You're all good actors Good Camera nice acting continue Piksay we know that you're the Head of these movies We trust in u if u stop acting then others again they will stop please continue A ngozo From ZAMBIA
Very nice kwa Malawi mutapitilidza kutele ndikuganiza kt Usova azaika pa top Malawi tsiku Lina nonsenu ndi ma actor abwino musamaziyanganile pansi kms ndipempe kumapanga mwachangu zinthuzi timaona kuchedwa thank you all.
Let's gather right here for Ganizani 😂😂😂 thus dude always make my day whenever new episode comes out 😅😅
Dolo😂
Big Up Man Gani,
Uyuyu ndi dolo ,kwatswiri ,katakwe, namatetule 😂😂
He has talent
Amangoyankhula mtima uli ziiiiii
Koma ganiyu gayezi😭🤣....can't take this man serious In real life olo atandilozeza mfuti🤣🤣🤣🤣🤣
Such a well-written and well-acted drama. Loving it, truly.
Let's gather here for Ganizani 😂😂😂😂 ati nduyenera ndipeze mkaziyo kkkkkk
Amene sanaitsate past seasons zomwe akunena sing'anga zawapeta apapa 😂😂😂😂😂
Shado woyeeeeee🎉
Ine ndayitulukila kkkk that's why watsata nkodzo wa A shado kkk
omwe we are here for Emmie let's gather here 🎉
Muli chikoka😂
You're all good actors Good Camera nice acting continue Piksay we know that you're the Head of these movies We trust in u if u stop acting then others again they will stop please continue A ngozo From ZAMBIA
Can you explain very well.
meaning you did not understand what I said
Very nice kwa Malawi mutapitilidza kutele ndikuganiza kt Usova azaika pa top Malawi tsiku Lina nonsenu ndi ma actor abwino musamaziyanganile pansi kms ndipempe kumapanga mwachangu zinthuzi timaona kuchedwa thank you all.
😂😂😂 ati ndimalemedwa ndimangozindikira ndayakhula🤣🤣🤣🤣🤣
Sing'anga uja watithera nthawi asazabwerenso aaah
😂😂😂😂
Muli bho guyz
I love that you've made the episodes longer. Sharp!
You deserve to have usauver channel to a certain tv station guys you have got Skill and talent achina ganizan big up broh.......
😭💔🤣koma gani
Kmatu sinathe bhoo 😂😂😂 next episode chonde fast fast izayambire pompo😂😂
Komaso asing'anga sanalakwise tu, paja Ashado ankanama kuti kwa Ngozo ndi kwawo 😂 and asing'anga akutsatila nkodzo🤣, Ashado ziwavutatu apa
Ati nanga ndizingothandiza ulere😂😂😂😂
Gani akufuna azipakula😂😂😂
Flirting yamasteniwo top notch 👍🤣....
Komatu Gan ndinkhan zina. Sizothandiza mwana wako ulele😂😂😂😂😂
Kodi moni waa mtundu wanji umenewooo asing'anga (dotolo) 😹😹😹😹😹
😀😊☺ashado ongoyenda ndinjala
Angogwila mfanayo nkono.avekele misala chani kapena akundifuna😂😂 eish chemwali awa hiyaa😂
Chemwaliwaa phokosoo kwabasii 😂😂
Koma amanthu mfundo ngati Rasta ..... Fuso ndiloti udziopa
Like my comment ❤
for what
f u
Mwna zizimba😅😅@@levisonmwale5443
Ganizani is always the best actor
Naye Sing'anga wapanga trace mkodzo uja 😂
Wa Shadow
Gani aise❤❤ iwe ndi vibe ya bho,,umatha aise
Watch from capetown, ndazikonda!!! Ngozo sakonda zausing'anga
Anawo ndizingowathandiza ulere😂😂😂😂😂Koma ganizani ndi dolo kkkk angozo simungazimvetse, msamangothandiza ulere
This guy Ganizani ndi chi vibe😂😂😂
Sitikuthandiza ulere😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 mwayithesa malo achabe kwambili!! Pamaso pa amathu 😅😅😅
Patiently waiting for the next episode 😂
😂😂😂😂 ati sing'anga wasochera eeee kma Gani😂😂😂😂😂
😂😂😂😂 Gani zothandiza ulele ayi akufuna chimanga.
Ganizani 😂😂😂😂 Ngozo flu yo bwanji ...nsinganga uzipesa eh eh eh 😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂 Emmie iwe nd zina zina asee😂😂
Aaaaaah mwauze asing'anga anuwo sakubebesa akungobhowesa iyah
Much love team yonse imu mulibe mbola
Naye sing'anga
I miss belita nsaname😢
Gani😅😅😅😅ATI chilichose chaukwati chatheka kale watsala ndinkazi opanga naye ukwatiyo😂😂😂😂
Ganizani uyu ayipisa maina onse otchedwa ganizani sure ngat dzina lako likufanana ND limenelo sinthani zed
😂😂 Nde ngozo ndi amathu mukanayankhulana Koma😂😂
Gan 😂 eeeh it's a actor 🔥 kma EDO timisechee timamuyanja😂
Bar man kudzakhala ngt wayamba kugwelamo mwa amathu, kenako alamu ake a Gani nkudzangofika😂😂😂 love u gusy
Next pliz ,,,,,, Tione kut Anguozo ndi amathu zitha bwanji kutengela kut apezana 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
The ending , now that's what we call a cliffhanger! Apapa mwatipatsa njala ya next episode
Kkkk man gan tsopano😂
Like my comment 🙏
Ati pepani eti ineyo nkoyamba kukhala pafupi chonchi ndi sing'anga🤣🤣😂😂🙌
Hahahahha Gan aaah iwe ukufunaso uziswa mtedzaaa day yothandizaaa please 🥺🥺🥺
Airtel money,Mpamba chan aaah😂😂😂Man Gani anabwela
Amathu, edo yo ngouma, tabwerani kwa ine timvane
Ashado mutu sugwira😂😂😂that's y namulondalo wa mu handbag walondola mkodzo😂😂😂😂😂😂😂😂🙌🏼🙌🏼🙌🏼
😂😂😂😂
Gani and Amathu! True artists!
