Mulungu akudalitseni cifukwa ca uthenga wanu olimbikitsa a malawi tamukumbukila APM 2025 ndiyemwe timvotele koma smart matic icoke thanx man of god, god blss u & blss our nation.
I totally agree with you Mr Benedicto..Mcp is here to finish Malawi .Chakwera is evil together with his cabinet and their families..akudzikundikira okha.imagine zinthu on the shops prices Are skyrocketing every single day..Chakwera is a Big lier Kunkuyu Basop Richard chimwendo basop Dont take AMalawi for granted, your time will soon come to an end Monca muuze Lazalo wakoyo ndi Nick wakoyo God is watching you
Ndipo anatipwetekesa a malawife ndi chilima boma iri silikanatizunza chonchi koma tingothokoza poti mulungu amapanga chinthu ndicholinga taphuzirapo bravo mbewe
osati zoipa za APM koma za Iyeyo ndi DPP. 1-kusalabadira chitetezo nayenso kunali a zikwanje 2-kulola ana a dadi 3-kusathana ndi katangale 4- kusayang'anila TIP yomwe inaonetsa ziphuphu ndi amwenye 5- kukondera anthu achilomwee tribalism and nepotism 6- kuononga chuma posangalatsa anthu achipani...this list goes on and on.
Tinavoteeadi MCP Koma nkhani yake siyimeneyi sitimafuna kulamura zaka 5 ayi Koma pano zikuonwka kuti sitikulamuranso chifukwa cha ulamuriro wa chisilu Ngati uwu haaaa chibwana Ku MCP
MULUNGU OONA timuike pasogolo zomwe mukuyankhula a Benedict ndizoona ine,,,,,,,,,,,2019 MULUNGU amandiuza ka APM kuti ndi emwe awine koma 2020 AMBUYE adandiuza kuti anthu asankha de taonani utsogoleri uwuwu children's of GOD open u'r eyes please,,,,,,,,,,,,,it doesn't matter if u'r a supporter of mcp but look de future of mother Malawi we're in trouble but they is hope in 2025 GOD will restore our glory through APM only (take my words)
History is the best teacher indeed my God Lord bless you Mr Benedicto
Mr Benedicto Mbewe, may God bless you richly, mMalawi wachilungamo, ine ndimaganizatu kuti ndinu waku Thyolo
Mr Benedicto, this you have talked is Very true. Ndipo atangoti ANTHU akavote pa mzere chakwera is losing before 9:30 am. Amen brother B.
Pasakhale zobela chisankho tidzasankha anthu amene tikufuna.A Benidco Ambuye akudalitseni.
Alemekezeke mulungu wakumwamba zosatheka ndi munthu zimatheka ndi mulungu Amen!!
Amen amen man of god let's pray hard malawi
Wayankhula bwino Bene God bless
History is best teacher
Mawu aphavu kwambiri brother B mbewe💪🏿💪🏿
Let's pray hard anthu oipawa achoke Mulungu atimenyele nkhondo
Amen 🙏 🙏 man of God
Mr Benedicto, you got my BIG YES. Boma ili palibe chanzeru olo chimozi chomwe achita..
Amen Ambuye tichitireni chifundo
Lets pray and do fasting oyipao achokeo ,,,,, GOd bless
Mulungu akudalitseni cifukwa ca uthenga wanu olimbikitsa a malawi tamukumbukila APM 2025 ndiyemwe timvotele koma smart matic icoke thanx man of god, god blss u & blss our nation.
Zoonadi akulu mukukambazi angakwiye nazo ndi mfiti
Amen Benedicto
Amen man of god🙏🙏🙏
Let the power of God prevail
Ndi zoona Mr ambewe a Malawi nsanje kwambiri
Mr mbewe u re true man mapempheladi auzeni chilungamo maonadi dziko lathu limene likuyenda koma ambewe pangani zomwezo amenewo awone mulungu kuti yona adziwe kuti tigwetsere madzi mafunde a the zoona zache adad akubwerela boma 2025 yes make spriual battle a Muone mulungu zodabwitsa pangani zomwezo Mr mbwe amen amen
Ndipo zooonadi mukunena chilungamo broz chakwera atipha ndi boma lake.. 💔💔
Mau ambavu bwana❤❤❤❤❤
Auzen. Ambuye akudaliseni.
