Thanks Bro Baghaya, you're highly appreciated for telling us different topics from where you live, one of the most popular regions in the globe, China/Far East (or Asia as whole)! As Geography, History, Tourism/Traveling & Current Affairs are among my favorites, I enjoy your posts very much, you add more precious things/knowledge to my brain. Go on brother to learn from you, we gain a lot! I hope I'll visit you but too tiresome reporting to police every 24 hours for my presence there in Chinise City ha ha ha ha ha ha! Also, tell me/us about religious issues (Christianity, Islam, rituals) in China in your next posts. Anyway, how long have you been in China, bro? Do you come here in Malawi for holidays or seeing relatives/friends or attending other ceremonies since you went to China? Umoyo Uweme Ku People's Republic of China, Ŵakuru Ŵa Baghaya !!!
Eeeeeeeeeeesh koma aise iwe mulungu akudalitse pali ma guys ena aku aku america amafotokozaso zomwe zimachitika ku china mbali ya mafuta ophikirawo, amaonetsaso mpunga wa plastic kumawadyetsa anthu ma Chinese kunena chilungamo ndi anthu achabechabe
Ngati kuli dziko lomwe solisangalasa olo Lili lolemera koma ndi ukaifi ndi china. Ndi azake ma communist monga north Korea even Russia mmm. Ku Africa kuno ndi Mozambique Sudan Libya
Chief, don't u think, despite the poverty, ifeyo ku Malawi we are better off coz kuli ufulu? Nanga kumeneko munthu angayankhule momasuka the way u talk about Malawi politics?
Waaaaaaoooooooooooop
Morton Bakili Muluzi TV 2
An eye opener thanks alot
Educative clip
Ukutiimilila fada, keep up the good work. We get to know China as if we're there😅
Thanks brother for the information
Bola Malawi emweyu 🙌🙌🙌
Ati mukaone masten saonaoneko muthu wakuda🤣🤣🤣🤣
Etii inu 😅😅
Ma video anyatwa Mr Mhango, zimaoneka ngati zachibwana koma mumakhala mukupezeka uthenga wamphavu. Kkkk iweyo umakeana
Thanks Bro Baghaya, you're highly appreciated for telling us different topics from where you live, one of the most popular regions in the globe, China/Far East (or Asia as whole)!
As Geography, History, Tourism/Traveling & Current Affairs are among my favorites, I enjoy your posts very much, you add more precious things/knowledge to my brain. Go on brother to learn from you, we gain a lot!
I hope I'll visit you but too tiresome reporting to police every 24 hours for my presence there in Chinise City ha ha ha ha ha ha!
Also, tell me/us about religious issues (Christianity, Islam, rituals) in China in your next posts.
Anyway, how long have you been in China, bro? Do you come here in Malawi for holidays or seeing relatives/friends or attending other ceremonies since you went to China?
Umoyo Uweme Ku People's Republic of China, Ŵakuru Ŵa Baghaya !!!
Iwe uli boo kusiyana ndi enawa amangokhalira kutukwanawa akuti kwa iwowo ndiye kutchuka. KEEP IT UP.
Africa tiri pamtendere ndichifukwa chake akudzadzana kuno kuti atilowerere mu njira zonse .
We love you Morton💜
Love you too!
Eeeeeeeeeeesh koma aise iwe mulungu akudalitse pali ma guys ena aku aku america amafotokozaso zomwe zimachitika ku china mbali ya mafuta ophikirawo, amaonetsaso mpunga wa plastic kumawadyetsa anthu ma Chinese kunena chilungamo ndi anthu achabechabe
Okay. So how do they manage to live longer when water and food is devastating?
That’s why I prefer to live in Taiwan 🇹🇼 haha. I make videos about Taiwan too. Nice work 😊
Cool, thanks
Wow
Uzipanga a chichewa 😅😅😅
@ it’s not only for Malawians.
It's okay mama
One Internet,two Food safety 💯 True.
Thanks brother this should not be the beginning of the end but beginning of the beginning
Ati ukapeza nzako wa chi china onvana nae chichewa 😂
This video is lit. But I heard shenzhen is the silicon valley of China. Mukapeza mpata mupiteko, tione
Great
Kuvesela mwachidwi 🙇
Zabwino,nanga zoti amadya nyama ya munthu mukutipo bwanji?
Nice video, i think your just misunderstood with your crazy jokes on social media, otherwise ayi ndithu watichezetsa bho.
komatu umayenda wapasi eeee
Thanks bro
Tamva nawo
Ma Nigeria ndikonse kuipisatu ndipo ndi anthu akwa frica oipa kwambiri dziko ili
A very good story but just poor reporting.Very interesting one
Thank You Morton
Ndakhala kuchina zaka 16 ndipo ndikutsimikiza kuti zonse muvideomu ndizoona.
Ku Gaunzgho Kuli ma Nigerians Ambiri...and they control many parts ... Amachita kukhala ngati Kwawo 😂
Talk of pa Airport.... Ma Chinese kuchita kuopa
Tsopano kulibe achifwamba kapena mbava chifukwa wayenda kwambiri opanda kukuzunguza
@@ismaelmmera8027 kulibe...olo utayenda 2am
I prefer Malawi 😊
We live here in Malawi 4 months with zero kwacha airtime
analemela mwa uchitsilu😂😂😂
Internet po nde worse TU
Unali museum eeet ndankunvesesa
Umakwana Mutabaluka
Nanga bwanji akumakonza mafoni,ndiye kuti heta technology.Ndiye chmatheka ndichiyani?
That's why i love the USA
moni kwa xi jinping
That's why timati the matrix is real👍🏽
Kulimbana ndi zandale zija ndi umphawi anthu kumeneko amakhala busy ndi ndalama not ndale cuz ndale says man sizakunozi zaisiluzi
So a Mau Mau aku Hong Kong aja analimba mtima bwanji kuti axipanga mademo
Mwayenda akulooooko eeeeeh
Bola asakusowesetu😂😂
amwene tikasowa muzaziwa
Zili bwino big
Ngati kuli dziko lomwe solisangalasa olo Lili lolemera koma ndi ukaifi ndi china. Ndi azake ma communist monga north Korea even Russia mmm. Ku Africa kuno ndi Mozambique Sudan Libya
@@GeorgeChiwanda nah, don't play... this is all that is bad...if we got to the good, you would be mind-blown
Chief, don't u think, despite the poverty, ifeyo ku Malawi we are better off coz kuli ufulu? Nanga kumeneko munthu angayankhule momasuka the way u talk about Malawi politics?
@shamisokambwili8456 no, development is freedom.
What's your destination akulo
kudeni
Fuso mkumati zonsezo amapanga chifukwa chani???
A video koma awa
A bad reporting making a shot story very long and nuisance
Kkk
Thanks
Nde iwe ukufuna kut azugu abwereso kuno south kuzatan
Zoti amadya anthu ndizoona??
Not in this Morden world, its past history on 1900’ when hunger hit the whole world
Nkhope eeeeeh
😂😂😂😂😂😂😂
Kod mukupita kut akulu😅😅😅 coz nde mwayendatu
ku shamba
Tanvanao bhobho
inu yo mulinayo cad yo
Lembani mu chizungu tione ngat sakuthamangitsani
The owner of internet is USA army.
😂😂😂😂😂😂
Ndipo live anthu timangoona kuichemelera china koma ufulu kulibed