Mbenjere Kung'alula Mcp? 😳😳 amene akudziwa Za Nyimbooyi Tiuzeni ko pilizi 😂

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 дек 2024

Комментарии • 347

  • @HusseinKalima-f4z
    @HusseinKalima-f4z 28 дней назад +2

    Big up to you Mbenjere, phunzitsani uwuzeni mtundu wa aMalawi adziwe kuti chiphaso chawo sichofunika kumupatsa munthu wina iyayi. May God bless you Mbenjere.

  • @KassimIssa-bn3od
    @KassimIssa-bn3od Месяц назад +18

    Wazindikila chilungamo ndiyemweyo 😂

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 Месяц назад +5

    Ameneyu ndiye timati Legend Mbenjere💪 Not anyapapi omwe akumakayimba ku MCP music Show!

  • @GanizaniMaulana
    @GanizaniMaulana Месяц назад +10

    Yaaaah bro ndimbenjere ameneyo I know this guy he has also another style of singing

    • @PhillimonMwale
      @PhillimonMwale Месяц назад

      Inu Nd nyimbo yake imenei Nd nyimbo ya 2013- 14 time ya Joyce Banda

    • @BazaarShaibu
      @BazaarShaibu Месяц назад +1

      ​@@PhillimonMwale ndiye 2013 kunali lipoti la ndege?

    • @kingbravious1
      @kingbravious1 Месяц назад

      Yes mbenjere has three styles of singing

    • @MichaelJohnMbewe-sk7jd
      @MichaelJohnMbewe-sk7jd 26 дней назад +1

      ​@@BazaarShaibukomadi nthawi yimene ija kudalibe za report ya ndege 😂😂😂

    • @BazaarShaibu
      @BazaarShaibu 26 дней назад

      @@MichaelJohnMbewe-sk7jd akutinamiza awa

  • @isaacimmantambala5294
    @isaacimmantambala5294 Месяц назад +8

    anthutu chilungamo akuchidziwa mutha kuona & mbenjele ndi ozindikila😂😂

    • @symoldicky
      @symoldicky Месяц назад

      Kkkkk wazindikila cuz Ali kuchikangawa party? Ndipo Kodi akat kuzindikira nchani ngat sikuchikuta zinthu mwanzeru munthawi yoyenera? So ngat nkuzindikira KO kwagona pati pot posatengera ndale or chipan chosatira koma kuima pachilungamo zinthu sizili bwino pankhan ya umoyo kamba Ka usogoleri ulipo omwe anthu Ake akukhala ngati agontha komaso khungu moti sakuoan ndikunva mmene anthu Ake akuvutukira then kod Munthu ozindikira panthawi iyiyi yomwe anthu akuvutika ndipo akusowa anthu omwe angathe kuwayankhulira zammene uli Moyo angasapote zomwe zikuzunzitsa anthuzo?

    • @paulgchabvunya
      @paulgchabvunya 25 дней назад

      Ndi inu mbuluchabe. Nyimbo ya nthawi yabongi... Ma vote a20 Mya adalichakachanj

    • @LindyRich
      @LindyRich 17 дней назад

      ​@@paulgchabvunyaInu ndiinu achitsiru zedi, so apanga upload wa ndiosadziwa odziwa ndiinuyo. Mbuzi Garu tombololombo iwe ndithu mwana wahule obadwira mistake condom ataphulika

  • @ulemummangisa3150
    @ulemummangisa3150 Месяц назад +5

    Yes his voice is there ya mbenjere even the beats are his

  • @judgeMinjolo
    @judgeMinjolo 10 дней назад

    Mbenjere,uziyenda mosamala akuyika musaka anthu akwiya nawe awa🤣😂🤣

  • @WillieKalipinde
    @WillieKalipinde Месяц назад +4

    Nyimbo waswa iyi eeeeh, mpaka Mr Chi........ atayimva Mmmmh

  • @Harrychokanda
    @Harrychokanda Месяц назад +7

    Mbenjele kubaya pa liwombo 😂

  • @DanJohn-ws5gl
    @DanJohn-ws5gl Месяц назад +9

    Nice song mbenjele tufuna izizi iyi ndiye sound yanzelu

  • @AbdulrazaqHussain
    @AbdulrazaqHussain Месяц назад +1

    Yaphedukadi for real, big up!!!love it

  • @MayaMilanzie
    @MayaMilanzie Месяц назад +1

    Anthu alowetsapo zawo apa mbenjere maimbidwe ake timawadziwa kkkkkkk izizi ndingati zomwe zinawachitikira mablacks kungowanamizira😂😂😂😂

