Osamwa Juwisi wa Enjoy!

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 окт 2024
  • Muvulaza Ana!

Комментарии • 297

  • @christophermukaka7403
    @christophermukaka7403 3 месяца назад +6

    The best drink is water or thobwa koma anthu timaona ngati za chimidzi

  • @AndrewChiponga
    @AndrewChiponga 2 месяца назад +2

    Ase tizimwa Iya kusiyana ndikudya khono umadya zidya

  • @GloriaKalimamikundi
    @GloriaKalimamikundi 3 месяца назад +4

    Thanks for sharing.Wofunira moyo wake zabwino apanga chisankho yekha.Enafe ana athu anadwalapo nazo.Timangopanga za local basi

  • @ndabaningichisiza9574
    @ndabaningichisiza9574 4 месяца назад +5

    There was a time my Son could not sleep until 1 Am! This juice is bad indeed.......but which cheaper brand is good abale, nanga tingakwanitse kugula series muwiri daily? Lol

    • @LywellChilupsa
      @LywellChilupsa 4 месяца назад +1

      Ine mwana wanga akamwa amadwala chifuwa sizinaoneke

    • @yamzyboumar502
      @yamzyboumar502 4 месяца назад +1

      Good thing is kumampatsa phala basi apo ayi azidya kwambiri nsima with ndio zothira nsinjiro osati mafuta kwenikweni

    • @premakiyi
      @premakiyi 4 месяца назад

      Are you sure the insomnia was due to a Juice?

  • @BinwellMayani
    @BinwellMayani 3 месяца назад +3

    Bwana Morton,pitilizani kutiphunzitsa coz zambr sitikuzidziwa

  • @BrianMandhlopa
    @BrianMandhlopa 4 месяца назад +4

    Malawi bureau of standard is a sleeping cat.....

  • @situationmalawi3646
    @situationmalawi3646 4 месяца назад +2

    Ndiye mMalawi kumuuza izi aziti ukumupangira nsanje.... you'll hear them saying "if you can't aford don't tell me not to" 🤣

    • @mutafire
      @mutafire  4 месяца назад

      bola apeza info...zinazo azipangano akuziwa mbali zonse

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 3 месяца назад +2

    Zimvele mtolo. Ofuna kumwa adzimwabe, amene wamvela asiya.

  • @mayesokazembe5880
    @mayesokazembe5880 3 месяца назад +2

    Can be true, bola asakusumileni……..

  • @DanielZunguza
    @DanielZunguza 4 месяца назад +3

    Ndidzowona olo mwana akamwesa enjoy, Chifuwa sichitha ndidzachabechabe.

    • @LywellChilupsa
      @LywellChilupsa 4 месяца назад

      Same us mine amadwala chifuwa chandithu

  • @deborahngwira724
    @deborahngwira724 3 месяца назад +1

    Thank you...ineyo honestly v never thought kuti in the juice wa enjoy muli real stuff, n if you open to see the ingredients you can vomit.

  • @kingstonechisale978
    @kingstonechisale978 4 месяца назад +2

    Ndi chilichonse akulu! Check Sobo simukhala chipatso chilichonse ndi ma flavors okhaokha. Nde musaopsezepo anthu apa 🥱

  • @charlokapalamula9299
    @charlokapalamula9299 4 месяца назад +2

    Thanks for opening people's eyes. Amene wamva wamva basi....

  • @shongafilms3925
    @shongafilms3925 3 месяца назад +1

    Even chimanga chomwe tikudyachi amakhala ayikako zimankhwala zambiri kuti chidzicha msanga.
    Palibe infa kuithawa.......zokupha si izi ayi amachita kuzikwelera bus anthu

  • @noelmsiska3692
    @noelmsiska3692 3 месяца назад +2

    Zidyani nokha poisoniyo munthuyu akunena zoona ineyo juice ameneyu ndimamumva irritating throat this guy is right

  • @BMadhlopa
    @BMadhlopa 3 месяца назад +1

    Someone is alerting people about hazardous food /drinks, how can he be mad? Calling him mad is preposterous!!

