Kodi Baibulo limene timawerenga ku Malawi kuno linachokera dziko lanji?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 дек 2024

Комментарии • 132

  • @sakmosmediatv7015
    @sakmosmediatv7015 Год назад +11

    Am a Zambian and a keen follower of this page continue with the great work

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 Год назад +4

    Ndiwe dolo pa history m'makwana bg. Thanks very much. Muzinde mmiyoyo ya anthu aziwe choonada allah bless you

  • @AshrafJumah9665
    @AshrafJumah9665 Год назад +3

    Keep up good work. mumatitsegula maso brother

  • @KingsleyWakusa
    @KingsleyWakusa Год назад +4

    Brother you deserve much respect....Malawi its so blessed by dis historical wisdom from heavy...
    I wish I will know you in my life,b4 death,coz you a teachest man,in my life,,may the Lord keep you safe from enemies,,, Good Luck...

  • @clementmanyesa
    @clementmanyesa Год назад +1

    You are best brother umavesa kukoma mix chichewa eeee timavesatu bwino heavy

  • @alimonngwinja9514
    @alimonngwinja9514 Год назад +6

    Enlightened. Now we can understand why they are so many inconveniences in the bible.. zambiri mzopeka

  • @afritouch4660
    @afritouch4660 Год назад +2

    Zikumveka wawa..!! Keep it up

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Год назад +2

    Thanks for the extensive variety of information we get from your bank of knowledge
    Continue providing a well and extensive information daily

  • @geee7672
    @geee7672 Год назад

    ....your skills are getting better and better

  • @ismailkhuneya3346
    @ismailkhuneya3346 Год назад

    Your nothing but a hero of history we proud of you brother ❤❤

  • @StuartMlomboji
    @StuartMlomboji 3 месяца назад

    Keep it up brother wunabwera kuzatisegula maso

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 4 месяца назад +1

    Komatu munthuyu siwamasewela ayi ndipo zonse zimene amatiuza za ndale ndi zenizeni ndithu .....munthuyu ineyo ndachita nawo chidwi kwambili ngati nkotheka akanabwelela kuno kumuzi kuti azitiuza zenizeni tikumuona

  • @EmmanuelZembere
    @EmmanuelZembere 2 месяца назад +1

    God bless you

  • @harrisonnavayah6480
    @harrisonnavayah6480 Год назад +2

    You're my number one

  • @ZahnoorMilan-pe3ys
    @ZahnoorMilan-pe3ys Год назад +1

    Q.U.R.A.N z de best ever
    Mumakwana big

    • @NoahKalima
      @NoahKalima Год назад +1

      Munamuchosesa mbili yachisilam,mumuuze abwelese mbili yachigawenga Muhammad pano,anachoselanji mbili yachigawenga

    • @chawanangwamkandawire5850
      @chawanangwamkandawire5850 2 месяца назад

      Inu nde bola mukanango khala chete, chikristu ndi chisilamu ndi zipembezo zomwe zazunguza dziko lapansi kuposa zipembezo zina zonse, amafano alikonso bwino kuposa zipembezo ziwirizi, ndi slave trade yomwe azungu omwe anali a chrisitu anachita ku kopera kwa aluya mene amagonjetsa ndiku khazikitsa ukapolo mitundu Ina pa kugwiritsa ncito chipembezo chawo cha chisilamu.

  • @wilsonsawasawa3794
    @wilsonsawasawa3794 Год назад +1

    Thumbs up Bigman!

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Год назад +1

    Your tops brother man!!

  • @footballskillsandhighlight7974
    @footballskillsandhighlight7974 Год назад +1

    keep your good work mumatha

  • @frstyhavoc6678
    @frstyhavoc6678 Год назад +6

    And the King James Version is the greatest version

  • @irenechirwa9710
    @irenechirwa9710 Год назад +2

    Brother munazayankhulapo mbiri yachi silamu panali part 1&2 koma sikuwoneka pa utube panu bwanji.

    • @NoahKalima
      @NoahKalima Год назад +1

      Anaichosa asilamu ambili anakwiya,mbili ya chisilamu ndiyoipa,sangainene poyera,

    • @irenechirwa9710
      @irenechirwa9710 Год назад

      @@NoahKalima vuto safuna anthu aziwe zoona angofuna aziwapusitsa koma ndi kuwalakwira anthu.

