Minyama yathu ngati amalawi ikuchokera pati?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 дек 2024

Комментарии • 224

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Год назад +12

    Mkhoza kuona nokha kuti zikhaleyo kuyipa nkhope angakhale ndichisoni. Tomorrow never end will see

  • @farookousmane715
    @farookousmane715 Год назад +13

    We are all Africans...when I see a burund person I see myself.

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Год назад +11

    You're the great man in malawi!!

  • @markoviskyhernandez9706
    @markoviskyhernandez9706 Год назад +12

    Thank you very much brother!! You are the best even though you tell people who have no ears nor brains!!
    Pepani ndithu!!

    • @greychizaka4088
      @greychizaka4088 Год назад +2

      anthu odzikonda chabe

    • @raytavares2256
      @raytavares2256 Год назад +1

      It's sad even in Angola Malawians used to sell its former Africans who were fighting the regime and that's how they killed my father and tortured my mother as a Christian missionary helping children who were forced on armed labour. My mum helped and was hiding those children to a place of safety.

    • @markoviskyhernandez9706
      @markoviskyhernandez9706 Год назад +1

      @@raytavares2256 Sorry Dear Sister/Brother😔!! It's very sad to hear 🙆🙆!! But most of the time, the governments of Malawi and many Malawians show a surprising behavior!! Imagine that Malawi was the only black country which was supporting discriminating government in South Africa!! Can you imagine that!!??🤔🙆!!
      Go there in Malawi right now and see what they are doing to black african refugees. It's shameful!! Remember that there are more than 6 millions malawians in South Africa, more than 5 millions malawians in Zimbabwe, more than 1.5 millions in Botswana, .... without forgeting in Europe, America and other different regions of this Earth. But the animosity that they are inflicting to the refugees is surprising!! Nothing to say 🤔😔!!

  • @BenissoneErnesto-kn9bd
    @BenissoneErnesto-kn9bd Год назад +2

    Komaditu brother Malawi ndikachani panagaga ngati pamenepa anyamatuso ambir Ali maiko ena kuthawa kupandako kanthu kumalawi zinkhale Ng,OMA watani kd komatu zimenezi siku Lina zizamusata

  • @raspeterkasengwa1390
    @raspeterkasengwa1390 Год назад +4

    Though you don't show your identity. You remain iconic

  • @AhmaduWilson-jl2br
    @AhmaduWilson-jl2br Год назад +4

    Umakwana ulemuwanu big thanks for telling us true

  • @thomassimbaya197
    @thomassimbaya197 Год назад +4

    watching from zambia you are great big man ,thy is a gold scalndal that has just happened here in zambia at K K international airport which is very compliceted i wish u could search about it

  • @rickiez
    @rickiez Год назад +1

    And I quoted "za mawa sizidziwika" ndili wokudzika kwambiri. Thanks for the information may God bless you

  • @SufiaanMsusa
    @SufiaanMsusa Год назад +1

    Am here waiting you boss from Johannesburg

  • @Wesleywisk-lf5hw
    @Wesleywisk-lf5hw Год назад +4

    Achakwelaso uthengau ukupezeni

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 Год назад +23

    Malawi Congress Party is a party that was not supposed to rule Malawi again

  • @HusseinMm-z3j
    @HusseinMm-z3j Год назад +3

    Zikomo brother mumatitsangalasa 🙏🙏🙏🙏

  • @stevechikaonda3145
    @stevechikaonda3145 4 месяца назад +1

    I must admit that this unknown guy is intelligent and wise

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 4 месяца назад +1

    Malawians people please let's wake up and fight for this country chakwela akutitenga wezi kwambili

  • @anafieintuka8090
    @anafieintuka8090 Год назад +1

    Good history sir
    Inu mumatiuza zoona zokazoka, thanks sir

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w Год назад +1

    This is very powerful massage ❤❤

  • @frankfriday3141
    @frankfriday3141 Год назад +1

    From Johannesburg near alberton ulemu wanu Big nde chifukwe chake aku Mozambique samatipasa magesi khamusu anatenga gawo ifa ya Zamora

  • @abudardachilangwe6791
    @abudardachilangwe6791 Год назад

    It's true...ndinakumana ndi muthu mu Bank kuno ku South Africa ndipo anati Dr banda munthu akathawa ku South Africa mkubwela ku malawi kamuzu amamugwila ndikumtumiza ku South Africa ndipo akafika ku South Africa amaphedwa ndikumangidwa.....I was ashamed kumva zimenezi

