MOBILE MONEY - Episode 152

Поделиться
HTML-код

Комментарии • 219

  • @clesheinvestments
    @clesheinvestments Год назад

    Che Mandota Imfa yakukwanirani basi.
    Mwaonjeza kuba kwambiri.
    More fire Che Mandota

  • @JumaRajab-fc2tc
    @JumaRajab-fc2tc Год назад +1

    ndimayamba kuseka ndisanaonere ma dota umakwana

  • @andrewjunior2932
    @andrewjunior2932 Год назад +3

    Kkkkkk menewayambila kunenakuti mwawona mwawona 😂😂😂😂😂😂
    Iwe ndikatundu big up❤

  • @Wachie07
    @Wachie07 Год назад

    Inu ndi Dolo 🔥,,koma ada awo kumapeto uko mkanamenya flashback kuti akukumbukirani ku hardware store kuja 🙏

  • @FelixWhite-i6x
    @FelixWhite-i6x Год назад

    Munthu ameneyo kungomugwira, eeehh!!! Kumuphwasula chi mutu chaocho.

  • @GraceMunthali-o7t
    @GraceMunthali-o7t 11 месяцев назад

    Ameneyo ndimbava,ndiye mbava timalanga

  • @NanchoKatchali-u6t
    @NanchoKatchali-u6t Год назад

    Iyíii mwaphq bg mn😂😂❤

  • @mackgozambia
    @mackgozambia Год назад

    Watching from Katete Zambia

  • @Maria-nv8ev
    @Maria-nv8ev Год назад

    Kkk taphunzira mobile money ya zibwana

  • @magretphili-un9up
    @magretphili-un9up Год назад

    Mr mandota musiye utanbwali akuphan anthu 😂😂😂😂

  • @HarryMbauleni
    @HarryMbauleni 8 дней назад +1

    🤣🤣🤣🤣🤣 Kma ndwe dolo aseh kkkkk

  • @YamikaniJolobala-xr7kz
    @YamikaniJolobala-xr7kz Год назад +3

    Akulu inoyo tsikulina ofunika azakupondeni zeni zeni kkkkkkkk

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 Год назад

    Chiphunzitso chachikulu, gud up chemandota

  • @YusufuAli-qz5bv
    @YusufuAli-qz5bv Год назад

    Wakhuba umafunikha khumenya bhasi monga che mandota umaitha mandota
    Whachiyawo wangalusa

  • @Ven-37
    @Ven-37 Год назад

    Koma ndikamuteme .... Mmene alili maluzi panyasapa

  • @linlymkwaila9334
    @linlymkwaila9334 Год назад

    Eishh basi law manja mwanga basi

  • @DalitsoSimango
    @DalitsoSimango Год назад

    Iweyo ndota bas ndiwe number one pa malawi PANO I lavizi you❤❤

  • @hossainsanudi3578
    @hossainsanudi3578 Год назад

    Lero chakagone nditu mchitolokosi hahaha

  • @Shemamwale
    @Shemamwale Год назад

    Ine ndimadabwatuu kuti uyu alipiraaa😂😂😂😂

  • @HajimaKhalid1714
    @HajimaKhalid1714 Год назад

    Mamairi anenepatu nzokuba proud of u mandota

  • @SamuelMainjeni-uh1pf
    @SamuelMainjeni-uh1pf Год назад

    Very educative

  • @juliusomar2005
    @juliusomar2005 Год назад

    ❤❤❤❤❤❤ mashallah 😅😅😅😅

  • @RajabNsini
    @RajabNsini 9 месяцев назад

    Kkkkkkk kma mandota ndiwan 🙏🙏🙏 apa timat akita wafa

  • @Esnart-or1dq
    @Esnart-or1dq Год назад

    Nice one but u could repeat that one with late atoht manje

  • @davidwakhokamoto1124
    @davidwakhokamoto1124 Год назад +1

    Kkkkkk ine sindimaziwa kut ndalama ikhoza kubwezedwa ku phone yamwini thaw yomweyo

  • @RachidEugenio
    @RachidEugenio Год назад

    Apo ndingopeza Ukabaza apopo😂😂😂😂

  • @franktembo2007
    @franktembo2007 Год назад

    Munthu woba ndalama ngati che mandota ukhara ine ndishi nsima azamupasira pa waya phone nitenga komanso ayenda apanda silipa.😜😜😭😭

  • @mathewsphiri6387
    @mathewsphiri6387 Год назад

    Akulu akulu,akita wafaaaa 😄
    I lavuzi you, More Love and respect from Lusaka Zambia 🇿🇲

