A Triephornia ku Equitorial Guinea Ankataniko?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 14 янв 2025

Комментарии • 383

  • @kittahlevie01
    @kittahlevie01 2 месяца назад +6

    All I have learnt in this video is that
    We need to work hard and smart to have more money.
    Coz everything is possible peacefully when you have wealth through God 🙌

  • @Zenilome57
    @Zenilome57 2 месяца назад +24

    Amalawi simuzatukuka mpakana kalekale...morton akupanga zokuti mutseguke maso koma inu mukuti nsanje...tizafa tili osauka ngati dziko..mwina 100 years ikubwerayo tizachita bwino

    • @alickkamanga1621
      @alickkamanga1621 2 месяца назад +1

      Eti man. Kapolo ukafuna kumupanga liberate amakuukiratu

    • @chriskhaiya9039
      @chriskhaiya9039 2 месяца назад

      munuwakeyo sakutukuka bwa

    • @alickkamanga1621
      @alickkamanga1621 2 месяца назад +1

      @@chriskhaiya9039 wakuuzani kuti target ya utolankhani wake potulutsa nkhaniyi ndi kuti iyeyo atukuke?

    • @chriskhaiya9039
      @chriskhaiya9039 2 месяца назад

      @@alickkamanga1621 nde muti malawi sazatukuka bwa?

    • @lindasiliya5931
      @lindasiliya5931 Месяц назад

      Malawians lack knowledge, malawians amangowombela mmanja xilizonse chifukwa chozolowera kupempha komanso umphawi. Koma kuti afufuze kuti zikuchokera kuti ayi, amalawi ndi aulesi kufufuza nkhani tikamva, chilichonse mumangoti jealous. No wonder out country is very poor.

  • @wongiemanda3827
    @wongiemanda3827 2 месяца назад +7

    Investigative journalism 🙌🏿🙌🏿🙌🏿

  • @MapempheroSuwande
    @MapempheroSuwande Месяц назад +1

    Ine ndinagwira Ambuye Yesu Ndipo zanga zilibwino. Amen!

  • @patrickkudambo3973
    @patrickkudambo3973 2 месяца назад +8

    🔥🔥🔥🔥 Siza hate. Apa koma kufufuza Bobo.. Iyi Wawa ase 🎉

  • @IvySIMWELA
    @IvySIMWELA 2 месяца назад +14

    Any luxury life has got it's own deep roots..

  • @ephraimmonche6246
    @ephraimmonche6246 2 месяца назад +4

    Your investigative & research skills are top notch ✌️

  • @sergiosimbi
    @sergiosimbi Месяц назад +2

    Wow ndawasilira Mai mpinganjira she's lil had worker ulemu wanu Mai mpinganjira

  • @MemoryMbewe-uc4iu
    @MemoryMbewe-uc4iu 2 месяца назад +8

    eee inu zina zimadabwitsadi ee🙌...theres no hate here,ichi mchilungamo ichi

  • @bonifacemakina9326
    @bonifacemakina9326 2 месяца назад +1

    Man this is great work. A sigh if relief at last.

  • @williamchuzu7774
    @williamchuzu7774 2 месяца назад +10

    Morton is something 🔥🔥

  • @chawanangwamkandawire5850
    @chawanangwamkandawire5850 2 месяца назад +8

    Seems this woman has done a lot to be where she is now, her ex husband Chris Daza exercised a lot of wisdom posafuna kupikisana naya after she left him for Mpinganjira.

  • @patrickmasala474
    @patrickmasala474 2 месяца назад +21

    Who has watched?

  • @ChristeenaChristeena-eb8mn
    @ChristeenaChristeena-eb8mn Месяц назад +4

    Oooogho tadziwa nawo ,Alice uja ndimangodana nayetu amadziwa ngamo eti

  • @FemachZamora-pb5ve
    @FemachZamora-pb5ve 2 месяца назад +10

    I didn't want to talk about koma you see why we shouldn't be jealous about other people

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 2 месяца назад +1

    mmmmm amdala, I salute you!.... mmaiyu waoneka tsopano kuti ndioipaaaa!

