Mandota ipase moto, ubwere ku mpamba trading center ku Nkhata Bay . Video iyi wayishuna bwino. Koma poitanila mpamene ukundisangalasa mzuzu University kkkkk tabwerezanso timve bwinobwino.
I will comment later, I'm in the hospital right now... My nephew swallowed 512Gb memory card and he is singing all songs in it. We are praying and hoping it doesn't reach the video folder! Ma liviidiyo onse aaah mandota eeeeh
This guy is a knee slapper.
Makes me laugh all day
Che Mandola,the best comedian,Luwiga cental Msuni
Koma anthu oonererawo anawonjeza, mudziwauza adzikhalako mbali ya uyo wojambulayo
Chemandota best comedian in the world ❤
KKK 🤣😮❤
That's being Malawian, in other countries u will never see people gathered to witness the shooting of a film.
Mandotaa my guy 😂😂 sashambaaa baziii .....ukagochedwetsa episode ina tigendaaa
Apapa Eni mudzi afika....king of comedian chemandota....😂😂😂😂😂😂 kachilungamo akubaya
Uku nde kilubwera munthu ukat ziii uzibwerako ndika unique like this one nice
Wakweza customer wachabe bwanawe🙌🔥😂
I love n like him though he is taking time panp kutipatsa ma comedy🎉
But he gave us a reason why it is so.
Unasowatu wabwela mwa moto mpaka kazitomale🤣🤣🤣
Chemandota mpaka ya boarding koma kulephelabe😅😅😅
Mandota umatha🔥🔥🔥 Komanso nawo anthu aku Mzuzu kusokoneza, kumangosokosa during shooting 🙄🙄
Bola pamenepo osati kusowa komwe mynasowaku iyayi timati kapena lusolija lantha 😂😂😂 kumakbapo luwinga sento suni koma😂😂😂😂
Big up guy , we have been waitng patiently for this nicer gist Mandota my homie❤
Koma nyamata wa Genta mene wathamangila kufuna change chake eeee😅😂😂😂😂😂
😂😂 Koma aripo Ena Ali ndi license koma kuyenfetsa sadziwa kk bolani chemadota😅
Wanthu wakwithu ku Mzuzu machita na kuonelera 😂😂
Mandota ipase moto, ubwere ku mpamba trading center ku Nkhata Bay .
Video iyi wayishuna bwino. Koma poitanila mpamene ukundisangalasa mzuzu University kkkkk tabwerezanso timve bwinobwino.
Malume ndagwada cha mumtima,,,chilichonse ndi funny umumu even galimoto yo 😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣kkkkkkk unandi 🔥🔥mandota umakwana usazafe uzangosowa
Wabwera mwaphamvu pakana kumukalupila kasitomala
Bwana mandota tiyeni tiyeni tiziopatsa moto🤣 miss u
When last did you post your video Mr Mendota? It's been months without finding your videos online
Kkkk pandisekesa ine ndipothawa mbola apo😅😅😅
My best comedian in MW
My favorite 💝 comedian much appreciated
kkkkkkk km mandota iweo ... jakisoni wachindoko wataaan🤣🤣🤣🤣
Nice
Kkkkk akut kutawa kae osati ku somba 😅😅😅😅
Aaah Zashamba bazi hahahaha koma uyu😂😂😂
Nde ati Mukhaleso telala 🤭🤣
Musamasowe kwambiri boss we lafusi you kwabasi
I will comment later, I'm in the hospital right now... My nephew swallowed 512Gb memory card and he is singing all songs in it. We are praying and hoping it doesn't reach the video folder!
Ma liviidiyo onse aaah mandota eeeeh
Chemandota ur the best comedia
Mumatanso kuyendeza🤣🤣🤣🤣 ugalimoto
Tinayamba kupanga zogendatu mwakhalitsa osatisangaratsa
Welcome back chemandota I lafusi yu we missed you
😂😂 koma mandota suzatheka 😅😂😂
A driver a mwano awaa😂😂😂
he is the best player
😂😂😂😂munthu wakulu mwachana2😂😂😂😂
Koma uyu sadzatheka 😂😂😂
Nice nice
mumakwana bra mandota km munasowa
Eee akulu inu mumandifoketsa😂😂
Adalaifala mwandiwasa kwabazi kuteteka kkkkkkkk
Chemandota ❤❤❤❤ iwey umakwana
mandota lavuziyu tu machi 🔥🔥🔥🔥
Best❤
Always it’s ur best comeia in Malawi
Chemandota😂😂
Mwabwera ngati coming mandota
Ntchana wathuwathu uyu 🔥🔥🔥🔥
Moto unandi 🔥🔥
Kkkk live ndizomwe zikumachitka
Timat wakulu afika pamalo Mandota
Kkkkkkkk l like you brother
Mandota ndi dolo 😂😂😂😂
Atumbuka mpaka akujambulatu
Kkkkk yemweyo Luwinga Centre Nsuni kkkkk
Nice kkk
Kankhan kmanso morogen asowatu
I was about to ask
Infomechoni😅😅😅😅
jakison wa chindoko
Ati musati imawawa ngat ife tinabayidwapo
😂😂😂 ma drive akewo
Mandota ulibe size timaku3la heavy
😂😂😂 big up to you Che mandota
Tilandile nawo phuma awa 🤣🤣
Umakwana tchoveli osamuoembedza passager
😅😅😅😅 anabwera kuzakhala
❤❤❤❤ Mandota usadzafe uzangosowa kkk
Uyu Amatha
Dzono mandota ukutawa sha?
Wathu wathu Chemandota in Mzuzu again
amadota wabwela zedi🔥🔥
Kuthawa mbola 😂😂😂
We are proud of you chemandota
🤣 Our best comedian in manyasa!
Big up fada
Kkkkkkk mumakwana boss wanga
Mandota uzihonga castomer
Dolo wanga 🔥🔥🔥🔥
Iwe ndiwani mandota usangowa bas
Km che mandota ndiokanika ngati jetu
Amubaya wachindoko😅😅😅😅
🔥
😂😂😂 km ndaseka
Best of the best
Tinakusowani chemandota❤
Kakhani asowa bwanji amandota
Nsuni yunifesite😂😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkkkk koma Mandota ainse
Keep on 🔥🔥🔥 ring
Munthu yu abaya jakisoni wachindoko
Driving school kkkkkkkkkkk mbambande
Chemandota adatha now akungoitanila malonda
Inuyo mukuona kutha koma ozindikila akuuzani kuti malondawa ndi ndalama nde sikuti munthu anatha koma akudya money basi through comedy 😂
😂🎉🎉❤❤❤Timakukondani
Kkkkkk jakisoni wachindoko kkkk che mandota ulemu wanu kkk
Wachindoko kuthamanga choncho? 😂😂😂
😂😂😂Lindota ❤