  • @KhadijahImedi
    @KhadijahImedi 3 месяца назад +3

    Ever since I stopped giving my baby enjoy chifuwa chake chinachepa eish

    • @mutafire
      @mutafire  3 месяца назад

      Wise choice!

    • @Sharoshining247
      @Sharoshining247 3 месяца назад +1

      Ndizoona akumapangitsa chifuwa 🤔🤔🤔

  • @ladyb9179
    @ladyb9179 4 месяца назад +2

    Tipilizani kuwatsegula mmaso a Malawi.

  • @hawabanda-xs5fx
    @hawabanda-xs5fx 4 месяца назад +1

    Izi zoona ine ndinagula cartoon for my son koma pomaliza cartoon ija mwana amadwala kusegula kumangosaza almost 2 weeks mwana paja Ku school samapita ndipo kuyambira pompo sindigulaso

  • @bonfesszinkomola6552
    @bonfesszinkomola6552 3 месяца назад +2

    Ndangomaliza kumene kumwa wa tropical

  • @alfordkuyenda2684
    @alfordkuyenda2684 3 месяца назад +1

    I have never like this guy but on this video am 100 % behind him, osangonyoza for the sake of kunyoza but follow the facts. Very good healthy tips!!!

  • @naBEthA
    @naBEthA 4 месяца назад +2

    Kma tamumwa eeesh😢😢😢

  • @Justman34_dislike
    @Justman34_dislike 3 месяца назад +1

    I started disliking Enjoy the moment I saw increased list of chemicals on its ingredients. Thanks for sharing

  • @hassanmpate7538
    @hassanmpate7538 9 дней назад

    Mtolankhani iwe unapanga za umoyo? chifuwa tili ndi malawi beaural of standards iwowo ndipmwe amapanga control zakudya za a Malawi. Mpaka mmbuyomu anawauza opanga zakumwa zimachokera ku Mozambique kut accepts acid, iweyo ulibe mphanvu yopanga zimenezo, mtolankhani iwe...

  • @MikeBanda-cr7ni
    @MikeBanda-cr7ni 3 месяца назад +1

    Zakudya zonse zopangidwa Ku factory ndi poison even nkhuku zachizungu izi sizabwino ayi. Matenda a cancer ankhagwira azungu kwambiri koma pano anayamba kuchuluka Kuno Ku Africa chifukwa timadya ma processed foods tinasiya kudya zakudya straight from farm

  • @DavidIsradoris
    @DavidIsradoris 4 месяца назад +2

    Mutipangileko check Maheu bwanj wakulu?

  • @LusayoSunga
    @LusayoSunga 4 месяца назад +2

    Wakumva ndewava

  • @GetrudeUseni
    @GetrudeUseni 3 месяца назад +1

    Ana ambiri akupezeka ndi nthenda ya sugar coz of these foods and drinks

  • @EthelOsman
    @EthelOsman 4 месяца назад +1

    Yes ineso ndi mboni chifuwa sichithelapo ayi abale koma yaa

  • @staymotivated1768
    @staymotivated1768 4 месяца назад +1

    Tikudya en kumwa ma chemicals oopsa, nkona ma cancer, ma sugar, ma bp angoti mbwee

  • @PemphoGwazaJere
    @PemphoGwazaJere 3 месяца назад +2

    Tiyeni tizimwa nthobwa magaye 🤣🤣

  • @kaymikundi7935
    @kaymikundi7935 4 месяца назад +1

    Hmmmm ndazizidwa. Totally mortified!

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 3 месяца назад +1

    Zoonadi izi koma tiuzeni za ukwaju pls

  • @yosefemwansapozimba1027
    @yosefemwansapozimba1027 4 месяца назад +1

    Ndamva iiii thanks for this

  • @EmmanuelMponda-ig9bm
    @EmmanuelMponda-ig9bm 4 месяца назад +1

    Akusowetsa 😂😂😂😂

  • @jamesjealous-p4v
    @jamesjealous-p4v 4 месяца назад +1

    Lol stop jealous bro shame on you 😂

  • @TachikoMwanamanga
    @TachikoMwanamanga 4 месяца назад +1

    Ndie ma nurse aku central hospital amachita kukakamiza kugulila ana akapangidwa admit 💔 ndinayambanako ndima nurse akundilesa kubweletsa 100% drink akut ndigule komweko enjoy ndiwabwino kwa ana💔😂 sometimes ku Malawi amangobweletsa zithu bola apange ndlama