  • @josephchitsulo5882
    @josephchitsulo5882 Год назад +1

    Ndizoona, tilikonkuno ndipo akutisunga ndiomwewa

  • @christophermomba7127
    @christophermomba7127 Год назад +1

    Thanks for information keep it up Bakili

  • @idrissaKGO
    @idrissaKGO Год назад +2

    Jerous siimapindula gyx amalawi

  • @charlesRajabu-cc4bx
    @charlesRajabu-cc4bx Год назад +2

    Always you mumanena chulungamo mumayipasa fire

  • @fedson2050
    @fedson2050 Год назад +2

    Chakwera suzamva Munthu opanda Nzeru iwe ndi Mnzako Zikhale N'goma

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev Год назад +1

    Apa ndizothekano kumagona thx bradah man

  • @OmarAskimu-cn4ti
    @OmarAskimu-cn4ti Год назад +2

    Even makolo athu anatiuza zakuipa kwa MCP

  • @johnman4619
    @johnman4619 Год назад +1

    Ndizomvetsa chisoni mbiri yadziko lathu mutati muoni the holl Africa ndife thokha amalawi tilindi mbiri yoyipa mu independence koma zonzezi ndi Cecelia and John tembo

  • @NgendahayoSosthene-qn7qn
    @NgendahayoSosthene-qn7qn Год назад +2

    mukanena dzina ra charichi cyo ndikanafufuza umboni wa nkhani imeneyo rero romwe.

  • @christophermkhize1991
    @christophermkhize1991 Год назад +1

    Koma big inuyo mumakwana "nyelele mukuziponda lero mawa zidzadya ntembo wanu" ndimawutu akulu kwambili ngati amvela zimenezi ayenela kusintha zamawa sizidziwika

  • @ThokiseWiriyam-ws1ec
    @ThokiseWiriyam-ws1ec Год назад +3

    Chakwera ndimbuzi

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Год назад +1

    Thanks very much continue doing that

  • @BlessingsBanda-qn7xr
    @BlessingsBanda-qn7xr Год назад +2

    Mngopusa zikhale mbale zake mapoto ake komaso paniyo pake 😂😂😂😂😂😂

  • @titomethiwa4213
    @titomethiwa4213 Год назад +2

    Zikhale ndichisilu ndimuthu oipa kwambiri

  • @anifoiuene6301
    @anifoiuene6301 Год назад

    Andrew chimwendo sanayendepo kupita ku dziko laeni asiye kuyankhula za utsilu.Anifo from Moçambique

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere Месяц назад

    Powerful news brother.

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 Год назад

    Thank you for revealing the TRUTH. You must write a book about this history. It's true Malawi never ever bothered to help South Africans and yet today they still go to South Africa to work. Even now they follow the same patterns. Look at how they prefer keeping criminals and yet on Sadec. Do you recall how Kwacha Ng"ambi committed crimes more than Bushiri in South Africa? And South Africa will always be loyal to Malawi. Look at the Wenela period?

  • @MussahGeorge-f5n
    @MussahGeorge-f5n Год назад +1

    From Pretoria, love ur stories

  • @wysonnamaona6497
    @wysonnamaona6497 Год назад

    With you all times... Thank you for opening up our eyes.

  • @Yanazihhk2Hussenih
    @Yanazihhk2Hussenih Месяц назад

    Chilunu ndizeru zachuma kwa ozindikila❤

  • @hopembendela
    @hopembendela Год назад

    Nkhuyu dzodwa mwana zipota mkulu thanks bro

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 Год назад +1

    Reference ya andrew chimwendo yandikhudza dont burn bridges you crossed.

  • @chrisboyce229
    @chrisboyce229 Год назад +2

    Zoonadi brother Jealous simasunga mudzi tikuyenera kusintha A Malawi chifukwa Cha mawa sichidziwika

  • @Gibbs-yp6um
    @Gibbs-yp6um Год назад +1

    Mumakwana munthu wa'kulu kip on giving us nothing but the best history.

