Location ya chiwembu sizikugwilizana ndi chiwembu chochokera ku boma coz maganizo oima PA trading pamenepa analysis are ogula katundu wa kunyumba kwawo palibe anatuma kutero
Koma aaa .bwana mukukwana ine ndimaona ngati kuti simutchula zolakwa zimene nthawi ya bakili muluzi .komampaka kumatchula muluzi mwiniwake wa tchanel aa bwana simukukondera zikomo
Always your history makes me feel happy when am listening bro KP it up to give us lekker lekker history🤝🤝
The best historical channel in Africa
This is the first time I have gotten some substantial news from this guy
History is the best teacher...
BM TV forever
It's my favourites Chanel until end of my life
Keep it up we love you God bless you.
sitizapezanso nsilikali olimba mtima ngati uyu not mbuzi tilinazo panozi malo mochotsa mbavazi R I P General Chigawa
Thanks for the information Chief.
Inu ndinu king wa history
Nthawi zonse timakupasani ulemu
Ur our hero big keep it up ❤❤
The best of the best 👌 ❤ 💓 ♥ 💕
Thanks for updating us the past history. We shd not forget what happened in the past.
Top channel in malawi!! You number one bro!! Keep it up!!
Keep it up my brother ❤❤
Chigawa zomba boy l miss you brother 😢
You are the best my bro
The best historic channel in malawi
From sauth Africa good job brather
Much love this Chanel ❤❤❤
Our own Manken Chigawa who learnt at Malosa secondary school we know him as the most intelligent person at Malosa RIP Chigawa 😢
More 🔥 fire wina asagone tulo ndi baliki muluzi TV
Akamuna inu❤❤❤❤❤❤🎉🎉
History is the Best teacher 😢
Each and every day ndimaonela video iyi apa pokha munagwila ntchito bgy💪
The great history am from Zambia I like it
Big. Can you please dig deep the history of Mkwapatira Mhango. Malawians need to know this journalist history who was a thorn to dictator Kamuzu Banda
Akakhala mbomamo asamaiwale kt Mulungu ndwamuyaya ndpo adzakumananaye a day to come
Koma kuyendesa ziko sikwamasewele zimene ndimaziwa tikaona ma history amaphulezideti. Zimakhala zovuta kumakhala kukhoza dziko musalowe chiphilikiti ndimunthu mmozi ndiye ukamatelo kwinakuso ndiwe okupha ndiye kaya. Taonapo anthu akufa ambiri chifukwa msilikali mmodzi akulanda Dziko kuyamba nkhondo ndiye polongosola zinthu umangosowesapo mmodzi poopa kuphesa ambiri
Bwanji mkubisa mayina adunawo zithu zinachitika 1995 tiuzeni ndunazo tiziziwe
Like your channel give us lekker history
Ndimamvesera mwachidwi ,kuyambira nkhani za ,Orton,Muwalo,Gwede,Gadama and mbiri zawo mumachula maina anduna zina komanso adindo ena aboma ndie apa zavuta bwanji kuchula maina andunazi
God never sleep nor slumber the truth nothing but the truth shall be known
BIG 👍
Top channel indeed just like someone has said... but I have been wondering... why did u name the chanel Bakili Muluzi?
Kkk even me too I do get confused with this name😅😅
Owooo ndi style yomwe amafuna kumpanga bon kalindo
Uremu wanu big boss mumati vesa kukoma✊
Number one❤❤❤
Well done bro....umazisata
Good job brother
Chigawa RIP
Good work keep it up
many old politicians have contributed a lot to the shed of innocent blood..... koma Malawi udaola
🎉 kip it up bro!¡
Thanks God bless you
Muthu wankulu ndikufunisisa muli ndi Moyo wauta mpaka kale
RIP General Chigawa
Well done brother
Osamalankhula zithu Zoti simudziwa,nkulu wawankhondo yemwe analowa muulamuliro wabakili muluzi sameneyu amene anali nkulu waasilikali anamwalira ndipo anayikidwa pa Lilongwe girls
Inu tiuzeni zoonazoo
Your the best brother
ku malawi kulibe tsogoleri wa chilungamu aaaaaa Rlp General chigawa
I like this channel
Noted with Thanks
Uku ndiko timati kuzukutadi...keep it up!