    • @NoahKalima
      @NoahKalima Год назад

      ​@@irenechirwa9710 chisilamu ND nkhondo,atanena zamuhammad asilamu ambili anakwiya , Muhammad ndchigawenga ,

  • @jamestsabola1376
    @jamestsabola1376 Год назад

    Pa 5 seconds ndayamba kuwonela timakunyadilani big man my first comment

  • @WilsonPhiri-vl1di
    @WilsonPhiri-vl1di 4 месяца назад

    Iweyo ndiwe big man

  • @JimmyMpinda
    @JimmyMpinda 3 месяца назад

    I like this guy

  • @aggogokina8992
    @aggogokina8992 Год назад +6

    Abale ndimadabwa mabaibulo kuchuluka omatsutsana zokamba, zili zongoyambitsa achina Jemusi aaa. Ndithu mau a Mulungu namalenga ndi Quran bas ndipo ndiimodzi yomweyo dziko lonse lapansi. Allah Akbar!

    • @NoahKalima
      @NoahKalima Год назад +1

      Ngat kuli buku losokelesa ND Quran,buku lopeka, Muhammad sintumiki ayi koma chgawenga

    • @aggogokina8992
      @aggogokina8992 Год назад

      Palibe chimene ukudziwa zipangani za Jemusizo bas ndizomwe mudazolowera. Zipangani malilimewo 😀😀😀😀

    • @irenechirwa9710
      @irenechirwa9710 Год назад

      ​@@aggogokina8992 inu mbiri yanu tinaimva kale muuzeni bakili muluzi ayipangeso post apa anthu omwe sanayimvele amve, anena apo kut amatanthauzira kuchoka muchiyankhulo china kupita ku chingelezi

  • @shadreckmatenje6629
    @shadreckmatenje6629 Год назад

    Thanks bro for your update

  • @phillipchiotcha3197
    @phillipchiotcha3197 Год назад

    I remember Papa amagulisa tima bukhu kwa akhristu ndikumawauza kuti akagula ndie kuti matchimo awo akhululukidwa iye amatero powauza kuti zalembedwa mu Bible panthawiyo kupeza Bible kudali kovuta amadziwa kuti anthu sangalipeze kuti aone pomwe palembedwa koma Martin Luther atapeza mwayi owerenga Bible adapeza kut zabodza zimenezo ,ndipo adalesa anthu kumagula tima bukhu tija zomwe zidapangisa kuti Papa amutchose Martin mu Roman Catholic

  • @WisdomMwitha
    @WisdomMwitha Год назад +1

    Timakuyamikani brother

  • @feldoxdax2787
    @feldoxdax2787 Год назад

    Keep up Good work

  • @NoahKalima
    @NoahKalima Год назад +1

    Tabwelesaniko mbili ya chgawenga Muhammad ,tibveko,zachikhilistu mwanena tabvako,Nanga mbili yabuku lokugwa kuziwanda la Quran munena liti,tanenaniko za chgawenga Muhammad

    • @folamitowing238
      @folamitowing238 Год назад

      Utiuze iweyo plus ma umboni onse kuti kuran ndi buku la ziwanda.osati zongo lota mubwerwtse ma umboni tikumveni.Mwayaluka inu mwakhala mukutsatila mdima

    • @ishmaeldouglas5962
      @ishmaeldouglas5962 9 месяцев назад

      Luka 19:27 Mr gututu tawerengani msetezi

    • @JoyceChimphwika
      @JoyceChimphwika 5 месяцев назад

      Kuyankhula kopepelatu uku,kusowa umunthu kapena kuleledwa mopusa

    • @MestreMaday-fv7qo
      @MestreMaday-fv7qo 4 месяца назад

      Siya mwano analipo azako amwano choncho

  • @salaam1089
    @salaam1089 Год назад +1

    Respect

  • @richmondkilembe5449
    @richmondkilembe5449 Год назад

    Umakwana brother mulungu akudalise umatuziwisa zambili

  • @eddiechiumba2381
    @eddiechiumba2381 Год назад +1

    Iweyo ndi washing machine mbambande

  • @JosephLuciano-d2h
    @JosephLuciano-d2h 24 дня назад

    Amina mmatha

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos 5 месяцев назад

    MASH Allah

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Год назад +1

    BIG 👍

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363
    @dhaoudhiabedinegomaseko2363 Год назад

    Kupanda inu ndikulumbila sibwezi Aitel ndi tnm akundidziwa pa mofaya ndi pamtsetse akuganizileni.
    Komatu bukuli lasinthidwa kwambiri and zoona umu ndizochepa ndithu eishhhh azungu anatipweteka

  • @luciascharles4345
    @luciascharles4345 Год назад

    Aaaaa ndale zidaononga dziko lapansi , chifukwa kusintha koseku Kwa ma Baibulo ndizifikwa za ndale