  • @LouisAndrew-jr1yj
    @LouisAndrew-jr1yj 4 месяца назад

    History is the best teacher ✌️

  • @MohommedMartin
    @MohommedMartin Год назад +1

    Andrew chimwendoyo pa mtumbo pake, galu ya chabe chabe

  • @johnsong7236
    @johnsong7236 Год назад +2

    i always smile and learn something at the same time

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Год назад +1

    Auzeni asiye majelous

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 3 месяца назад

    Zoonadi kamuzu amadana ndi anthu akuda km azungu chifukwa chasakho yakeyo ndie chilango chipite kwa kamuzuyo basi ctingamufunile zabwn kamuzu amuike ku mbawula ameneyo ameen 🙏 ameen

  • @PreciousDouglas-d7v
    @PreciousDouglas-d7v 9 месяцев назад

    Ur de best tv

  • @ALuz980
    @ALuz980 Год назад +1

    Ndizoona Khalidwe la nyau siligatithandize

  • @BensoPias
    @BensoPias Год назад

    Best historian your nomber one

  • @johndaka6368
    @johndaka6368 Год назад +1

    We are proud with u in Africa

  • @bjmtalimanja5073
    @bjmtalimanja5073 Год назад +1

    Andrew chimwendo kumwamba siwukalowa ndithu

  • @markoviskyhernandez9706
    @markoviskyhernandez9706 Год назад +2

    Anthu akuda amene amadana ndi akuda ena anzao, ndi zitsilu kwabas!!
    Nkhani ya Chimwendo ameneyo ndi onvesa chisoni 🤔🤔!!

  • @khumbozimba-r4h
    @khumbozimba-r4h Год назад +2

    Chanel yomwe ndimaikonda palibeso kuposer iyi ulemuwanu big

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Год назад +1

    Amalawi ambiri ndi ma illegal immigrants ku America, koma ali ndi ma business, amaloledwa kutenga loan ku bank even kugula nyumba kapena galimoto pa ngongole,, ndipo akuchita bwino kuposa ma americans. Boma la America limatolera misonkho kwa onse koma mabulutu amene akuyendetsa dziko la malawi sakuona patali.

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 4 месяца назад

    We still learned a lot from you ❤❤

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 Год назад

    That the fact ndithu thank you so much bg mn

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 3 месяца назад

    Uchitsilu basi, zelu ngat mazula ku john sadziwa businesses safuna ntchito koma jerous ndi anthu.

  • @sammyree8843
    @sammyree8843 Год назад +1

    I have been following for while brother very educative as we grew up in a country that real history was hidden to us.
    Please can I donate to you?

    • @henrysoko3283
      @henrysoko3283 Год назад

      I wish to donate too, this man has brain washed me

  • @markoviskyhernandez9706
    @markoviskyhernandez9706 Год назад +2

    Munthu wakuda kugwilizana ndi anthu omwe amapanga za Apartheid !??🤔🤔!! Za wutsilu ziminezo ndithu !! And they had no shame!!???🤔🤔
    There is nothing worst than to be on the wrong side 🤮🤮🤧🤧!!

  • @TriciaMalikebu
    @TriciaMalikebu 3 месяца назад

    Kamuzu & his party, MCP will never change

  • @eidchinkhunda7777
    @eidchinkhunda7777 4 месяца назад

    Long life big brother may Allah bless you

  • @daudimatolano1715
    @daudimatolano1715 Год назад

    Teach us, we are ready to support your work

  • @MefaKumwenda
    @MefaKumwenda Год назад +1

    Than you for explaining all history

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Год назад +1

    BIG 👍

  • @ElliasChikuluwadza
    @ElliasChikuluwadza 3 месяца назад

    Kkkkkk Kma mbakili muluz ndi mamunadi.

  • @DanielNgondo-rr9gd
    @DanielNgondo-rr9gd 4 месяца назад

    11 minutes ago.....58 thousand viewers....ayi zikomo

  • @RitaKainga
    @RitaKainga 4 месяца назад

    Salute you are a hero guys

  • @JafaliAlli-w7m
    @JafaliAlli-w7m Год назад

    zikhale ng'oma mulungu amulanga pompano ndi juma yemweyo mulungu akuwuona akuzunza anthu

  • @alexKaudzu-f6o
    @alexKaudzu-f6o Год назад +2

    Pilizani bro kutsegula maso a Malawi

  • @pastorbinuelf.lamusse6203
    @pastorbinuelf.lamusse6203 Год назад

    Timakunyandirani big kuchokera Kuno ku Moçambique Maputo.