Nthawi iyi bakili muluzi tv ndimamutsata heavy coz amakonda kufotokoza ma history osati za panozi every post against to a politicians
Totally agree with you
Udzatuzenso zimene DPP during Bingu & APM era. Usamangotiuze zoipa za MCP ndi za UDF. Utiuzenso za Chasowa ndi ena during DPP
But how does a high ranked military officer move without security detail?
History says he was with a side chick
Ndiye ma picture amenewe amapezeka bwanji popeza thawiyo panalibe yomwe amatenga mmmm god bless you bg boss
Aaaaa 😁😁😁😁😁Mr 1995 kusowa camera kom zoona 😔😔😔😔
😃😃😃😃 Anthu azikapezeka ndima picture anthawi ya atsamunda
Police Ndi tchito ya matembelero kwambiri Ambiri they will go to Helo of 🔥
Yinuyo ndakatundu basi yife mawulemu
Inuyo nkhani imeneyi pakufunika kukumangani mukayankhe bwino mlandu wakupha amalawi ndinuyo abakili
Bakili anali mafia...anasowesa basi coz mkuluyu akanalanda boma like it or not
Pa nsewo ochokera my Lilongwe kupita ku Blantyre pakatipo palibe Tsangano trading centre, koma pali Tsangano turn off
Bolako izi we can pay attention to listen,koma Zina zija nde kumakhala bodza lowonjeza
Zemban band akuimba kutiko lelo pa 19
Pozetsa democracypo wanama galu iwe achina chihana ndiomwe anamenyelera ufulu umenewo.
Mr history inuyo
Location ya chiwembu sizikugwilizana ndi chiwembu chochokera ku boma coz maganizo oima PA trading pamenepa analysis are ogula katundu wa kunyumba kwawo palibe anatuma kutero
Ulemu wina Wa Bakili muluzi TV ndi mmene mumapezela ma pic
U are the greatest historian
Mutipezerekonso mbiri ya Buleya Lule kuti anafa bwanji??
wankulu yankunaninso za kepedwa kwa Matafali, woyimba.
Akulu ameneo anaziphetsa okha
muluzi nayenso chinali chingawenga. Ndichifukwa chake UDF must go.
Iwish nkanazakhala mtsogoleni muno ndizayambila ulamuliro wa MCP mpka mu ulamuliro wanga
kp it up king
Iweyo ndi number one
pitilizani bro mukutitsegula mitu ma history omwe mukutipatsa akutitsegula mitu
how did the assassins know that Chigawa will make vegetable purchases at Tsangano?
They were following him
@@dysonmoyo8901 now it makes sense...
Best of best hestoric
Stili watching this story 4/11/24
Anachita mistake yekha
A Yao Ali ndi mwambi amati pakamwa pam'buleje m'mbujegwe😮
Pakamwa panapha mbuye wake
nayenso MULUZI ATENDEREDWE KU NDENDE WAPHA ANTHU AMBIRI.
Koma aaa .bwana mukukwana ine ndimaona ngati kuti simutchula zolakwa zimene nthawi ya bakili muluzi .komampaka kumatchula muluzi mwiniwake wa tchanel aa bwana simukukondera zikomo
Kodi Za braks ndi Dolla zikuti bwanji kapena simuna fufuze
Kambalamenso wakabaza Ku Lilongwe imfa yake sinafufuzidwe Komanso it was political silence killing
Dzina la bakili muluzi tv likuchokera pati?
❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Still here in 19/10/24
Dziko lodana ndi chilungamo ili
Bakili Muluzi TV ndi Pangolin
OK chabwin takumvan Sono ku Ukraine zili pat pano
Salute
❤❤❤❤
😢😢 very sad
Anamuchita bwino anamuthira onga akanalandadi boma ameneyo
Nanga akakhuta mtapasha aziti anzanga omwe ndinapanga nawo training ndi ma president pano iyaaaa zachamba
Bigman tiuzeni za Nelson mandela
Umaitha aise pano tayamba kuziwa zambiri
Amapeleka chiopsezo anachita bwino kumusowetsa
We cud hv learn ths to school