  • @KhoChambwe-sj3ii
    @KhoChambwe-sj3ii 2 месяца назад +2

    Can't wait

  • @AlickMaloya
    @AlickMaloya 2 месяца назад +2

    Ineyo that's why I like this guy

  • @immazulu6232
    @immazulu6232 2 месяца назад +7

    Ine ndimanena kuti if only madam wa anali ozichepetsa anthu sibwezi akuwafufuza.

  • @WisdomMwale-j9h
    @WisdomMwale-j9h Месяц назад +1

    Ndee Mwati A Dr T Amatani ku Equitorial Guine koma a Malawi 🙌🙌

  • @charlessaiwala3913
    @charlessaiwala3913 2 месяца назад +9

    Ati ndimapanga manage business site hahaha kaya ndekuti chani kaya. Money laundering I guess

  • @Whacko_66
    @Whacko_66 2 месяца назад +6

    Hit the like button for SKC .
    Forever in our hearts

  • @AusmanChikapa
    @AusmanChikapa 2 месяца назад +6

    My heart calm down it's not my first time to comment in English 😂😂🙌

  • @immazulu6232
    @immazulu6232 2 месяца назад +58

    Achina Brian ma exclusive interviews are paid and scripted

    • @dtanatheist
      @dtanatheist 2 месяца назад +2

      Exactly. I lost respect to Brian kalekale

    • @steviexrstnamaseko3055
      @steviexrstnamaseko3055 2 месяца назад +3

      Aaa come on man you can't force someone to speak on things zomwe sakufuna what were you expecting from Brian Banda umat atani ... Kkkkk AAA come on

    • @Debbie2004-x9q
      @Debbie2004-x9q Месяц назад

      Ndiyetu talk about most of the interviews tsopano. They agree on the questions and the answers they’re going to give beforehand

    • @261yin
      @261yin Месяц назад +1

      ​@@steviexrstnamaseko3055that's why he is called a journalist. He went to journalism school for exactly that, asking questions and fishing for answers using different tactics

  • @Chidzaology
    @Chidzaology 2 месяца назад +5

    Akanakhala 10May bwezi atakalowa 😂😂😂 bravo Morton

  • @Tepani-Wachiyao
    @Tepani-Wachiyao 2 месяца назад +6

    Wamisala anaona nkhondo

  • @rosemarymhango4379
    @rosemarymhango4379 Месяц назад +2

    Given the same opportunity bhaghaya nanuso u would take it, definitely.

  • @GivisonPhiri
    @GivisonPhiri 2 месяца назад +4

    My friend Told me ase Tay kuti ulemele munthu umayenera kupondeleza Ena. Ndalama yosaka mwa chilungamo sungalemere nayo mwanyasi. Ndimamutsutsa! Apapa ndi kumvomeleza.
    Komanso munthu sungafufuze gwelo lililonse LA bwana ako, Bola akukulipila gawo lako. Za corruption zo ndi zawo ka

  • @gradsonmayira9336
    @gradsonmayira9336 2 месяца назад +2

    Waiting

  • @WelemuSayizi
    @WelemuSayizi Месяц назад +5

    Mayi ameneyu malinga ndi ukadaulo Ali nawo mosakaika ndi amene akusowetsa
    Ma dollars mosakaika ndi tambwali wosamasilira zili zonse

  • @cassimmgeni597
    @cassimmgeni597 Месяц назад

    Investigative janalistee baghayaa 😂😂😂🙌🔥🔥💪

  • @Yamikie-yamikie
    @Yamikie-yamikie 2 месяца назад +2

    Waiting patiently😀

  • @wonganikaunda7704
    @wonganikaunda7704 2 месяца назад +1

    Well narrated

  • @lungu77
    @lungu77 2 месяца назад +2

    Abwana izi ndizowophya !