  • @papelariareis.e.
    @papelariareis.e. Год назад

    Respect brother

  • @isumailahuseni9394
    @isumailahuseni9394 Год назад

    Keep up the good work bra

    • @QIDHIRHASSAN
      @QIDHIRHASSAN Год назад

      Ndakaika ngati angakwanitse

    • @NoahKalima
      @NoahKalima Год назад

      Mumuuze abwelese mbili yachigawenga Muhammad pano, anachoselanji mbili yachisilam

  • @EnockKunje-o5t
    @EnockKunje-o5t Год назад

    Your #1

  • @David-y9i6h
    @David-y9i6h Год назад +2

    Chocho zikuonekatu kut baibuloli anangolemba azungu ,koma Leni Leni la mulungu Lili kut?

  • @tamimaosman7674
    @tamimaosman7674 Год назад

    Noted with Thanks🙏

  • @SamsonKamgusha-gp5fw
    @SamsonKamgusha-gp5fw 6 месяцев назад

    Nice 🎉

  • @hopeskafumbiphiri6011
    @hopeskafumbiphiri6011 Год назад +1

    achimwene mumakwana kwambiri zikomo mulungu akudalitseni

  • @LukaAfromad
    @LukaAfromad 4 месяца назад

    Km uyu ndi chiphe pa history 🙏🙏🙏

  • @phillipchiotcha3197
    @phillipchiotcha3197 Год назад +1

    Komanso ndipezerepo mwayi mukapeza mpata tifufuzireni chiyambi cha Football ena amati mpira udayambira ku Egypt ena ku Greece according to their gods

  • @aggogokina8992
    @aggogokina8992 Год назад +1

    Anthu ali bhize kulibashika mmatchalitchi ndi zinthu zongoyambitsa azungu ku Britain😂😂😂😂😂

    • @HamdanMasuku-b3n
      @HamdanMasuku-b3n Год назад

      𝐊𝐤𝐤 𝐧𝐝𝐩 𝐤𝐤𝐤𝐤

    • @NoahKalima
      @NoahKalima Год назад +1

      Ineso kudabwa anthu busy kumenyesa pasi zipumi ,chinthu choyambisa chgawenga Muhammad , odyedwa ND nkhumba uja

    • @aggogokina8992
      @aggogokina8992 Год назад

      M'bale upange ma research mokwanira udzadziwa kut tingamulambile bwanji kulambila sikuvina ndikuyimba za achina jemusi mumasiyanitsa bwanji ndi disco kapena ku tavern😀
      Uwerenge mokwana udzadziwa yesu kut amalambila Mulungu motani

    • @aggogokina8992
      @aggogokina8992 Год назад

      Usakhale busy kubakila zinthu zachina jemusi zilakamize kufufuza chilungamo kut ukhale munthu ozindikira jemus ndi martin luther sangakuthandize kanthu

  • @idrissaeliassa
    @idrissaeliassa Год назад +1

    I'M a Muslim there's no such destruction

    • @mosesdyelathu
      @mosesdyelathu Год назад

      But some people the agreed

    • @mishackstanour8747
      @mishackstanour8747 Год назад

      You don't know what you r talking about........go deep in Islam you will see the difference

    • @mosesdyelathu
      @mosesdyelathu Год назад

      @@mishackstanour8747 but this guy he has never mentioned Islam so how come 🙄

    • @mishackstanour8747
      @mishackstanour8747 Год назад

      @@mosesdyelathuBrother...... I thought you know how to read ....... first read the message yakeyo then yangayo

  • @davidmaulana9277
    @davidmaulana9277 Год назад +1

    Komatu azungu amenewa atidyesa manyi koopsa tiwabwezere baibulo lauli bas

    • @NoahKalima
      @NoahKalima Год назад

      Anakudyesani kale manyi,manyiwotu ND Quran ndchigawenga Muhammad,odyedwa ND nkhumba

    • @Razzaq2010
      @Razzaq2010 Год назад

      Kkkkkkkkkkkkkkk

    • @Razzaq2010
      @Razzaq2010 Год назад

      ​@@NoahKalimamanyi ndi awa mukudya a tindaly 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂,,bishop bible, mateyu bible nde chani zimenezo 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @ChembeSolomon
    @ChembeSolomon Год назад +1

    Never give up

  • @ganizanichisale1449
    @ganizanichisale1449 Год назад +1

    Mavuto sazatha kumusindilira mulungu

  • @Misasi19
    @Misasi19 Год назад

    Tadziwa nao thanks

  • @christopherbottoman9131
    @christopherbottoman9131 Год назад +1

    Zikomo kwambiri ambuye akudaliseni mumayesesa kutisangalasa

  • @AlihIbrahim-w6n
    @AlihIbrahim-w6n 11 месяцев назад

    Kaya tiwuzeni kuti lenileni lilikuti,,,,nangalowona ndiliti,,,,nanga tikhulupilila bwanji Bible poti lenilenilo analibisa,,nanga analibisilanji,,,kodi mulizowona ndimuti?