  • @ThomasMswayo
    @ThomasMswayo 27 дней назад

    Mbenjere ho yeeereeee😂 . Ndipo tonse tavomereza kuti ndiyemweyo Mbenjere basi

  • @WizBanda
    @WizBanda Месяц назад +1

    Kaya ayimba zandale Kaya Chani ine I just like any song imene yayimbidwa mwambenjere beat

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule Месяц назад +4

    Zoona Chakwera you must go, watikwana

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Месяц назад +6

    good composition Mbenjere amatha

  • @YammsyZebron
    @YammsyZebron Месяц назад +2

    😂Wathila mchenga mumpunga😂😂😂😂

  • @tarcisiusmasampopo8157
    @tarcisiusmasampopo8157 26 дней назад +3

    This song has been there for over 5 years

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 Месяц назад +1

    😂😂😂😂😂 kulitu ntchito yayikulu kunoku guys😂😂😂😂

  • @YobuGradison-k3m
    @YobuGradison-k3m 26 дней назад +3

    Adaimba nthawi ija joice banda sdagulitsa ndege ija

  • @NdegeWiily
    @NdegeWiily 24 дня назад +1

    Aaaa nyimbo ya 2019 iyi kkkkkk inu mwayivela kumene aaaaa zazi

  • @JosephBotoman
    @JosephBotoman 20 дней назад

    Nyimbo iyi anaimba ndi mbenjere mu 2020 nthawi yamavoti,ndiyakalekale amknena dpp

  • @MoosaSame
    @MoosaSame Месяц назад

    Ndiyemweyu mbenjere no matter how now you the truth more fire ❤❤❤❤❤

  • @WilliamRahman-d6o
    @WilliamRahman-d6o Месяц назад +1

    ❤❤❤ Komatu wakwapula beat iyi

  • @papelariareis.e.
    @papelariareis.e. Месяц назад

    Mbenjere motoo kuti booo koma guys mbenjere wagogoda sindikukhulupirira 😂😂😂😂😂❤❤❤❤

  • @JamesMsowoya-cp3lf
    @JamesMsowoya-cp3lf 27 дней назад +1

    Pure mbenjere .
    Nice song .

  • @OretarbadrBwanali
    @OretarbadrBwanali Месяц назад +1

    😂😂😂 Nyimbo nd iz zot ukamamvera uku ukunyekhula

  • @giftkalunga5076
    @giftkalunga5076 Месяц назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂
    Nyimbo ya kale kale ngati iyi

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 14 дней назад

    Zoona njomba umakwana i like it tili tonse koma ndimati ndikozepo pang'ono muziti cikangawa osati cakwera ndi mbuzi ya munthu, the gvmnt dat sees nothing, no nothing,duing nothing koma kuba, kupha ndikunyenga mkazi wa dan lu dats wat dey knw fools

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 Месяц назад +1

    He's the one 😂😂😂, galu wake yomwe wayamba kukuluma

    • @MoHaTri-g5u
      @MoHaTri-g5u Месяц назад

      Zikatelo imakhala minyama kwabasi

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Месяц назад

    Chorus ndi beat ndi mbenjere koma zinaz ndi wina 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @BwKwizombe-jp2ck
    @BwKwizombe-jp2ck 27 дней назад

    this is Mbejere ........Big up

  • @NedsonKamwaza
    @NedsonKamwaza 27 дней назад

    Koma ndiye mumangaza bro.big up good job

  • @PatriciaMbewe-xn7ke
    @PatriciaMbewe-xn7ke Месяц назад

    Eeeee koma anthu amakhala ndi mfundo 🙌🙌 na iyi waikazinga timvere basi

  • @phillipchampoxychapola4165
    @phillipchampoxychapola4165 28 дней назад

    Mbenjere ndavera kwambiri ine this is 100% mbenjere. Koma wabwela ndi moto hevy

  • @mathewschipande2885
    @mathewschipande2885 24 дня назад

    Waing'alula mbenjele😂😂😂

  • @AmiduScale-e8f
    @AmiduScale-e8f Месяц назад

    Nyimbo yiyi adayimba kale kwambiri thawi yomwe Joyce atagulitsa ndenge ya Malawi zango ndisangalatsa kuti zafanano ndi zofuna yena 😂😂😂😂

  • @DiversonMassa-w3y
    @DiversonMassa-w3y 14 дней назад

    Simbenjere ameneyu ngati munazolowera kupaka anthu bodza,apa ndiye zakukanikani.manyazi bwa?