  • @Thewarrior7093
    @Thewarrior7093 2 месяца назад +19

    This woman is a slay queen , I don't understand why Thom decided to marry her. One day she will eliminate him and get all his wealth and properties

    • @chitokussein
      @chitokussein Месяц назад +2

      His not that stupid

    • @Jimmy-e6r9x
      @Jimmy-e6r9x Месяц назад +1

      That wealth is no longer in his name though. But you're right, this woman doesn't suit Mpinganjira

    • @magolajacqueline4227
      @magolajacqueline4227 Месяц назад

      Ineso sizindingwila mtima

    • @motherofnations495
      @motherofnations495 Месяц назад

      Akudziwana boss..

    • @CHARLESMASINA-xx5kt
      @CHARLESMASINA-xx5kt Месяц назад

      Thom doesn't know the woman but he is wiser....I believe it wasn't proper to marry her

  • @GrantMlira
    @GrantMlira 2 месяца назад +1

    Waikakatula baghaya😂😂

  • @peterthawi
    @peterthawi 2 месяца назад +2

    baghaya...😂😂😂 wafukula nkhuni nkhani.izi

  • @joanafelix5646
    @joanafelix5646 Месяц назад +3

    & ndukumbukila mu interview ija Brian Banda atawafunsa kuti inali ntchito yanji anangoti iwowo sanganene coz eni akewo malamulo awo amakana what kind of ntchito😂😂😂😂😂
    Ndanena zoti mnava pakamwa pawo coz ndimkaonela live nde musandimangitse loya ndi ndekhandilibe kanthu ine😅😅
    Eeee ineyo zopanga support munthu zilizonse idont like
    Ndisiyeni ndi umphawi wangawu

  • @wileewaitetachawinga2306
    @wileewaitetachawinga2306 2 месяца назад +1

    That's where the flashy life comes from oky money is happiness ada

  • @matetediva-bf2kl
    @matetediva-bf2kl 2 месяца назад +2

    Seeing things in a different light now

  • @lukepeter8290
    @lukepeter8290 Месяц назад +2

    Eeesh tisangosilila zinazilizose

  • @godfreynyasulu5129
    @godfreynyasulu5129 Месяц назад +2

    Nde ifeyo zitithandiza chani...

  • @tamimudaudisaikonde5624
    @tamimudaudisaikonde5624 Месяц назад +3

    Bwinotu bathasar

  • @MartianX95
    @MartianX95 Месяц назад +7

    Zikuoneka kuti madam awa chuma chawo anachipeza kudzela mu money laundering, amachapa ma million dollars ama corrupt politicians aku equitorial guinea pogwiritsa ntchito business yawo ya mtendza komaso bank ya biggy aja, biggy aja akudziwaponso kanthu.

  • @ChrisZuze-hk6yq
    @ChrisZuze-hk6yq 2 месяца назад +2

    Waiting 😅

  • @WisdomMwale-j9h
    @WisdomMwale-j9h Месяц назад +2

    Tiyeni, Tizingolimbikira Ntchito Basi....Zapa Dziko Izi💔🙆😴

    • @ExKay7
      @ExKay7 Месяц назад

      Ntchitoso ndiyapadziko😂

  • @EnalaChakanika
    @EnalaChakanika 2 месяца назад +1

    Morton bhagaya 🙌🏻

  • @Chidzaology
    @Chidzaology 2 месяца назад +2

    Following

  • @isabelmajawa8319
    @isabelmajawa8319 2 месяца назад +1

    Aaaah za ziii

  • @beakab2378
    @beakab2378 Месяц назад

    Very very interesting 🤔

  • @ChristinaKamwambi
    @ChristinaKamwambi 2 месяца назад +1

    Surviving is winning Morton,

  • @AbleBefore
    @AbleBefore 2 месяца назад +1

    😂😂😂😂😂 kuthandiza bwanji kupakula bizi

  • @peterlongwe4122
    @peterlongwe4122 2 месяца назад +4

    I think zambirizi anthu mulungu mmamunamizila wakupasani ndi iyeyo😅

  • @BlessingsMasakala
    @BlessingsMasakala 2 месяца назад +2

    Eeeee ayi ayi munthu uyuyu ndidolo popanga ma video clip 😂😂😂wasemphanisa maganizo awanthu aise kkkk koma anyway keep it up anthu amaona ngat ungalulatu lelo wathawa ndimau eeeish😂😂😂😂