    • @EffieMalonda
      @EffieMalonda 4 месяца назад

      Thanks longosi I've never seen u serious like this izizi ineyo I will use it..... no more enjoy in my house

  • @leonardmalirana7423
    @leonardmalirana7423 3 месяца назад +1

    Kamdzukulu kanga timavutikanako kumangoyendayenda osakhazikika mwina ndi enjoy yemweyo.anthu Ena ngati angakasume basi kungotenga enjoy anachita umboni yekha

    • @MaudKapakasa
      @MaudKapakasa 3 месяца назад

      Hypa, more sugar kids are become crazy eish

  • @HANCENENTERPRISE-yw4mr
    @HANCENENTERPRISE-yw4mr 4 месяца назад +1

    Iweyo man umalikonda dziko lako.

  • @veronicasimuka3882
    @veronicasimuka3882 4 месяца назад +1

    Its true siwabwino ine wandidwaritsa kwambiri

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 4 месяца назад +2

    Ndaleka kumwa ine

    • @mutafire
      @mutafire  4 месяца назад +1

      wise choice

  • @Sharongimo
    @Sharongimo 3 месяца назад +1

    Kuwaonongera business anzanu. Mai wina ku Nigeria is in Jail for bad comment on tomato puree

    • @mutafire
      @mutafire  3 месяца назад

      you know you are allowed to comment and speak on any issues as long as it is the truth, right? do not fear. Say it if you are sure of the facts.

  • @chemapa
    @chemapa 4 месяца назад +1

    ZIKUPHA ANTHU A KU AFRICA THESE DAYS SIZIMENEZI.

  • @NthambiLipenga-jw5gc
    @NthambiLipenga-jw5gc 4 месяца назад +1

    EEEEh Koma adha ndi mbora game yih

  • @AidahNazombe
    @AidahNazombe 3 месяца назад +1

    Tizingomwa thobwa basi chete

  • @Allieshaibu8612
    @Allieshaibu8612 4 месяца назад +1

    Wayakhula zonad aaaaa

  • @masozibanda7473
    @masozibanda7473 3 месяца назад +1

    Maka anthu opasa Ana enjoy mmaganiza bwa...

  • @LywellChilupsa
    @LywellChilupsa 4 месяца назад +1

    Mutichilenso check more

  • @bnamandwa44
    @bnamandwa44 3 месяца назад +1

    Powerful Boss

  • @emmanuelmwanyali750
    @emmanuelmwanyali750 4 месяца назад +1

    Try zima 100% fruit Juice zija

  • @tinamitunda8420
    @tinamitunda8420 4 месяца назад +1

    Tizimwa thobwa zokonza tokha

  • @MussahKajenere
    @MussahKajenere 4 месяца назад +1

    Iwe ndimbudzi sukulu yake iti yolemphera even to kuwerenga kuti timve bwino

    • @GiftPhir
      @GiftPhir 4 месяца назад

      Inu ndi ophunzira yet, you can't even do simple punctuations. Kukanika kulemba Chichewa. "yolemphera" nde kuti chani?

  • @BizweckFred
    @BizweckFred 4 месяца назад +1

    Ndiye chiputu chanyatu

  • @Alien_design2
    @Alien_design2 4 месяца назад +1

    Share more broz eye opener cheers

  • @newtonsindo5952
    @newtonsindo5952 4 месяца назад +1

    I am finished

  • @GriberthaKalulu
    @GriberthaKalulu 3 месяца назад +1

    Wasowa zoika pa net iwe

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 4 месяца назад +1

    What about energy drink?