  • @Ahlubyt
    @Ahlubyt Месяц назад

    😂😂😂😂Kaya ndi iyeyo kaya si iyeyo nyimbo yi ilibwino😂😂😂

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i Месяц назад

    Mbenjere ulemu wanu big brother be strong 💪 🙏 that is true 👍 🙏 👏 🙌 😄 😆

  • @SamuelChiwere
    @SamuelChiwere Месяц назад

    Tikumva kuti wamangidwaso anyway Mchinji simagawa kamba😂😂😂

  • @Enock-g8x
    @Enock-g8x 27 дней назад

    Undihale Ku inbox ndikuponyere kangachepe, nice song.

  • @saidiwilliam9832
    @saidiwilliam9832 Месяц назад

    Ya full bwanji 😂😂😂😂 ndiyemweyu uyuu

  • @RojasJere
    @RojasJere Месяц назад

    Ndiyemweyo mbenjere kkkk koma ndiye wabayatu

  • @lloydwilliam7313
    @lloydwilliam7313 28 дней назад

    That's him,Koma ndiyakale airplane mentioned it's air Malawi nthwawi ya amayi

  • @MussaZimba
    @MussaZimba Месяц назад +1

    Mbenjele katundu wa amalawi uyu 😂😂😂

  • @HopesonJailosi-vd6ou
    @HopesonJailosi-vd6ou Месяц назад

    Ndiyomweyo,Kodi munthu amene amalikonda dziko lake sangawayikire kumbuyo dziko lavuta

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO 22 дня назад

    😂😂😂 koma ndi mbenjeledi uyu? Si edit iyi? Koma ngatidi ndi iye ndiye watopa ndi ululu wamu mcp ndithu

  • @KondwaniGumba
    @KondwaniGumba Месяц назад

    Ndikalekale nyimbo iyi kkkkkkk , inu mwaivera kumene.

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli Месяц назад

    Kkkkkkkkk koma ayi mcp mwanyanayo basi sinchewa ameneyi ayi zikomo

  • @EvanceSandifolo-tq3kp
    @EvanceSandifolo-tq3kp 25 дней назад

    Koma nyimbo imeneyo anaimba 2019 ndiyakare kwambili ine ndilinayo kare .anayimba ndimbenjere ndithu koma siyapano ayi

    • @HamiltonLucius
      @HamiltonLucius 24 дня назад

      Iwe wabodza kwambiri kalero kunaliso nkhani yokhudza ndege??

  • @PeaceNkhoma
    @PeaceNkhoma Месяц назад

    😂😂😂😂 ndiyemweyo....

  • @SaimonBanda-ez6km
    @SaimonBanda-ez6km Месяц назад

    😂😂😂😂 zikolapasi 😢

  • @FladielMwase
    @FladielMwase Месяц назад

    Ndi mbenjere ameneyo 😂😂😂😂😂😂

  • @LameckThomPhiri
    @LameckThomPhiri 24 дня назад

    Beautiful Mbenjere

  • @KacherengaAntony
    @KacherengaAntony 28 дней назад

    Ndi mbenjere uyu nanu....mchinyimbo chakalekale zedi ichi. No remix

  • @KassimWilson-g6m
    @KassimWilson-g6m Месяц назад

    Zoonad ndi mbenjele 😂😂😂😂

  • @DesireNkosi-p6b
    @DesireNkosi-p6b 25 дней назад

    Big up mbenjere

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 22 дня назад

    Program ili conco cikangawa timucotsa dan lu amvele nyimboyi kunena kwainu amaona ngati alipo yekha mfana wacikape.umakwana nyimbo ili boh tilitonse osadanda cikangawa acoke

  • @Ahamadissah-p7l
    @Ahamadissah-p7l Месяц назад

    😂😂Ndamumva ndiyemweyo

  • @EliasKaboma-v2l
    @EliasKaboma-v2l Месяц назад

    Kkkkk zoona ombenjere

  • @captainmedia
    @captainmedia Месяц назад +1

    Akuti ndikavote pa 20 pano. Meaning Nyimbo iyi Mbenjere anaimba dzaka zambuyozo. Chorus ndiya Mbenjere koma wina walowa ma verse`wo ndi kuika zomwe zachitika chaka chino cha 2024.

