Morton Baghaya
Morton Baghaya
  • Видео 446
  • Просмотров 1 397 898
Parking Allowed
Parking Allowed
Просмотров: 430

Видео

Idiot Driver - One Fool Can Ruin Everyone's Day
Просмотров 15216 часов назад
Idiot Driver - One Fool Can Ruin Everyone's Day
Blew It Kitty
Просмотров 18716 часов назад
Blew It Kitty
Malawi is sitting on massive gold deposits
Просмотров 2,1 тыс.16 часов назад
Malawi is sitting on massive gold deposits
A Bwana a ku MBC akuti Boma Ndilomweli Eti
Просмотров 282День назад
A Bwana a ku MBC akuti Boma Ndilomweli Eti
He is fine
Просмотров 262День назад
He is fine
Next Stop: Church
Просмотров 1,8 тыс.День назад
Next Stop: Church
He is Fine but surely educated
Просмотров 468День назад
He is Fine but surely educated
The American Dream - In China
Просмотров 150День назад
The American Dream - In China
Happy New Year, I guess
Просмотров 80День назад
Happy New Year, I guess
How fast was he going?
Просмотров 2,1 тыс.День назад
How fast was he going?
MA SLIMMING TEA AKUPHA AZIMAYI KWINAKU
Просмотров 2,6 тыс.Месяц назад
MA SLIMMING TEA AKUPHA AZIMAYI KWINAKU
OSAMWA MKAKA - MKAKA NDIWOYIPA
Просмотров 41 тыс.Месяц назад
OSAMWA MKAKA - MKAKA NDIWOYIPA
MA DEGREE ACHULUKITSA
Просмотров 7 тыс.Месяц назад
MA DEGREE ACHULUKITSA
CHIKANGAWA ABWERENSO
Просмотров 3,8 тыс.Месяц назад
CHIKANGAWA ABWERENSO
Kalata Ya Morton Kupita Kwa a Maumau a MCP
Просмотров 10 тыс.Месяц назад
Kalata Ya Morton Kupita Kwa a Maumau a MCP
Ma China Imatumiza Katundu Wofooka ku Malawi
Просмотров 2,8 тыс.Месяц назад
Ma China Imatumiza Katundu Wofooka ku Malawi
Mbuzi Zisamavote - Demokalase Imafunika Anthu Odziwa
Просмотров 2 тыс.Месяц назад
Mbuzi Zisamavote - Demokalase Imafunika Anthu Odziwa
Vimbuza Kulije - Kuli Mwatesi Pera
Просмотров 322Месяц назад
Vimbuza Kulije - Kuli Mwatesi Pera
Nthenda Ya 'Bola Mchewa Mzathu' Ndiyoopsa
Просмотров 2,8 тыс.Месяц назад
Nthenda Ya 'Bola Mchewa Mzathu' Ndiyoopsa
Ndinapita ku Tcalitchi Cha Apuse-Apuse Mulungu Afuna Ana
Просмотров 4 тыс.Месяц назад
Ndinapita ku Tcalitchi Cha Apuse-Apuse Mulungu Afuna Ana
China Sikumwamba - Zoyipa 10 Za Ku China
Просмотров 15 тыс.Месяц назад
China Sikumwamba - Zoyipa 10 Za Ku China
Azungu Abwerenso - Dziko Talikanika
Просмотров 9 тыс.Месяц назад
Azungu Abwerenso - Dziko Talikanika
A Tumbuka Ndi a Sankho, Odzikonda ndipo Asazalamulire Dzikoli
Просмотров 1,8 тыс.Месяц назад
A Tumbuka Ndi a Sankho, Odzikonda ndipo Asazalamulire Dzikoli
A Triephornia ku Equitorial Guinea Ankataniko?
Просмотров 72 тыс.Месяц назад
A Triephornia ku Equitorial Guinea Ankataniko?
Do Nothing for 8 Minutes as I Descend the Shaolin Temple Mountain
Просмотров 4232 месяца назад
Do Nothing for 8 Minutes as I Descend the Shaolin Temple Mountain
Tsogolo la America pansi pa Ulamuliro wa Trump
Просмотров 2,3 тыс.2 месяца назад
Tsogolo la America pansi pa Ulamuliro wa Trump
Surrogacy Itha Kubweretsa Forex Kuposa Fodya
Просмотров 1,1 тыс.2 месяца назад
Surrogacy Itha Kubweretsa Forex Kuposa Fodya
Wati Mkaka Nguwemi Yaye
Просмотров 4772 месяца назад
Wati Mkaka Nguwemi Yaye
Robert Chasowa Anali Chigawenga
Просмотров 115 тыс.2 месяца назад
Robert Chasowa Anali Chigawenga

Комментарии

  • @EmmanuelGordon-q9s
    @EmmanuelGordon-q9s 34 минуты назад

    Morton tasowa ma videos Anu aja ophuzisa n kuziwisa😅...mwati ziiiii ponyan

  • @keithchiumya910
    @keithchiumya910 53 минуты назад

    The west is extremely sick from greed.

