Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Iweyo uli bho aise, ulinso ndi nzeru zambiri. Ndizioneraonera izizi🔥🔥🔥
Umatiziwisa Ku China koma kulankhula zolaula uchepese pepani I'm fOllowing you
😂Your character 😅nyc apapa tikamaliza tufuna robert chasowa part two. Following bwana
Dziko labwanji ili miseu yabwino ma buliding abwino koma kuli ziiiii ndipo very clean environment
Ndizowonadi ndithud bro simukunama ulemu wanu🤝
Otapisa samapezekako ngati mahure😊
Komatu sukunama ayise anthu akuvutika mayiko enawa olo kuno ku South Africa 🇿🇦 kuliso mavuto kwambiri azimayi alibe maukwati amunaso osakwatila nkhanizake kulowola kulipila ndalama kuti ukwatile komaso ukakwatila azimayiwoso ndi amwano kwambiri samalemekeza mamuna ife a malawi 🇲🇼 tizidziva kukoma kwambiri tili pabwino mkazi waulele komaso wamwambo❤ komaso olo kubeleka mwana kuno umachita kulila azimayi ake ndiovuta😢. I'm proud to be Malawi 🇲🇼 ❤️
Of course zoterezo zimapangitsa amuna kutumbwa...timafunika tizithamanga ngati anzathuwa
@mutafire kutumbwa kwanji palibe ayise pano anthu kuno ku South akumwa mowa moonjeza nkhani zake zomwezo mavuto ndiosayamba lemekeza mkazi wako iwe amene ukuva zimene ena akukumana nazozi, lemekeza banja lako lemekeza makolo
Damn sounds like a good deal
sounds like malonda
Enafe Facebook sikwenikweni please upload videos here mwati ziii
@@iPrinceoflove I should indeed.
Dolo
Ma dunthu kkkkk
Ndekt 1.billion kwacha
Dolo kwabasi.
Zikiti zikiti sapato panja km iweyo 😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣
Inenso ndimadabwatu 😂😂😂
Umatha ase
Eeee koma ada 🤣🤣🤣🤣🤣
Mmakwana bigy
Thanks tadziwa nawo
Maduntu shaaa😂
Umatha ayise😂
👍👍👍
Wow
Umatha 🎉
Koma umatukwana sibweni kkkkk mwai chikomera otero
Undione modz chiduntuyo nganyaa
Auzeni atipeze kuno,
i undestand why sunakwatile panopa morto
Iweyo ndi chidolo
Kodi ku Facebook zikuti bwanji?.You're no where to be seen...
Interracial bwanji kumeneko?
Naonga Mzala
Inetu madabwa kuti mkazi uja umaimanae uja bwanj
Ndemwat chonenepa klkkk ndiw dolo
Umaziwa yathu ija aku Malawi
Apa cfkwaa chot magaye ayaa ,,yakulimbika chomene tachimanyaa
Indeed.
Koma ku china😢😢
Mungalimbe?
Kodi anthu a kumeneko amakhala kutiko maka maka, there's no one in your videos🤔🤔 ku background kuli ziiiii
i go out mmawa kwambiri, or when it is too cold or too hot.
Still waiting for that Facebook monetization video
That will definitely come within 48 hours ndipo.
Still waiting brother
koma titleyo bahaya
size ya ma yufi
😂😂
Umakwanira
Sindizasiya kutsata Chanel imeneyi, nda yamika, nda nyadira, ndikupereka ulemu m'paka kale kale.❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Hahaha boss, mwatipopaso kwambiri
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Umatha🫶🇦🇷
Thanks taphuzira nawo

Kodi ku Facebook zikuti bwanji?.
You're no where to be seen...
Interracial bwanji kumeneko?
Naonga Mzala
Inetu madabwa kuti mkazi uja umaimanae uja bwanj
Ndemwat chonenepa klkkk ndiw dolo
Umaziwa yathu ija aku Malawi
Apa cfkwaa chot magaye ayaa ,,yakulimbika chomene tachimanyaa
Indeed.
Koma ku china😢😢
Mungalimbe?
Kodi anthu a kumeneko amakhala kutiko maka maka, there's no one in your videos🤔🤔 ku background kuli ziiiii
i go out mmawa kwambiri, or when it is too cold or too hot.
Still waiting for that Facebook monetization video
That will definitely come within 48 hours ndipo.
Still waiting brother
koma titleyo bahaya
size ya ma yufi
😂😂
Umakwanira
Sindizasiya kutsata Chanel imeneyi, nda yamika, nda nyadira, ndikupereka ulemu m'paka kale kale.
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Hahaha boss, mwatipopaso kwambiri
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Umatha🫶🇦🇷
Thanks taphuzira nawo
Umatha 🎉