This episode deserves an award for sure. Big up guys. You are improving in each episode. I'm casting my flowers to the whole crew starting from the camera handlers 🎉🔥💯
Nkhani ya kobwe yokhayo ngakhale ine nditha kulowa fast yosafunatu until khobwe athere2 mnyumba 😂😂. #pat#Gan# Ngozo achita kuthawira2 serie yonse osaonekako kuzemba ndiwo khobwe.❤much love from South Africa guys mumatha.
Tili apaaaaaa mesa Cheteeeee kudikilira kut Gani nanga Patricia and Mtebede aza zanji osaiwala Langwani NGAUZOOOOOOOO🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥USAUVER TO THE WORLD 🌍🌎
Ma fans a Ganizani tilikuti
pano hahahahh
🤙
We here
Ife pano amathu
Ife Pano 😂
Let's gather here for ganizani 🔥🔥🔥🔥this dude is so protective 🙌
Ndimunthu wamkulu
What do you mean protective kapena you wanted to say Proactive??
🤣🤣🤣🤣🤣
Super mumakwana
Amene timayembekezera kut hyphen amupezelera mkazi wake ndi Mashasi tikweze manja😂😂😂😂😂😂😂😂
Ndipo ine pano thought ali munyumba momo
😊
Kkkkk koma Gani guys wandikumbutsa kale ndithu .... Mpaka Tonde .... Nyooo
Inde ife tikampanga zimenezo 😂😂
Sangie ndi vibe kwambiri🙌🙌🙌. Sungaonere part yoti pali sangie munthu osasekai. Ahhhh bigup Sangie. Ahhh ndakutaira mitengo yonse🙌🙌🙌🙌
🙌🙌🙌🤸🤸🤸
Ndipo chomwe chandisangalatsa pa Usauver ndichoti yayambira pomwe inathera 5 ndipo muzitero guys keep high high
🎉
Nane ndazikonda
Kkkkkkk guys mmatha
Ganizani ndi actor mbambane mmmmmm uyu anakonza
Patricia and Ganizan acting ili good heavy, big up guys🙏
Kkkkkkkk koma ziboo amixsa boo m,tchana
Best comedy ever 🎉 koma muja anapangira MPUGWEPU kuopseza a shadow asadzabwerezeso fukwa ineso ndnachita nawo mantha 😂😂😂😂
Aaaaa ndiwausilu amene uja bwanji ,nanetu ndinazizimuka kkkkkkkkk!
😂😂😂😂😂😂
Atha kukhaladi sing'anga weniweni. Zizimba
Ndipo anatutumusa gulu😂
Mzimu unathawamo nane hahahaha
Ine Gani amandiwaza😂😂😂. He is so calm koma zimayankhulidwazo🙌🙌
This episode deserves an award for sure. Big up guys. You are improving in each episode. I'm casting my flowers to the whole crew starting from the camera handlers 🎉🔥💯
Ganizani akhale ambassador # take care for young girls
Emmie ya sugar Mamie akuyitha, sangie is just the best, Gani is very natural excellent. Keep it up guys and kamwana kaja kakuitha heavy
Kma sangie🤣🤣🙌 nde it's the song for me and I like ganizani too, he is a natural
Iyi nde best ever eeh yachuluka fans bwino....
Keep it up guys camera kuposa tv ya bomatu koma ganizani machine ❤
Koma Patricia ati muyende bwino ndikudziwana kwanu🤣🤣🤣🤣🤣
zipongwe🤣🤣
Gwamabodza Patr
😂😂😂😂ndipo Patricia iih
😅😅ndpo pat mabodza
I just love this episode 😍, hyphen adzafa ndi BP tu akangodziwa🤣🤣🤣
Amangozipezera mavuto okha okha..kk
Coming every Friday to check for next episode to find nothing is boring 😭.
Nice, good camera balancing, nice camera angles, amathu amatha, nice effort.....
Km Patricia wandsekesa pakat pa usiku ndipo ndmangobwerez pamodz pompo ' akaxi awo amenewo, akazi awo atsopano, akuziwan nd matious, 🤣🤣🤣🤣 nsaname keep the fire burning, moto kuti 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kandiwaza kameneka😂😂😂😂😂😂
Amashas asalapang ono kuti onse akome ku den kwangozo ayambazii kkkk
takoma tonse..., in Ngozo's Voice
And the song at the end is so nice,simungatuluse
I like it too
Kkkk akuti tonde nyooo koma gani 😂😂 big up guys
😂
Patricia n Ganizani eeee u pipo😂😂,,,,, but the song hits so hard in my heart😢😢
I see great creativity in our movie industry in coming two years 🔥🔥💪
wow this is amazing
Ganizan you're now my favorite actor 🔥🔥🔥🔥
Tonde.... Nyooooo..... You have reminded our childhood😂😂😂😂😂
I saw Ganizani at Kamuzu stadium. Dazi lija ndizazenizeni eti, ndimaona ngati ndimu usauver mokhamu
😂😂😂😂😂
Uli ndi mwano adha
Kķk
Mucheza bwanji koma?😂😂
Mashasii eee mashasiii😂😂😂
iyiy yzpangidwa premier pa ma tv kumalawi kuno zinangoyamba mwachibwana kma ❤❤❤
Khobweyo akupeza akukudikirani kkkkkkkk
Koma sangre 😂😂😂 ndiwe wamabodza😂😂😂😂😂 applause for ganizani🎉🎉🎉
Nkhani ya kobwe yokhayo ngakhale ine nditha kulowa fast yosafunatu until khobwe athere2 mnyumba 😂😂. #pat#Gan# Ngozo achita kuthawira2 serie yonse osaonekako kuzemba ndiwo khobwe.❤much love from South Africa guys mumatha.