Kuyankhula konveka brother osabwelela kumbuyo
Rest in peace madala BINGU WA MUTHARIKAAA!!!!!!❤❤❤❤❤
U are very peaceful indeed I know u personally
I totally agree with you Mr Benedicto..Mcp is here to finish Malawi .Chakwera is evil together with his cabinet and their families..akudzikundikira okha.imagine zinthu on the shops prices Are skyrocketing every single day..Chakwera is a Big lier
Kunkuyu Basop
Richard chimwendo basop
Dont take AMalawi for granted, your time will soon come to an end
Monca muuze Lazalo wakoyo ndi Nick wakoyo God is watching you
Very true amwene, anthu wa akumati "Boma ndilomweli" kuopa kuchotsedwa timaudindo
Mulungu apanga zozizwa pompano anthu enanu mukhumudwa
Nanga munthu ogwira tchito chipikulero ndizimenezo. Olakwa kwambiri ndiguru lachina chilima lija ndilime linaononga dzinthu.
Zonsezi ndi Chilima inde😢
Ndipo anatipwetekesa a malawife ndi chilima boma iri silikanatizunza chonchi koma tingothokoza poti mulungu amapanga chinthu ndicholinga taphuzirapo bravo mbewe
🎉🎉🎉🎉🎉🎉True speaking 100%
Mr mbewe mukuyankhula bwino ndithu
Almighty God is all knowing koma Chakwera adzatuluka mamina maso
osati zoipa za APM koma za Iyeyo ndi DPP.
1-kusalabadira chitetezo nayenso kunali a zikwanje
2-kulola ana a dadi
3-kusathana ndi katangale
4- kusayang'anila TIP yomwe inaonetsa ziphuphu ndi amwenye
5- kukondera anthu achilomwee tribalism and nepotism
6- kuononga chuma posangalatsa anthu achipani...this list goes on and on.
Chakwera alibe nzeru komanso akawona ngat president ndi ndi nyuu zikufanana
Sangalankhule cifukwa akuwatuma ndi cimwendoyo ndi cikangawa boma ili ndi ladzigawenga zokha zokha. Inu oposition ndi nonse amene mudathandiza mcp kulowa boma muwuze olo mabungwe akunja alowelelepo cifukwa comwe tikuona dziko muno ndi magazi.
Mawu Amen bro
Kuona molondola osatinso ndale bwana Mbewe
Amen bro
Padziko lapatsi palibe mpando wa mwana wamulungu tisapusisike ndikuti adali m'busa
Mau omanga osati kupasula 🙏🙏🙏
Mawu onveka bwino ndithu
Malawi taphuzila MCP tikaitulatsa mboma tiuze ana athu Kuti no matter what never put MCP in power again
Ndipo zoona zeni zeni tinazigwira kumaso mmanja muli sabola chakwera waliwononga dzikoli
Kodi olo mmene ankati anaberedwatu Chakwerayo,anachenjezedwa ndi maloya kuti muluza nayo imeneyo koma kwerani ya Chilima yokuti masankho sadayende bwino mpamene kumapeto anajoina UTM mpakana kuwina mlandu ku court
Ada awa ayankhula za Nzeru ndipo iiii Chakwera ayi Zikomo
Boma la anthu onyadira uchimo😢
Mukurankhura mau oveka bwino ndithu brother
Ukundiye kulakhula kwaphavu mr b mbewe
mukunena zoona brother or muwone mumene chakwera ankabangulira nthawi ija ya Peter muntharika kufuna upresident
Kuyankhula kwa nzeru
Zikomo kwambiri Mr mau ano akumveka bwino kwambiri ndipo tikumva ndinthu
Zikomo big man ulemu wanu mcp anthu AMAGADZIDI awa
Nkhwidzi basi
Ya mages yo kuno ku 25 almost week
Ukunena zoona lero tikulira
Kuyankhula moona komanso mokonda dziko lathu la malawi.
Mcp yaononga kwambiri.