    • @deejaymlexmw1042
      @deejaymlexmw1042 2 месяца назад

      Legend 🔥🔥🔥

    • @Blessings-s3g
      @Blessings-s3g 2 месяца назад

      Ati ndikanalowa deep ndi video iyiyi koma ndimangofuna ndimenye one take😂

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 2 месяца назад +3

    Family ya engonga 😂

  • @hardygondwe625
    @hardygondwe625 Месяц назад +2

    A Thomas afela za eni shaa akulu mwanakazi uyu ntchipolopolo chiheni chomene

  • @boolay9641
    @boolay9641 2 месяца назад +4

    Tell us....

  • @Samuel-c1j1t
    @Samuel-c1j1t Месяц назад

    Morton we love your channel❤

  • @lucaskaunda3595
    @lucaskaunda3595 2 месяца назад +1

    Morton you do analysis man😊

  • @nursenyambi2145
    @nursenyambi2145 Месяц назад

    Basitu! Kwayipiratu

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 2 месяца назад +3

    Mayiyu siomanga naye banja mupinganjila anapala akufuna pofela

  • @blessingskaliati7951
    @blessingskaliati7951 2 месяца назад +1

    Ok Boy

  • @aaronziyeretsa6420
    @aaronziyeretsa6420 Месяц назад +7

    Now i understand why adamumangitsa mwana uja thats her character adazolowera kukhala ndi anthu oopsa ndi opanda chisoni,
    Theres no way munthu angammangitse mwana uja ndi nkhani imene ija yomwe mudali kachilungamo kkkk

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie Месяц назад +1

    Lawyer ndiribe ine

  • @timothykayesa1143
    @timothykayesa1143 2 месяца назад +1

    Every life has its own story

  • @Sheena-w2h
    @Sheena-w2h Месяц назад +1

    Ive learnt one Or two things here

  • @ikmusic-s9f
    @ikmusic-s9f Месяц назад

    Great

  • @HENRYMAKHASU
    @HENRYMAKHASU Месяц назад +3

    Sadawapakule koma amangwetu?

  • @InnocentKalenga-u2o
    @InnocentKalenga-u2o 2 месяца назад +3

    Bwana vkuti wuli apa

  • @ConfidenceBanda
    @ConfidenceBanda 2 месяца назад +1

    😂Shalom Malawi Shalom. Hiyayi😅

  • @whaaacka4162
    @whaaacka4162 Месяц назад +2

    eee Morton ndiwe shasha

  • @AbleBefore
    @AbleBefore 2 месяца назад +5

    I was manye managing 😢😢😢😢

  • @ericdisi7941
    @ericdisi7941 2 месяца назад +1

    Eeeh achina Morton ndiachabe😂😂

  • @VictorMwaungulu-cj4qs
    @VictorMwaungulu-cj4qs 2 месяца назад +4

    Ife mmene tinaona kt guinea timaongati apalulidwq ndi Kasongo Engonga

  • @agnesgwaza9165
    @agnesgwaza9165 2 месяца назад +1

    😂anthu a ndalam Eeee kumangotipatsa pressure😅😅

  • @ananiaclememtmwinuka
    @ananiaclememtmwinuka 2 месяца назад +2

    Analysis yachabe

  • @IsaacMbobo-y2o
    @IsaacMbobo-y2o 2 месяца назад +1

    Mupwetekana

  • @MartinNyirenda-gd8yz
    @MartinNyirenda-gd8yz 2 месяца назад +4

    Koma kwen kwen mfuna mtiuze chan

  • @petroayami02
    @petroayami02 2 месяца назад +4

    That woman cleans money ndthu

  • @Don_Taylor
    @Don_Taylor 2 месяца назад +1

    LMBO 😂😂😂😂 okay! Okay!