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 4 месяца назад

    Awawa ndi machine akuluqkulu

  • @khalifacalvinajass9998
    @khalifacalvinajass9998 Год назад +1

    Koma adha awawa eeeeee ndi machine

  • @NgalandeRobert-to2mz
    @NgalandeRobert-to2mz Год назад +1

    Wadza wadza😂

  • @eunicemoyo6024
    @eunicemoyo6024 Год назад

    Zikukhala ngat king James uyu adaliko owopako mulungu 🙄🙄

  • @yasinkamwendo-jf7sc
    @yasinkamwendo-jf7sc Год назад

    Lov❤ bro

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 Год назад

    Koma pa nkhani ya Mau a Mulungu uku musapiteko mulakwisa man zikufunika anthu.opemphela izi

  • @Razzaq2010
    @Razzaq2010 Год назад

    Dzimvele wekha mbale wanga

  • @aggogokina8992
    @aggogokina8992 Год назад +1

    Awa ndi akamuna katundu omanga ndi mawaya awuzen big

    • @NoahKalima
      @NoahKalima Год назад

      Mumuuze aneneko mbili yachigawenga Muhammad,wanenako zachikhilistu tabva Nanga mbili ya Muhammad chgawenga chigwililira anena liti,

    • @aggogokina8992
      @aggogokina8992 Год назад

      Sizingatheke kuti anene sinanga mtumiki Muhammad peace and blessings be upin him si jemusi nchifukwa chake olo bukhu la quran ndi limodzi dziko lonse lapans. M'bale chilungamo chimaineka chokha.

    • @Asibu24
      @Asibu24 7 месяцев назад

      ​@user-nt4fr2le3f anagwilira mayi ako?

  • @QIDHIRHASSAN
    @QIDHIRHASSAN Год назад +1

    Ndekuti mipingoyi ili ndiayini ake anthu osati mulungu eeeeeee ife tikuti lowani mchipemphezo chamulungu yemwe adakulengani pachiyambi kwaiyenso mkomwe tibwerele tonse

    • @NoahKalima
      @NoahKalima Год назад +1

      Chisilamu ndchipembezo chamafano, Muhammad odyedwa ND nkhumba chgawenga ndamene anayambisa chisilamu,ngati ukulesa muuze abwelese mbili yachisilamu,anachoselanji mbili ya Muhammad ,

    • @shakiraameen8001
      @shakiraameen8001 10 месяцев назад

      ​@@NoahKalimatrue brother,,even me ,am now out of that cult,,,sanadyedwe ndi nkhumba,,koma atafa anamusunga masiku atatu mnyumba akuti azuke ngati momwe yesu christ anazukila koma zomvesa chisoni amaola asanakatikidwe mmanda so agalu ndi ntchenje was everywhere

    • @shakiraameen8001
      @shakiraameen8001 10 месяцев назад

      Brother go and read surat AL Imran 3vs 64,,which said ee inu eni a buku (la mulungu) Ayuda ndi Akhrisitu,,they didn't say Aslam why??? Which means the owners of book of God is jews and christians

    • @shakiraameen8001
      @shakiraameen8001 10 месяцев назад

      And go to surat 5vs68 AL ma Idah which says ee you people of this book,quran,,,you are nothing pachipembezo until muimilile kusatila malamulo a ma book a Taurat( old testament ) and Injili(newest testament) which means the book of God was allready there before quran

  • @happygondwe4774
    @happygondwe4774 Год назад

    No voice why?

  • @hassammaulana4529
    @hassammaulana4529 Год назад

    Ulemu wanu bro

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 Год назад

    Pena ndichifukwa chake azungu ambiri sapemphera coz they don't trust bible

  • @cephasnkhoma2301
    @cephasnkhoma2301 Год назад

    Koma ma Hebrew amatipo bwanji pachisokonezo ichi?