  • @BonfaceMpokosa
    @BonfaceMpokosa 12 дней назад

    A Bagaya ndaleka kukukhupilirani

  • @pemphoashani4619
    @pemphoashani4619 4 месяца назад +1

    Great

  • @innongwenyah
    @innongwenyah 3 месяца назад +3

    No mkulu uyu despite kuti amakonda zotukwana, koma ndi mdala wa mnzeru. Zomwe akunenazo zitha kukhala zothandiza kwa winawake.
    The best way possible ndiyoti MBS itithandize kupanga regulate ma standards a ma products athu. Ineyo I love enjoy juice koopsya, coz ndimadana ndi zakumwa za gas like achina Coca-Cola ndi Fanta, koma I didn't care kuti what are the ingredients of this juice.
    Sinayambe ndafatsako kuwelenga, and mwina nkupanga understand ma ingredients wo coz ambiri ndi ma technical terms. But this video is an eye 👁‍🗨 opener ndithu, will consider other ways of supplementing my diet.
    Let's be positive guys, munthuyu sakupanga de-campagn enjoy juice, no, he's only exposing stuff yosakhala bwino.
    We'd really love to support ma products opangidwa kwathu konkuno, koma nanga tifa nazo tu tsono.
    As Malawians 🇲🇼 let's normalise kumapanga ma products abwino that are of international standard.
    Tisafe coz mwatimwetsa poison tisakufuna please.

    • @mutafire
      @mutafire  3 месяца назад

      A great summarize my message, we love local industry but people should know.

    • @innongwenyah
      @innongwenyah 3 месяца назад +1

      @@mutafire Exactly, anthu adziwe kuti akamwa enjoy juice akumwanso ma chemicals oipa.
      Ndeno ma guys opanga enjoy nanu, Try to improve ma products wo, otherwise eeeish mutipweteka. Lol 😂

  • @AidahNazombe
    @AidahNazombe 3 месяца назад +1

    Tamva koma vuto ma 100 percent juice wo are expensive

    • @mutafire
      @mutafire  3 месяца назад +1

      you can go with water or milk

  • @FAB_ONE_PICTURES
    @FAB_ONE_PICTURES 3 месяца назад

    Zambiri zimenez timadya zimakhara ndi ma preservatives amwene almost every processed food has these kind of chemicals

  • @viollachilemba
    @viollachilemba 4 месяца назад +1

    Not me watching while enjoying enjoy 😉 😅

  • @NovahiwaTchereniLihonga
    @NovahiwaTchereniLihonga 3 месяца назад +1

    What r ur commendation pa juice wabho km wotchipa

    • @mutafire
      @mutafire  3 месяца назад

      green tea is the best

  • @NorahBanda-he1dt
    @NorahBanda-he1dt 4 месяца назад +1

    Why did I come across this video abale aaaah pita kawasumira opanga enjoy wo if you have enough proof otherwise sindingaleke kumwa

  • @leviecashmere7555
    @leviecashmere7555 4 месяца назад +1

    Kmano iweyo umakwana km tiuzeniko juice wa bwino

    • @mutafire
      @mutafire  4 месяца назад

      opanga nokha

  • @PatriciaMajawa
    @PatriciaMajawa 3 месяца назад +1

    Zikhoza kukhala zoona coz madokotala anandiuzapo kt ana tiziwaikira madzi mmalo mwa ma juice and anthu ena anandiuzapo kt enjoy iz bad

  • @chekiamaabdul5083
    @chekiamaabdul5083 3 месяца назад

    Osamangodya achule akowo kumeneko bwanji. Chinkhope ngati iweyo.

  • @SherifaG.Mlelemba
    @SherifaG.Mlelemba 3 месяца назад

    Amaika mankhwala etii? Iiii! Zaphazo ndiye ndizambiri.... No where to run...

  • @HaroonMKWANDA-r4x
    @HaroonMKWANDA-r4x 3 месяца назад +1

    My favorite Juice Enjoy mawa ndimwa mwina I can notice something but if not ndekut ndizimwabe

    • @mutafire
      @mutafire  3 месяца назад

      Come back in 20 years.