Hahahahaha eeeeeh Tonde nyooo
Komatu kamkaz ka hyphen sikanachenjele bwno😂😂😂
Sangie eeh iweyo Ai fenkis 🙌🤣🤣
Ndee kuyankhatu eti ndakufusa maganizo ako evekere tonde nyooooo😂😂😂😂😂
Anthu inuy mukukita bwino nsaname much love you guys ❤
Kma a gani makwana much love from phweya's family
Am waiting patently am I really need to see this
Tili apaaaaaa mesa
Cheteeeee kudikilira kut Gani nanga Patricia and Mtebede aza zanji osaiwala Langwani NGAUZOOOOOOOO🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥USAUVER TO THE WORLD 🌍🌎
This episode was dope eeeh, guys mumatha inuyo
❤❤❤ sangie mundiitane ku ukwati pa wife material paja ndendende maturity yake ya mayi wa ana folotu scene iyiyi ndi yako basi big up
Aganizan amapanga zofoira Koma zibwana sama zifuna 😃😂😅
😂😅😂 and I quote dzulo dzana lero kumangolangizana chinzake chabwanji agani
Tonde!! Nyoo!! 😂😂😂mwadza guys mukupanga zochitika guys kkk
Emmie umatha
Keep the fire burning magaye🤗
Wow 🎉🎉 sangie 🔥🔥🔥🔥
We miss Ngozo please
The song at the end it's giving ❤
😂😂😂😂 ati tonde uziti nyooo koma guys ndaseka. Gani ndi zina zake
Sangie ndwe Dolo aseh❤😅😂😂
Gani more fire watikumbutsa yakale kkkk
A Gani next episode muwapephe alamu anu Juzi lanyowani
😂😂😂😂😂 kma Gan adha amakhala serious
komano windows xp zamukhudza chani.. lol. Great job akulu akulu
Nice guys,,today's episode was dope!!!!! Everyone was at high note,,, kuyambira wa Camera
Kkkkkk koma ndee mulizipongwe😮😮😮😮😮😮😊😊😊😂😂
Nah man 😂😂😂 Sangie is too good🔥🙌
Gani is slowly becoming a good and reasonable man😂
You never disappoint, keep it up!!
please i need that song in the background more especially at the end of this
Patricia will always be my favorite,she spices the show❤
Ndikumuvera chison Albert in next episode
It's ndimwa nsanadye for me???uyuyu ndendende ine😅😅😅😅😅
Kkkkkk tonde nyooo😂😂😂😂😅
Gani and Patricia ndi perfect match ya pa chibale. Komano I think Albert banja silikumayanja😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Albert azingokumana ndi akazi omuchitila😂😂
Leroli ndaseka ngat ndalipira kale rent😅😅😅
Patricia ndi m'bale waki ati ndiyakhobwe lero😂😂😂😂koma belita wasowa,,zikomo iyi mwaonjezelako nthawi bola
chimfana choziwika ndi?
Koma Patricia ndi mnchimwene wake Gani iiih🤣🤣😂🤣
koma akaziwa mmawatola kuti man albert eish hahahahahahaha
Kumakuwaaa 😅😅😅😅 Tonde .... nyoooo😅😅😅😅
😂😂😂😂 mpungwepu koma akufuna ndani
Mpungwepu ati mchani Kodi? Akuzadzuka modzidzimuka ngati akufuna kupuntha woimirira bwanji? Kkkkkkkkk
Gan is always best actor
Nyoooo😂😂😂
Ati ndikakuitana uziti nyoooo😂😂😂😂😂koma ganizaani
Ganizani😅😅 watikumbusa chikale tu
amathu zoona kumukana gan 😂😂😂😂km naye mkaz wa abat 😂😂😂😂😂
Gani simply man of the moment ❤
Iiiiih Sangie iweyo ndi vibe❤🎉😂😂😂
Akazawotu amenewo 😂😂😂aaah ine Patricia
Kkkkkkkk koma ganizani... Fanta wamathu
Akuti ndafunsa maganizo ako...???? Hah😅😅😅
Kma Gani ndi katundu 🔥🔥
Gani wasandukatu akomesi😂
Emmie is acting well❤️🙌
Anthuwa ndiwoyipa😂😂😂😂😂🔥🔥
It's always Sangie and the vibes she gives 😊😊😊
Tikufuna nawo nyimboyi chonde
Kkkk mpaka khobwe aikidwe mu container
Sangie ndi vibe❤
A head Gani😂😂
Anthuwa ndi afitiii
Waiting patiently 🎉
Gani iweo anakonza. Man Andy takuonani
Iyiyi koma izituluka every 3 days ❤
😂😂😂😂 ati ndikakuyitana uziti nyooo😅
Waiting mwantintiii
Patricia ndi fireeeee
Sekulu my boi .. kukonda zinthu