Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
My best comedian in the entire southern Africa,as a matter of fact I lavuzi you She Mandota.More love and respect from Lusaka Zambia 🇿🇲
Che Mandota mukupitirizabe kutiphunzitsa bwino ndithu.Ndiye a Mologeni mwagwamo mu nkhani yosaidziwa.So educative and entertaining.Keep it up Che Mandota.
mandota umaganiza mwa thinking iweyo.... award ndiyako ❤❤❤
Kkkkk bwana mandota mwejo adolo mnole ajenu amtisire
Live from United Kingdom, I lavusi you
Zomwe ndnagulira bundle yanga zatheka
Where’s Ma mayiri Please..!! Fantastic woman.. I miss her..! 🎉
Muwafuna inu kkkkkk
Kkkkk video ya bwino
Me 2
Kkkk
Umakwana boss
😂😂😂 menyeni ameneyo ngwachibwana😅😅
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣Tsiku silimatha asanapepere chemandotaLiparty ikachitikira kumanda basi
😂EEEee km mandota andu asakupani inu nice vidio 🎉🎉🎉
Kkkkkkk koma inuyo man mutu umagwira 😂😂😂😂😂😂 kunamizira maliro
Nzelu zimenezo mandota... Dyalatu zapamalilo pako... Kkkkkkk
Ndasekaaa mokuwaaa you guys eeeee ndinu agaluu 😂😂
😂😂😂😂😂😂km fundo za chemandota pamaliro anga musadzandisonkhere eishii
Izi zikuchitika m, Malo momwe tikukhala akumba achuluka kunamizila malilo
😂😂😂 sopano mukufuna afe nd njara adyeretu bas iyaaa😂😂😂
Mandota anthu azakuphaa 😂😂😂😂😂 iwe zoona mudzi onse ikasonkhe ya libefidee yakooo Nawesoo Mologeni uzifufuzaa 😂😂😂😂
🎉🎉🎉🎉kod ulendo uno akupanga nomenee ku maso award
Eya andipanga voting ili mkati
😂😂 and I quote pamaliro panga musazandisonkhere
Koma CHE Mandota mwansokhetsa kale za BIRTHDAY 🎂 🥳 🎉 🎈 kikikiikiki plus Hahaha 😆 😂 💖 💕 😄 nice one .
Congratulations 🎉🎉🎉🎉 chemandota
❤That's great one
Pa maliro ake musazamusongele 😂😂😂😂
Chemandota 😂😂, inu kagoneni kumanda ine ndikagona kwa maMaili. Ndawasowa maMaili
Very good morogen
Morogeni ndinkhani Zina nicy one homeboy❤
Bring back mamaili plz but all in all mandoto nsanga umandinfeza kukoma
😊😊😊 Mwaonaaaaa
Koma ache mologeni as a matter of fact 😂😂😂😂
Keep up good work
Mandota😂😂😂 iwe ndi galu basi😂😂😂
Nkhaniyo ndiyoona chemadota asadzakusokheleni mwadyera2❤
B🎉🎉🎉 boss mumaziyamba dala 😅😅mukakumana ndi mizukwa kumanda Akita wafa congratulations
😂😂😂 love you guys number one
Kkkkkkkkkkl muthu akakhare nd mizukwa kwa masiku atatu aaa😅😅😅😅
😂😂😂😂😂😂😂pakufunika mateyera awochedwe basi
😂😂😂😂😂 ati pamalilo panga musazasonkhetse
Kkkk umanjoyatu ndikunyamulidwa mandota
Umakwana munthu wakulu😂
Good job braza
Kkkkkkk aise mandota umatha kwabasi
Nsapato ya Morogeni..... Made In simongoliya😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 chee ❤
Morogeni kuizemba kwake😂😂😂
Vuto ndi anthuna😅
Kkkk iwe Mandota sumamva ndithu, zoona kubela mudzi onset, koma nyamataaaaaa😂😂😂
kudya za mmudzi basi iyah😄😄
Mandota wabaya bwino kwabasi kkkkkkkkkkkk
Kkkkkkk koma chemandota mupole 💥💥🔥🔥🔥🔥🔥
Iweyo aise umakwana hvy Mot ngat sukhalaso best comedian of the year Ndie kut alowetsapo bosh😆😆😆Keep up bulasa dyamelo shikakuda💪💪💪💪💪
Nyumbayo ndi pepa😂😂
Kkkk iwe uzafela mmanja mwa anthu
Koma mandota suzatheka basi😂😂😂
I love you che Mandota ma video anu amanditseketsa 😂😂
Koma madolo akakumana pamachemadi😂😂😂😂
Kkkkkkkk akulu inuyo nde ndinu osokoneza kwambiritu kkkkkkkk
😂😂😂 Koma mandota mumakwana
Kkkkk malingana mkugwa Kwa kwacha
Osamasonkha pa maliro pokha pa birthday kumasonkhanso,,mandota umakwana...🤣🤣🤣🤣
Wachiyawo wangalusa baba kkkkk
Libefide lafuta kuno🤣🤣🤣
Iweyo ndi katundu waboma umatha mandota
😂😂😂 kusonkha ya birthday aaaaaaa asamuke basi
Mumakwana blasa man🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mama iri guys amakometsa guyz alikut kod tiuzeni guys
Aaah kma Mandota ndiwe Tambwali🙌💔😂
Keep it up Che Mandota 🎉
Big up🤝
Che mandota kusonkha za berefide 😂😂😂
Nice one guys
nice one 🎉🎉🎉❤❤❤
Kkkkkk kma mandota umatha iwe
My favorite umakwana ❤❤❤
Kkkk iweyo ndidolo aise
Nice one❤😂😂
Iweyo simuzatheka umakwan
Imenei ndi deal 😂😂 waphulira Mandota za Birthday,
Che mandoto sazatheka ❤
😂😂😂akita wava che Mandota
Call 😂😂😂 the police kuno 😂😂😂😂😅😅😅😅😅😅
Kod 😂😂😂😂 ndimadabwa tu
Munthu musiyeni wadyelatu zake
😂😂😂😂koma mandota ndi one
Km Mbasada aise kkkkkk
Kkkkk mandota sazatheka
Mwachita mwayi poti panabee kangani
Mandota anthu azakupweteka ndithu
My guy mandota iwe unabwera😂😂😂ubwino wake wasunga zalibefidezo sanakulande... After 3 days ukapanga pwando😂😂😂
Big up Blaza
Number one
Ati tikadzamwalira musazandisonkhere
😂😂😂😂 koma Doxy ukagona kumanda lero ukhaula ribarthday ukapanga ndi mizimu 😂😂😂
Kkkkkkkk i like anthu enawo nga sirious
Akakumangilile kumanda zoona
Nice🎉 work🎉🎉🎉
Nice one
Nice 🔥
Mr kod lelo simutulusa ife tikudikilatu
Ikubwela
Umakwana iweyo Dota
😂😂😂😂😂 koma ndaseka
My part at the end mukufuna kundipaa
My best comedian in the entire southern Africa,as a matter of fact I lavuzi you She Mandota.
