Uhule zimveka
Kkkkk Farao your my number one

Azimveka khalikani iya
Naweso muthinda uti diso mphinyimphinyi kwa mtsikana wa ntchito bwanji
Falao waiphula bs apo banja latheka😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 koma aziveka 😂😂😂😂 amatha
Akuti mamuna uja Wapitha kujon 😂😂😂
Farao woyeeeeee
Tiyen nazoñ maguyz
Koma a zimveka amazichemelera ndalama
farao uyu siwa Bible uja ayi uyu ndiwina wabwino 😆😆😆
😂😂Asamala mimba kkk
Pharaoh wachena
Dollar bambo ako ndi hure😂😂
Good but you guys are late yesesani kumatulusa fast
Zimveka akamuna kkkkkkk
More 🔥
King Farao mmmmm kkkkkkk hahahaha
😂😂😂😂Koma Farao pachoka mzako Pali malo
Waiting
Mole waphya uyo muganizileni bas anagwila ntchito ameneyo
Zikuoneka kut muthinda uli watnchto waulemutu eeee nde ndzako zija wayamba kuionamonso kkkk
Aunt davie😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Aziveka sazatheka kodi mfumu William ndi Gaga alikuti
Kkkkkk koma zaveka ndi hure
Pharaoh the hero
Zimveka ndiwe psyuta otheratu
😅😅😅 mwa Farao muli luso
Ziveka sazantheka😂😂
Aunt Davie 😅😅😅
Kd moleni naye wavala chani😂😂😂😂
Farso amakwana km ........
My number one gayz
Farao
wawina chigayo sopano kkkkkkkk