😂😂😂😂! Koma ai zikomo chakwelayu wabwelesa mavuto akuluka coz siutendele uwu apa tikuti ndi comedy koma zikuchitika live live ishiiii fans ikuvutika ndithu .
Che Mandota osamangojoina anzanu muzifunsa kaye. Anzanu adajoina kumaliza maliro a eni nkumati sister wanga wapita anthu nkuwaitanira pa mbali nkuwauza kuti amwalirawa ndi amuna. Then adangosintha chuni 😂😂
Kd mundu wamkulu shipewashi ndi shomweshija kapena china komabe iwe ndi my best acting wanga tili mbuyo mwako fada
Mandota you deserve this winning award ❤❤❤
That's right
We are always proud of you brother wachiyao wangalusa u are enough for us❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉
Love bro much 💞 let's talk
100% brother jamilu s chikakuda
Muzangosowa mesa 😂😅😂😂
😂😂😂🔥
Você tambem me fsx sorrir
😂😂😂😂! Koma ai zikomo chakwelayu wabwelesa mavuto akuluka coz siutendele uwu apa tikuti ndi comedy koma zikuchitika live live ishiiii fans ikuvutika ndithu .
Nice one mandota .mzuli mwasintha 😂😂😂
Wasokesa wina
Nangojoina 😂😂😂😂
Fantastic new hurt
Ndipeze shulushulu yoti ndidye😂😂😂😂
Mundu adangodyoyina uyuuu😂😂😂 eeeh mandotaa ayi ndithu
Votini zausande nayini handiledi kkkkkkkkkkkk
😂 mumayontha Mr tikumva kukoma ndima mphiziso Anu Muthu wakulu
Apa nde actor Wafa 😅
My favourite comedian
Komatu ndye umanyamulidwa mosavuta eti kkkkkkk
Mbasadatu anthu adzakupwetekera tchetela 😅😅😅😅😅😅😅
Kkkkk koma mandota😅😅😅😂😂😂😂😂
Mandota umaziyamba dala😂😂😂😂
My home boy Mandota l always respect you bro❤
mandota iweee dolo kwambiri😂😂😂
Blue 7 ilichomcho km ine ndikumaphunzira ziwiri zitatu 🔥🔥 ulemu wanu mundu wamkulu🙏
Nice Mendota 😂😂😂 very impressive 🎉❤❤
Mandota wapanga bwino akuuza bwanji za fees
Umakwana ❤❤❤
Kkķkkkķ mesiya mpulumusi uku chips chikutha🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂😂😂 Ati mkanjo ndimapangira ma li comedy
My home town Mzuzu❤
Mandota you are the best ❤😂
U are the best
Che Mandota ndi Akamuna.
Phunziro labwino kwambiri osamangojowera zirizonse mulibe nazo information yolondola
😂😂😂😂 zithu zidasitha makaniko kugula fanta😂😂
Brilliant acting 👏...chemandota ndiwe dolo basi❤
😂😂Mandota please
Muthu wakulu
Mzuli mwasitha liti😂
😂😂😂😂😂😂😂ndakomoka
kkkkkkkkkkkkk mesiya mpulumus yodyera imeneyo kkkkkk km mandota
Mwakungatu abwana kkkkk
Iiiiiiiii koma mandota eeeeee😂😂😂😂😂
Vendor oyenda olusa kale😂😂😂😂😂😂
😂😂😂 Kodi a she kankhani alikut??.....makwana 🔥🔥
😂😂😂😂😂 amandota kususuka ati kukamba zmpira ngati amazitsta kkkk umatja mandota
Japaji ndakuona pachiwaya ukudya chips nndichamandota umatha
Umakwana chemandota koma ndaseka 🔥😂
Hope this video mwajambilila pa Mzuzu
Unali mtaun osandiuza??
Muli bho man pitilizani kutisangalasa aMalawi❤❤
Mzuzu more🔥🔥
Mazda yo ndiyakut?
Takulandirani chemandota again 😂😂😂 njala imalamula kungo joina bazi zinatso ukhakuta😂😂😂
That u did it in mzuzu makes me happy 😂😂🎉
Che Mandota ndi mo 🔥
I'm a comedian and I wish to be followed by you ❤️
Zavuta basi 😂😂😂lijekete lija lapita
Mavuto sazakutherani kkk😊 u r # 1
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Mandoooooo🗣️🗣️🗣️🗣️🗣️🗣️🗣️
Mwamva iweyoo 😮😮koma muthu wankuluuu
🔥🔥
Koma mandota 😂😂😂😂😂😂😂😂
Ndotaz ndinkhani zina😂😂😂
Eating from plans❤ thinking
Kkkkkkkk ati pipiyasi
Kkkkkkkkk ee masi ya😂
Che Mandota osamangojoina anzanu muzifunsa kaye. Anzanu adajoina kumaliza maliro a eni nkumati sister wanga wapita anthu nkuwaitanira pa mbali nkuwauza kuti amwalirawa ndi amuna. Then adangosintha chuni 😂😂
Mbambande video 🔥 🔥❤❤
Kkkkk koma ndaseka❤❤❤❤
Inu mbiri dapanga
One day actor will win I guess 😅😅
Umaziwa kunyengerela mandota
🔥🔥🔥🔥✊
😂😂😂😂😂 ❤❤❤koma yaaa
Mandota takulandira ku Mzuzu 😂😂
Mumakwana inuyo
Mumakwanira ❤❤❤
Wachiyao brasa wangalusa pamalopo pasojolapo
😅😅😅😅😅 che Mandota umakwana
Kadi uripo ll❤ve u so much aise
😂😂😂😂😂 mapipiyasi
Kkkkk mandota ndi dolo koma kusokoneza kwambili
Kkkkkk mwanyanya
Fisi ya mwana 😅
Madota you is number one i like u
Nice
🎉❤
Massive 🔥👏
😂😂😂😂 𝗪𝗛𝗜𝗖𝗛 𝗖𝗢𝗨𝗡𝗧𝗥𝗬 𝗜𝗦 𝗧𝗛𝗜𝗦?
kalibhooo😂😂😂😂😂😂
mumakwana inuyo 🔥🔥🔥💥💥💥
❤❤mumakwaka mbazada
Amakaniki tanyozekatu kkkkkk
Mbambande video 🔥🔥🔥🔥
😂😂😂yooo
Koma mandota mmene amandipezelamo or akumachedwesa video koma chomchobe poti naye ndi munthu
Man muli bho
Mbambande
Kod ase anakuyambitsa za ma comedy ndan ?
Iwee umandiwaz zedi
Live from Ntchisi 🔥
kkkkkkkk uzatheretu mmanja mwa anthu iwe
Mapipiyasi ndasekatu kkkkkk
Mandota😂😂
😂😂koma Mandota umatha iweyo