Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
😂😂😂😂😂😂 iweyo no matter what koma ndiwe king of comedian...umatha chemandota...brilliant acting 👏 👌 May the Allah continue blessings you 🙏
😂😂😂😂 Iwe mufuna chani?
🎉🎉🎉 awesome ndipo inuyo ndikatundu waboma Masha Allah
Mandota try to mind your business sometimes 😂😂😂😂😂 mutu wamzanu walakwa chani😂😂😂😂
Mumativesa kukoma mandota GOD bless you
😂😂😂😂 ndipo chemandota ngat Allah analemba inu ndi forever 😂😂😂😂
Mwaona ❤I lavusi you jamilu chikakuda
Koma ase mandota unayamba waiwinapo iwe 😂 😂 😂 😂
😂😂😂😂😂 mandota matama oseyaja ulibe ndalama wadya dzokudya dzaulele Kkkk nice mandota
😂😂😂😂😂 Akita uja kunoo big up
Kkķkkkķ chemandota kodi inu munenepa liti kulimbana ndikugemula anzanu🤣🤣🤣🤣🤣🤣 love to you mooooo
🤣🤣🤣🤣 koma mandota adha, crazy genius
Mandota wapeza formula yodyera patauni 🤣🤣🤣🙌
Ndox uzathela m,manjatu iwe 😂🤣 uzikhalako chete
Koma she Nandita uli ndi Experience yokuba etii😂😂😂😂😂
Kuyenda ngati pachibaletu
Munakasuta eti 😂Nkhope ngat mdimsMutu wa upstairs 😂😂😂😂
😂😂😂😂chipumi kuti chilode pa status ma GB angati💀😂that was sick
😂😂😂😂😂😂 koma ndikanagona osatseka..mandota chonde osamanyoza anthu ngt uli ndi kathu 😂😂😂😂😂
I love you mandota una talent Malawi yote ❤❤❤❤
😂😂😂Hahhaa mukamagemula musamanene zenizeni
Mwejo akatundu Mwini film
Proud to yu chemandota
Umakwana iweyo ✌️ ghetto
Kkkkk mandota tsuzatekha koma iwe umakwana ndizute fodya kunjaku omwewo ozabwera 😂😂😂 I like you for you comedy ❤❤❤
Kkkkkk koma iwey ndota unabwera nangq mandota Mesa ndambili nde tizingot ndota monga lilipo limoz
Kkkkk Ali kusazivera chisoni kkkk kumenyedwa umakusaka Mandota kkkk
Ndikamaonera ma comedy ako ndimangoseka all along...😂 Gud tchuduleni...🙌
Talent man ❤mumakwana😂😂😂
😅😅😅😅😅😅😅 king of comedian
🤣🤣🤣🤣🤣🤣Lero sanakunyamulenitu che mandota I lafusi yuo
Mandota uzafera mmanja mwa anthu😂😂😂
Nice che mandota
Kkkkk mandota ndi dolo km suumachedwa kutha
Ndatha mwesi umodzi osaonela ma livideo ako ase mnakusowa apa nde ndiyambeso😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂Km iwe😂😂😂 eee
Ati shokani mbafa inu😂😂umakhwana mandota
Ahaaa nkhope ngat sima
U come to stay bwanawe kkkkkk mpaka chipumi mkasi wansanu
Love you chemandota
amvere ....akakuonongelani mtundu
Munthu wamkulu tsopano❤
Mandota unabwera kudzakhala iweyo kkkkkkkkkk
Kkkkkkk apa akita wava atakhuta😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂...koma mandota ndiwe dololo osati dolo
Happy to be among the first hundred views to this week's video ❤
Iweyo ndi king pa ma comedy
Eish ndiribe mawu ine 😂😂
Proud to see this every Wednesday
😂😂😂😂😂😂 Eeeeeeeshi mundu wamkulu mpaka ngope ngat mdima
Frankly speaking umatha mandota
Umatha iweyo ❤
🤣🤣🤣😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂akut chipumi chimenechi kut chilode ndi ma GB angati 😃😃😃😃😃😃😃che mandota ndipangileni kanga ineeeee 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Akulu awa amwene 🙌😂
Ati nkhope ngati mdima,mutu wa upstairs kkkkkkkkkk
Your are number Mr comedian I loves you 🎉🎉🎉🎉
Mmakwana chemandota
Mandota iweyo umatha 🤣🤣🤣
Mandota udzathera mmanja mwa anthu❤❤❤❤
😂 km mandota
😂😂😂😂😂😂 Mandota umakwana
😂😂😂 mbazada angosuta panjapa kkk
Che Mandota ,😅😅 Mpeni ndiwachan
Umatha mandota 😂😂😂
Moto unandi 🔥🔥
😂😂😂inuyo ndi more
Ma Gb angati ? Uku ndye kuiputa ndeu😂😂😂😂
Kkkkkkkk koma chemandota 😅😅😅😅😅
Che mandota umatha kwambiri 😂😂😂}
😁😁😁 mpaka chipumi chonyasa
Koma mandota umaitha
"Mwaona"😂😂
😂😂😂 kusasifela chizoni
Mandota anabadwa kudzatisangalatsa ndithu 😅😅😅 bola anawo akudya nakhuta 😂
Kkkkkkkkkk akaononga mtundu
😂😂😂 I m behind Mr chemandota
Kkkkk mandota
Mandota adabwera kudzakhala 🔥🔥
🎉🎉mumatha
Apa ndye wafad Akita🤣🤣🤣
Koma kuchenjera uku mandota 😆😆😆😁😁
Dolo🎉
😂😂😂more 🔥 Mandota
Ndingosuta panja😂😂😂
😅😅😅😅😅😅😅😅 chemandota umakwana
Kkkkkk ndizaBobe week ya Mawa kkkkkk
Kkkkkkk
😂😂😂😂 km ndaseka 🙌
Iwe children😂😂😂😂
Umakwana mandoto ndiazako
Mandota😂😂😂
❤❤❤❤❤
Koma muzawinako actor
Che mandota sumachimina😂😂😂😂😂
Ndoxy anafaya🤣🤣
Ndiwe dolo chemandota, umaitha🤣🤣🤣
Akut mbava inu nkuzathawanso
😂😂😂😂😂 Mutu wa up steyers omwewo 😢😢😢😢
😂😂😂😂 iweo ndi one
Che mandota fans let's gather here ❤❤
Follow you big
Nkangala Mandota. Umakwanila
Interesting 😂

Munakasuta eti 😂
Nkhope ngat mdims
Mutu wa upstairs 😂😂😂😂
😂😂😂😂chipumi kuti chilode pa status ma GB angati💀😂that was sick
😂😂😂😂😂😂 koma ndikanagona osatseka..mandota chonde osamanyoza anthu ngt uli ndi kathu 😂😂😂😂😂
I love you mandota una talent Malawi yote ❤❤❤❤
😂😂😂Hahhaa mukamagemula musamanene zenizeni
Mwejo akatundu
Mwini film