  • @queenchawinga3493
    @queenchawinga3493 Час назад

    ndipo zoona izi zinazi timangodyera kusaziwa koma zambiri zimapangidwa ndi ma chemical oipa ku moyo wamunthu

  • @JenniferHannila
    @JenniferHannila 10 часов назад

    😂😂😂

  • @asimenyekalambo8065
    @asimenyekalambo8065 13 часов назад

    So many reasons for elon musk to divert his attention to Malawi

  • @EmmanuelGordon-q9s
    @EmmanuelGordon-q9s День назад

    Ponyani video..yanu ija yophuzisa n kutiziwisa...asamasowa chonchi ku RUclips

  • @JuniorSaine-d6r
    @JuniorSaine-d6r День назад

    Sudziwa kumwa chabe iwe 😂😂😂...ukadzadziwa kukoma kwa Enyoy tropical sudzanena za nonsense zakozo 😂

  • @JuniorSaine-d6r
    @JuniorSaine-d6r День назад

    Udzipanga zako zakumwanzo

  • @StevenSamuel-m6z
    @StevenSamuel-m6z 2 дня назад

    Zamasiku osiza izi guys usataniki waukulu nkulimboka job bas😅

  • @KingSoftMw
    @KingSoftMw 2 дня назад

    Koma mumangidwa mpaka mugone ndi mwana 😅😅😅

  • @LucyBanda-m7z
    @LucyBanda-m7z 2 дня назад

    Ndip zoon mwan akamwa zimenez amadwal chifuwa ndip ukangosiy kumpats amasiyans kudwal ndithuu😢😢😢

  • @ComfortMakupe
    @ComfortMakupe 2 дня назад

    😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂

  • @immaculatechitsakamile252
    @immaculatechitsakamile252 3 дня назад

    Iweyo uzingokhala ku China....kwakoko😂😂😂

  • @AubreyChazika
    @AubreyChazika 3 дня назад

    Anthu akubwera ndi tizikhalidwe toipa

  • @earthlyvibes23
    @earthlyvibes23 3 дня назад

    Vuto aliyense amafuna akhale ndi kapinga 😂

  • @FunnyGanuel
    @FunnyGanuel 3 дня назад

    Uyuyu samandiwaza

  • @williamnthala5942
    @williamnthala5942 3 дня назад

    Dzibakhala choncho. Otherwise mmene dzikubera dzandaledzi even if mining starts, it'll only benefit the few

  • @towerankhoma1380
    @towerankhoma1380 3 дня назад

    Who sang that song please

  • @Rattymakana-m4p
    @Rattymakana-m4p 4 дня назад

    Thanks for sharing

  • @MeliahSillie
    @MeliahSillie 4 дня назад

    Ndipo enjoy kungomwa mwana wanga amadwala chifuwa pano ndinasiya kumupasa anasiyanso kudwala pompo

  • @martinbanda2059
    @martinbanda2059 4 дня назад

    You're an Idiot

  • @simonandrewkambwera4475
    @simonandrewkambwera4475 4 дня назад

    ?

  • @SellinaChauma
    @SellinaChauma 4 дня назад

    Koma zakumwa zachilingamo zopanda vuto ziliko?

  • @Alex01azandaMkwinda
    @Alex01azandaMkwinda 4 дня назад

    Koma zowoona ?? ndimadabwa kuyitanira pa ma social media, mbava izii

  • @Alex01azandaMkwinda
    @Alex01azandaMkwinda 4 дня назад

    Wakuba uyu

  • @goldfishmasumbu-p8u
    @goldfishmasumbu-p8u 4 дня назад

    Nde bwanji amalawi burea of standard samabana?