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick Месяц назад

      Iwe wabodza nyimbo yaimbidwa Pompano usaname

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick Месяц назад

      Uzinva nyimboyo message yake, Kodi mesa zotenga ziphatso Kuti abere mavoti zikuchita pompanopa kumawanamiza anthu Kuti awapatsa chimanga apititse ma ID. Open your eyes big Amalawi ndiochenjera MCP Siingatipusitse

  • @HaleemaAllie
    @HaleemaAllie Месяц назад

    Ndiya chinkangawa yoo😂😂😂😂

  • @AnnastasiaChakwiya
    @AnnastasiaChakwiya Месяц назад

    Mbenjere yemweyo😂😂😂😂😂😂

  • @AbdulaheemNkhomah
    @AbdulaheemNkhomah 18 дней назад

    Km ngt akukana aziwe kuti nyumboyi ndye ili bwino ndipo ndaikonda

  • @MathewsChitsulo
    @MathewsChitsulo 9 дней назад

    Zoona chilingamo mukuchidziwa. Dzopatdidwa dzisiyana ndi zako

  • @AcklenMuhammad
    @AcklenMuhammad Месяц назад

    Ndiyemweyu don't forget oyimba amagwilisa ntchito kuimba akafuna kugawa uthenga

  • @AlufeyoBanda-cv2we
    @AlufeyoBanda-cv2we Месяц назад

    Mbenjere ya kalekaleyi inuyo mwaimva lero koma kumalawi kkkkk

  • @Staphelsavimbindhlovu
    @Staphelsavimbindhlovu Месяц назад

    😂😂😂😂😂❤❤❤ mbenjere

  • @RichardMdala-ml4hx
    @RichardMdala-ml4hx 29 дней назад

    Nyimbo yakalekale iyi nanunso aaah si yong'alula MCP ayi

  • @YamikanAbubakary-my4ie
    @YamikanAbubakary-my4ie Месяц назад +3

    Km boma ndilomweri stikusintha m'paka 2030 wooooo
    Yemwe akufuna kusintha
    boma angosintha mkanzi oro mwamuna pamenepo ndiyekuti zimunthekera
    😂😂😂😂😂😂

    • @StevoZimba
      @StevoZimba Месяц назад

      Imbwaiwe

    • @AchinaKellz
      @AchinaKellz Месяц назад +2

      Mbuzi 😂ndi mbuzi olokuyingenda pompo imaona ngati dzuro

    • @PartsonMdeza
      @PartsonMdeza Месяц назад

      ine ndikusitha ndi vote yanga

    • @MangulenjeTwangu
      @MangulenjeTwangu Месяц назад

      Wakhuta chan

    • @PhillipLipenga-b9e
      @PhillipLipenga-b9e 24 дня назад

      Ekha ekhatu angompasa ka data 😂😂 ati anene kuti boma ndilomweli😂😂😂😂

  • @petermsamariamapira8933
    @petermsamariamapira8933 Месяц назад

    I like mbenjere they song sound malawi ❤

  • @LEMANCHAPOLA
    @LEMANCHAPOLA 6 дней назад

    Ndiyemweyo mbenjele waing'alula

  • @BrianMuleke
    @BrianMuleke Месяц назад

    Kkkkk ndiyemweyo😊

  • @RachaelPhiri-q3f
    @RachaelPhiri-q3f Месяц назад

    ndyemweyo , cyakareso cmukuva akukamba zandege

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya Месяц назад

    Big man Mbenjele nyamata wama suit otchena

  • @MaxwellKalungo
    @MaxwellKalungo 14 дней назад

    Chakwetekwete nd nyimbo yakele koma. Winayo wangomiksa bas

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 Месяц назад

    Wawonatu mbenjele😅😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @AubreyKabango-g8l
    @AubreyKabango-g8l 3 дня назад