  • @evelynsadwala4697
    @evelynsadwala4697 Год назад

    kumupeza ndi teyala basi chibwana ai kkkkkk

  • @MussahImulan-yp4fs
    @MussahImulan-yp4fs Год назад

    Wachiyo wangalusa ulemu wao adalawo mandota

  • @shanlaljith5389
    @shanlaljith5389 Год назад

    Kkķkkkķ hiiìiiiì inu somuzathrkatu🤣🤣🤣🤣🤣

  • @TrustMataura-ii5wt
    @TrustMataura-ii5wt Год назад

    Ndye kuzimvatu kkkk at mundpeza pat

  • @willardrajab5382
    @willardrajab5382 Год назад

    Kkkkk mwayamba kuba che mandota 🤣🤣🤣🔥❤️❤️

  • @faluqmayere
    @faluqmayere Год назад

    May Allah azikupatsa moyo wautali.........inshahllah 🤗
    Hahahah che mandota utangaso award this year

  • @gabrielmaluwa1038
    @gabrielmaluwa1038 Год назад

    😂😂iweyo ndi dolo..... ngondo kubed

  • @StatesManP-zq4ic
    @StatesManP-zq4ic Год назад

    Ine kungoyerekeza kumugwira munthu oteleyu ndingamudule malibatire ndithuuu maDurata😂😂😂

  • @williamsmwale8481
    @williamsmwale8481 Год назад

    Eee Koma iweyo mandota umaganiza mwa thinking 😂😂😂 mwali Za Kuno Ife tinasiya zokutumizila mu Fon muli phunziro kwambiri mu episode imeneyi ndaikonda 🎉🎉🎉

  • @LloydMkandawile-c9p
    @LloydMkandawile-c9p Год назад

    Kumuwocha basi ndiwakuba😅😅

  • @WitnessChigodo
    @WitnessChigodo Год назад

    Mwampha.... Video ya nzelu

  • @LloydPitros-iu7wp
    @LloydPitros-iu7wp Год назад

    You are the best

  • @YusufMaganga-rn3ju
    @YusufMaganga-rn3ju Год назад

    Chemadota osazalowa muchop mwanga mwalowa umbafa😂😂 anyway umakwana iweyo

  • @jefreykazembe8691
    @jefreykazembe8691 Год назад

    😂😂😂😂😂😂 Mwandikumbutsa kulijubeki
    King of comedian.. U teach us a lot of things.. Almighty allah continue blessings you chemandota🙏🙏🙏🤸‍♂️🤸‍♂️🤸‍♂️🤸‍♂️

  • @MagretKatuli-it5ss
    @MagretKatuli-it5ss День назад

    Koma chemandota simasewera , umatha iweyo. Usadzafe

  • @JustinHKhoviwa
    @JustinHKhoviwa Год назад

    Anthu amukang'antha oteroyo osamuseweretsa ndi mbava imeneyo

  • @bornfacemaduka8658
    @bornfacemaduka8658 Год назад

    kunveka tyre mkumuyasa ndalama yavuta pa Malawi 😅😅😅😅

  • @MercyFilipo-kh4gt
    @MercyFilipo-kh4gt Год назад

    Koma ndingamuphetu😅

  • @idrissamalinga3175
    @idrissamalinga3175 Год назад

    adzakupweteka m'bale wanga

  • @EstherLongwe-k8d
    @EstherLongwe-k8d Год назад

    Ndikhoza kumumangitsa bas

  • @stenarabyson6895
    @stenarabyson6895 Год назад

    Che mandota bola amapuma Bax eeeh😅😅😅😅😅

  • @ruzuwanmoyenda23
    @ruzuwanmoyenda23 Год назад +2

    U deserve an award bro😂😂😂😂

  • @jamirahmuhyuddin7358
    @jamirahmuhyuddin7358 Год назад

    Ine ndimadziphere ndekha munthu ameneko😂

  • @simonandrewkambwera4475
    @simonandrewkambwera4475 Год назад +1

    😂😂😂You're deserve award

  • @frankkachigumba187
    @frankkachigumba187 Год назад

    Taimaniii kayeyo sigwira muthu iwe mandota 😮😮😮😮😮😮 situation is very critical apap

  • @IbrahimHassanAbdulrashid-zi1yu

    Kumuneneza ku police yomwe tili nayo pafupi.

  • @jonathanmaseko6057
    @jonathanmaseko6057 Год назад

    Teyala basi ndalama zikuvuta izi😂😂😂😂😂

  • @praisemandota2711
    @praisemandota2711 Год назад

    Koma zovala sija osafala bwa😂😂

  • @STEVIEKANTAZI
    @STEVIEKANTAZI Год назад +1

    Iyi akulu enake anandimenyako 😢😂😂

  • @VictoriaWilliam-gn1xw
    @VictoriaWilliam-gn1xw Год назад

    Kkkkkkkk ameneyo ndiye mandota mapeto azonse amanyamulidwa basi 🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @SprianoAndrew-kf7gd
    @SprianoAndrew-kf7gd Год назад