  • @josephchitsulo5882
    @josephchitsulo5882 Год назад

    Tamugwileni mum'menye nachimutuyo, ana omwe anabadwila ku Malawi ko, ndi Malawian, chotelo akuzunzisa anawo

  • @UthmanKapungu
    @UthmanKapungu 4 месяца назад

    Congress is a total blood of Malawian and it's to us to choose again

  • @aubreykanyenda8008
    @aubreykanyenda8008 Год назад +2

    Please TEACH US and don't stop teaching this Government too

  • @EphraimNaveya-fc4iu
    @EphraimNaveya-fc4iu Год назад

    Nice 👍 talking sir,mcp it's one party that makes Malawi to be poor/minyama country

  • @davenchimadzi6529
    @davenchimadzi6529 Год назад +1

    Power bro.

  • @ModaAckson-sd2yq
    @ModaAckson-sd2yq Год назад +1

    Koma 🇲🇼 anatengadi minyama

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 Год назад

    Ife kuno ndiye tilipo samativutisaso achewa ngovuta ndaonela pa chakwela

  • @PromiseBarton-em1ll
    @PromiseBarton-em1ll Год назад +1

    Chakwera zikhale ng'oma anthu awa ndimbuzi za anthu😭😭😭

  • @josephchitsulo5882
    @josephchitsulo5882 Год назад

    Tamuuzeni kumeneko chitsiluyo, ifenso tilikuno kudziko la eni

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e 7 месяцев назад

    This shows exactly that we are acursed nation

  • @SandraMoses-y4l
    @SandraMoses-y4l 3 месяца назад

    Abale anzanga zikufunika tikavote mwanzelu serious chakwela ayi ndithu

  • @daviemafunga
    @daviemafunga Год назад

    Inuyo is bstter kukhara brother wanga

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Год назад

    Chakwera, zikhale ng'oma MCP yonse panyini pa mawo,ifeyo panopa tiri kunja poyamba timalandira ulemu koma panopa tiku funa kumama ngiridwa ma camp amalawi akuvutika akuthawira maiko akunja komanso inuyo mukakhala kumeneko ku malawiko muna voteranji MCP kamuzu anawa siyira mizimu ya Ziwanda panyero pa amawo

  • @jameschipula4475
    @jameschipula4475 Год назад +1

    Mumatha ndinu madala-madala

  • @AleksaWilliams
    @AleksaWilliams Год назад +1

    Kumakhaladi ndi umunthu,ndizoyilanad zithuzi

  • @sipplezulu
    @sipplezulu Год назад

    Africa tigwirizane ndife anthu amodzi

  • @TonyBanda-ch6vo
    @TonyBanda-ch6vo Год назад

    Koma inuyo bigy munabwera respect to you .

  • @kondwanivyalema9449
    @kondwanivyalema9449 3 месяца назад

    Mzimu wa Chilima SKC uwuse mutendere

  • @shabanitendo4781
    @shabanitendo4781 Год назад

    My bro now ur coming brz sizachilendo simukumuona chakwela amagwadra azungu

  • @YAKOBEJUMAH
    @YAKOBEJUMAH Год назад +2

  • @jeanmariehavugineza9382
    @jeanmariehavugineza9382 Год назад

    ine ndimafuna gupana support nchito zanu mutipatse number kapena njira yina kuti titandize nshito yi

  • @eunicemoyo6024
    @eunicemoyo6024 Год назад

    Shaaaaa kom malawi nsanje ndi ulesi wake ufiti bas kom mukuti ndi mbusaso 😏😏😏

  • @AfiyakazembeKazembe
    @AfiyakazembeKazembe Год назад +1

    Zoona big ine Kuno Western Cape Harare

  • @MkaiFrancisBendera
    @MkaiFrancisBendera 3 месяца назад

    Yes that's true 😂😂😂

  • @LloydMkandawile-c9p
    @LloydMkandawile-c9p Год назад

    Kulibe zuko lomwe lilibe wobwela ziko lose lapasi kuli athu wobwela so tisamapange zithu ngati wozindikila kwambi pomwe tili wosawuka

  • @manphiri2778
    @manphiri2778 Год назад

    Koma nchewa mwamunyoza kkkkkkkkk amangodziwa kudambwe eti

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Год назад

    Always Ur great history and truth

  • @horagerva
    @horagerva Год назад

    Mulungu akudalitseni. Zoona mukunenazo.