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 2 месяца назад

    Thanks Mr morton

  • @ChimwemweMaposa
    @ChimwemweMaposa 2 месяца назад

    Morton Baghaya 😎

  • @hannahmoses480
    @hannahmoses480 Месяц назад +1

    Who doesn't want a good life???
    Leave here alone

  • @madalitsoshepherd4134
    @madalitsoshepherd4134 Месяц назад +4

    Chouluka chidzatera dziko lapansi its not as it seems

  • @ChisomoMakanda
    @ChisomoMakanda 2 месяца назад +2

    Frankly speaking iwe ukuyitha

  • @AllanMwakalenga-wn5ib
    @AllanMwakalenga-wn5ib 2 месяца назад +2

    Albathazar? The Kasongo anali konko😂😂😂

  • @handsomenkonde2552
    @handsomenkonde2552 2 месяца назад +1

    Morton
    Our own

  • @williamchirwa7730
    @williamchirwa7730 Месяц назад +2

    You are in China and enjoying life and critical of one Mrs. Mpinganjira. Is China a free country and corruption free? Tineman Square massacre Hong Kong suppression of democracy and human rights abuses to mention just a few issues. If you are working there did you make a research of your employer how he or she gets the monies

  • @AlickChima
    @AlickChima 2 месяца назад +4

    video iyiyi itsegula m'maso boma what kind of people we are dealing with..their integrity and source of income..there is so much laundering taking place

    • @susanmkandawire-bw1ui
      @susanmkandawire-bw1ui 2 месяца назад

      Do you think they don't know? Amadziwa koma they choose to keep quiet

    • @AlickChima
      @AlickChima Месяц назад

      @susanmkandawire-bw1ui mmm, timaona ngati tili safe mudziko lino koma aaaaah..chisomo basi tsiku lina tizamba kuti the country is sold. people yake ndi yomweyi. I feel sad for Dr. Mpinganjira he is just another victim of love

    • @hannahmoses480
      @hannahmoses480 Месяц назад

      Bomaloso nde ili worse kaya
      Same Whatsapp group

  • @RhodriquesMajawa
    @RhodriquesMajawa Месяц назад +2

    Please leave madam Mpinganjira alone. She found an opportunity to make money and she seized it. Who doesn't want a good life? 🤔

  • @AmosJames-iv6wz
    @AmosJames-iv6wz Месяц назад +2

    Inu takapangan ndalama sizitithandiza izi ngat dziko inu ndiye oyelawo aaaaaaah

  • @sydneysimbi9821
    @sydneysimbi9821 Месяц назад

    Eeeeeeh 🤣🤣🤣 ati access ya vice president..

  • @stevezizwenyirenda5706
    @stevezizwenyirenda5706 Месяц назад +2

    Beansiness Triphonia

  • @Yanei-Sir
    @Yanei-Sir 2 месяца назад +2

    Kulemera sikophweka 😂😂😂😂

  • @GweynmargauxMwale
    @GweynmargauxMwale Месяц назад +3

    Sikwa 400 plus women in kuja uku😅😅😅okay okay

  • @overtonchirwa9756
    @overtonchirwa9756 2 месяца назад +2

    Kwakholatu Maji pafupi

  • @pempheronehiya56
    @pempheronehiya56 Месяц назад

    Muwawuze atriphonia wooo atigayire ndalama zoo

  • @PearsonSalima
    @PearsonSalima Месяц назад

    Amzanthu akuziwonq bola ifenso

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Месяц назад +2

    Mchamatama ichi ine chimandinyasa bwanji

  • @mikegausi8552
    @mikegausi8552 2 месяца назад +2

    mpaka in 4 hours?