    Ameneyo akufunika akwidzingidwe ase

  • @TomHardy-b4x
    @TomHardy-b4x Год назад

    Chemandota umatha umasekesa munthu or atakwiya

  • @anniewhite3497
    @anniewhite3497 Год назад

    Suzatheka mandota kumeneko ndikuba😂😂

  • @YounusuGerald
    @YounusuGerald Год назад

    Koma zosayenda kwambiri km anthu ake

  • @MoffatMzumala-r3f
    @MoffatMzumala-r3f Год назад

    Kumumangitsa bs ndiwakuba

  • @saukanistambulimaupo
    @saukanistambulimaupo Год назад

    Mandota nd one

  • @BledderSting
    @BledderSting Год назад

    kkkk koma iweo ndidolo

  • @masanjalaor247
    @masanjalaor247 Год назад

    U so talented brother mwaona mwaona mwaona

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 10 месяцев назад

    😂😂😂 asaaaaa Che Mandota ulindiluso bro

  • @KambalameKambalamesumayy-qo9qz

    mawuchuga awiliiiiiii 😆 😂 😆 😂 😆 😂 hahahaaaa

  • @StevenMussah-nj6qx
    @StevenMussah-nj6qx Год назад

    Fire mandota

  • @Thyolomalawi
    @Thyolomalawi Год назад

    Apa ndiye wafa bas 😂😂😂

  • @nenanigamela5572
    @nenanigamela5572 Год назад

    Yandiphunzitsa kwambiri

  • @FrancisMatolino
    @FrancisMatolino 11 месяцев назад

    Ndikhalidwe lonyasa kumapanga reverse ndalama .utamugwira ndye kut bas waku police kukamumangisa

  • @EmmanuelMazani
    @EmmanuelMazani Год назад

    Apa ndie award inja akupatsiletu

  • @lastlevel1999
    @lastlevel1999 Год назад

    Mpaka kuyiwala drink eeeeh ine mistake imeneyo sindingapange

  • @samsonvyakusi
    @samsonvyakusi 11 месяцев назад

    Nice

  • @victorbwanali9898
    @victorbwanali9898 11 месяцев назад

    Great concepts.
    Just try to make the video clips as short as possible. Good work

  • @moosathomas6440
    @moosathomas6440 Год назад

    Zandichitikirapo ine kuno ku RSA last week munthu kutumiza ndalama pa e wallet ndikubwezaso eshiii anthu akuba masiku ano guys wake up

  • @NyeroYako
    @NyeroYako 11 месяцев назад

    Ndimudula mutua

  • @ivyfrankie-jf2eq
    @ivyfrankie-jf2eq Год назад

    Mandota unabwera❤ titha kumutibulatu😂😂😂

  • @Cooliodaxymw
    @Cooliodaxymw Год назад

    Umatha Mandota

  • @mhandrew1872
    @mhandrew1872 Год назад

    Iwe utengaso award bas odiii ndkavoteso

  • @bornfacealuchamgwera-qx7ot
    @bornfacealuchamgwera-qx7ot Год назад

    Kulijubeki😂😂😂😂

  • @mailosyasin3110
    @mailosyasin3110 Год назад

    Apa taphunzira zambiri more fire mandota

  • @AnafieIntuka
    @AnafieIntuka Год назад

    Timamukonda mandota ckf nthawi zose sizimamuthera bwino

  • @MussaChiwaya-c7r
    @MussaChiwaya-c7r Год назад

    Kkkk kod kuli kubalalika bulasa

  • @cannanmtika9305
    @cannanmtika9305 Год назад

    Mwabesa cocacola kws chemando

  • @michaelkhunga3676
    @michaelkhunga3676 Год назад

    ndi Inno build ubale unatha ?

  • @ImraanJafali-dk7rg
    @ImraanJafali-dk7rg Год назад

    Kkkkk petwere bro

  • @Martha1436
    @Martha1436 Год назад

    Mandota ufela m‘manja mwa a nthu

  • @DJHOAXMAN-kk8rt
    @DJHOAXMAN-kk8rt Год назад

    Timung'amba

  • @EliasSailesi-o8c
    @EliasSailesi-o8c Год назад

    Ulemu wanu boss

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Год назад

    Nyc

  • @muhammadlysan7643
    @muhammadlysan7643 Год назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂 bwanawe akhoza ku kupanga kazato

  • @Witman265
    @Witman265 Год назад

    Mudzathera mpanja😂

  • @mphatsoramsy6954
    @mphatsoramsy6954 11 месяцев назад

    Big up ❤️💪 bro ...

  • @realsu7816
    @realsu7816 Год назад

    Mwaona Mwaona Mwaona 😅😅

  • @ezekielbanda2867
    @ezekielbanda2867 Год назад

    Ai aaah osadandaula

  • @vitumbikomphepo5237
    @vitumbikomphepo5237 Год назад

    ❤😂😂 kumuchekacheka kkk

  • @XavierPatissoniWiressi
    @XavierPatissoniWiressi Год назад

    I like it more than normal

  • @MoustapherMakupe
    @MoustapherMakupe Год назад

    Umakwana chemandota 😮