    • @ElishaMfune
      @ElishaMfune 3 месяца назад

      The best juice to drink its water, take it or leave it but at end you regret for taking these deadly juices

    • @HaroonMKWANDA-r4x
      @HaroonMKWANDA-r4x 3 месяца назад

      ​@@ElishaMfunendakumva Eli

    • @christophermukaka7403
      @christophermukaka7403 3 месяца назад

      The best drink is water or kumangophika thobwa

  • @goldenselenje686
    @goldenselenje686 4 месяца назад +1

    Akusumiranitu che morotoni owo

  • @lindakondowole8021
    @lindakondowole8021 3 месяца назад

    Thank you for sharing this helpful information, zinazi timangotsutsa coz ndife amalawi mkukhala kwathu

  • @TamandaTikoma
    @TamandaTikoma 3 месяца назад

    Zikomo kwambili, nde tithandizeni ndi drink wanji otchipa wabwino oti titha kumapatsa anawa chifukwa dzachulukatu dzamwenyezi. Komanso makambawa tatiuzeni abwino.

  • @MarthaBango
    @MarthaBango 4 месяца назад +1

    Zamkakazo zikuti bwaji ?

    • @mutafire
      @mutafire  4 месяца назад

      mkaka ngoyipa

  • @giftstima2613
    @giftstima2613 4 месяца назад

    Komano translation ya Google simachitsata chichewa 😂😂😂😂😂

  • @mackwellingsphiri3646
    @mackwellingsphiri3646 3 месяца назад

    Thanks for the alert. Information is power; consumers need to understand and not just know what goes into their body and how it affects their health.

  • @KonzaniZinthu
    @KonzaniZinthu 4 месяца назад

    A Malawi musavutike ndi mantha. Chilichonse chopangidwa ku fakitale ndi choopsya komanso ngakhale nsima mukudyayo imayambitsa nkhansa chongofunika ndi kasinthasintha basi. Musadziphe ndi ma 100% omwe dzipatso dzake ndi dza GMO mudwalabe basi.

  • @GeorgeChipanda
    @GeorgeChipanda 3 месяца назад

    Ndi zoona mukunenazi koma anthu ndi osamva ndi chifukwa chake ambiri akupanga makani apa, zinthu zimenezi ndi zoipa zimapha komanso chifukwa chochuluka sugar munthu umakalamba mwansanga, ma juice onse opangidwa ku factory ndi oyipa ngakhale anene kuti 100% fruit juice, preservative free ndi zabodza, ngati mukufuna 100% juice pangani nokha, osakhulupirira zopangidwa ku factory za moyo wanu alibe nazo ntchito bola iwo akupanga ndalama

  • @evancemataka950
    @evancemataka950 4 месяца назад

    Malawi Bureau of standards .....a Useless parastatal chinyengo 2 much

  • @josephchidwala2697
    @josephchidwala2697 3 месяца назад

    Taphunzira, kwakhala tipeze alternative drinks otherwise anawa ativutatu

  • @fanuelh.ckhuluzah6852
    @fanuelh.ckhuluzah6852 3 месяца назад

    It's not juice , it's for those that can not afford real juice.

  • @Josenkuth
    @Josenkuth 4 месяца назад +12

    Mad man, dont u know almost everything we eat nawadays is harmful. Even masamba enieni akudimbawa are full of very toxic residual chemicals. What about these common processed meats, tinned fish are common too aren't they. Maybe that's far fetched, did u know even bottled water has recently been proved to contain harmful plastic carcinogen particles secreted by their contaners. Nde mukanene za Enjoy. Come on guys, have some sense. Kambaniso za Sobo Orange Squash

    • @Kamangaify
      @Kamangaify 4 месяца назад +1

      Koditu momwe akukamba za Enjoy mu, sizutanthauza kuti zina zonse zili bwino.

    • @romeomhone744
      @romeomhone744 3 месяца назад +1

      Bola mwamva zili ndiiwe kunyozela

    • @MatthewKanyenda
      @MatthewKanyenda 3 месяца назад

      Ichi ndi chidziwitso,zili ndiweyo kuzipha Koma langizo ili akuti avoid juice wa enjoy tu. Vuto kusamvetsetsa a Malawi shame on you.

    • @DinaJere
      @DinaJere 3 месяца назад

      😂pepani kwambiri anthu itse

    • @DinaJere
      @DinaJere 3 месяца назад

      😂pepani kwambiri anthu itse❤

  • @MrsNankhumwa
    @MrsNankhumwa 3 месяца назад +1

    Tathokoza mwatitsegula maso

    • @mutafire
      @mutafire  3 месяца назад

      You are welcome.

