Ndikona kuli sipani sambili munthu Ali ndi choice kusanga Ngati mzika yamalawi palakwika ndiphati kwa Dani Lu akaliyati sanali Ku DPP lelo Ali kuthi amutalika anapezeka bwanji Ku DPP kuyiukila UDF muziyeni Dani Lu Amenye ndikugwenza kwacha 1-2milion❤❤❤😅
Palib kutuluka ukweche chfukwa chaiyeyo ndindani alibe nzeru vuto lake ndye kulimbana ndi chsru Dan Lu ungapuse ndweyo koz Dan Lu mchsru mchamunthu chabe
JB ndi mbuzi

Siufulu ena limagokhala dyela
Choice yake fire Dan lu 😅
JB ndidolotu 🔥🔥🔥
Chakwela Ku menyanya Ku gwesa , 🔥🔥🔥🔥🔥 or wamu tukwane, chakwela aimatso 🔥🔥❤️ I love you Dan lu
Eya anapanga moyenela ndiufuluwake
Sam mavitha umatiyimilila kwambili ndipo upitilize kufukula ngani ❤❤❤❤❤❤
More fire
Kape ameneyo
❤❤❤❤❤
Palibe chalakwika dan lu kuimbira chakwera tonse sitingakhale abulets ena ndi a noma ena a silver koma mpira ndiymodzi
Dan luu more fire
Ndi galu dani lu timusamusa kumangochi
Dan lu wachitabwino MAKAPE asamamuuze zochita ngati amadya kwawo
Palib kutuluka ukweche chfukwa chaiyeyo ndindani alibe nzeru vuto lake ndye kulimbana ndi chsru Dan Lu ungapuse ndweyo koz Dan Lu mchsru mchamunthu chabe
Naye ndi munthuu Ali ndi zisankho zake ndpo kuyimbaa kwakwe ndi business palibe vuto apa km kungot amalaw Ali ndi vuto
Wawonetselatu kuti ndiwadyela amafuna komwe kukuyenda
Wachamba Dan Lu ine ndinamutuluka
Ine ndikuti sanapange chisango chabwino cz iyeyo akuchemelela zinthu zoti sizikuchitka
Atuluke ukweche ndamache
No
Am Elias ndimafuna kunena zomwe wapanga Dan Luu sanapange bho coz azibare athu akufa ndinjara iye n,Kumati boma ndilomweri wayamba misara Uyo fack
Ukweche
ukweche
Azazindikira bwino pa songolo zomwe Dan lu akuchita Koma sakupusisa Malawi zikazamubwelera azaziwa choona chake Koma Dan lu ndiwa usiru❤
Wapoila iyeyo saanaganizile mavuto omwe anthu akukumana nawo
Dan lu wapanga big mistake