Right zakumanizanano 😂😂😂 Kodi ngozo athawidwanso can't wait
😂😂😂😂😂namulondola wamu handbag wafoilatu ameneyo 😅😅
eeer kma gani 😂😂ati zonse zaukwati zatheka kwatsala kupeza mkaz ndi dollar 😂😂
Ganizan ukufuna chibwenziso 😂😂😂😂 chifukwa cha ana
Palimbe kungothandiza ulele ayi koma make akhale mugalaundi😂😂😂😂😅
Namulondola wamu hand bag wafoila 🤣🤣🤣🙌🙌🙌
agani ndi mulamu wawoyi mmmmmm ayi kkkkk keep it up guys mumakwana ndithu mumafasa osati zaphokoso ayi
Edo amalemedwa Ndi nkhani zoonaa😂😂😂
Iyiyi nde yatha isanayambe and big up to Gani😹😹🔥
Nonse part yanu mumatha kkk
Koma Edo adzathera mmanja mwa anthu kkkk
Edo anthu adzamukanganilana😂😂😂
Gani ndi biggy! Umatha 😂😂😂
Koma ganizan ndi alam akee iiiiii 😂😂😂😂
Ngonzo ukuoneka ukuononga zithutu iwe kkkk all the time u go kwa Edo umakumana ndi mathu km manthutu akuti sakuziwa nde usamale mayakhulidwe 😂😂😂😂😂
Gan km nd actor mbambande💥💥💥💥💥
Heavy
Uyuyu ndikatswiri
Ganizani 😂😂😂
Kumuyang'anatu dotolo🤣🤣🤣
Kom.kasewelo akaka ine ndizalowe nawo ndithu. I feel so good. Kamandichotsa tima stress 😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤
Koma komwe unakamutenga Ganizani ko adha kkkk unaganiza bhooo. Ndichemwali ake omwe, eee anthu amenewa eee😂
Amathutu mukuonjeza kunama😂😂😂😂😂
Aah koma gani nd alamwake amandwazaa🎉😂😂
Ganizani😂 ati ndidzingowathandiza anawo ulere😂
Ati namulondola wa mu handbag🎉🎉❤
Am craving for the next episode abeg ooh
Ganiii and amathuu inuyo ndi more 🔥🔥🔥🔥
Amathu ndi a mfundo tu😁
Pachi brazii😂😂😂 afuna cash
😂😂😂 man gun mumaipasa moto, namulondola wapoila😂😂😂😂
But guys gani amatha am telling you😅😅😅 I like this guy indeed
Edo anabwera kudzakhala,,, ma guys mumatha eeeeeee ❤❤❤
Tamuuze abweretse chakumwacho 😂😂😂😂😂 Che Mkope tsopano
This series is dope. Just needs subtitles
Amathu frits hard,,,komanso Ganie ati nzingowathandiza ulele 😂😂
Koma Gani🙌🙌🤣🤣🤣
😅😂😂😂😂😂😂😂oky I have alot of comments.... buh first... Ngozo ndi Patricia... it's time we see a Juniour 😂😂😂😂😂
Amathu hitting on Edo so hard😅😅😅😅😅😅
Koma Gani ase😂😂 Mula kuimila inu osakuuzan😂
Shadow mutu wake sumagwra 😂😂😂😂
Edo ndi zimayi 💔😂
Naye dokotala wabwera ndzake😂😂
Kod what's the title of the soundtrack yakumapetoyi?😢
😂😂Gani akuti namulondola wamu hand bag wafoila😅😅
Sing'anga kupanga trace mkodzo wa Last year eish
Namulondola wake ndiwaukali
Mpaka kununkhizaso kamwana ka ashado 🤣🤣🤣🤣🙌🇲🇼🔥
🤣🤣
Nde sing'anga muli kupeleka Moni, kukhwima chani ansaaa .. amafuna amfunsile sister wanga kkkkk....😂😂😂 Kupusa eeh acting yanji iyi kkkk... Ati napanga naye business kkkk
Big up man gani
Ndiwe dolo kwambili 😅
Nanga anawo mzingowathandiza ulere😅😅😅
Koma inu Emmie yu😂😂😂😂🙌🙌
Uli Nd mkaz ai osatheka 😂😂😂😂🤣
Imagine😂😂
@@mariedulani7454 🤣🤣eddo kuuma
Ma green lights mbweee,
Koma man Edo sakuthayima 😂😂
Akuti don’t talk about me 😂😂😂
Ali kuti wachakumwa uja 😅
Gani anakonza 😂😂😂 sin'ganga😂😂😂
😂😂😂😂Koma gani ndibgalu aaaaaaaah ati nanga ndizingothandiza ulele