  • @GeorgeMalunga-qu1jc
    @GeorgeMalunga-qu1jc 3 месяца назад

    Amwene this juice is really bad ndinamwapo komano anandipanga zinthu moti sindimufnanso mmmh.

  • @peggymkandawire-mw9xj
    @peggymkandawire-mw9xj 3 месяца назад

    Nde tumizani ndalama kut tizigula ma juice abwino.... Nanga ife tingakwanise ma juice omwe mukumwa Inu?

  • @hanifah6293
    @hanifah6293 3 месяца назад

    I've never liked zakumwa izi, ngati ndimadziwa. Koma zakudya zambiri amapanga amwenyewa iwo samadya. I saw this mnyumba zambiri zachimwenye ndikuphunzitsa ana awo. Zimakamba zazitali zija, zima jigizi, soya pieces, etc. they prefer kudya zakumaiko akunja. Bola za universal industries, bola.

    • @violetpotani
      @violetpotani Месяц назад

      Komadi anthu awawa zinthu zawo samadya tingopwetekeka ndife yo.. Koma a MBS ntchito yawo mchani

  • @chemapa
    @chemapa 4 месяца назад

    of all the poisonous juices in malawi, the least I expected you cud condemn is enjoy.

  • @JohnMota-jd1gt
    @JohnMota-jd1gt 3 месяца назад

    Vuto limene tirinalo ku mudzikuno .ndi la.MB.S..kumeneko amalemba athu opanda chikondi ndi dziko lao kumene makaphu zira kuti satha kusiyanisa pa zimene munezo amangolowesa katangale omafa nkumafa bola adzigulisa basi nao oyanganira MBS kaya anaphunziradi kaya amangolembedwa kamba ka mukudziwa inu tiyenimuziona nokha

  • @NIKSYCHIMA
    @NIKSYCHIMA 3 месяца назад +1

    Enjoy ndiotchipa nanga

  • @twavysibale4751
    @twavysibale4751 4 месяца назад

    Much respect boss,do more videos like this,..

  • @PatrickJuma-v5n
    @PatrickJuma-v5n 3 месяца назад

    Thats true it's not juice preach on brother

  • @marygoza1205
    @marygoza1205 4 месяца назад

    The truth is that these processed foods are not nice at all. May God help us

  • @staprickskilled8589
    @staprickskilled8589 3 месяца назад

    Nde tikasiya kumwako sitizafa ? Iwetu ukukamba zausilu

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 4 месяца назад

    We don't have MALAWl bureau of standard ,

  • @MaryTembo-oj6dj
    @MaryTembo-oj6dj 4 месяца назад

    Iwe nd katakwe😂 umatichosa umbuli

  • @ElizabethPhiri-ky1wm
    @ElizabethPhiri-ky1wm 3 месяца назад

    Komatu izi ndizoona ngati simu simikiza pitililani kumwa koma maliyake alike ache ndi ma tenda

  • @JohnMota-jd1gt
    @JohnMota-jd1gt 3 месяца назад

    Kunena mukunena nanga boma liti chani?? Boma lopanda
    Chikondi ndi athu ake bola litolere mtsokho athu adzifa chikondi alibe a Boma mupite mukafu fuze osati mutseke makutu

  • @FadheelahMalovu
    @FadheelahMalovu 3 месяца назад

    Ukamaletsa anzako kumwa juice uzinenaso juice amenetiyenela kugula and from your opinion zambiri zomwe tikumwa kapena kudya masiku ano ndizoopsa kumene coz of modern world akupanga introduce zinthu zambirimbiri zinazi tikazitengela mwambiri ndetisiya kudya zambiritu coz since enjoy yekha amene alindi zolakwika zambiri

  • @JimmyMaster-l1x
    @JimmyMaster-l1x 4 месяца назад

    oOoOO brother ndakhu.mudwa koooopya

  • @MirriamRaja
    @MirriamRaja 4 месяца назад

    Nde juice wabwino ndi utiyo? Ti7zeñ please