    • @mutafire
      @mutafire 4 дня назад

      sintchito yawo...same as mmene sabanira fodya olo mowa

  • @albertokanene5669
    @albertokanene5669 4 дня назад

    Munthu akamangidwa kuno amati ndi political witch-hunt

  • @mustaphamanjawira4747
    @mustaphamanjawira4747 4 дня назад

    All this just to end up in the hands of Mr President. I heard the constitution states that the president is the custodian of all the mineral deposits found in the land

  • @CarloMeddusa
    @CarloMeddusa 4 дня назад

    Ndkuchoka pokumwaso apapa

  • @Fewzyrapa777
    @Fewzyrapa777 5 дней назад

    😂😂😂 eeeeeeh

  • @Josephinebanda-k3x
    @Josephinebanda-k3x 5 дней назад

    Thank you for sharing this powerful information, I am watching from Zambia

  • @TendaiBandah-b3q
    @TendaiBandah-b3q 5 дней назад

    Inutu muzalipira nazo pa court,,achitsiru, kuipa

  • @piliranimalama6090
    @piliranimalama6090 5 дней назад

    Siya iweyo zako zimenezo

  • @twavysibale4751
    @twavysibale4751 5 дней назад

    But we wont benefit anything from it...malawi is corrupted,..

  • @aleksandarcvetanov7809
    @aleksandarcvetanov7809 5 дней назад

    този човек явно е направен от гума

  • @DavieVizier
    @DavieVizier 5 дней назад

    Unfortunately, the likelihood of a war is now certain. That's Africa I know. Chakwera sangalore mgodi uwuwu upite.

  • @GLA-od7ce
    @GLA-od7ce 5 дней назад

    😂😂👍🏾🔥

  • @GLA-od7ce
    @GLA-od7ce 5 дней назад

    True😂😂

  • @AngelinaNantima
    @AngelinaNantima 5 дней назад

    He is talking of too much sugar These days ku chipatala kupezeka ndi Tiana todwala sugar komaso bp I support him

  • @Doctor_k845
    @Doctor_k845 5 дней назад

    Hope this benefits us as Malawians

  • @mbanikmbaku4297
    @mbanikmbaku4297 5 дней назад

    This country better be rich by the end of that 25 years. First of all the Malawi government should come forward and tell the people what the plan is. Salima Sugar and Kayelekela stupidity should never be repeated. Also Presidential candidates better come up with concrete plans regarding this treasure. No fairy tales.

  • @Wongiezo_265
    @Wongiezo_265 5 дней назад

    Trust me, the only ones who will benefit from these projects are the leaders not the entire Malawians …We have stupid and selfish leaders who are only interested in lining their pockets ….Morton taonga chomene

    • @Iweumati-td4mb
      @Iweumati-td4mb 5 дней назад

      Mwinanso awadyetsa kale ma buns🙌😭

  • @hydra_mw
    @hydra_mw 6 дней назад

    Maybe that's why they have been making us poorer so they can buy it for cheap

  • @brendachirwa-u2q
    @brendachirwa-u2q 6 дней назад

    Maybe Ali ndi gas yeah

  • @mdyombamw7659
    @mdyombamw7659 6 дней назад

    Paja boma amapanga promote adding value Kuma raw materials... Tionela pa titanium uyu

  • @franklinrashid8804
    @franklinrashid8804 6 дней назад

    We better sit on these minerals till we get wise leaders

    • @Iweumati-td4mb
      @Iweumati-td4mb 5 дней назад

      Exactly my thought we can't redo kayelekera all again infact we should abandon this company they already failed us

    • @mwai19
      @mwai19 4 дня назад

      And you think these people would just be waiting for you?

  • @SheffieldMagonagona
    @SheffieldMagonagona 6 дней назад

    Boma lathu litakhala la Jackup this can solve the forex scarcity issue.

    • @mbanikmbaku4297
      @mbanikmbaku4297 5 дней назад

      True. this is the country's lifeline. This should solve most of the country's problems.

    • @SheffieldMagonagona
      @SheffieldMagonagona 5 дней назад

      @mbanikmbaku4297 the only problem ministry of mining ija ndi dzina chabe sitikupindula nayo

  • @mutumwathongethonge7892
    @mutumwathongethonge7892 6 дней назад

    MCP yataya chikwama apa

  • @francistonysanena5349
    @francistonysanena5349 6 дней назад

    You can edit the title... Its Rutile not Gold

    • @mutafire
      @mutafire 6 дней назад

      hahaha a Fula, you know I am like 1 hour away from being a professor, right? sizoti the title is wrong... the 'gold' is English for riches.

    • @thekuhespodcast
      @thekuhespodcast 5 дней назад

      😂​@@mutafire

  • @LoneyMateleka
    @LoneyMateleka 6 дней назад

    This is huge news for our economy albeit our malfunctioning systems in place..can't be very much optimistic..we know where all that money will end up..