    Munthu wa Nkulu kwambiri Mbenjere

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate Месяц назад

    😂😂😂😂lpatse moto ❤❤

  • @Moses51
    @Moses51 Месяц назад +1

    Yomweyo mbenjele 😂😂😂

  • @GutuJemus
    @GutuJemus Месяц назад

    Kkkkkk koma zithu zake

  • @JoyceChisale-ip1rc
    @JoyceChisale-ip1rc 28 дней назад +3

    😂ndiyakale 2019

    • @djnyau7468
      @djnyau7468 26 дней назад

      2019 kunagwaso Ndege kod? kapena sinave bwino ndine nyimboyi

  • @ZanazoniMsiska
    @ZanazoniMsiska Месяц назад

    Nyimbo iyo ndiyakale nthawi ya joice Banda kumamvekanso nkhani yobera chisankho, ndege akuyimbaso iyo ndi ija anagulisa JB osati yachikangawa mmmm amalawi kusowa zochita

  • @hagayichiluwe
    @hagayichiluwe Месяц назад

    Nyimbo ndiyakalekale iyi 😂 koma cadet ali pa job

  • @khidhwirzaynabadharwashali5873
    @khidhwirzaynabadharwashali5873 Месяц назад

    Madobadoba amujudula mbenjere,
    Nyimbo ndi ziwiri zosiyananso

  • @JayTwo-y9h
    @JayTwo-y9h Месяц назад

    Ombenjele ndinu ozindikila muli boh🎉

  • @MoHaTri-g5u
    @MoHaTri-g5u Месяц назад

    Apaso mkuchitaso kufunsa apa MBENJELE uyu ,our own

  • @DysonTummiesSajiwa
    @DysonTummiesSajiwa Месяц назад +1

    Ine mbenjele ndimakhala naye kuno uyuyu simbenjela koma amene wayimba nyimboyi wangotengako ma part ena ambenjele anyimbo zakale

  • @StaphelMvula
    @StaphelMvula Месяц назад

    Nyimbo iyi ndiyakale. Muvere akuti pa 20 pano ndimati ndikavote. Fufuzani chaka chimene tinakaponya vote pa 20 probably pa 20 May. Mwachidule ndizakale izizi

  • @BiliatMzungudala
    @BiliatMzungudala Месяц назад

    Mbenjele uyu wabandulatu ✔️

  • @KondwanipieKaonga-d8m
    @KondwanipieKaonga-d8m 11 дней назад

    Tamayankhulani za nzeru nyimbo ili apoyo siyomwe siyomwe mukunenapo ndinalipi Apo musamatipombonyese muzitiuza zanzeru

  • @cmsanyama200
    @cmsanyama200 Месяц назад

    Uyutu ndibwezi akumangopitiliza kuyimba chifukwa samaguga ngati mmene alili ambili a reggae a ku Jamaica

  • @lexchuley1817
    @lexchuley1817 Месяц назад

    kodi mbenjere amadana ndi MCP bwanji pamene iyeyo ndinchewa komaso ngwakunchinji

  • @HlamuChavalala
    @HlamuChavalala Месяц назад

    Uyu ndikatundu oimba onseo akuwatengao adzatulutsa nyimbo pamodzi ndipo ndipo adzamutuluka chikangawa oyimba singapange nao ubale nyimboyabwela mutuyo amafuna iveke basi ayembekeze zovuta mu MCP kutsogoloku

  • @paulgchabvunya
    @paulgchabvunya 25 дней назад

    Ndichakachti chomwe todavota Pa 20may...nyombo yakalekale iyi

  • @Elias-q7n6b
    @Elias-q7n6b 12 дней назад

    Ndiyomweyo

  • @phillipchampoxychapola4165
    @phillipchampoxychapola4165 28 дней назад

    Wadziwa choonad ndiyemweyo ndipo sitikukamiza choonad saphimba

  • @thomaswyson-e2q
    @thomaswyson-e2q Месяц назад +1

    Ameneyi ndimbenjele emweyo komansotu paja anaimbakale yatinkat tambalawakuda komandimloza

  • @ChrispinKashosha
    @ChrispinKashosha 12 дней назад

    Nanuso tinene kangat kut nyimbo iyi siyalelo ife tayivinapo in 2015 to 2016