More love and respect from Lusaka Zambia 🇿🇲
Che Mandota mukupitirizabe kutiphunzitsa bwino ndithu.
Ndiye a Mologeni mwagwamo mu nkhani yosaidziwa.
So educative and entertaining.
Keep it up Che Mandota.
mandota umaganiza mwa thinking iweyo.... award ndiyako ❤❤❤
Kkkkk bwana mandota mwejo adolo mnole ajenu amtisire
Live from United Kingdom, I lavusi you
Zomwe ndnagulira bundle yanga zatheka
Where’s Ma mayiri Please..!! Fantastic woman.. I miss her..! 🎉
Muwafuna inu kkkkkk
Kkkkk video ya bwino
Me 2
Kkkk
Umakwana boss
😂😂😂 menyeni ameneyo ngwachibwana😅😅
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣Tsiku silimatha asanapepere chemandota
Liparty ikachitikira kumanda basi
😂EEEee km mandota andu asakupani inu
nice vidio 🎉🎉🎉
Kkkkkkk koma inuyo man mutu umagwira 😂😂😂😂😂😂 kunamizira maliro
Nzelu zimenezo mandota... Dyalatu zapamalilo pako... Kkkkkkk
Ndasekaaa mokuwaaa you guys eeeee ndinu agaluu 😂😂
😂😂😂😂😂😂km fundo za chemandota pamaliro anga musadzandisonkhere eishii
Izi zikuchitika m, Malo momwe tikukhala akumba achuluka kunamizila malilo
😂😂😂 sopano mukufuna afe nd njara adyeretu bas iyaaa😂😂😂
Mandota anthu azakuphaa 😂😂😂😂😂 iwe zoona mudzi onse ikasonkhe ya libefidee yakooo
Nawesoo Mologeni uzifufuzaa 😂😂😂😂
🎉🎉🎉🎉kod ulendo uno akupanga nomenee ku maso award
Eya andipanga voting ili mkati
😂😂 and I quote pamaliro panga musazandisonkhere
Koma CHE Mandota mwansokhetsa kale za BIRTHDAY 🎂 🥳 🎉 🎈 kikikiikiki plus Hahaha 😆 😂 💖 💕 😄 nice one .
Congratulations 🎉🎉🎉🎉 chemandota
❤That's great one
Pa maliro ake musazamusongele 😂😂😂😂
Chemandota 😂😂, inu kagoneni kumanda ine ndikagona kwa maMaili. Ndawasowa maMaili
Very good morogen
Morogeni ndinkhani Zina nicy one homeboy❤
Bring back mamaili plz but all in all mandoto nsanga umandinfeza kukoma
😊😊😊 Mwaonaaaaa
Koma ache mologeni as a matter of fact 😂😂😂😂
Keep up good work
Mandota😂😂😂 iwe ndi galu basi😂😂😂
Nkhaniyo ndiyoona chemadota asadzakusokheleni mwadyera2❤
B🎉🎉🎉 boss mumaziyamba dala 😅😅mukakumana ndi mizukwa kumanda Akita wafa congratulations
😂😂😂 love you guys number one
Kkkkkkkkkkl muthu akakhare nd mizukwa kwa masiku atatu aaa😅😅😅😅
😂😂😂😂😂😂😂pakufunika mateyera awochedwe basi
😂😂😂😂😂 ati pamalilo panga musazasonkhetse
Kkkk umanjoyatu ndikunyamulidwa mandota
Umakwana munthu wakulu😂
Good job braza
Kkkkkkk aise mandota umatha kwabasi
Nsapato ya Morogeni..... Made In simongoliya😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 chee ❤
Morogeni kuizemba kwake😂😂😂
Vuto ndi anthuna😅
Kkkk iwe Mandota sumamva ndithu, zoona kubela mudzi onset, koma nyamataaaaaa😂😂😂
kudya za mmudzi basi iyah😄😄
Mandota wabaya bwino kwabasi kkkkkkkkkkkk
Kkkkkkk koma chemandota mupole 💥💥🔥🔥🔥🔥🔥
Iweyo aise umakwana hvy Mot ngat sukhalaso best comedian of the year Ndie kut alowetsapo bosh😆😆😆
Keep up bulasa dyamelo shikakuda💪💪💪💪💪