Chitsanzo ndi kwa Nsundwe, kuli ophunzira mmodzi yekha komanso wa JCE basi the rest ndi a Std 2,3 koma pokavota onse ndi MCP chifukwa amati ndi chipani cha kwao 😭😭😭
Imagine a very successful business person, big time taxpayer opanda MSCE.. kenako kape wina wake wa MSCE yapa Good Maganizo ongokanda.. nde mwati who is supposed to have a say on choice of leaders? Civics can be taught to illiterate villagers and educated elites (Phds) can still and do vote on tribal basis.. My point being it's not that simple Dada Mhango.
@zamadulasimango6972 no need to spend more time and civics is not about money...nor is democracy about money. To pass MSCE you know enough about the world...biology, agriculture, politi, history, history, English and so on
Mbuzi iwe, ndinakupempha kut ukambe za system ya education ya ku china komanso yaku Malawi pajatu amati timaphunzira parts of grasshopper or birds ya ku china ndiyotan
Your sense is making more sense
I am a Philosopher. You are making much sense.
On Point Aise Morton
Chitsanzo ndi kwa Nsundwe, kuli ophunzira mmodzi yekha komanso wa JCE basi the rest ndi a Std 2,3 koma pokavota onse ndi MCP chifukwa amati ndi chipani cha kwao 😭😭😭
Morton panopa umandiwaza kwambili
Chilungamo choopsa kwambiri. Koma wina chifukwa cha dyera atha kutukwana pa nzeru ngati iyi... Malawi anafika pa nthenda ya Cancer mmmm😭😭😭
Wapala fundo iyiyi
Real talk men❤🎉
Exactly Morton malawi.ambiri ndi mbuli
Apapa pokha wayankhula nfundo yabwino kwambiri 😊
Mfundo Ili bhoo
Ndiwe Dolo!
live live
Chilungamo 😂😂😂❤
Komaso minster azikhala waku university osati akangqnyawa
😂😂😂 Amalawi ndi mbuzi man a president akeso mbolo. yinatota kale pano akungobaya nyini
Mbuli now days zimaganiza bhooo kuposa wa MSCE, nkhan Nd civic education kwa anthu onse
mmmmmmh bodza ili. munthu oti analowako mclass and has been forced to think beyond the horizon sangapange zofanana
Ndiwe dolo
Inu ena ife 4 sitifike koma kaganizidwe Kathu mkangwilo mapwala anuso pati
Facts 😅
Imagine a very successful business person, big time taxpayer opanda MSCE.. kenako kape wina wake wa MSCE yapa Good Maganizo ongokanda.. nde mwati who is supposed to have a say on choice of leaders? Civics can be taught to illiterate villagers and educated elites (Phds) can still and do vote on tribal basis.. My point being it's not that simple Dada Mhango.
@zamadulasimango6972 no need to spend more time and civics is not about money...nor is democracy about money. To pass MSCE you know enough about the world...biology, agriculture, politi, history, history, English and so on
Ukawone amene ali muma udindo akuluakulu ndi mbuliso achina manganya
You are not serious are you?
ASE manganya Ali ndi doctorate musiye amene uja sungamake ASE ndiophuxla amene uja
@siwedmataya7429 maphunziro ake siokwanila poyendesa boma ali ngati lazalo
@siwedmataya7429 manganya ndi namwino azikagwira kobelekesa
Mbuzi iwe, ndinakupempha kut ukambe za system ya education ya ku china komanso yaku Malawi pajatu amati timaphunzira parts of grasshopper or birds ya ku china ndiyotan