Nsanje amalawi ndichifukwa tili pamavuto
Zooooonah!!!!!❤❤❤
Mulungu sangatisiye kuti tizilira mpaka kalekale.
Amen 🙏
Zoona 🎉
Tatiyenitu tiligwese tipemphe ambuye atithandize
Amen and amen
Kamunthu aka kayankhula zanzeru kwabasi, kumbuyoku ndimaona ngati mutu sugwira.
Osaopa osafoooka osaopa amen amen
Mcp mulibe wanzeru.
Zoonadi amalawi ndife ajerous
Ambuye alemekezeke ❤
Ndipo akadzatuluka m'boma awawa adzaphedwe basi ngati Akani iyaaaaa atizunzitsa mokwana agalu amenewa.
Tiyeni tipemphere kwambiri Mulungu atichotsere ameneyu
Anti lakwila chilima
Amen
Kulankhula kopanda kusinjilira, Koopa Mulungu. Well said.
Tinavoteeadi MCP Koma nkhani yake siyimeneyi sitimafuna kulamura zaka 5 ayi Koma pano zikuonwka kuti sitikulamuranso chifukwa cha ulamuriro wa chisilu Ngati uwu haaaa chibwana Ku MCP
Ziregwalegwa taziona
Ineyo sindisapota chipani chilichose, but I just support the positive things, zoona zinthu zakwera mwa umve kwabasi....
Ameen 🙏🙏
Ma plan analibedi ankangofuna dzina loti a president
Wandikumbutsa zakwathu ndi zakwathudi yooh mulipo?
❤❤❤❤❤❤❤
Sindine wandale sindine wachipani koma zikundikhuza ndikomwe akulowela Malawi wathu
😢😢😢😢😢😢😢Yes
chakwera sa dziwa kupaputa thako nde ayedetsa dziko ya malawi bwanji.......apwedwe ngati iyeyo wapha nzathu waku nchewu.........
Eya ndikugwilizana nazo
Kuyakhula km kumeneko mulungu atiwone amalawi
Kunali mfumu farao ku igypt,uyu musiyeni adzalira mu 2025😢😢😢
🔥🔥💪💪
MULUNGU OONA timuike pasogolo zomwe mukuyankhula a Benedict ndizoona ine,,,,,,,,,,,2019 MULUNGU amandiuza ka APM kuti ndi emwe awine koma 2020 AMBUYE adandiuza kuti anthu asankha de taonani utsogoleri uwuwu children's of GOD open u'r eyes please,,,,,,,,,,,,,it doesn't matter if u'r a supporter of mcp but look de future of mother Malawi we're in trouble but they is hope in 2025 GOD will restore our glory through APM only (take my words)
Ambuye akutetezeni mwayankhula zabwino ndithu zonadi ziko Lili pamoto iri
❤❤❤❤❤❤❤❤❤😢😢
Ndipo zoona zake APM he is coming back in Government 2025
Anena bwanji apuleo poti akuwatuma ndiiwowo anthu azikwanjeo mwaona akuyakhulapo zovesa chisoni
Malawi tonse tisaonelele malawi akuonongeka chifukwa cha anthu atatu amenewa
nchito ya chakwera ndi kudzadza thumba yake basi....inu amalawi mukungu gona basi.....
Achakwela achimwendo akukhuyu aziwe kuti azafa mowawa chifukwa wina azalolela kupeleka moyo wake bola athane ndi agalu amenewa asazitenge ngati ndiopambana kapena ochenjera
Tsiku limodzi Ana awo adzikazi awo ndi abale awo Malawi adzawakulila akulila
Kmasotu mafutawo pena amatsikanso mtengo pena ma mk13,500 20 Lt
Malemu agogo anandiuza za mcp sure koma izi ndazionadi ndiye chakwera mutu mwangozaza mamina
Mwayakhula bwino kwabasi zikomo osamangana koma kukonza zithu
Pangani zomwezo basi we have tired with this
Ndipo ineyo ndimanena kuti palibe angandinamize za boma LA dpp tinkanjoya zedi kumati Malawi nde ameneyu osati Malawi wa lero ongikhalira kulira daily