  • @ganizanichisale1449
    @ganizanichisale1449 Год назад +1

    Mukuti bwanji mbiri ya quran achalume kapena simuziwa kanthu ndinu bububu pa zimenezi

    • @irenechirwa9710
      @irenechirwa9710 Год назад

      Akuyiziwa A to Z anazapangapo post apa part 1&2 koma inu munalibe kabwino mbir yake ndi yoopsa enafe tinayimvesera ndithu. ndeno ati asilamu anamuukira kut achose nanga si anadziwa kut anthu akaziwa chitsitsi chawo ndeku zinthu zaipa

  • @mkupabanda-nd2vb
    @mkupabanda-nd2vb 5 месяцев назад

    Inuyo ndi mbambande madala

  • @JohnChibanda-h6b
    @JohnChibanda-h6b Год назад

    Who is erusmas

  • @abdulsalammkwepu3321
    @abdulsalammkwepu3321 Год назад

    Nde wina adziti bible original ndi bukhu lopatulika ndilo mau a mulungu ... wamvatu apa mubale wanga

  • @cephasnkhoma2301
    @cephasnkhoma2301 Год назад

    Koma ine mwandipangila zomwe ndikafunafuna. mau a YHV sana lembedwe bwino ndintu mukawerenga 1 samuel 13:vs1 muma bible monga (KJv) (mbuku lopatulika) (chi lenje or Cina mukuni ) ndi (TANACH Hebrew English version ) eee inu nacheepa ine.

  • @shakiraameen8001
    @shakiraameen8001 10 месяцев назад

    Read surat AL kahf 18vs85 86 even mohamad being a last and favorite prophet but he didn't even know where the sun set ,,as he said the sun set on a mouldy hot water

  • @MestreMaday-fv7qo
    @MestreMaday-fv7qo 4 месяца назад

    BODZA ABWELE KUMALAWI UKUNENA ZOWONADI IWEYO TAGANIZA BWINO

  • @petermasenti2084
    @petermasenti2084 Год назад

    Mumakwana big

  • @argentchilanga3246
    @argentchilanga3246 Год назад +1

    Am Malawian but we are really blessed with this historic man .God bless you

  • @androidgame7484
    @androidgame7484 Год назад

    Lachizungu or english

  • @ganizanichisale1449
    @ganizanichisale1449 Год назад

    Mpaka kulemba mau nkumati amulungu

    • @bravemsiska8039
      @bravemsiska8039 Год назад +1

      Azungu anango masulira ndimene wafotokozera m' baleyu koma kuti uonetsetse upezakuti Moses anelembanawo ku old testament after ataudzidwa ndi mulungu. So it was written in Hebrew and Greek language.

  • @StevenFombe-v2o
    @StevenFombe-v2o Год назад

    ❤❤❤❤❤🎉

  • @Ishmaelmsash5598
    @Ishmaelmsash5598 Год назад

    Ndiwe dolo kwambir

  • @ChisomoNgulube-cu7hv
    @ChisomoNgulube-cu7hv 2 месяца назад

    Bible is full of questions

  • @ganizanimoffat-ef4dz
    @ganizanimoffat-ef4dz 4 месяца назад

    Mwandisegura maso

  • @JeofreyNamalima-yn4tj
    @JeofreyNamalima-yn4tj Год назад

    Inu nkatundu bigy

  • @leyydavido-qd9gv
    @leyydavido-qd9gv Год назад

    Mumakwana malume

  • @shakiraameen8001
    @shakiraameen8001 10 месяцев назад

    Why can't you bring nkhani ya Mohammad yogonana ndi mwana Poor little gal Aisha at the age of 9

  • @lastonkachala6624
    @lastonkachala6624 Год назад

    Tilitonse

  • @shakiraameen8001
    @shakiraameen8001 10 месяцев назад

    Even the quran itself seems like a copy of Taurat and Injili

  • @shakiraameen8001
    @shakiraameen8001 10 месяцев назад

    And did you tell people that Allah had three daughters AL lat,,,AL uzah and manat??

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu2599 Год назад

    Useless information 🚮🚮🚮🚮🚮🚮🚮

  • @maviekuwili378
    @maviekuwili378 Год назад +1

    Tikufuna mbili ya Quran ngati uli dolo

    • @shakiraameen8001
      @shakiraameen8001 10 месяцев назад

      Tell him to tell us about mohamad who went to snatch his son wife zynab from zayd and sleep with little child Aisha at the age of 9 shame while he was 53

    • @Asibu24
      @Asibu24 7 месяцев назад

      ​@@shakiraameen8001zinalembedwa pati

  • @HamdanMasuku-b3n
    @HamdanMasuku-b3n Год назад

    𝐊𝐞𝐞𝐩 𝐮𝐩